A MICHAEL USI KUYANKHULA PAMASO PA PRESIDENT -27 March 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 26 мар 2024

Комментарии • 209

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt 3 месяца назад +3

    Mr president how many advisor do you have? Is it a speech to tell malawians? That is speechless, am not against with you but as president mumayenera kukhala ndi fundo zogwilika, zopasa chiyembekezo koma mmmmmmm tidabesa amalawi koma Mulungu atichitira chifundo

  • @frasermoyo8999
    @frasermoyo8999 3 месяца назад +2

    Mr president,,,,you're responsible to bring the solutions,,,,not asking us the way forward,,,,just command what suppose to be done,,,,adzikupisani mr ussi,,,fundo

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o 3 месяца назад +2

    SKC my vote

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b 3 месяца назад +8

    Usi zinazo wangoyankhulira ntchito koma mwainu mulibe sogolo labwino kuposa kuba kupha ndikuononga

  • @user-cv3zw9ic6d
    @user-cv3zw9ic6d 3 месяца назад +1

    Kkkkkk inu kodi ndindani mukamakhala mumati ndini ndani Eliya wabwera Abushiri alipano mukawauze Ambuyanu kuti Eliya wabwera mukamalira Achilima ali apo Achakwera ali apo dziwani kuti aEliya wabwera amanena ndani Bushiri kapena ndani mManganya sazatheka

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 3 месяца назад +3

    Ise tikufuna anyamata president ngati Senegal chilima bomaa

  • @user-jk8sh7fh2d
    @user-jk8sh7fh2d 3 месяца назад +11

    Andale inu muziyamika chifukwa kuno ndi ku malawi, koma kunakakhala kuti ndi ziko la mkhongo ine ndinakakhala mmgulu lopanga upo okuphani for sure inu nonse ndi mbeu yoipa kwambili.

  • @user-fv3mb2qm7n
    @user-fv3mb2qm7n 3 месяца назад +1

    Chilungamo, kuvotela (Ras Chikomeni Chirwa) munthu wapadela, amene ali ndi mfundo zothandiza dziko la Malawi, Dpp, Utm,Mcp Udf, no more we need new leadership.

  • @patricgama4788
    @patricgama4788 3 месяца назад +4

    My vote is for apm

  • @christophergibson72
    @christophergibson72 3 месяца назад +1

    Chakwera my vote. Osati opanda Mano mkamwa uja ngati wadya chimanga chotentha

  • @user-jn2oc3cn3q
    @user-jn2oc3cn3q 3 месяца назад +3

    Fundo zapa maliro 2% zandare 89%

  • @issahkagansamussah
    @issahkagansamussah 3 месяца назад +3

    Amalawi munansanga wolakwika mbambadi course wochakwela wolibe mfundo nthawi zonse amakalila mawu amodzi please next time we need be very careful pangani yonsanga upule chifukwa ntchito iyi sintchito yamasewela ayi yy😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @emmanuelchavula7144
    @emmanuelchavula7144 3 месяца назад +2

    😂😂😂 utm is not a small. Party it has brilliant brains 😊

  • @isaacchagwa2917
    @isaacchagwa2917 3 месяца назад +1

    Wise saying Dr Utsi we really need to pray for our leaders as good citizens and that has promises attached before God.

  • @SamuelMakalani
    @SamuelMakalani 3 месяца назад +1

    Apm my vote

  • @KnowxySainet
    @KnowxySainet 3 месяца назад +1

    Bwanji Vice president bcz phindu asamayendenawo sindikuona

  • @AlexisKantondo
    @AlexisKantondo 3 месяца назад +3

    Powerful message

  • @user-ip4kz3jo8y
    @user-ip4kz3jo8y 2 месяца назад

    Powerful massage

  • @jackwilfrednyangazi2756
    @jackwilfrednyangazi2756 3 месяца назад +1

    Very few of us know who Eliya is

  • @PatrishaHamish
    @PatrishaHamish 20 дней назад +1

    Mr utsi anatumidwadi ndi mzimu anthuwa tikanawaika mmapemphero pazomwe zachitikazi

  • @lukempata3086
    @lukempata3086 2 месяца назад +1

    Wakumva wamva osamva sanamve zomwe wanena Manganya

  • @LenardWillard-nu6fr
    @LenardWillard-nu6fr 3 месяца назад +1

    Mr Michael usi amatha heavy

  • @TimothyKwangu
    @TimothyKwangu 2 месяца назад

    Great speaker

  • @DitebogoMarutle-wy8qo
    @DitebogoMarutle-wy8qo 3 месяца назад +4

    Mmmmm koma pa chakwela nde tidabetsa basi kuchitakusowa ndi mfundozomwe iiiiii amalawi basi tilibe chiyembekezo? Chakwela ndi panja pa munthu😢😢😢😢😢💔💔💔💔💔

    • @OwenNyangu-nv1yt
      @OwenNyangu-nv1yt 3 месяца назад

      Inu munthalika mumavapo fundo zanji? Bodzalokhalokha basi

  • @charitylyson7350
    @charitylyson7350 3 месяца назад +1

    Anthu aku Mulanje angopitilako kut akakuziweni palibe vote ya Chakwera pa anthu onsewo😂😂😂

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 3 месяца назад +5

    I can't waste my time honestly,I have important burning issues to pray for, don't provoke me please 😠😠

  • @chisomotolani1186
    @chisomotolani1186 3 месяца назад +1

    Usi zining'a mumachulutsa sometimes kungoyankhula straight forward ndibwino, Ena akuwomba mmanja koma sanamve zomwe mwatanthauza pazomwe mwayankhula, #eliya wabwela

  • @user-hx9mg6ei1t
    @user-hx9mg6ei1t 3 месяца назад +6

    Ndalezo zikufunako chani kumaliroko

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e 3 месяца назад +2

    Ukupanga zosankhana mitundu ndi iweyo Chakwela ma udindobonse azibalewawo ndi ana ako

  • @MaganizoSalima
    @MaganizoSalima 2 месяца назад +1

    Tidziyankhula zinthu ndikuzichitq

  • @user-ue8eb9hj6s
    @user-ue8eb9hj6s 3 месяца назад +1

    Anthu tizikupemphelelan kt mupange cha, takupemphelelan 4years tapindula chan kwainu

  • @user-lz5tl7gn4v
    @user-lz5tl7gn4v 3 месяца назад +1

    Zachamba eti Kodi odzutsa president samakhala vice mesa

  • @JamesAjibu-ff6rf
    @JamesAjibu-ff6rf 3 месяца назад

  • @samuelbrian3409
    @samuelbrian3409 3 месяца назад +1

    See you next year September guys, you really fooling down any time

  • @AsinasLiomba
    @AsinasLiomba 16 дней назад

    Cyclone politics ija yachitikatu tsopano. Kd chakwera ndani?? Ulemu wanu a USI

  • @MathewsMANDUTU-lh6oo
    @MathewsMANDUTU-lh6oo 3 месяца назад +2

    Palibe chomwe tapidula ife ndi chakwera bola Apm

  • @Jermah51kennias
    @Jermah51kennias 3 месяца назад

    A usi koma muli ndi ku mudzi inu,? Ngat mulinako mmapita koma? Mwayankhula ngat mukukhala kunja kwa dziko linotu, kuyankhula kot akuchemeleleni mabwana anuwo zomwe zili zaziiiiiiii ndizotipsetsa ife mitima

  • @owenmoses9434
    @owenmoses9434 3 месяца назад

    APM my vote

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 3 месяца назад

    2 let for mama.2025,kuba mukubaku uku,mudzabvala,ma silipasi okutha.amalawi,alipopaja.

  • @user-ol1hf7ru1v
    @user-ol1hf7ru1v 18 дней назад

    Kupempherera kt asagwidwe pa mulandu wakupha😢😢😢

  • @jabulilemngomezulu3243
    @jabulilemngomezulu3243 3 месяца назад +1

    Ndale ndi kumaliro komwe kma chakwela ndi otsekesa kwambili

  • @DavieZimba-hr4vs
    @DavieZimba-hr4vs 2 месяца назад

    Thus very true

  • @homeremedys3748
    @homeremedys3748 3 месяца назад +1

    Mbomba lija anakonzekela mademo akalindo

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 3 месяца назад +2

    Chakwela mbava

  • @noahtsamdoka1172
    @noahtsamdoka1172 3 месяца назад

    Abanja limodzi kodi ena mkudya ena akugona njala‼️‼️ ife ndima opharn bax 😳😳

  • @AustinPanja
    @AustinPanja 3 месяца назад +1

    Kwatsara pan'gono kucha

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 3 месяца назад

    Oooooooh my bando yawonongeka pazadzi koma galuyu

  • @user-go1eh4fq3i
    @user-go1eh4fq3i 3 месяца назад

    Komatu anthu Inu panachitikila Freddy paja mukabwere lero,manyazi mulibe

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 3 месяца назад

    Funso labwino kwambiri, Chakwera Ndi ndani?yankho, Chakwera Ndi mbava 💯 10:42

  • @user-qx3dd7xt9c
    @user-qx3dd7xt9c 3 месяца назад

    Apm team we are

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 3 месяца назад +2

    Apa sindinanvepo fundo yeni yeni, chakwera alibe nfundo, ndipo sakukwana pa u President ayi. Za ziiiiiiiii! Bola michael Usi.

    • @FOSTERLUPIYA-zc1xv
      @FOSTERLUPIYA-zc1xv 3 месяца назад

      Osakonda mtendere akunenedwayo ndi Inuyo.Adzwinansotu a Chakwera.

  • @amaleeehmuzik-official
    @amaleeehmuzik-official 2 месяца назад

    This country we have start war 😢 guyz amene mwakozekha bweran ku Dm tayamba group yomwe tingayambitse force acting komaso u'll get salaries b4 kulowa nchire

  • @user-ud9wl8yg1t
    @user-ud9wl8yg1t 3 месяца назад

    Mapephelo ndiwofunika koma ukusokoneza zithu ndi iweyo kusakhana mitundu ndiweyo mwangozazana palipose achigawo cha phakati nokha nokha uziwona thawi ikubwela

  • @user-eh1gn1nj9d
    @user-eh1gn1nj9d 3 месяца назад +2

    Malawi dziko lomvesa chisoni always doing politics very shameful

  • @WadalitsoChinguwo
    @WadalitsoChinguwo 3 месяца назад

    Mbambande Mr usi

  • @AustinChiyembekezo-cx4mz
    @AustinChiyembekezo-cx4mz 3 месяца назад +1

    Bwana chilima mukukalambatu

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b 3 месяца назад

    Muzizipemphelela nokha ndani amene angamataye nthawi yake ya padela ndikumapanga za inuo ngakhale iweo usi fodya bas uzipemphelele wekha wamva iwe za ugalu basi

  • @user-xv5pr3ji6w
    @user-xv5pr3ji6w 3 месяца назад

    Izi nde za ziiii

  • @user-id1oo9hl5x
    @user-id1oo9hl5x 2 месяца назад +3

    Keep the fire burning Mr Usi❤

  • @mphatsojuliostandy4918
    @mphatsojuliostandy4918 3 месяца назад +2

    Mbuzi za anthu

  • @josephkalulu4320
    @josephkalulu4320 2 месяца назад

    Za ziiiii

  • @user-mw6zl2dt5t
    @user-mw6zl2dt5t 2 месяца назад

    Usi zining'a zakozo uzatipweteketsa nazo....nfundo zabwino koma kuzikoletsakoletsa...ma drama paliponse kodi....kumakhala serious koma

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b 3 месяца назад

    Tilibe nthawi yowapemphelera achilima ndi chakwera masataniki nkhati amenewo

  • @JohnKanjete
    @JohnKanjete 3 месяца назад

    😂😂😂 Komatu akulu awa amayankhula mwachidule😂

  • @user-pw1kl3vo5d
    @user-pw1kl3vo5d 3 месяца назад

    Pemphelo, loti lipite kuti kwayani lipite kwasatana lazalas ndi nkazake chilima

  • @AlbertDuke-of9nn
    @AlbertDuke-of9nn 3 месяца назад +3

    chakwera ine sindingamupepherere😢

  • @HopeNandola-ew8td
    @HopeNandola-ew8td 3 месяца назад

    Akupasa chani

  • @WonderfulSalifu
    @WonderfulSalifu 2 месяца назад

    Kkkkk watera ndege pompano kkkkk ndie kt chan?

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 3 месяца назад

    Watipha Lazaro,wawononga dziko

  • @Abdul-xk8dq
    @Abdul-xk8dq 3 месяца назад

    Azapenphelela ndani awusi zaziiii

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 3 месяца назад

    Usi ndi team yako yonse ya tonse alliance simukuziwa chomwe mukunena, munataya pangano posachita zomwe munalonjeza God will punish you. Iwe Usi uzikanyadira kuthandizidwa zoona pomwe inu mungoba ndalama xa misonkho??? Shame on you tonse alliance.

  • @user-dn5sf3md5t
    @user-dn5sf3md5t 3 месяца назад

    Ndiye kusowazochita kukhala bize kupempherera chakwera aaaaaaa kusowantchito ? Chani

  • @user-bi6pb5gc8t
    @user-bi6pb5gc8t 3 месяца назад +1

    Uyu sichilima iyi ndindondocha yachilima chifukwa chilima amene timamudziwa Kuti amalankhula ichi ndichikwangwani nchifukwa sichikulankhula chilichonse

  • @user-nr7st1ox7y
    @user-nr7st1ox7y 3 месяца назад

    😮😮

  • @user-dh4io2cb2b
    @user-dh4io2cb2b 3 месяца назад

    Chifukwa unadana ndi bon kalindo ulibe mfundo ine ndimaona Ngati Uli ndi mzerutu

  • @LuckyBiyere
    @LuckyBiyere Месяц назад

    Takambaniko zazeru akulu 15:11

  • @MaliGomani
    @MaliGomani 3 месяца назад

    😂😂😂 Koma malawi ife tizipephelera achuma mmalo motipephera anthu osaukafe

  • @africanmusichits265
    @africanmusichits265 3 месяца назад

    Michael Usi ndi katundu samaopa 😅

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h 3 месяца назад

    Kkkkkk a usi tidaikatu chikhulupilirotu mwainu koma aaaasa madzi a mphutsi

  • @AshlafHakimi
    @AshlafHakimi 13 дней назад

    Chakwela ankaganiza zawembu

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 3 месяца назад

    Kkkkkkk koma dziko ndi anthu akhe

  • @user-vx5vk5ss6k
    @user-vx5vk5ss6k 3 месяца назад

    For what Mbuzi ngati zimenezi

  • @SungeniNgombero
    @SungeniNgombero 3 месяца назад

    Mr president 😂😂 tandipasani dzina la amene wakulembeni speech😢

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 3 месяца назад

    Ndipo m’mutu mwachakwera mulidi mphuzi anabwerellanji 😢

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e 3 месяца назад

    Michel usi umatha mwachinsisi kkkk zimenezo ndiye ndale

  • @user-vo7cb4cv5d
    @user-vo7cb4cv5d 3 месяца назад

    Ine mau ambiri ndilibe always mau ambiri ndilibe kkkk

  • @user-nx7yz4qo8f
    @user-nx7yz4qo8f 3 месяца назад

    Mapephero achani kod? Osamasewera ndi Mulungu anthu àmbiri akuvutika

  • @Daneck-rm1gg
    @Daneck-rm1gg 3 месяца назад

    13:49 kuyankhula KWA nzelu michale usi

  • @user-cb2cv9fz7m
    @user-cb2cv9fz7m 3 месяца назад

    Bodza ili usi bwanji samuuze chilima monga Vice President Kut adzutse chakwera zazi

  • @KassimmwSteven-og8ny
    @KassimmwSteven-og8ny 3 месяца назад

    Iwe Siwa yamba NDI iwe zosakhanazo buzi

  • @AlexZambia-hq2jk
    @AlexZambia-hq2jk 3 месяца назад

    Anthu oipa awa kobasi amatitenga ngati chitosi

  • @violetmahachi7673
    @violetmahachi7673 3 месяца назад

    Kuona mtima muyambe inu achakwera chifukwa kuyakhura mumatha koma ndiinu munthu ovensa chisoni kwa mbiri

  • @user-rr8kq2dc9j
    @user-rr8kq2dc9j 2 месяца назад

    Iweyo ndipambali penipen

  • @MwawiMinga
    @MwawiMinga 2 месяца назад

    Usi ndimwana wanzeru

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx Месяц назад

    Usi amakwana kuyankhula mopanda mantha

  • @Mbwanaayami-hp3xk
    @Mbwanaayami-hp3xk 3 месяца назад

    Choka iwe galu

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w 3 месяца назад

    Chakwera amaziopa nduna zozisankhira okha .olo zitachita zinthu zoononga amangokhala chete kuziopa

  • @user-yu9pn8ux1k
    @user-yu9pn8ux1k 3 месяца назад

    Chakwela amaganizanso ngati Mbuzi kwabasi

  • @brightkaunda920
    @brightkaunda920 3 месяца назад

    Kodi mesa odzutsa president akanakhala achilima?

  • @mphatsomonjeza4371
    @mphatsomonjeza4371 3 месяца назад

    Zaziiii okufa nkudzuka yekha ndi amene angamvere za Chakwera ndi Chilima you take Malawians like their dom? not again guys enough is enough to mr Chakwera end Chilima