Wadzafotokoza economics yokhudza ma remissions ndi impact mu recipient country. The logic is very clear, koma ma economist athu akukanika bwanji? Koma sukulu siyimachotsadi umbuli. Ma economist athu ambiri ndi mbuli zophunzira.
Mbambande interview,, welcome back Mr Chakhaza tamudziwano Tabitha she's very humble komas ay muli macheza ndthu Big up 💪 Tabitha maloto Ako akwanilitsidwa zonse n nthaw 🥳🎉🥳🤗😊🔥🔥🔥
Tabitha🔥. Koma kodi Tabitha ndi wa mmuna chifukwa dzina ndi lachikazi koma akuoneka wa mmuna maunso wammuna ndingodziwa. Otherwise is a role model to many
She's very humble and sound mature keep up sister.
I still have faith in Malawi because of people like these. Thanks Joab for another insightful interview. You are the best!!!
Khalidwe ndi chuma. This lady represents our nation well. So proud of her.
Tabitha is so funny. I can’t stop laughing. So proud of you. Don’t pay attention to the hater’s comments Tabitha. They are jealous
Koma Tabitha is very humble eeee. Munthu wa ndalama zake koma ougwira mtima😅
Guys please let us keep our comments very respectful no need for any negativity🙏
I'm happy to see this interview
Wadzafotokoza economics yokhudza ma remissions ndi impact mu recipient country. The logic is very clear, koma ma economist athu akukanika bwanji? Koma sukulu siyimachotsadi umbuli. Ma economist athu ambiri ndi mbuli zophunzira.
Mbambande interview,, welcome back Mr Chakhaza tamudziwano Tabitha she's very humble komas ay muli macheza ndthu Big up 💪 Tabitha maloto Ako akwanilitsidwa zonse n nthaw 🥳🎉🥳🤗😊🔥🔥🔥
Thanks Big up Tabitha Miss TC11 your a big motivator to all girls in our Country.
You're such an amazing soul Tabie may God watch over you.. I'm not a football fan but you have inspired me alot🎉🎉🎉🎉🎉🎉. Thumbs up Joab great macheza
this one is so humble, and so much comedy in this I loved it 😂😂😂
Amakhala pa goal atavala dress thats the real meaning of gender z performative ❤🎉 proud of u sister girl🎉🎉🎉
All the best TC 11...Mr Chakhaza Would you bring Us Nyakwawa Matumbi please at some Point...
LOOKS, VOICE, STAMINA THIS ONE IS A MAN
Tabitha you are amazing,so humble even disclosing your humble back ground,👏👏👏no wonder you are a celebrity.
I never see joab be happy like this in an interview 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
God bless you sis keep doing what you know best keep on shining darling sis much love from the UK ❤
I like her voice. Malawi is opposite in many ways
Eee😂😂😂
This is a very touching story, how life changes
Our own ghetto celebrity from area 25 sector 7 Lilongwe am proud of you
She is very humble....
Good job Mr Joab
Tamuziwa nawo Tabitha
Welcome back Joab.. Nice interview🎉🎉
Tabitha, you are blessed ❤
Am happy for you chawinga
My comment is coming as like a question, kunkhani ya chikondi, does she fall in love or is she inlove with someone else???
The host deserves a ballon d'or for his laughter
Tabitha🔥. Koma kodi Tabitha ndi wa mmuna chifukwa dzina ndi lachikazi koma akuoneka wa mmuna maunso wammuna ndingodziwa. Otherwise is a role model to many
Ndi mtsimana guys si mnyamata. Mulungu amalenga anthu mosiyanasiyana
Ndi mkazi
Nice Joab and good luck to TC11,,your future is bright❤
❤or even chakhaza amavaa bwino
I have some questions kwa Tabitha Chawinga
Tabitha Ambuye akudalitse Ndipo adzikutetedzera
Madala ndinu dolo, mumakunga bwino. Listening.....
This was an interesting interview tisaname.
Anthu ena mmmm mdalitso ungowayenera mmm
Ine Tabitha amanditsangalatsa Ambuye adzikutetedzera mwanawe kuno ku Thyolo thekerani
Kodi is it live kapena it's old enterview
Mu malawi muno apulila ndee timachokela kuno ku mpoto
Tili ndi luso atumbuka mumfuse gaba uyoo
Tabitha Mmmh ndiwetu mwana okongola ngati anthu ena amayakhula monyoza sakudziwa chomwe akutathaudza koma sindiwe onyozeka
Tabitha Big bos ❤❤❤🔥🔥🔥🙏🙏🙏
Life is through steps,, from standing at goal post whilst in dress now she's in PSG as the best striker
Tabitha much love❤❤❤
Congrats to you Tabitha eeeeh hard voice than l a boy
And I like your uniqueness... Very beautiful and an outstanding creature Gods masterpiece ❤❤❤❤❤❤
Pm
❤
I think a mr Joab andyerela maso. Chiphaliwali cha pa radio
Ma hope anga temwa Chawinga ❤
Tambie ❤
From Hewe, Rumphi to Italy. God is really good and is not a man.
Zigoli zikamabwera Pena mpira umasakamila mu dress ,, now she is star waika Malawi pa map
Yes it is good I agree
Interesting ❤
She love God that's why zikumuyendere
Koma analipeza banja ?
Tabitha ❤🎉🎉
ndalamu awina wake amenewo
Interesting......
Voice🙄🙌
Sister waife from HEWE
Tabitha 😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤🙏🙏🙏🙏🙏
This woman's voice is deep 😅
Koma a chakhaza munakhalalitsatu osapanga upload ma video any way koma timakunyadirani kwambili ankolo
big up mtumbuka munyane
Mbambande interview
❤
Joan why ukumukakamiza Tabitha zamankhwala, tayi tee ndikumudziwa ameneyo amakonda kupemphera
Ndimamuna uyu""
❤❤❤❤❤
Oklahoma❤
Mtsikana uyuyu ndi ambassador oyimilira atsikana onse mdziko la Malawi.
World Class player
Ulemu wako Tabitha umakwanira iweyo ambuye azikutetezera wamva mwana wakwathu wakumalawi
uyu ndi mwamuna kapena mkazi because mau okhowo ndi he basi😅
Ndimwamuna ameneyo,just like simenya waku south Africa
Koma mau abes bwanji ngati mwamuna atumbuka
Big up TC11 the real meaning of a star❤❤
T11 machine 💪💪
Kodi ameneyu ndi Madala kapena Masiteni??
😂😂
Osamanena zopepela ndimana basi sazakhala mkazi ayi
Kodi mukuti bwanji 😔 munthuyi ndiwamkazi kapena mamuna? Ine ndikuwona ngati mamunatu ngakhaleso mawuwo😂
Mamuna uyu, ukazi ulipati apa?
yah Ali ndi thupi lachina simenya basi
Tidziweko za boyfriend kapena girlfriend coz mmmm palibe choonetsa kuti ndimkazi
Tifusileni achakhaza ali ndi boy freind kapena girl freind
Kodi ndi live kapena it's old interview
How old is she, she looks so intelligent 🧠
Mpila umasakamila mu dress , anthu kumaonangati achinya kkkkkkkkk😂😂😂😂
Hahahahahah moyo umachoka patali
Hahahaha😂😂😂 koma iwe wandipha ndiphwete
Kodi ameneyu mau amenewa ndi achizimayi???
Ngati muzimayi
Koma yes
A Joab you are being overly dramatic. Nice Interview though
So dramatic
Eeee koma Joab amaseka
ay tava nawo a tc11
Beautiful girl
Eeee the voice as aman😮
koma voice ndi mkazidi ameneyo nanga boyfriend ali nayo?
Mwana wanaluso uyu
Eeeeee Joab kunalidi kukondwaa
Esteroides voz profunda cara masculina
MCP 2025 boma!!!
A Joab mkazi kukuposani mawu
Joab kusekaku si original
😅😅😅
May the good Lord increase your territory