CRUISE 5 WITH MICHAEL MANGANYA USI
HTML-код
- Опубликовано: 5 фев 2025
- Michael Manganya Usi is a man of many talents. Comedian, Actor, Producer, Singer, Social Commentator. He currently works for ADRA as the Executive Director (to retire soon). He met Joyce Banda former Malawi President and told her that her government was corrupt. He is currently promoting a political philosophy - Odya Zache Alibe Mlandu.
Anyone else who is watching this in 2024
Meeeee
Mee 😊
Mee😂
Uncle mukunena zoonadi mukabwela kumudzi kumulanje kwa gorden kuchem'kwanda mumathandiza aliyense mumakwana DR usi stay blessed God bless you big
Malangizo a bwino abro Manganya. Problem with our Country is selfish and greedy leaders. 🇲🇼👏👏👏👏
Mr Usi keep the Chitenje for me pliz.....am coming there next year...kuti tiyende limodzi ndi odya zake alibe mulandu.....
Uncle Usi, may God continue blessing you and I praise God for giving you such a good heart... Much love
More 🔥 Dr Michael Usi.
This is great Dr Micheal Usi, i like the way you always do your things, you have great things to the country especially on leadership.
instablaster...
Such a genius
Ure the Best mr usi..all the best inuo mmakwanitsa kobasi
Mr Usi keep it up.....go ahead one day you will be a president of Malawi.....am watching from Kuwait.....more fire kuti buuuu......🔥....
Iwe umakhala ngat walota bwanj😂
😂❤ inu nda prophet 😅
Mr usi my home boy he is genius indeed and I know that one day he will become the president of MALAWI manganya he is a game changer believe that
He sounds visionary leader.....
Michael Usi has a lot of constructing points. He is a guy who is focussed. Other people speak because they just want to speak something but Usi speaks because he has something to.... I like him and I owe him my total support
Manganya ndimamusata coz amaziwa kuvutika ka amalawi...koma khani za ku malawi zinafika sondiwawisa mutu chifukwa anthu ake ndiwongokoma mkamwa, komano kut asithe zinthu ngat achitira mayiko ena samatha. Maiko ambiri mu Africa akutukuka ndithu pomwe Malawi palibe chanzeru chikuwoneka Mmitu mwangozaza mamina okhaokha basi...Watching fro Yokohama, Japan
Thanks Joab that's marvellous and Mr usi matiimirila
These guy is so genius. .so sweet
Wow manganya
Very enlightening interview
Dziko lino silingapite kuli konse bwanawe, we don't have a dream that shapes us... Until we get to know what we do need boom our way to ho
koma nde alipo nigwiranugwiranu nofumu..makoponi avuta..like the songs by Katwell and phwanyaphwanya boys
This man is wise...what an influence!!!
i missed this
is so amazing keep it up joab
Nice music
Am proud of you Mr Manganya. More fire!! Koma nsaluyo nane ndikuifuna.
Eee koma Mr ussi mumandisangalatsa Chimodzimodzi simufuna kukamba zoipa kumbali I like it
The interview I was waiting !!
please Mr chankhaza I wish you host Andrea Thonyiwa (Mr Jokes)
kkkkkkkkk amaganya
That was exclusive interview with my boy usiman manganya dembele
Great interview ...
So za azimayi anakuphuzisa ndani kuti uziti ndi yamwe chokozela
Masikono
Usi is absolutely right. I don't like current DPP leardership though but if we as malawians need to change a party we really need to examine it. What new can MCP bring to Malawians? What about UDF, Aford etc?
Dziwani Paul mukuchedwa mukamalimbambana ndi dpp afana chezani lna
You sound immature to argue with...
This aged really well!
Wandilimbikitsa manganya
Michael Usi is smart
Who else has noted? Mdidi by faith mussa preferred by most guests of cruise 5
OSWARD MULENGA That's true. It's a favourite for many, Patience Namadingo as well.
I think Madam Mary chilima chose the same song !!!!!!nyimboyi inaimbidwa jealous down!!!!!!!!!
Joab kkkkkk ukutinamiza zakuoneka kwako before kkkkkk like kapuku
This has been so sweet
Foreigner Manganyayu
Mr Manganya wodya zake alibe mulandu kkkkkkkkk nsaluyo tikuyifuna
Zowona mr usi, l respect you ndipo ma president athu akanakhala anthu ozindikila ngatinu bwemzi tilipatali
Ambuye akutsogolereni. Awotu sanabvutikire mpandowo anangolandira.keep on brother.
Muli fundo akuluwa.
But Manganya amakaliila anthu kuntchito akamuitana kuti mangaya now akuvomera coz akufuna upresident, whats that
The bass guitar is great
Kikkkkk the last questions seems the same you asked Dr Lazarus Chakwera
Chimene chimawononga dziko NDI chifukwa chozikonda
KATIWELO & PHANYAPHANYA BOI LIVE PERFEMANCE ILI BHO,KUMENYA DZIDA MWASILIYASI KIPI ITI APU
Manganya amakwana
manga wakublawayo kkkk
It's me here 😂
Michael Usi is such genius
nice cruise 5 team
Manganya ali ndi nzeru kwambiri koma akanangonena kuti he's contesting 2019 ino
Joyce Banda wakubayu amafuna kunkumenya wayaskanya joyce
nice
Joyce banda imformer president
wasala winiko
Odya zake alibe mulandu party 😂
Aaaa manganya atizuza askhale president ndithu kkkkk kuumira
You so much sound like uli ndi ubwenzi kwambiri ndi azungu zomwe zili zosakhala bwino.
Palibe akukufuna iwe ungovutika kupita ku chisankho sukawina zipita ku MCP konko
Mr Usi please send me one nsalu .Im in Zimbabwe
vuto amalawi presdent mumafuna kaya akuvulireni akuonetseni kumatakoko kwake kaya aliyense azadya thukuta lake
Kwinaku a m'boma akuba zomwe wina wake akugwirira ntchito ? Your reasoning is pathetic and cheap though.
wamasewela sakudziwa chomwe akufuna
Ndiye munaona kuti dzipewa ndi salu m'malawi zamukwana umphawi watha kkkkkkkk mulindisoka
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 lero muli ku boma mukupanga chiyan
Anthu andalenu masomphenya anu amakhala abwino koma mukalowa kuti muzichite iiiiii Kodi nanga tisonkhe ndani??
Joab Frank Chakhaza r u politician or Journalist???????? plz stop boring people OKY
Zikomo. Maganizo anu amveka.
Timothy E Weldone boring how???
ziko LA Ku Malawi lafikapa chimozimozi kukhala opanda purezideti. chifukwa palibe chikuwoneka
Nixon Patrick amalawi umphawi ndi ulesi kumalimbqna ndi president zopanda mphindu ukhala choncho lwe kape opanda nzeru
aaaaaa broh u boring me serious r u politician ????
Who are you referring to?
Dont worry Joab he might be one of DPP die hard cadet
is so amazing keep it up joab
Issah Waphee thanks indeed.