MKULU YEMWE WAZIPASA YEKHA MBENDELA YA MALAWI WAPELEKA ZIFUKWA 20 KUTI CHAKWERA ATULE PANSI LERO

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 29 янв 2025

Комментарии • 124

  • @MALAWITRANSFORMATIONUNION
    @MALAWITRANSFORMATIONUNION 7 дней назад +11

    Mahata the real definition of a good leader,,,very intelligent young man...plz mpatseni dzikoli uyu alikonze.

  • @OfesiMakuwalo
    @OfesiMakuwalo 4 дня назад +6

    Uyu ndi mmalawi weniweni osati enawa ndikupanga join ♥️ bas

  • @SamisonLevison-z5p
    @SamisonLevison-z5p 3 дня назад +3

    Chakwera chomwe anapitila ku statehouse ndikudya ndikupita ku chimbuzi basi.

  • @Ruthgomonda
    @Ruthgomonda 4 дня назад +4

    Mmmm sidawone munthu wa intelligent ngat Mr Mahata l like you brother 🙏🙏💪

  • @IrenaMashaba
    @IrenaMashaba 3 дня назад +4

    Very powerful young man..tikusapota

  • @stevenbanda6665
    @stevenbanda6665 3 дня назад +3

    Powerful words bro

  • @BOSTONMALISAWO55
    @BOSTONMALISAWO55 3 дня назад +3

    KODI KU MALAWI UKO TILISO NDI ANTHU NGATI AWA EISH AKUFUNIKA CHITETEZO ENAFE TIKUKUONELA KUNJA KWA ZIKO LA MALAWI.

  • @RuthJopilo
    @RuthJopilo 2 дня назад +1

    Ambuye apitilize kukupatsa mphamvu ndi nfundo zakayankhulidwe.very proud cause of you my brother Mahata❤❤

  • @BOSTONMALISAWO55
    @BOSTONMALISAWO55 3 дня назад +3

    Zoona big god bless you

  • @EdwardGeorgeB
    @EdwardGeorgeB 3 дня назад +2

    Ndikanakonda kumdziwa ameneyu kodi ndiyensa mkukhala Bakili muluzi TV uja ameneyu 😂😂😂alibho kwambiri much love you brother keep it up 👍👍stay blessed on that vision 💪💪🙏

  • @Dainaphiri-v8e
    @Dainaphiri-v8e 7 дней назад +3

    Good point Mr commored mahatma young man more future God will must serve u

  • @Anderson-zx8hi
    @Anderson-zx8hi 4 дня назад +3

    Intelligent man i like you bro

  • @BOSTONMALISAWO55
    @BOSTONMALISAWO55 3 дня назад +2

    Anthu atopa ndi mcp yawaipila moti ndikuona nkhondo yoopsa kumalawi

  • @KastoNoel
    @KastoNoel 4 дня назад +1

    We need people like you mr Mahata for your intelligence God bless you ❤

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 7 дней назад +3

    100% mr. Mahata, Chakwera atule pansi udindo, pitiliza brother nkhani yimeneni. Ma president onse analephela koma Chakwera is worse.

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 10 часов назад

    Strong vision of leadership my brother and that's what exactly Malawians are going through

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 2 дня назад +1

    Iwetu ndiwe nduna wa finance and planning

  • @Rafick-jq8ts
    @Rafick-jq8ts 6 дней назад +2

    This is a leader we want in our country

  • @Alexmaonga-kg5wn
    @Alexmaonga-kg5wn День назад +1

    Live koma 👏👏

  • @AbdulkarimPhiri-q6w
    @AbdulkarimPhiri-q6w 11 часов назад

    He made me focus on his interagency if you won’t change your leadership will be great Mr Mahata

  • @BlessingsPhiri-j4i
    @BlessingsPhiri-j4i 4 дня назад +1

    Very powerful points, you may a good leader, a young man

  • @DaudiHAllie-kk1en
    @DaudiHAllie-kk1en 2 дня назад

    I just dropped some tears with his speech 😢

  • @FrolahChikopa
    @FrolahChikopa 4 дня назад +1

    Oh Jesus please came soon....this one is a good leader

  • @jerryl.chadziwika8527
    @jerryl.chadziwika8527 4 дня назад +1

    Our Traore our Malema, young blood n more future.
    Economic Freedom fighters, fighter n fighters

  • @happymoyo2374
    @happymoyo2374 2 дня назад

    The guy is a God Saint, he is telling us exactly what is needed to be done

  • @franktsoka
    @franktsoka День назад

    We need people like
    U boss

  • @patrickdamalekani9863
    @patrickdamalekani9863 День назад

    Respect brother ❤

  • @HamzyRashidPhiri
    @HamzyRashidPhiri 2 дня назад +1

    Wazeru ngati pulesideti wa ku bokina faso mulungu apatse mpata samzy from zambia tikuvetsera mwachete

  • @KinziWindasoni-h4b
    @KinziWindasoni-h4b 4 дня назад +2

    We are with you bro

  • @khanilapozo-fj5tq
    @khanilapozo-fj5tq 3 дня назад +1

    Ndigawikenkoni nambala ya Bwana Mahata inenso nkhani yanga ndi akuluwa ikufanana ndipo ndikukayimira kudera langa

  • @shongweisaiahmoses01-ro6rk
    @shongweisaiahmoses01-ro6rk 4 дня назад +1

    This one is brilliant IQ no 1

  • @AbubakarAmin-u2g
    @AbubakarAmin-u2g 3 дня назад +1

    Never give up

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio 3 дня назад

    From Mocambique keep it upi like you may God protect u.

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 4 дня назад +1

    My vote for you ❤❤❤❤❤

  • @MikeKalungulu
    @MikeKalungulu День назад

    More 🔥 🔥 fire

  • @MasterMwandira-d3k
    @MasterMwandira-d3k 7 дней назад +2

    Ameneyo ndi J's Malema junior

  • @axtongilbert8048
    @axtongilbert8048 2 дня назад

    Very brilliant

  • @RitaKainga
    @RitaKainga 3 дня назад

    ❤ keep the fire burning bro

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 3 дня назад +1

    Mahata ukhaluse uzapulumusa ziko like trore

  • @ThedMmela-e1g
    @ThedMmela-e1g День назад

    Good I dear ❤️❤️

  • @BigJeff-n7j
    @BigJeff-n7j 11 часов назад

    Zoona brother

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 3 дня назад

    Watching live from SA

  • @FrankKathumba-u4f
    @FrankKathumba-u4f 7 дней назад +2

    This is true

  • @MikeKalungulu
    @MikeKalungulu День назад

    I will support you, tell them!!!!!

  • @FoxCassiem
    @FoxCassiem 4 дня назад

    Respect big brother

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 4 дня назад

    Big man ❤

  • @IbrahimJackson-i8h
    @IbrahimJackson-i8h 6 дней назад +1

    Koma inuyo Amahata i respect 🙏 🫡 👏 👌

  • @nsikoh_mzimela
    @nsikoh_mzimela 2 дня назад

    U will be malawians president one day in the name of Jesus I play for that

  • @dikenzthomo8284
    @dikenzthomo8284 7 дней назад +1

    Zangondikumbutsa za Rastafarian Chikomeni.Kanundu.Tikayandikira zisankho kuchuluka zoliralira.Zina ndi zimenezi

  • @charlesmaseko7118
    @charlesmaseko7118 12 часов назад

    Mahata deserve to be the president of Malawians

  • @GeorgeMakina-j9x
    @GeorgeMakina-j9x 4 дня назад

    Carry on brother God is good one day will rescue us

  • @GearardPhiri
    @GearardPhiri 4 дня назад

    I love it your word

  • @Riah8091
    @Riah8091 4 дня назад

    Powerful man n God bless

  • @FumbulaElia
    @FumbulaElia 4 дня назад

    I like it. Very patriitic

  • @StoneckJali-s3n
    @StoneckJali-s3n 6 дней назад +1

    Too late for tears voting is around the corner

  • @TurnsonKaliza
    @TurnsonKaliza 3 дня назад

    Respect mahata

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 6 дней назад +1

    Uyu ndiyeno kuyangula kopanda manda chakwera achoke kumene 16September sakufunika

  • @MemoryNdhlovu-e4w
    @MemoryNdhlovu-e4w 3 дня назад

    Congratulations to Mr mahata join Dpp party

  • @MphatsoKakole
    @MphatsoKakole 5 дней назад +1

    Good

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 4 дня назад +1

    Mwana wanzeru

  • @user-ep6wv3pj2c
    @user-ep6wv3pj2c 6 дней назад

    Listening attentively

  • @KinziWindasoni-h4b
    @KinziWindasoni-h4b 4 дня назад

    Intelligent man

  • @francisbilly2226
    @francisbilly2226 4 дня назад

    Mahata ✌️✌️

  • @Mordecai-c1e
    @Mordecai-c1e 6 дней назад

    Keep it up 🎉🎉🎉🎉I

  • @AlexNganya
    @AlexNganya 3 дня назад

  • @Idah-m9p
    @Idah-m9p 3 дня назад

    God is good aona potiika

  • @MikeKalungulu
    @MikeKalungulu День назад

    May you quickly go to state house now to be a president plz

  • @disolamalawi
    @disolamalawi 6 дней назад

    Powerful

  • @JohannaPretoruis
    @JohannaPretoruis 4 дня назад

    Exactly

  • @TroubleMuthala
    @TroubleMuthala 4 дня назад

    My ☑️

  • @Arthur-oc7ri
    @Arthur-oc7ri 4 дня назад

    The man is intelligent

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 6 дней назад

    My vote for you

  • @RodrickSmart
    @RodrickSmart 7 дней назад

    We have genius in this country

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 4 дня назад

    Achakwera please handover the position of president to Denis ❤❤❤❤

  • @thulambale2836
    @thulambale2836 7 дней назад +2

    I support this guy

  • @GiftFrancesco
    @GiftFrancesco 6 дней назад +1

    Nthaw yoyesa chipan Cho new inatha

  • @CourageBanda-d1g
    @CourageBanda-d1g 4 дня назад

    ❤❤❤

  • @TroubleMuthala
    @TroubleMuthala 4 дня назад

    👏👏👏👏👏👏👏👏👏👏👏👏

  • @KizzFrank-g1v
    @KizzFrank-g1v 3 дня назад

    Mr mahata tilikumboyo kwanu

  • @jamestembo6724
    @jamestembo6724 7 дней назад +1

    Katundu waziko

  • @IsaacSombani-b8v
    @IsaacSombani-b8v 3 дня назад

    I think Mr Muthalika atamutenga uyu zithandidza hvy

  • @HarryMsudzula
    @HarryMsudzula 4 дня назад

    Mahata/Kabambe FT Mr Tobias guys Malawi unoyo muli hope kuti tizachita bwino koma vuto amalawi timavotera mu thu chifukwa chotchuka kapena kuti ndiwamtundu wanga

  • @Mikekadewere-c6c
    @Mikekadewere-c6c 3 дня назад

    ndkuona kuti munthu ameyi akuziwa zambiri zamoyo uno chimene ndziwa ndichoti Mulungu akudalisen kwambiri chifukwa chimene ndichisisi choopsa kwambiri ndipo ndichamphavu kuziko lapasi

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 4 дня назад

    Mafumunso nde anyanya chikangawa akayitana angothamanga kukatenga 2000, mafumu ombwambwana. Pamene anthu awo akumzumzika ndicifukwa ine ndinawuza amfumu anga kuti kobili dzidyani ine voti yanga APM .

  • @IshmaelWhite-s9w
    @IshmaelWhite-s9w 2 дня назад

    Wachedwa zomuvotela coz it will take time kt anthu azamuziwe a joine Ku dpp nthwi ndiyomweyi akhoza kuzasitha dzikoli

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 4 дня назад

    Patseni dziko nyamatayo Mahata
    Alikhoze mwina tione dzina

  • @RabeccaMkandawire-i9j
    @RabeccaMkandawire-i9j День назад

    SKC 2

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 4 дня назад

    1 _ Tikaopa kuyankhula chifukwa choopa kumangidwa , MALAWI Will be finished by mcp .
    2 _ Tisakhale mugulu la anthu ombwambwana omwe amati boma ndilomweli , chifukwa izo zinabadwa zili kale zitsilu .

  • @MasterMwandira-d3k
    @MasterMwandira-d3k 7 дней назад

    Kapena tingati Malema waku Malawi

  • @GivesonBanda
    @GivesonBanda 7 дней назад

    Ndimanena tu mobweleza kuti ku malawi kuli azisogoleli abwino omwe angapindulile malawi ziko lathu muthuyi zomwe akunena apapazi ndi zowona zokhazokha

  • @FortyoneHarwa
    @FortyoneHarwa 6 дней назад

    Dennis mahata iwe ndiwe dolo umandisangalatsa uli ndi voti yanga umati imilira ifeyo amalawi

  • @MikeMtunduwatha
    @MikeMtunduwatha 3 дня назад

    Zoona zake mfundoizi zilibwino kwambili

  • @PatrickKapendo
    @PatrickKapendo 6 дней назад

    Mahata let us go to vote is only way we can use to change the ruling part not comand like this very soon tivota

  • @CharlieChirwa
    @CharlieChirwa 7 дней назад

    Ineso ndili momo

  • @YahyaIsmail-b8o
    @YahyaIsmail-b8o 3 дня назад

    Mahata lowa pa ground tili pambuyo pako basi

  • @ElizaKanyama-fq8jy
    @ElizaKanyama-fq8jy 5 дней назад

    Manyaka ndi iwe yo ,chulungamo chimaveka ngati mwanatu chikanga wa watikwana iyaaaa achoke kumene ameneyu

  • @MarthaMalola
    @MarthaMalola 4 дня назад

    Kachilungamo bola mukaziwatione. Tione zina bas

  • @EvansEgra
    @EvansEgra 5 дней назад

    Wasuta chamba uyo? Kumalawiko anthu amangoti akakhuta kulankhula ngati anzeru, Koma akungofuna cholowa basi, waona nthaw ino yadzisankho.

  • @WisikiFainolo
    @WisikiFainolo 7 дней назад

    Ukamati sakuopa kumangidwa ndekuti chani kodi ulimbali iti iwe siunganve chisoni ndimmene lilili dzikoli achoke kumene mulungu alowelele kuchosa satana ameneyu

  • @GenialaChalera
    @GenialaChalera 4 дня назад

    Mesa muti chakwera ndi munthu woti sawina bwanji osangosiya kuyankhulako mudikire kuti aluze zitsiru ndinu zadziwika kuti mukumuwopa