GOVERNMENT PRESS BRIEFING | 1 FEBRUARY 2025

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 31 янв 2025
  • #malawi #africa

Комментарии • 43

  • @peterjere6672
    @peterjere6672 3 часа назад +1

    This is a great move our Cabinet ministers, continue coming to the public and engage on the issues affecting the people.

  • @JohnKayila
    @JohnKayila 43 минуты назад +1

    Too late guys where were you the whole past 4 years

  • @SikaKalirani
    @SikaKalirani 24 минуты назад

    This is great our ministers

  • @CharlesNkhanga-qi4xu
    @CharlesNkhanga-qi4xu Час назад

    Loving this minister of Tourism
    She knows the industry very well

  • @MadalitsoMeyah
    @MadalitsoMeyah 53 минуты назад +1

    Hahahaha nonsense briefing

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 Час назад

    Unity first in MalawiNo Unity no Freedom.No Freedom no Development. No national Development----mendicancy, specialization rut, wrangles and destitution prevail.

  • @QspyKtmSlmn
    @QspyKtmSlmn Минуту назад

    Yes of course MCP ikupita but you will be Minister under DPP government mosakaika Vitumbiko Mumba I really like your actions 💪

  • @ShamdanAjangale
    @ShamdanAjangale 2 часа назад +3

    Ufumu wanu wathaaaaaa

  • @SamuelKabambe
    @SamuelKabambe 2 часа назад

    These people must deliver other wise we are fed up with you 😢😢

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela Час назад

    this government has approved themselves that have not fulfill the hi 5 philosophy.citizens we intend to change the leader .

  • @MuhammadRAHIM-d5z
    @MuhammadRAHIM-d5z Час назад +1

    Kupitilizabe kuononga misokha ayamalawi zomwemuchitazo

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 Минуту назад

    Time is over

  • @TimothyvascoVasco-j6d
    @TimothyvascoVasco-j6d Час назад

    Pamene MCP yazindikila Kuti tiliza mavote yagwilozana yipomboneze amalawi Kuti akawavotele pachisakho nchaka chino musanamizidwe amalawi tisithe boma awa agwilizana zowopswa kwambili koma akunama kwambili boma tikuditha utsogoleli chakwela ndi nduna zake zonse out amitu yolimba poganiza ndikutukula malawi kuchepetsa njala

  • @JohnEzelohMagawa-fl8sw
    @JohnEzelohMagawa-fl8sw 48 минут назад

    No matter what but you have loose trust of Malawian

  • @MarveSoko
    @MarveSoko 46 минут назад

    Kuziyamba lero tatsegulatsegula mmimba. MBS sankaziwa ntchito yawo. Nonsenu dolo ndi Vitumbiko wakugogodani mmutu. Inu munali bola alowa.

  • @ZivanaiGwatura
    @ZivanaiGwatura Час назад

    Inuyo aboma muonese chitsanzo ndi mega farms awili or atatu osati private sector daily

  • @MphatsoLuka-gn3lr
    @MphatsoLuka-gn3lr 15 минут назад

    Awa diamene agwesa malawi

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 45 минут назад

    Adayiwala imfa anthu awa wonyasa pa maso pa mulungu

  • @MphatsoLuka-gn3lr
    @MphatsoLuka-gn3lr 26 минут назад

    Bava zikukambilana mene zabela

  • @ChrissyBhima
    @ChrissyBhima Час назад

    Feteleza mikumunanayo ndiye UTI? Kumulanje mupite mukafunse,anthu sanagule feteleza,ndiye muliphwi pamenepo kufuna kunamiza amalawi,mulindinsambi,ubwino wake mulungu akuwona

  • @MercyNkhoma-k1k
    @MercyNkhoma-k1k Час назад

    Mutati mwanena kwa amalawi kut zativuta sikuti tikanatu ayi kukamwa komwe kwayasamula sikuti mkukuwa ayi

  • @MarveSoko
    @MarveSoko 45 минут назад

    MBS imalandira ziphuphu inu

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 12 минут назад

    Zaziiiiiiiii

  • @JafarAnusa
    @JafarAnusa 28 минут назад

    Mbanva inu ife tili ndinjala inu mwadya so ngankhale motayakhula zazeru palibe tinganve ife yambani kuika kwa admac

  • @MartinRajab-w5e
    @MartinRajab-w5e 2 часа назад

    Ofutsa mafunso wa mcp oyankha wa mcp

  • @FrankPhiri-u5e
    @FrankPhiri-u5e 30 минут назад

    Zikomo anduna pokhala poyela ndinu oyamba kupanga izi

  • @jackalview7491
    @jackalview7491 Час назад

    Kodi black box yilikuti iwe kunkuyu

  • @DorothyMatola-kg8ph
    @DorothyMatola-kg8ph 2 часа назад

    Tikolola bwanji feteleza talephera kugula mvula mulungu mwachisomo chake watipatsa

  • @SamsonChitezi-o6g
    @SamsonChitezi-o6g Час назад

    Zisru zokhozokha .mwarima bwanji mumarima agaru inu

  • @HassanSaid-q8q
    @HassanSaid-q8q Час назад

    Koma mulibe manyanyazi ...mulungu akulangeni ndithu masatana inu😂muli pa mkumano umenewo

  • @McdonaldChirwa
    @McdonaldChirwa 2 часа назад

    Vitumbiko akufunika Ku uNduna wa Agriculture

  • @LimbaniSamueli
    @LimbaniSamueli 55 минут назад

    Thawi yakutherani athu akupha inu, ,.

  • @SliviaJosephy
    @SliviaJosephy Час назад

    Kodi muli busy be kuwononga ndalama inu anthu amcp simuva kudzudzulidwa

  • @robinbinali8431
    @robinbinali8431 2 часа назад

    Failure's!!!! Kagweren uko!!

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 33 минуты назад

    Too late azunza mokwana anali kuti monsemuja akagwere uko

  • @ClementBanda-x5q
    @ClementBanda-x5q 3 часа назад

    Yendaninso ku ma construction company osamangoyenda ku estate ndima company ena komaso ku construction company kuli nyasi

  • @MuhammadRAHIM-d5z
    @MuhammadRAHIM-d5z Час назад

    Ndiyinu athu ovesachisokwambili athusakufunatu kuyakhula mwalephela mwalephela basi ulendo ulipo

  • @HappyPinball-sg5bn
    @HappyPinball-sg5bn Час назад

    Kodi a moses ndi ntolankhani?

  • @JackMvura
    @JackMvura 2 часа назад

    Apa tudikira kukamwa kwamakadet zawayipira kale

  • @GibsonBankha
    @GibsonBankha 2 часа назад

    Pitilizani ndizimene tikufuna amalawingakhale otsutsandiwotsutsandithu sangalephele

    • @Jafari-s3c
      @Jafari-s3c 2 часа назад

      Mmene ankatsutsira chakwera Ali ku oposition muja pajatu ankakana nsewu wakukasiya kwao komwe

    • @FannyWadson-zg4oj
      @FannyWadson-zg4oj 6 минут назад

      A gbiso zero mulibe ifenso timalikonda boma ili koma azindikila mochedwa athuwa ndiwosanva mcp ndimakani kuba too murch tidakhumudwa nawo kale

  • @LacksonMchawa
    @LacksonMchawa Час назад

    Missing you sweet enjoy your night u