Malawi should support Israel because the land was owned by Israel before Palestine claimed it & bible can teach you better. We don’t support terrorists. Shame on you
That bible that you're referring to says it's ok to kill innocent women & children...? I thought killing was one of the commandments "not to do"...? Please exlplain.
Why fight over the lake when we are not making any profitable use of it? Africa should continue to look to unity not divisions. I agree 100% with the Israel/Palestinian issue. We are on the wrong side of history for as long as our government supports Israeli genocide.
Kwa ine Mike Nguluwe Anamiwa ndi amzanu ulemu wanu anthu Azeru wow ona patli a chikondi wosazikonda wonganizira za athu ena wosakonda ndalama tikuyamikilen tithanzeni kukoza zikoli tiili ndi ana tonse tikupita ku tsongolo ulemu
Am second tired with Chakwera Go to Ntcheu Dzunje area No good roads No good infrastructure No clean water I am here now Where is Malawi government? This is the home of my father But authorities please give them good tarmac road Thank you
Ndipo mai olemekezeka dr Joyce Banda solved it very well ndipo muthawi yochepa. It may look simple kokano that boundary tizalira tizapanga regret malawi will still remain poor and land locked. We already have few resources and we are failing to manage then instead tikungobetsa kwa azungu ndi maiko oyandikana nao thats being unreasonable
I like your voice namiwa you are one continue nyanja ndi yathu not Tanzania apo bii ikhalapo nkhondo M v T tiona kut zikutha bwanja amene angavomeleze zanyanja asowa on this year 😢
Tanzanians are our relatives, and nobody from around the border with Tanzania will want any conflict with our relatives over a useless topic which only serves people who have no relatives from either side of the border.
Nuff respect!....chakwera can not sell the lake ndikuchindila ndalama zonse mahule ndi achina chimwendo kunkuyu ndi zikhale kamajekete...osaiwala hule nanse mbeto
Hei, Malawi is just a grain of sand full in a wheelbarrow..we aren't even counted worldwide... Check, all presidents except Her Excellency Joyce Banda and Kamuzu Banda,have had fuel crisis shortages of fuel supply..We see no angels here apart from the exceptional two.... Was it not Bingu who said, *Kagoneni pa mseu ngati galimoto sizikupondani* Is this a lie? Or he sounded Eddie Murphy?... Lake Malawi issue: Tanzania Government cannot just change boundary.. Neither Malawi nor TZ can just wake up and draw new boundaries... Country boundaries were a colonial baby, not a single African country drew its boundaries...Go back to Archieves in Zomba and check boundaries as demarcated by colonialists... Northern Malawi border was an agreement for reasons discussed between the British and Germans...Mbeya was part of Nyasaland (Malawi) while North east of Lake Nyasa(Malawi)..belonged to Tanganyika(Tz) The British and Germans settled for a swap... The British released Mbeya to the Germans,(Tanganyika), likewise the Germans released North East of Lake Nyasa (Malawi)to the British... What you must know is that no single country can just wake up and make new boundary without international consultation... it's not an easy process...I see no reason why politicians and some NGOs are shaking knees for nothing.. Those who made such boundaries, the British and Germans governments must negotiate it on a round table..If Tz wants North East of Lake Malawi,then Tz must secede Mbeya City back to Malawi as was the agreement between the British and Germans... International Law on Common Waters was born after this agreement.. They give us back Mbeya City and be part of Common Waters..No such a thing will work until Tz gives back Mbeya City to Malawi... unedited text...
MCP is a cased party. Any one who joins MCP, no matter how blessed he or she is but will be cased as well. You must pray and watch Which party to join.
Ngati malire amavuta a Munda mzere umodzi mpaka zikwanje nde mukanene dziko we have defence force and their major responsibility is to defend the territory akuchedwa pati let them go their anyamata a mmadzi akateteze nyanja go
Malawi should support Israel because the land was owned by Israel before Palestine claimed it & bible can teach you better. We don’t support terrorists. Shame on you
Uku ndikusamvetseta history and Bible.
These are Jews fighting and killing Christians.
That bible that you're referring to says it's ok to kill innocent women & children...? I thought killing was one of the commandments "not to do"...? Please exlplain.
Mwapupulumatu kunena kuti Shame on you, 😂😂😂😂😂😂😂😂, Killing is not a good act, Thy shall not murder! Komanso ndiwe wa MCP nde kupha sivuto
Machende ako iweyo shame for yourself
Munthu osazindikira uyu musiyeni
Bravo namiwa ndi team yanu yonse tili kumbali yanu simulinokha ❤❤
Cded group,,keep it up!God bless n protect yu in Jesus christ name
Viva Comrade Namiwa..enough is enough
Akulu akulu Namiwa ndi chibinyira chokanika kusenza awa ndi akamunadi amene ayima pa cholungamo mopanda mantha. Power to that💪💪💪👍
Mr namiwa and his team may good lord protect them and continue their job in the name of Jesus,,,,
Viva comrade namiwa big up
Nsaname ine Chakwerayi amandisowesa choyankhura eeeish☹.
Landilan Maluwa anu Mr Namiwa,Amalawi ochuluka tili mbali yanu.
Big up Comrade Namiwa Osaopa Osafooka Osatopa.
Question kodi abwana athuwa analidi aku church kapena amkagwila ntchitito basi zikudabwisa???
Namiwa he is my favourite person
Why fight over the lake when we are not making any profitable use of it? Africa should continue to look to unity not divisions.
I agree 100% with the Israel/Palestinian issue. We are on the wrong side of history for as long as our government supports Israeli genocide.
Umatiimirila more fire Namiwa
Very wise and intelligent Namiwa go on,,,, osaopa osafooka osatopa 🔥
Please go ahead Mr Namiwa
Powerful our saviour
God bless you namiwa
Apa tinaimbila mfiti m'manja tilibe mau a 🇲🇼 malawi
Ndipo zoonadi tinayimbira mfiti m'manja ndi chani chomwe chinatilodza ife? Tinapusitsika ndi ubusa, anavala chigoba cha ubusa
@VeronicaChirwa-ct4os ndipo kwambili
Great man
May God bless you Comrade
Chilungamo poyela together with Malawi
Nice briefing
God z with u comrades ❤
never give up Namiwa
Atola nkhani nawonso zuwakhuza that's why akusowa mafunso. We need God's presence on this..........
God bless you guys ❤
Let's continue comrade never give up
Worm heart of Africa ija ikusapota nkhondo chifukwa cha chakwera
Worm😢
Kkkk😂😂😂
The other problem we have in Malawi is that we employ soldiers who are our very young children who cannot withstand the pressure and fight.
exactly
Namiwa is a true Malawian
God bless you guys ✊️
Go go go
Mr Namiwa big up bro
Number 1
I like the confidence from Mr. Phiri.. Good composure
@@nthawigolowa5158 Why is Israel in Gaza?
@KumbukaiMtawaliWaMoffat why are u asking me that? Didn't u hear from the briefing
@@nthawigolowa5158, Kodi awa ndi azibusa mumati Ojiya waja akusiyana bwanji?
We have had a lot of briefings......are we making progress??
Comrade Phiri mu kunveka ngat Namadingonamadingo eeh😊
Big up!
Kodi asilikaliwa ncthito yayo ndichiyani Kodi iwowo siwoteteza dziko chaka ndi chaka kulemba asilikali akati ateteza dziko ndikumademo zoona ndalama zathu zikungopita ndizowona asilikali athu adzisiya kuteteza dzi dzikolawo adzikateteza mayikol akunja zoona kunsanke analanda kumachinga analanda kumwanza analanda sizoonayi anamiwa mwayitenga bwino koma musakhale mwasamila chipani musawonetse mbali nenani chalakwikacho mbalizose mukatelo amalawi ose adzikuvetselani Imani panokha chonde mupange zadziko lose
Ndi opepera awa amangodziwa kupita ku DRC
Asilikali amayendera ma orders, ngati atsogolero ali chete, asilikali sangangopakira mifuti ulendo ayi. Nyanja yapita basi. Alandira bwanji map achilendo nkukhala chete?
Honestly asilikali akumalawi ndopepela maiko ena kukamachitika zopusa kuboma amatha kuchosa president ndkukonza dziko koma athuwa mmmmmmmm
Asilikali athu pano ali ngati Tambala onyowa
Ayi alowa ndale ngati police
Comrade Namiwa big Up ana anthu adzavutika ndi ziganizo zopusa.
God bless you guys ❤ mulungu azikutetezani kuti malawi amulumuke kunzela mwainu chiyembekezo cha amalawi chili pa inu ❤❤❤❤❤
Namiwa anabadwa kudzapereka chiyembekezo kwa olema ndi othodwa. Ndimamumvetsetsa pazomwe amapanga,amafuna zabwino zizichitikira pa a Malawi
Ndipo kwambiri
Namiwa uremu 🎉🎉🎉 mukutiyimiriradi my God bless you
Elder ....Nàmiwa ....Respect....❤🔥🔥🔥🔥
Mr. Namiwa mulisinthadi dzikoli
Kwa ine Mike Nguluwe Anamiwa ndi amzanu ulemu wanu anthu Azeru wow ona patli a chikondi wosazikonda wonganizira za athu ena wosakonda ndalama tikuyamikilen tithanzeni kukoza zikoli tiili ndi ana tonse tikupita ku tsongolo ulemu
Am second tired with Chakwera
Go to Ntcheu Dzunje area
No good roads
No good infrastructure
No clean water
I am here now
Where is Malawi government?
This is the home of my father
But authorities please give them good tarmac road
Thank you
Mr namiwa timakunyadilani pokhala nafe amalawi❤
Ndipo mai olemekezeka dr Joyce Banda solved it very well ndipo muthawi yochepa. It may look simple kokano that boundary tizalira tizapanga regret malawi will still remain poor and land locked. We already have few resources and we are failing to manage then instead tikungobetsa kwa azungu ndi maiko oyandikana nao thats being unreasonable
Big up namiwa
Koma awawa ayankhura kachiwiriwo akufunika adziyankhura yankhura plz mr Namiwa
Our hero Mr
Katundu waboma uyu he's a freedom fighter
NAMIWA THE BIG MAN🎉😊
Mukhalira yomweyo Chakwera mukunenayo awinanso
muza winila kubela osati za chilungamo mukunama man
Mutu wao sungwir ntchito pan aprezident anth ndip sakudziwa chomwe akuchit akufunik kumtemela srs
I trust namiwa hiro
Baba Namiwa god bless ❤️
I like your voice namiwa you are one continue nyanja ndi yathu not Tanzania apo bii ikhalapo nkhondo M v T tiona kut zikutha bwanja amene angavomeleze zanyanja asowa on this year 😢
Tanzanians are our relatives, and nobody from around the border with Tanzania will want any conflict with our relatives over a useless topic which only serves people who have no relatives from either side of the border.
Kodi munthu ngati amakonda anthu ake angadane naye chakwera ndi galu kapena mbuzi iweso ukusapota chakwera ndiwe galu kwabasi munthu osaganiza komaso wosaganizila ziko kapena amalawi.namiwa continue tili pa mbuyo pano tichela ziko lanthu
Namiwa ndi deal, keep it up
Asilikali,nanuso mukuopa Tanzania?
Much respect Mr Namiwa 🙏
Namiwa timakuyamikani kwambili..mcp ichoke pa 16 Sept 2024
Nuff respect!....chakwera can not sell the lake ndikuchindila ndalama zonse mahule ndi achina chimwendo kunkuyu ndi zikhale kamajekete...osaiwala hule nanse mbeto
Za nyanja yokhayi asayelekeze ndiyathu amalawi. We will die for it
Alomwe awa they want muthalika mu longwe nzawo agalu
galu ndiweyo nose ndi chakwera fiti lnu
Big up Namiwa mumatiyimilila
Nyanja imeneyo lazaro adzabweza ndalamazo...
Hei, Malawi is just a grain of sand full in a wheelbarrow..we aren't even counted worldwide... Check, all presidents except Her Excellency Joyce Banda and Kamuzu Banda,have had fuel crisis shortages of fuel supply..We see no angels here apart from the exceptional two.... Was it not Bingu who said, *Kagoneni pa mseu ngati galimoto sizikupondani* Is this a lie? Or he sounded Eddie Murphy?... Lake Malawi issue: Tanzania Government cannot just change boundary.. Neither Malawi nor TZ can just wake up and draw new boundaries... Country boundaries were a colonial baby, not a single African country drew its boundaries...Go back to Archieves in Zomba and check boundaries as demarcated by colonialists... Northern Malawi border was an agreement for reasons discussed between the British and Germans...Mbeya was part of Nyasaland (Malawi) while North east of Lake Nyasa(Malawi)..belonged to Tanganyika(Tz) The British and Germans settled for a swap... The British released Mbeya to the Germans,(Tanganyika), likewise the Germans released North East of Lake Nyasa (Malawi)to the British... What you must know is that no single country can just wake up and make new boundary without international consultation... it's not an easy process...I see no reason why politicians and some NGOs are shaking knees for nothing.. Those who made such boundaries, the British and Germans governments must negotiate it on a round table..If Tz wants North East of Lake Malawi,then Tz must secede Mbeya City back to Malawi as was the agreement between the British and Germans... International Law on Common Waters was born after this agreement.. They give us back Mbeya City and be part of Common Waters..No such a thing will work until Tz gives back Mbeya City to Malawi... unedited text...
Thanks boss, ndalimbako mtima
Sure
Ngati anatseka admark zogulitsa nyanja tisakaikire tilindi gwape wa president oti mmutu mwake mulibemo kanthu
This chakwera regime is not chifuniro cha Mulungu yes,
Chakwera wamaliza dziko lathu zed Nyanja yapita bas
MCP is a cased party. Any one who joins MCP, no matter how blessed he or she is but will be cased as well. You must pray and watch Which party to join.
👊✊💪🏿💪🏿
Ngati malire amavuta a Munda mzere umodzi mpaka zikwanje nde mukanene dziko we have defence force and their major responsibility is to defend the territory akuchedwa pati let them go their anyamata a mmadzi akateteze nyanja go
Namiwa and his team are just more than Chilembwetu pena
Zamphavu 🔥
Bwerela zokhazokha, palibe cha nzeru chimwe ndatolapo
Muchira simunati muzingomwa mwandondomeko
Anthu akufa kumeneko sasilamu okha ena ndi achi khilisitu
Timakusapotani a Namiwa, Komano history ya Palestine anena awo a supporter a Hamas wo ndi yabodza. Mwina sakudziwa.
Mawu......Mawu.....!
Uyu atule pansi udindo wa HRDC sakukwana wangokhala odzazidwa ndiukali koma mulibe utsogoleri pasankhidwe wina basi
Namiwa Big man ❤
Abiti mumakwana landlani maluwa anu (achakwela asatibwezelese m'mbuyo)
Koma uyo Asabuni, be careful with that guy.
That's the point icc ukufunika ndithu
Free Palestine chakwera anavotela Israel Kuti izipha ana Ku Palestine mapwala ake chakwera panyapakepo ndintu 😢😢
Akristu ena ndiwozitsata eeee 😂😂😂😂
Kristy nsilam tosefe ndi amozi palibe kusiyana apa km chigawenga ichi mumati chakwela azafa ifa yowawa kwambili
@NdaonaMsowoya 😂😂😂😂😂adzafa ngati chitete chofela pa tsekela
Keep it up good work 😇 Namiwa no peace for the wicked chikangawa akapuma kumwamba 😅
Sulute CDEDI💪
Bravo CDEDI
2025 CDEDI yoyeeeee yanyanjayi tikhalitsepo
Zanyanja aprezident a Tanzania ndi wankazi mkutheka amadziwana mwanseli ndi chifukwa akusowa poyakhulala.
Wachiwiri kurankhurawe mmmmm ndakupatsa ulemu .uli ndimfundo komaso umadziwa kutambasura nkhani.History it's a best teacher
So sad 😢😢
Nthawi ya malemu Kamuzu ankalimbikisa ubale ndi Israel apa awanso akupanga chimodzimodzi chilipo amapindula no doubt about that
Namiwa your the best for me with your comrade
Namiwa umatha
A Mtondo Namiwa
Atule pansi udindo mr chikangawa