BON KALINDO LERO PA 31 JANUARY

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 31 янв 2025

Комментарии • 56

  • @RuthTimothyChirwa
    @RuthTimothyChirwa 21 час назад +4

    Moto Mr Boni 🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤

  • @JosephGabriel-y7w
    @JosephGabriel-y7w 11 часов назад

    Bon kalindo iweyo ife timagula madata kuti tivele inu ma bigy l love ❤❤❤❤

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 23 часа назад +1

    ❤❤❤mwana wa mama Malawi muno bon kalindo God ahead u my brother. from Cape Town mitchells plain town centre

  • @MariaDandazaraJSDmoio2024e
    @MariaDandazaraJSDmoio2024e 23 часа назад +4

    Moto 🎉🎉🎉🎉🎉 Dc Bon Kalindo auseni kuti aziwe zeneni kuti achite bwino fire ❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @AbdulrashidPhiri-c6k
    @AbdulrashidPhiri-c6k 9 часов назад

    The DC boooooooorn kalindooo ❤

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 22 часа назад +3

    Manganya, Nankhumwa ndinu makapa

  • @LookmanAdamu
    @LookmanAdamu 23 часа назад +2

    Mumatiyimilila akalindo❤❤❤❤

  • @ChimwemweBanda-g7o
    @ChimwemweBanda-g7o 10 часов назад

    Bon kalindo wathu wathu waku mulanje kuno👉🏔️

  • @DannieChimenya
    @DannieChimenya 23 часа назад

    Booon Kalindo the DC 🔥🔥💪💪 mwana wachabe kwambili 💪

  • @austingsmaganizo
    @austingsmaganizo 21 час назад

    DPP idasosolera pa msampha imafuna chithandizo pakalowa njoka.Zikatheka basi mmati paliponse pakhale wanu wachilomwe.UDF ndiye mudaichita chipongwe kale singabwerezeso.Boma ndilomweli ndipo palibe kusinth.Mufune musafune Dr Chakwera mpaka 2030 woooo

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 21 час назад

    THE DC OSUTSA BOMA CHONDE MUTIPETSA AMALAWI KU MCP IYU CHIPANICHO ANALEPHELA KUWINA ACHILIMA KAMABE NDANITSO ATUPELE SANGAWINE PANGANI CHIMODZI MUTIPULUMUTSE AMALAWI KUYIPHELA APA MCP BASI CHIPANI CHIMODZI UYU NDIKAGAME ATSIYANA ADZIMA PA VOTE PAKA KALE

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 23 часа назад

    The DC ❤..Zoona zokhazokha ❤❤❤❤❤❤

  • @PaulMwachande
    @PaulMwachande День назад +1

    AA DC KUNENA ZONA MUMALANKHULA CHILUNGAMO KOMA AZIPNI ZOSUSA SAMVA AYI M'BUSA WINA KWA VUMBWE AMAWAWUZA LIVE PA MALILO A MWANANVEKA KUTI NGATI AKUFUNA KUWINA OFUNIKA ,M,NGWILIZANO KOMA ANTHU AKEWA KUDZINVA TOO MUCH

  • @annievitumbikonkhoswe770
    @annievitumbikonkhoswe770 13 часов назад

    Mulipachi ntchito bwana😂. Zikomo tikumverako zambiri

  • @RitaKainga
    @RitaKainga 14 часов назад +1

    Aopparition"wa atipweteketsa chifukwa chosamva

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 Час назад

    A opposition kukula mtima kwambiri malangizo akupasidwa kusamva

  • @adamdiss1868
    @adamdiss1868 День назад +1

    Mwauze big

  • @ZuzaPrecious
    @ZuzaPrecious 21 час назад

    DC 🔥🔥🔥

  • @QspyKtmSlmn
    @QspyKtmSlmn День назад +1

    Truly ❤

  • @kamowafelamo2652
    @kamowafelamo2652 21 час назад

    💥💥💥💥💥💥 bon kalindo machine kasongo one

  • @SannahAbdulAzizi
    @SannahAbdulAzizi 23 часа назад

    The DC mwana owoopsa kwa mbili

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 22 часа назад

    Kuswa×2 mosayang'ana chipani kapena nkhope oposition nkhani ndimeneyo mu umodzi muli mphamvu

  • @WilsonChiona
    @WilsonChiona 22 часа назад

    DC🔥😊

  • @PatrickMaluwah-bx9or
    @PatrickMaluwah-bx9or 23 часа назад

    The DC,Mulungu akudalitseni kwambiri,anthuwa mumaamudza chilungamo koma sakumva,vuto kusamva kwao kuzaika a Malawi mavuto.

  • @AnnesiChiwere
    @AnnesiChiwere 23 часа назад

    ❤❤❤❤❤❤❤

  • @YassenYasin-v6o
    @YassenYasin-v6o День назад +5

    Ausen boss ❤

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 10 часов назад

    Osaopa osatopa osafooka comrade the dc

  • @maxwelljuwaophiri
    @maxwelljuwaophiri 22 часа назад

    Mumakwana Bwana DC Honorable Kalindo..
    Pitilizani kuwayimirira a Malawi

  • @LouisMW-x1w
    @LouisMW-x1w День назад +1

  • @DorothyPhiri-q2i
    @DorothyPhiri-q2i 23 часа назад

    Powerful ❤

  • @SaileyeMaster
    @SaileyeMaster 23 часа назад

    Awuzen chilungamo akhumudwe akhumudwe chilungamo mutanena madala bola ava andale kkk

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 21 час назад

    Bas ntchito kumanga anthu mmalo mothesa njala anyani amenewa

  • @WilsonMbendela
    @WilsonMbendela День назад +1

    True

  • @jameskamanga628
    @jameskamanga628 13 часов назад

    😂😂😂😂😂😂😂

  • @ChrissyNdemanga
    @ChrissyNdemanga 18 часов назад

    The DC mwana owoopysa kwambili

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO 23 часа назад

    Denis Mahata ndiye Yankho la tsala ku malawi. Ibrahim Traore wa ku Malawi

  • @MaluNamalamba
    @MaluNamalamba День назад

    I hope amva asadzalile pa mawa kuti zisankho sizinayende bwino

  • @JosephyTembwe
    @JosephyTembwe 23 часа назад

    Ife nde tudzakupangan follow m'ka kale

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 21 час назад

    Awuzeni aopposition ife tikudalira iwowo

  • @DominiqueChitimbe
    @DominiqueChitimbe 21 час назад +1

    the DC akatundu 🔥 chesaopa ukali wanu ❤❤❤❤❤💪💪🔥

  • @evancemadyo1792
    @evancemadyo1792 23 часа назад

    Osazinyenga ndchala ohooo

  • @PeterNgulube-d7v
    @PeterNgulube-d7v 22 часа назад

    Koma wawawuza wanzelu atorepo kanthu

  • @medsontembulo9459
    @medsontembulo9459 2 часа назад

    Chilungamo chilungamo

  • @FrancisHussain-k5p
    @FrancisHussain-k5p День назад

    The Dc mumakwana

  • @ZebeRashied
    @ZebeRashied 21 час назад

    Ati kasongo 😂

  • @ThomasJohn-f2l
    @ThomasJohn-f2l День назад

    Zipani zakumana zokumana zokula mitima zokha zokha

  • @ChifundoFrazer
    @ChifundoFrazer 21 час назад

    Bon kalindo machine operator,

  • @ModesterChagwira
    @ModesterChagwira День назад

    Mumakwana Apure athu

  • @BantonBanda
    @BantonBanda День назад +1

    The DC power

  • @NeliaGlaciano
    @NeliaGlaciano День назад +1

    Mumatiimilila

  • @NaomiNyangulu-l1p
    @NaomiNyangulu-l1p 23 часа назад

    Ndinu one a kalindo

  • @Mirriumkamwendo
    @Mirriumkamwendo 22 часа назад

    Koma chakwera ndioyipa

  • @MariamAkimu-t5p
    @MariamAkimu-t5p День назад

    The DC

  • @YusufByson
    @YusufByson 19 часов назад