BON KALINDO KWAUZA DR CHAKWELA LERO PA 2 August 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 20 окт 2024

Комментарии • 81

  • @JafaliAjusa-zg2xi
    @JafaliAjusa-zg2xi 2 месяца назад

    Powerful message Mr bon kalindo,mukugwila ncthito pomwe ma advicer a president angodya ndalama zamphawi osathandiza president

  • @HorrisMbendera
    @HorrisMbendera 2 месяца назад

    More 🔥🔥🔥🔥🔥 my president❤❤❤❤❤❤

  • @PeterChombo-f5r
    @PeterChombo-f5r 2 месяца назад +1

    Powerful speech freedom fighter born kalindo

  • @SaudhaKatete
    @SaudhaKatete 2 месяца назад +4

    Power full speach Mr bon kalindo. More fire

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 месяца назад +3

    Mr dcccccc. Muka wona fumu ikusiya kukapepe maliro kunyumba ya maliro ndikukapepesa malo olakwika muziwe mafumu kumeneko akupezako chuma. Akuziwa kuti kwa marry chilima sakabwerako ndi makobiri.ndichifukwa amapota kumene ndalama sizivuta kuzipeza. Anthu asiya mawu a Mulungu woti munthu adzadya thukuta lake pano aliyese akufuna kudya thukuta lazake. Anthu ena akulemerera ngati wina wagweredwa mavuto ndipamene amapeza mupata wodyerapo. N

  • @MatthewsJohn-kv8fj
    @MatthewsJohn-kv8fj 2 месяца назад

    President wathu ife osauka ❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @KhalideNerve-mu1eq
    @KhalideNerve-mu1eq 2 месяца назад +1

    Ndipo true aziona sanati😂
    And what l believe its that soon apita komwe watsogoza azake kuja trust and Mark my words 💔

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 месяца назад

    ✊💪✊ our president ❤❤ we waiting for demonstration bwan

  • @VictorChimbuvu
    @VictorChimbuvu 2 месяца назад

    Kalindo the great

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 2 месяца назад

    Our KING

  • @JafaliChiwimbi
    @JafaliChiwimbi 2 месяца назад +2

    Mr boooon kalindo mumatiyimilila kwambili ife tili pambuyo panu❤️❤️💪💪💪💪💪

  • @StywellMunthari-hd4ul
    @StywellMunthari-hd4ul 2 месяца назад

    Tilinanu pamoz bwana 💪💪

  • @OmarManjawira-up3ns
    @OmarManjawira-up3ns 2 месяца назад +1

    The DC, imfa ndiyowawa straight up and sakuyenera kupanga zibwana pa issue imeneyo 😢

  • @lyiemax
    @lyiemax 2 месяца назад

    That's our president speaking on our behalf ❤❤❤

  • @Bosschangaputwa
    @Bosschangaputwa 2 месяца назад

    Bon is the best before❤

  • @LukaAron-el5qh
    @LukaAron-el5qh 2 месяца назад +3

    Koma amalawi tiyeni tidzuke chifukwa chiyani maliro akwina kukapepesa maliro kwina zinayamba zitachitikapo zoterozo,komaso iyeyo akubisa report chifukwa chiyani amalawi akuyenela kudziwa za report

  • @ArnoldThomson-d6v
    @ArnoldThomson-d6v 2 месяца назад

    Komatu tikufuna report, lakuchikangawa

  • @ZIINGZANGFOSSALLISAHMUSTAPHER
    @ZIINGZANGFOSSALLISAHMUSTAPHER 2 месяца назад +1

    ❤❤❤❤❤❤ give it 🔥 🔥 🔥

  • @kelvindickson
    @kelvindickson 2 месяца назад

    This is time of ng'alulaizeshoni

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela 2 месяца назад

    Inu ndi bwana bon kalindo

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 месяца назад

    Kalindo is a lady? Very talkative

  • @MEGANABIGAILMNTHALI
    @MEGANABIGAILMNTHALI 2 месяца назад

    Our Hero Mr born kalindo mumatiimila ife timakukondani

  • @FillanyaudaNyauda
    @FillanyaudaNyauda 2 месяца назад

    ❤ I love you too ❤️

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef 2 месяца назад

    More 🔥🔥🔥 the DC

  • @DENSONZULU
    @DENSONZULU 2 месяца назад +3

    Bwana bon kalindo

  • @GeoffreyMaulana-rh5rx
    @GeoffreyMaulana-rh5rx 2 месяца назад

    We love you mr Bon kalindo❤❤❤

  • @isaacmsumba127
    @isaacmsumba127 2 месяца назад

    First person to view

  • @TiyamikeMakande
    @TiyamikeMakande 2 месяца назад

    Tiyankhulireni bwana❤ azimai amasiye sakutipatsa ndrama za.malemu ku Capital hill pano zaka zitatu tikungovutika ndi ana bambo awo anamwalira kalekale koma ndrama zikukanika kutuluka ma demo asalepheleke

    • @MoosaChirwa
      @MoosaChirwa 2 месяца назад

      Sorry ukapitaso Pena amatha kukuuza Kuti utigailako zingati Kuti zituluke changu ndalama zimenezo

  • @BwanaliSayilence
    @BwanaliSayilence 2 месяца назад

    Kuswakuswa chilungamo

  • @anthonynkhoma4265
    @anthonynkhoma4265 2 месяца назад

    Kalindo chindere chakufikapo

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pg 2 месяца назад

    We love you kalindoooooooooooooo!!!!!!!!!

  • @RafickChiwangulinda
    @RafickChiwangulinda 2 месяца назад

    We love you brother born kalindo

  • @OffsetimranWyson
    @OffsetimranWyson 2 месяца назад

    The DC ndi no 1

  • @MahommedIsaacBwawa
    @MahommedIsaacBwawa 2 месяца назад

    Umakwana DC

  • @MosesFanuel-k3u
    @MosesFanuel-k3u 2 месяца назад

    Go ahead the DC.

  • @IshmaelJamesChimera
    @IshmaelJamesChimera 2 месяца назад

    The DC God bless you

  • @AiameAdamo-su1nt
    @AiameAdamo-su1nt 2 месяца назад

    Atukwanidwa zenizeni a dr Chikangawa aziona.

  • @elizaBernado
    @elizaBernado 2 месяца назад +2

    booooooooooooonnnnnnnnnnnn kalindo

  • @VictoriaSibande
    @VictoriaSibande 2 месяца назад

    Ku Malawi kulibe chifunga choti chingagwetse NDEGE, maiko ena ndege zimayenda muchifunga osati ngati wathu kuno komaso ndege zimatha kuyenda ndi chifunga koma usiku ndiye Boma lingopeleka chifukwa chenicheni basi osati kumatinamiza ngati akunamiza ana
    Zikomo Bon Kalindo chifukwa cha message yamphavu

  • @yusufbakali
    @yusufbakali 2 месяца назад

    Chakwela must park and go

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 2 месяца назад +1

    sangatuluse lipoti chigawenga chinapha a chilima ndichomwecho chakwera

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 2 месяца назад

    More fire 🔥 Booooon kalindoooo

  • @mdokayusuf4390
    @mdokayusuf4390 2 месяца назад

    Koma pa pension po ndiye mwalasa a DC komaso Pali za P9 ku MRA sakupeleka chiloweleni achakwera mu 2020 mpaka pano.

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 2 месяца назад

    Ndipo akanakhala President wa mzeru pofuna kupewa Kuti anthu asamamunene Mr Chikangawa anayenera kuchosa Cabinet yonse imene ikumupasa maganizo opepera . Koma ngati akuyisungabe Cabinet yake yokubayo ndiye kuti Mr Lazarus Macathy Chikangawa ndi Mtsogoleri wa nyansi zonse zikuchitika Mmalawi.
    You are evil Mr Chakwera and your Cabinet.

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba 2 месяца назад

    Ife alend athu azasamusidwa muzaapasa nyumba ku bomako

  • @EdwinKachepa
    @EdwinKachepa 2 месяца назад

    💪💪🔥🔥

  • @FelixChikaondagama
    @FelixChikaondagama 2 месяца назад

    Zikomo the DC mene zililimu mafuso atha taziwa kuti anachita kukoza simukuona panopa akuvala ma black titedi kkkk eti amachita manyazi

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 2 месяца назад

    Vumbwe wa munthu chakwera, munthu ungabise report something is wrong apule 😮

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 2 месяца назад

    Tikufuna Mademo asalephereke please,, Chakwera akulephera kuwauza a Malawi report la Ngozi ya Ndege, ndipo zikuonetsa kuti akudziwapo kanthu za imfa ya anthu 9 aja.

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 2 месяца назад

    Power full speach chakwera sakuganizira anthu amalawi tikuvutika ndiye ndiye aziti munthu WA reti azipereka misokho ndarama zomwe mukungo mwaza mumisika ndi mumisokhano zachepa ase

  • @malianeantonio
    @malianeantonio 2 месяца назад

    😢😢

  • @mbonilekisebe2286
    @mbonilekisebe2286 2 месяца назад

    Munthu ngati sunalakwe, if you are innocent sungadandaule but when you're guilty nde umapupulumadi ndi kumakwiya.anthu akamayankhula kuti wagwetsa ndenge. God will surely punish him

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 2 месяца назад

    Olo atuluse report anapha vice wake munthu denge kusowa 10 o'clock kukayamba akufuna munthu 5 o'clock zoona

  • @TiyamikeMakande
    @TiyamikeMakande 2 месяца назад

    Koma nde afiti afiti eeeeee chonena ndilibe

  • @TroubleKatsala-jp2li
    @TroubleKatsala-jp2li 2 месяца назад

    Anyozedwaditu sanati ndipo aziona

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hi 2 месяца назад

    The DDDDDDDDDCCCCCCCCCCCC bon kalindo 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼

  • @HarryMakwale
    @HarryMakwale 2 месяца назад

    Moto kuti ❤❤❤❤

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 месяца назад

    Mbiri yamuipila amene uja

  • @StainKapitao
    @StainKapitao 2 месяца назад

    Hahaha umatha the Dc

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 2 месяца назад

    Mafumu wo akumapita kukapepesa maliro kapena kukalandira ndalama???

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 месяца назад

    Kuchema

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember 2 месяца назад

    😂😂😂😂😂😂second person to view

  • @samueldickson3575
    @samueldickson3575 2 месяца назад

    Ng,alulalaizetion

  • @Japlennthondowa
    @Japlennthondowa 2 месяца назад

    Ambuyanu

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w 2 месяца назад

    Kodi tifunika ukapepesa kuti , pakati pa chikangawa chakwera olo ku banja ya chilima .
    Ndiye muziti anthu ali utukwana .report ituluke

  • @angellinanhlema5308
    @angellinanhlema5308 2 месяца назад

    Koma ma VN anthu akumuzi akumamvela

  • @TimeAfickpayere
    @TimeAfickpayere 2 месяца назад

    Kkkk

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 месяца назад +2

    Komatu mutukwane palibe chomwe mungapindule

    • @LawrenceBelson
      @LawrenceBelson 2 месяца назад +1

      Nde ngt palibe chomwe tingapindule nanga akuyakhuliranji mr chikangawayo

    • @SydneyMwale-u9w
      @SydneyMwale-u9w 2 месяца назад +1

      Nanga akudandauliranji. Naweso uli wa chikangawa kapena

    • @MatthewsJohn-kv8fj
      @MatthewsJohn-kv8fj 2 месяца назад

      Tipindula ife ndo bon karindo anaba ndalama za bamboo anga awa za chibalo

    • @MatthewsJohn-kv8fj
      @MatthewsJohn-kv8fj 2 месяца назад

      Chakwera anaba mumene tikuvutikila kuno inu amangoti muzipereka ndalama kukama mkaka ng'ombe yo wonderful kare

    • @MatthewsJohn-kv8fj
      @MatthewsJohn-kv8fj 2 месяца назад

      Bon kalindo my president

  • @GiftHaward
    @GiftHaward 2 месяца назад

    Kkkkkk the DCccccccc

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson 2 месяца назад

    Bon the DC ndipo uthenga wa ma demo ukhale wakuti atule udindo basi.