BON KALINDO LERO PA 23 JANUARY WAULURA IZI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 фев 2025

Комментарии • 165

  • @EsterSamuel-x9f
    @EsterSamuel-x9f 8 дней назад

    Bon kalindo woyeeeee! Mumatiyimilira inuyo mulungu azikudalisani pamene mungayende ndi pamene mungakhale keep it up

  • @RichardHetekere
    @RichardHetekere 9 дней назад +1

    Umakwana here from Capetown God bless you ❤

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 10 дней назад +6

    Ndipo wina ayaluka pa ground chifukwa ndi Mfundo zomwe alibe amawakwapulira Mfundo ndiye anamutafunira ku CHIKANGAWA. Chi........te cha President kudzolowera kuphyodza Magazi ndi mikodzo .
    Ngakhale Ku ma MP MCP ilira .
    Tilipano kuonera.
    Keep moving forward the DC Bon Kalindo

    • @ErnestChansa
      @ErnestChansa 9 дней назад

      🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 more more more more more fire fire mr God bless you nd protect you

    • @EsnatKandeu
      @EsnatKandeu 9 дней назад

      Amen 🙏🙏🙏 God bless you the DC everything for you amen 🙏🙏🙏

  • @GeorgeNkhoma-x9r
    @GeorgeNkhoma-x9r 10 дней назад +1

    Listening from Capetown more fire Kalindo I'm behind you. ❤

  • @JabuAdam
    @JabuAdam 8 дней назад

    Ipaseni Moto lfe pambuyo panu bass💥💥💥💥💥🔥👍👍

  • @DannieChimenya
    @DannieChimenya 9 дней назад +2

    Booon Kalindo the DC 🔥🔥💪💪 mwana wachabe kwambili

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 10 дней назад +2

    The best one brother Bon Kalindo 🔥🔥🔥🔥

  • @nickmumba2131
    @nickmumba2131 10 дней назад +1

    Viva the DC viva we want peace in our country not peaces 😢

  • @CatherineMsaya
    @CatherineMsaya 9 дней назад

    The DC may God bless you and protect you ❤❤❤

  • @YassinzaoZao
    @YassinzaoZao 9 дней назад

    The DC mumakwana❤❤

  • @MwateroNamalima-c4k
    @MwateroNamalima-c4k 10 дней назад

    Big up the DC forward ever backwards never,,,God bless you

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 10 дней назад +2

    We are in democracy.I wish to suggest national re-registration of voters.First, form Government of Unity for free and fair Sept. tripartite polls.

  • @BeatriceNgulo
    @BeatriceNgulo 10 дней назад +1

    Mwana owopsaaaaaaa kwambiri ❤❤❤❤

  • @Stevesmon
    @Stevesmon 10 дней назад

    Bon kalindo God bless you all the time am with you

  • @TabithaThyolani
    @TabithaThyolani 10 дней назад

    i will always pray for you, may the GOOD GOD CONTINUE TO PROTECT YOU 🙏🙏😅

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 10 дней назад

    bon kalindo ❤from Cape Town mitchells plain town centre

  • @FrancisHussain-k5p
    @FrancisHussain-k5p 9 дней назад

    The Dc❤❤❤❤

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs 9 дней назад

    The DC❤❤❤

  • @DominiqueChitimbe
    @DominiqueChitimbe 10 дней назад +1

    the DC akatundu 🔥🔥💪 chesaopa

  • @MartinNice-z9n
    @MartinNice-z9n 9 дней назад

    Umatimilira The Dc

  • @OwenNyambose
    @OwenNyambose 10 дней назад +1

    The dc ❤️❤️

  • @maxwelljuwaophiri
    @maxwelljuwaophiri 10 дней назад

    The DC the President of the less privileged people in Malawi.
    You represent Us

  • @WadsonVincent
    @WadsonVincent 10 дней назад +1

    Born kalindo more fire atikwana amenewa😮😮😮😮

  • @jaymillez-c9y
    @jaymillez-c9y 9 дней назад

    Big ulemu wanu 😂😂

  • @redsonchakanika
    @redsonchakanika 10 дней назад

    The DC🎉🎉

  • @PatrickDavidTembo
    @PatrickDavidTembo 9 дней назад

    Dc🎉🎉🎉

  • @IsabelLuka-i8f
    @IsabelLuka-i8f 10 дней назад

    THE DC🎉🎉🎉,mumakwana bigeeee

  • @ReubenKapesi
    @ReubenKapesi 10 дней назад +1

    Long live legend ❤❤

  • @ziggympandakwaya3054
    @ziggympandakwaya3054 10 дней назад

    You are the one Bon kalindo

  • @JaysonChimphamba
    @JaysonChimphamba 10 дней назад

    The DC 🔥🔥🔥🔥

  • @asantebenga
    @asantebenga 10 дней назад

    Osafoka DC ❤❤

  • @MwaiKalinde
    @MwaiKalinde 10 дней назад

    The DC♥️♥️♥️😊

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 10 дней назад

    😅😅😅😅 koma the DC umakwana more 🔥 am coming 🎉🎉🎉🎉

  • @JamesMkanamwano
    @JamesMkanamwano 9 дней назад

    Yes Yes

  • @JosephMwadzama-f4u
    @JosephMwadzama-f4u 10 дней назад +1

    Kkkkkkkk akulakula matako eti ali abambo koma akulakula matako ngat azimayi 😂😂😂😂

  • @HenryFashi
    @HenryFashi 10 дней назад +1

    Viva Kalindo Viva!!!!!!!

  • @Jamaat-m7l
    @Jamaat-m7l 10 дней назад

    Mwana woooooooopsa kwambili ❤❤❤❤❤

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 9 дней назад

    Mcp ndaona makape koma mcp kuli makape thawi sikuyima kkkkkkkk olo mungone ikuyenda😂zitsiru

  • @DavieKandikole
    @DavieKandikole 10 дней назад

    Thanks Born Kalindo mwainu tikondwera

  • @Isaac-u3v
    @Isaac-u3v 10 дней назад

    Uyu mkatundu omanga ndimawaya tiyenaooooo,😮😮😮😮😮😮❤❤❤❤❤🎉

  • @omarduwa3441
    @omarduwa3441 9 дней назад

    Awe

  • @MaxwellMinikwa
    @MaxwellMinikwa 9 дней назад

    Mmakwana akalindo

  • @GersonMadikhula-y7h
    @GersonMadikhula-y7h 10 дней назад

    But you Bon Kalindo, 😅😅😅😅,you are someone ..😂😂

  • @EmiryMaponya
    @EmiryMaponya 9 дней назад

    Mwana owopsa kwambiri

  • @WatsonPhiri-u6u
    @WatsonPhiri-u6u 10 дней назад

    Fire Mr born kalindo timadara inuyo

  • @BeautyMtambo
    @BeautyMtambo 9 дней назад

    DC UMATIYIMILILA IFE OSAWUKA TILI PAMBUYO PANU

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 10 дней назад

    The DC❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @KondwaniLungu-b8b
    @KondwaniLungu-b8b 8 дней назад

    Eya ku Dpp-ku eeeh sikunali bwino, koma ngati Mulungu angawapase mmpata akuenela ku zasintha basi .

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s 10 дней назад

    Nthata zanjala zikuyamwa mazi wa amalawi modetsa nkhawa,DCamanena zoona pamodzi ndi amnzake aja.Mayi akutitakata.Nthawi inu a opposition mukugona tulo chenjerani.These are turning up every stone not leaving any stone unturned.

  • @StoraStora-d5l
    @StoraStora-d5l 9 дней назад

    Ndimakuziwa Dc sumawopa

  • @lordwinsankhan4606
    @lordwinsankhan4606 9 дней назад

    Umakwana the DC

  • @EstherMatapila-z8r
    @EstherMatapila-z8r 10 дней назад

    Dc munabwela osafooka💪💪

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 10 дней назад

    😂😂😂 DC 🎉🎉🎉

  • @ChrispineMuzungu-l8h
    @ChrispineMuzungu-l8h 10 дней назад

    The DC 🎉🎉🎉

  • @Halisenasimia
    @Halisenasimia 10 дней назад

    Yes muthu wakulu never give up 🏃‍♂️🏃‍♂️🤸‍♂️

  • @EliasMsamala
    @EliasMsamala 10 дней назад

    The DC......❤

  • @JonaSato-j8e
    @JonaSato-j8e 10 дней назад

    The Dc ❤😂😂😂

  • @catherinekadwala3839
    @catherinekadwala3839 10 дней назад +1

    Tatulusani ndodozo the DC plz

  • @YassenYasin-v6o
    @YassenYasin-v6o 10 дней назад

    Inuyo ndimachine🎉🎉🎉❤❤Dc❤

  • @WakisaSichali-p9n
    @WakisaSichali-p9n 10 дней назад

    Ayelekeze kukumanga ife tikachezela pa area 30 po ndizibwana zimenezo

  • @HildaMbizi
    @HildaMbizi 9 дней назад

    Mumukumbukenge skc pa campaign imwe wa mcp

  • @olivemkumba
    @olivemkumba 9 дней назад

    Katswiri,🔥

  • @CharlesMphanda
    @CharlesMphanda 10 дней назад

    I love you boss

  • @HenryKatopola
    @HenryKatopola 10 дней назад

    The DC ❤❤❤❤❤❤❤❤❤😂😂😂😂

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela 10 дней назад

    kalindo yes yes kkkkk minatha

  • @Malani41
    @Malani41 10 дней назад +1

    Kalindo is a culprit!

  • @NelsonSambo-e2s
    @NelsonSambo-e2s 9 дней назад

    Pango lini

  • @Aubreyffindmindozo
    @Aubreyffindmindozo 9 дней назад

    Dpp sinalakwe, unapangisa ndiyiweyo kalindo Ntambo chilima kaliyati, anthu inuyo ndamene munaika amalawi pamoto

    • @temwekamlenje4358
      @temwekamlenje4358 8 дней назад

      Amayendera chiungamo DPP imalakwisanso. Musiyeni ali ndi chilungamo. Amanena momwe zilili

  • @PatrickDavidTembo
    @PatrickDavidTembo 9 дней назад

    😂😂😂😂Dc

  • @mbonilekisebe2286
    @mbonilekisebe2286 9 дней назад

    Uyu akuti chimwendo Banda matako kutalika mpaka kufika mu nsana koma mimba kuchita kuyambila ku khosi abale. Tamadyani bwino ndalamazi. Savage

  • @Felie-p7l
    @Felie-p7l 10 дней назад

    Boncalindo mulungu azikutetezerani timadalila inuyo bro

  • @FelixJumby
    @FelixJumby 10 дней назад

    😂😂😂😂😂 ATI ine sindi manyengelera nd mangonena eeeee DC sadzatheka 😂😂😂😂

    • @faithKwakwasa
      @faithKwakwasa 10 дней назад

      Ati ndingobwera ndekha kapena 🤣🤣🤣🤣🤣

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 10 дней назад +1

    a opposition azang'wempha adzatuluka mamina MPHUNO MKAMWA NDI MMAKUTU kuzimva kwambiri

  • @JosephMwadzama-f4u
    @JosephMwadzama-f4u 10 дней назад

    The DCCCCC❤❤❤❤❤❤❤

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 10 дней назад

    Solution yomupha chilima kunali kuganiza mwaumbuli kwa MCP Chifukwa chilima anali mmalawi and it was agreed kuti mulamulila 5 yrs winanso 5yrs, Achakwela ngati mumapemphela mumangotaya nthawi yanu

  • @JanaJovian
    @JanaJovian 10 дней назад

    ❤❤❤❤

  • @GoodceeDehkasongoh
    @GoodceeDehkasongoh 10 дней назад

    Yaa

  • @MaggieMaseko-m6s
    @MaggieMaseko-m6s 9 дней назад

    Mumatiimilila bwana, mumanena chilungamo

  • @MphatsoGamah-v3v
    @MphatsoGamah-v3v 8 дней назад

    DC mwana wachabe kkkkkkkk

  • @ChiccoJali
    @ChiccoJali 10 дней назад

    Viva kalindo

  • @blessingschirwa7292
    @blessingschirwa7292 10 дней назад

    Iwe wati nthata zanjala 😂😂😂😂😂😂 zoona

  • @FiskaniChidatha
    @FiskaniChidatha 10 дней назад

    Auzeni zenizeni a DPP ankameraso mapiko kwabasi kuiwala kuti Malawi amaona Ndipo asinthe adzapoze mabala tilinawowa

  • @JonesMangazi
    @JonesMangazi 10 дней назад

    Malawi Sali bwino dziko anthuwa aliwononga 1 rand panopa ikusinthidwa pa 183 kwacha for the very first time in malawi history but am sure ifika 200 soon

  • @Jonathankachulu
    @Jonathankachulu 9 дней назад

    The DC mwana wakwathu kumulanje

  • @BysonPhiri-gu4io
    @BysonPhiri-gu4io 10 дней назад

    Iwe ndidolo

  • @ChiccoJali
    @ChiccoJali 10 дней назад

    Viva kalindo DC

  • @PeterKampiraBanda
    @PeterKampiraBanda 10 дней назад

    The DC

  • @NdaonaMsowoya
    @NdaonaMsowoya 10 дней назад

    Vuto anthuwa safuna kt azatese mavuto km azigwadilidwa ngati mulungu vuto Malawi tilibe umozi tidakali ntulo kukonda ndale mwalo molikonda ziko lathu

  • @Openjkick
    @Openjkick 10 дней назад +1

    ruclips.net/video/o0g35X9MOE0/видео.htmlfeature=shared

  • @chifundowachitedze3952
    @chifundowachitedze3952 9 дней назад

    Mphamvu the dc

  • @FrankMoses-x3v
    @FrankMoses-x3v 9 дней назад

    Umakwana

  • @DerrickDillarh
    @DerrickDillarh 10 дней назад

    M'banga weni weni

  • @DavieDulani
    @DavieDulani 10 дней назад +8

    Big Big umatiyimilatu

  • @emmanuelnyirenda3289
    @emmanuelnyirenda3289 10 дней назад

    Koma pa mumba ndiye ukunyika kwambiri

  • @CollinaChirwa-dh7qx
    @CollinaChirwa-dh7qx 8 дней назад

    😂😂😂😂komaa kupereka phone number kodi

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 10 дней назад

    Ndimanena nthawi zonse kuti maboma a mbuyomu amaba inde koma timadya komanso dzinthu dzimayenda bwino osati idzidzi kuba kopanda plan ndichifukwa tikuti APM abwelele

  • @HarrisonJames-h9s
    @HarrisonJames-h9s 10 дней назад

    Ngat mumange kalindo Ineso mundimange

  • @KHOOMJIFUMBENKHATA
    @KHOOMJIFUMBENKHATA 10 дней назад

    😂😂😂😂 eti inu munthu mmodzi koma a police mbwelele apapa

  • @temwekamlenje4358
    @temwekamlenje4358 8 дней назад

    Tribalism a DPP ndi quarter system mbola
    MCP mfiti

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 10 дней назад +1

    Mr DC tili pa mbuyo panu