KODI YA NORMAN CHISALE MWAIMVA? NAYE ZAMUVUTA NDIPO A POLICE AKUMUSAKA KOMA IYE WAYANKHULA IZI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 22 янв 2025

Комментарии • 144

  • @shampoomvula2896
    @shampoomvula2896 15 дней назад +18

    Mupha anthu angati and mumanga anthu angati poor governor

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya 15 дней назад +8

    Chikuvuta nkungovomereza basi kuti zawakanika anthu akupha awa, no more MCP

  • @WhyteSmart
    @WhyteSmart 15 дней назад +8

    Kod chimwendo zomwe amayankhura zija bwanji samangidwa????

  • @josephalfred5138
    @josephalfred5138 15 дней назад +5

    Munthu akamafa amayamba kugontha mmakutu ndipo sangamve kanthu MCP ingothelatu pa 16 September pa

  • @MineMoyo
    @MineMoyo 15 дней назад +5

    😂😂😂😂 koma MCP ndale zakuvutani mukutipasa manyazi kumaiko akunja kwa dzikolino tasinthani please....kumangana si deal

  • @josephalfred5138
    @josephalfred5138 15 дней назад +11

    Pano Kuno Ku south African tafika pomakana Kuti siine mmalawi chifukwa chazomwe akuchita chikangawayo galu was mtsogoleli mbuzi yeniyeni chakwela

    • @FrancoMwamlima
      @FrancoMwamlima 15 дней назад

      😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊

    • @Amiduj
      @Amiduj 15 дней назад

      Soona serious

    • @WysonChilonga
      @WysonChilonga 15 дней назад

      @@josephalfred5138 mwangoyenera

  • @OdalaBanda-i9c
    @OdalaBanda-i9c 15 дней назад +4

    Kod a mcp imeneo ndi solution kt muzingomanga a dpp mmalo mokoza mavuto omwe a Malawi akukumana naowa ngat simukuziwa kut mukwaika pa map?

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 15 дней назад +6

    MCP yayamba civil war in peoples minds be careful

  • @NOVABOUY
    @NOVABOUY 15 дней назад +2

    Amene akuganiza zozavotera MCP ambuye muwapheretu asafike mu September ayi Chifukwa mcp ndyakhupha . Mapwara awo agalu amenewa azingomanga azawo panyero pawo plus chakwerayo 😢😢

  • @LimbaniSamueli
    @LimbaniSamueli 15 дней назад +2

    Dpp ibweleleso m’boma tizigula zotchipa 💙

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 15 дней назад +3

    Kodi omwe anasunga black box aja bwanji sanangidwe?

  • @PeterPhiri-di1ux
    @PeterPhiri-di1ux 15 дней назад +5

    ndie kuti anthu tilibe ufulu oyankhula

  • @MustafaBotoman
    @MustafaBotoman 15 дней назад +4

    Mwagundika kumanga athu Malo moti mobweletse black box

  • @JohnMalunga-h5l
    @JohnMalunga-h5l 15 дней назад +1

    Abomawa atha nzeru awa, akupitiabe kuononga misonkho ya aMalawi ?

  • @GraceChikosa
    @GraceChikosa 15 дней назад +1

    Koma MCP yavuta bwanji ,cholinga akamumanga Chisale apeze mpata okuti akamuphe Peter Munthalika? Akunamatu amenewo .. Peter ndiotetezedwa ndi Mulungu wathu wa Moyo ,,God please punish all MCP members ndipo muwakanthe ndi moto wanu a mzimu woyera chifukwa akulimbana ndi ana Anu osalakwa 🎉🎉🎉

  • @PromiseBonya
    @PromiseBonya 15 дней назад +4

    McP matha mudzingomanga anthu osalakwa vomerezani zakuvutani bas ,musalimbane ndi anthu osalakwa

  • @AbellMlashi
    @AbellMlashi 15 дней назад +1

    Kd anthu enawo bwanji simukuwamanga km MCP aii mwanyanya please dzilongedzani nthawi yakuntherani

  • @JeniferKananji
    @JeniferKananji 15 дней назад +4

    Chimwendoso amangidwe chifukwa amanyozaso APM why

  • @sheedampama1462
    @sheedampama1462 15 дней назад +3

    Koma MCP muli pa ntchito iiiiiii😅

  • @JohnPaul-r4u
    @JohnPaul-r4u 15 дней назад

    Koma akuti ndichani MCP 😅😅

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 15 дней назад +1

    Nde mumange onsetu..mwaiopela kutali..campaign yikubolani mimba

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz 15 дней назад +1

    A MCP ndi mbuli zokha zokha basi mmalo mokonza zithu akhalira kumanga anzawo???,mmawa ndi inuuuuu

  • @JudieBanda
    @JudieBanda 15 дней назад

    Mizimu 9 ija osazaiphweketsa
    Anthu akupenga kuno kkkkkk mitu sikugwira olo pang'ono
    Wina ayenda maliseche ndithu kkkkkk
    Apm my vote

  • @charlessulumba2521
    @charlessulumba2521 15 дней назад

    Issue ya Chisaleyo, ndie ndi fodya weniweni ndithu, misala at climax

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 15 дней назад +1

    If political wrangles in Malawi were philanthropic bounties, lam double sure ever Malawian would be a billionaire--real magnate.

  • @YassinzaoZao
    @YassinzaoZao 15 дней назад

    😂😂koma mcp yayamba kuwopa tayamba Kumanga anthu koma akunama kuvuta kwambiri

  • @AndrewDeebastola-kd4mq
    @AndrewDeebastola-kd4mq 15 дней назад

    Chaka timenyanapo nkhondo ndinthu

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 15 дней назад +1

    Kod Iwo a mcp muja amatukwanira nzimai uja amati Jessie kabwira chimwedo Banda kutukwana peter bwanji samamangidwa km ndale zakumalawi zafikapo ziko lonyasa makhalidwe ake kumachita kuchira manyazi kuvomeleza kut ndiwe wakumalawi

  • @GrantLivata
    @GrantLivata 14 дней назад

    Ku MCP sakagona tulo

  • @CharmaineGoncalves-k7e
    @CharmaineGoncalves-k7e 15 дней назад +3

    Izi zalowa misala ndithu 😂😂😂 apolice athu angogwilitsidwa ntchito ngati ma remote control boma la MCP lizamva kuwawa Chakwera aziziwa kuti sanamangidwepo mchifukwa ndi Chimwendo wakeyo

  • @Christopheryakobe1989
    @Christopheryakobe1989 15 дней назад +2

    Mcp ikuchita mantha ndi dpp

  • @TexonPhiri
    @TexonPhiri 15 дней назад +1

    Kusowa zifukwa zomangra anthu apule awa😂😂😂

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 15 дней назад

    Kodi MCP mwadya Chipwisi cha kanyimbi or bwanji, mkazi wamunthu uja osazauphweketsa😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂yomweyo Chikangawa party mwanya nayo mwalowa chiwewe chomanga anthu 😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂🎉😂

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 15 дней назад

    Akumusaka bwanji kwawo sakukuziwa mukulimbana ndi anthu a DPP bwanji mukunjenjemelanawo kwambilitu

  • @ChisomoMijoso
    @ChisomoMijoso 15 дней назад

    Causing Fear and Alarm??? Nanga a zikwanje samachita cause Fear and Alarm? Are you serious?

  • @DamsonMpasu
    @DamsonMpasu 15 дней назад

    Dzanja lalemba pakhoma ufumu wanu wayesedwa ndipo wapelewela

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 15 дней назад +1

    Kodi MCP muku panga chani koma zopusa zimene muku pangaziiiii

  • @MaloneFundo
    @MaloneFundo 15 дней назад +1

    Downfall of government 😊

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 15 дней назад +2

    Uwunso ndi umboni wakuti MCP inapha Chilima. Atafa Raph Kasambala panapita mthawi yochepa Chilima kuphedwanso, pamodzi ndi anthu a muchipani mwake. Kenako anaphedwa Lucious Banda. Leronso mmasiku oyandikana anthu a DPP akumangidwa. Mwanamveka==>Suleman==>Kabambe==>Chisale. Zonsezi zikuchitika mmasiku oyandikana ngati mmene anaphedwera Chilima

    • @WelingsLongwe
      @WelingsLongwe 15 дней назад

      Palibe umboni apa zoti anapha anthu nkhani ndiyoti anasikeza ndalama musaohatikize nkhani tikambe nkhani imene munthu amunjatila ngati anasokoneza ayimbidwe mlandu basi kubisa chilungamo bwa amene anafa akuziwa wokha chimene chinachitika amene tili ndi moyo palibe chimene tingakambe alekeni mizimu yawo ipume

    • @WelingsLongwe
      @WelingsLongwe 15 дней назад

      Dziko pano likivutika chifukwa Cha anthu ake womwewa anawononga chuma pano azitiohimba mumaso kuti dziko silikuyenda bwino chosecho ndalama anaba

    • @ElizabethMajiga
      @ElizabethMajiga 15 дней назад

      Kodi munali kokuja kukamwa nawo magazi aja etiii mupenga limoziii​@@WelingsLongwe

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 15 дней назад

      Kkkk chikangawa​@@WelingsLongwe

  • @HenryKuyewawa-h3k
    @HenryKuyewawa-h3k 15 дней назад

    Pandisangalasa ndipokhapo pa kangachepepo

  • @LoyceChipwaila
    @LoyceChipwaila 15 дней назад

    Zifika paja poti amalawi saziopaso police chifukwa yikungotumikira mcp ..
    Yasanduka police yachipani.

  • @MaulanaIriyasa
    @MaulanaIriyasa 15 дней назад

    Mcp how many people you want to arrest In Malawi now we are tired to hear warrant of arrest

  • @HalimaKalera
    @HalimaKalera 15 дней назад

    A mcp akuona ngati afikapo

  • @AngelaGraysham
    @AngelaGraysham 15 дней назад

    Thats the kicks of the dying horse

  • @FelixKChisale
    @FelixKChisale 15 дней назад

    Ngat nkhani za salima sugar zikumukhudza akuyenela kumangidwa bas

  • @Ruthgomonda
    @Ruthgomonda 15 дней назад

    Osawopa Mr chisale zikamatelo kulipafupi kucha

  • @InacioCement-t7n
    @InacioCement-t7n 15 дней назад +1

    Apoli ake a Mcp tu mai yolamu

  • @ChikkaLemani-qw6fn
    @ChikkaLemani-qw6fn 15 дней назад

    Mmmm koma

  • @StandwellNjoka
    @StandwellNjoka 15 дней назад

    Apite nkumene akamutenge chisale tione,manyi akutherani awathera a mcp

  • @YusufMaulidi-b2c
    @YusufMaulidi-b2c 15 дней назад +1

    Musaiwale kuti anthu omwewa ndiamene anakuvoterani ngati sakusangalala sikuti adana nanu koma akudana ndi zichitochito zanu

  • @MartinNgoma-tp2jk
    @MartinNgoma-tp2jk 9 дней назад

    Koma sinazionepo mcp nigalu sakuva olo otamumenya

  • @JeniferKananji
    @JeniferKananji 15 дней назад

    Magadzit ndichithu choophya kwambiri asavuka sanat chakwela apenga

  • @Vincentrami-m9v
    @Vincentrami-m9v 15 дней назад

    Anomani apolici akabwera kunyumba kwanu muwa menye onseo

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal 15 дней назад

    Koma MCP uchitsilu umenewu muthana nawo liti mwangokhala mbuzi zokha zokha basi?? zalowa misala sopano

  • @EMMANUELJsefasi
    @EMMANUELJsefasi 15 дней назад

    Norman chisale ndi Moto osaona madzi tiyeni nazoni zikuvutani

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 15 дней назад

    Mcp ikufuna kuyambitsa nkhondo mudziko

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 15 дней назад

    Nanga pamenepo amanama nomary chisale zoona ayangulaso bwino upekere milandu ina wosati iyisabhosa

  • @GeorgeFrank-k1q
    @GeorgeFrank-k1q 15 дней назад

    Chimwendo amayakhula mwano bwanji musakumumanga?

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 15 дней назад

    Poor police 😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂😅😅😅

  • @MercyChiwaya-um6us
    @MercyChiwaya-um6us 15 дней назад

    Kodi akusowa chochita basi tikhalile zimenezi

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 15 дней назад +2

    Hahahaha MCP chitseko chawapana kkkkkkk yomweyo galu iwe

  • @JohnmjigoMalinda
    @JohnmjigoMalinda 15 дней назад

    Kodi chimwendo banda bwanji amalakhula kuti Apm asowe koma samamangidwa ,mcp ikufuna khondo basi tiyeni nazo

  • @mikekaliza-bw4yg
    @mikekaliza-bw4yg 15 дней назад

    kodi anthu ophuzilani ndinu makape eti lelo ndadziwa kodi apolic akumalawi mukufuna kuti tizichita mantha kuti timangidwa oll bwanji tilolera kupheda oll ngakhale nkhondo iyi mwayiyambayi tisatila mwazi wathu ana amawa

  • @YusufujohnSeruweke
    @YusufujohnSeruweke 15 дней назад

    apolisiwo mitu yawo ndimfundoso zimenez

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 15 дней назад

    Zitsiru za mcp.

  • @ChimtamboWiliam
    @ChimtamboWiliam 15 дней назад

    Kma mutimaliza

  • @ChrisantKapandansalu
    @ChrisantKapandansalu 15 дней назад +1

    Koma Boma mumamva bwanj kumanga munthu usikuawa m,mawa mudzimva kuti watuluka

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 15 дней назад

    Basi MCP maganizo awo ndi opha anthu ndi kumanga anthu ayimani MCP mwanyanya bwanji kodi ndiye kuti anthu omse aku MCP ndiopa mtima basi ndiye kuti palibe wabwino mtima? palibe odzudzula mzake omse amangoti eeee zikhale momwemo ayimani sisiii.

    • @Ester-c6y9t
      @Ester-c6y9t 15 дней назад

      A MCP mwationjeza nonse mukungokhala ngat munabadwa banja limodz kuipa ntima chonchi bwanj mbudz za anthu chitilanit upandu wanuwu mu September munya manyiiiiii

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 15 дней назад

    Anthu a mcp eeesh

  • @DennisKankhuni-b8l
    @DennisKankhuni-b8l 15 дней назад

    Koma zina abale sofuta kwabas😅😅

  • @ChrisJere-m4b
    @ChrisJere-m4b 15 дней назад

    Akunama

  • @FelixKChisale
    @FelixKChisale 15 дней назад

    Kod a dpp sanaleke zokolezela zi wawa m dziko

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera 15 дней назад

    Chisale and all other DPP members are not bringing interfear in Malawi but those who killed SKC and eight others.

  • @ChpCosmass
    @ChpCosmass 15 дней назад

    Km mumaganixako xot inuso muxachokapo pampandop?? Ifet nde txangokukokan mapwala

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l 15 дней назад

    MCP mawa musazalire chifukwa mukuzikumbira nokha zenjee

  • @EdwardSinoya
    @EdwardSinoya 15 дней назад

    Cholinga nsonkhano wa DPP ku Blantyre ulephereke? kapena mukufuna moyo wa APM ukhale pa chiopsyezo? SHAME!

  • @EvasonThupilifana
    @EvasonThupilifana 15 дней назад

    Koma boma ili ndila mbuli zonkhazokha chakwela kwa mtumbo pako ndithu

  • @ZelifaMwale
    @ZelifaMwale 15 дней назад

    Koma mcp asavuka zoona azingomanga azawo

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 15 дней назад

    Kodi nanga chimwendo osamanga bwanji osamanga omwe adaba ndalama nduna za boma niki

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 15 дней назад

    Koma ndiye Ali buystu alimbikire a MCP kumanga anthu anthu a DPP kuti azawine mosavuta akuwamenyera nkhondo Iwo Ali pheeee mmalo molimbana ndi njala komanso fetereza amene aasakupezeka mdziko muno mbuzi za ziiiiii

  • @IbrahimAlidi
    @IbrahimAlidi 15 дней назад +1

    Mcp agalu achabechabe

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 15 дней назад

    Za ziiii

  • @FelixKChisale
    @FelixKChisale 15 дней назад

    Palibe mfundo apo zaziiii

  • @DuncanTmware
    @DuncanTmware 15 дней назад

    Or umange anthu km ife nda kukasungu iwe tikumanga pamavot

  • @HopeMakoka
    @HopeMakoka 15 дней назад

    Kodi MCP mukufuna a DPP asamapangitse misonkhano eti??? Kupusaaaaaaaaaa

  • @HildaLamwa-y7b
    @HildaLamwa-y7b 15 дней назад

    Asowa zochita awa Malo momema anthu kuti tipemphelere mvula ikuvutayi

  • @wallezysmooth4169
    @wallezysmooth4169 15 дней назад

    😂😂😂MCP arephera avomereze bac Dpp irowe Boma bac

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 15 дней назад

    Kodi awa ntchito yawo ndi yongomanga anthu? Shame on you

  • @MecksonChikumbutso
    @MecksonChikumbutso 12 дней назад

    Mbambande

  • @AtupereSadiki
    @AtupereSadiki 15 дней назад

    Kmatu A Mcp musatibhowe mwanva zopepera basi

  • @kennedymadise
    @kennedymadise 15 дней назад

    Limamanga munthu ndi kuphwanya lamulo osati chipani, umenewo ndi umbuli

    • @WelingsLongwe
      @WelingsLongwe 15 дней назад

      Tizisiyanisa Zimene zikuchitika Kodi munthu akalakwisa basi azingomuyanganila komaso zipani zimalowa natuluka koma police ndiyomweyo amayendera malamulo malamulo sachioani ndi aboma tiyeni tikonde dziko lathu ngati anthu ena akufuna kukoza zithu azikoze wosamangowombela mmanja akupasani kangachepe koma mabanja anu akulira ndi njara ena sayimila nawo athera kuwire bcoz munthu wokonda dziko lake sangasekelele mbava zowononga dziko awa mmene anali muboma amawona ngati sazachoka amangidwe basi

  • @FortuneDavie-n6z
    @FortuneDavie-n6z 15 дней назад

    Aaaaa mcp kusowa zochita eti

  • @BillyBentryMunthali
    @BillyBentryMunthali 15 дней назад

    Mbava zinazi

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 15 дней назад

    Mcp kodi mkulodzedwa kapena chani kutha kwa shasa uku.

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f 15 дней назад +1

    Kuombela mmanja mbava, kkkkk koma zachisoni.

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 15 дней назад

      Bolani ankaba anthu mkumakhuta.osati izi zazii nyau, nyikwi ntchito kusamba matope onunkha

  • @sheedampama1462
    @sheedampama1462 15 дней назад

    nde mwati zimenezi mukafika nazo kuti .....?

  • @OdalaBanda-i9c
    @OdalaBanda-i9c 15 дней назад

    Kod mukuona ngat ndinu amuyaya? Nyapanu boma lolandalo kupanda chilima munamupha uja mulindan inu shame on u

  • @LimzeySande-b9n
    @LimzeySande-b9n 15 дней назад

    Boma koma ili 💙💙💙💦

  • @PeterNyandolo
    @PeterNyandolo 15 дней назад

    Mcp yatheratu sidzapedzekanso muno mMalawi

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 15 дней назад

    Dpp APM bomaaa