ZOMWE AYANKHULA VICE PRESIDENT MICHAEL USI.21 June 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 фев 2025

Комментарии • 495

  • @JacobBanda-s1f
    @JacobBanda-s1f 7 месяцев назад +13

    Your words DR Sir has deeply touched me,may the good LORD direct you.Mwalankhulazi ndizimene timati nzeru

    • @FrankNkhoma-mz3nb
      @FrankNkhoma-mz3nb 7 месяцев назад

      Tingopempha mulungu akutsogolelen inuo simungalolere kut tizbvutika

  • @VictorKachulu-y3n
    @VictorKachulu-y3n 7 месяцев назад +7

    This is what God normally does when he chooses a man to Lead congratulations mr usi komabe ena salephera kukuwa angakhale a mnyumba mwawo momwemo muwona anthu umbuli unawapangitsa khungu amafunabe balaba kusiya yesu 😊😊

  • @kelvinmhango-z3q
    @kelvinmhango-z3q 7 месяцев назад +16

    My the soul of Dr klausi chilima and sadik Mia continues to rest in peace

    • @williamsalexmbonga
      @williamsalexmbonga 7 месяцев назад +1

      Nkhani yake yomweyi ?

    • @amourvido8027
      @amourvido8027 7 месяцев назад

      Amalawi a nsanje amwene aaaah😂😂. Zugwirizana bwanji

    • @amourvido8027
      @amourvido8027 7 месяцев назад

      ​@@williamsalexmbonga😂😂😂

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa 7 месяцев назад

      Mulibe nzeru mukuyikira kumbuyo inu munthu wanzeru akat sakuopa kukhala pa mpando kwa tsiku limodziro ayambe kuchuluka nzeru kkkk mau amat komwe kwasala tchire ndkomwe kumapita moto just wait n see u believe me

  • @vitumbikomunthali8185
    @vitumbikomunthali8185 7 месяцев назад +1

    Looking forward to what you can offer Dr Michael Usi..All in all congratulations Dr Manga, wishing you all the best man🎉

  • @mosesbwalya1305
    @mosesbwalya1305 7 месяцев назад +3

    Wishing you Sir all the best in your new post and May the God Lord protect you in that office

  • @bekithembasibanda8096
    @bekithembasibanda8096 7 месяцев назад

    Very very very Good words God is leading him .. according to his words u feel confidence..thats great too

  • @sultannatha5556
    @sultannatha5556 7 месяцев назад

    Very very very and very good speach. This man is going to do his best. Let's help him. From Mozambique.

  • @manzimatekwe8808
    @manzimatekwe8808 7 месяцев назад +2

    Am so happy that the chosen vice president mr usi, is so good for the people of Malawi, lets hope and trust that he will work well for the people of Malawi, good luck mr usi.

  • @ElizabethKuputu
    @ElizabethKuputu 7 месяцев назад +12

    Michel usi you are very intelligent and ontop of that Iwish you all the best in this new office

  • @MatiasChimsakasa
    @MatiasChimsakasa 7 месяцев назад +10

    Nyimbo ikhale adzakuiwala udzasanduka dothi kaya adaimba uja ndani 😊

  • @Lexkasonkanji
    @Lexkasonkanji 7 месяцев назад +31

    😢chilima wanga😢

    • @mercyjubeck5905
      @mercyjubeck5905 7 месяцев назад

      I believe in you Mr Usi you will deliver ❤️

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 7 месяцев назад +20

    Ngati kulotatu,anachita sewelo,la kamuzu banda lero ndi izi.congra

  • @towerankhoma1380
    @towerankhoma1380 7 месяцев назад +7

    Zikhale Ng'oma kusekeleratu mission yatheka 😢

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd 7 месяцев назад +7

    Mcp is happy because chilima amawapatsa mphuma...nkhani ya ngwirizanoh!!!!!!

  • @alinuswengwira-yu6mg
    @alinuswengwira-yu6mg 7 месяцев назад

    Manganya💪 Dr Michael za nzeru zimenezo mpaka ma Judge anaseka mkuluyu anakonza

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 7 месяцев назад +1

    Kkkkk l am not satisfied ndingonena kt mulungu atipatse utsogoleri wabwino Masha Allah

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 7 месяцев назад +8

    Chilima amakunyansani chani azikhale ng'oma koma ngati udzitumidwa kumapanga zopusa Maga uwamva kuwawa alomwe anzako

    • @JohnmarkNazombe-hi9xd
      @JohnmarkNazombe-hi9xd 7 месяцев назад

      Ayi big chilima amawapatsa mphuma nkhani ya u president....

  • @StanleyBaluwa
    @StanleyBaluwa 7 месяцев назад +11

    My name is Stanley Baluwa, let me thank the President Dr Lazarus Chakwera for appointing Dr Michael usi to be the Vice president of Malawi, this shows that there's is a great wisdom in the Mind of President, lastly don't worry about what people are saying about you, Mr President God will help you ❤

    • @KepherChinyama
      @KepherChinyama 7 месяцев назад

      Amen this is true

    • @CeniaMayeni
      @CeniaMayeni 7 месяцев назад +1

      Zitsiru ngati inu ndi amene mukufunika kudulidwa makosi you applaud rubbish

    • @pemphokatembe443
      @pemphokatembe443 7 месяцев назад

      ​@@CeniaMayeniNdipo inuu aah

    • @blessingsmunthali9202
      @blessingsmunthali9202 7 месяцев назад

      ​@@CeniaMayeniOk inu a nzelu

    • @RoseMose-ry2sh
      @RoseMose-ry2sh 7 месяцев назад

      I like your comment t

  • @DianahMatiki
    @DianahMatiki 7 месяцев назад +20

    Ayi ndithu dziko lizatiyiwaladi😢

    • @suprianomgalla5512
      @suprianomgalla5512 7 месяцев назад

      Ndipo inuu😢😢😢, eti anthu kusangalala mpaka ana achepa

    • @SamuelJoseGaviteni
      @SamuelJoseGaviteni 7 месяцев назад +1

    • @Xris241
      @Xris241 7 месяцев назад

      The dead shall b forgotten and b replaced by the alive,so better accept it,the world has to move even though we mourning

    • @kingzack8999
      @kingzack8999 7 месяцев назад

      @@suprianomgalla5512 wina ndikutenganso mkazi wako

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np 7 месяцев назад +8

    Good Mr usi...kulankhura mwa mzeru mowopa Yehova 🎉🎉🎉🎉

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi 7 месяцев назад +16

    Zanu wapita mwapha Inu mukusangalala

    • @fxmw
      @fxmw 7 месяцев назад

      Ndiwe kape

    • @BlakRedGrin
      @BlakRedGrin 7 месяцев назад

      Mumafuna kuti ku mwambo olumbilitsa anthu aziliranso? There's time for everything

    • @TestKambalanje
      @TestKambalanje 7 месяцев назад +1

      Kodi mumafuna anyamule bokosi

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 7 месяцев назад +20

    Malawi omvesa chison ndithu

    • @fxmw
      @fxmw 7 месяцев назад +1

      Mmafuna asankhe bambo Ako?

    • @StanleyChinsewu
      @StanleyChinsewu 7 месяцев назад +1

      Once a comedian always a comedian the presidency does not really matter

    • @fxmw
      @fxmw 7 месяцев назад +2

      @@StanleyChinsewu and people forget that before becoming VP he was also a VP wa chilima. And anali chilima yemweyo amene anamusankha. He has all requirements for being a VP and he's well educated kuposanso chakwera. Anthu akuona manganya osati Michael Usi that's the problem

  • @FatimaJuma-k3k
    @FatimaJuma-k3k 7 месяцев назад

    Congratulations Mr Usi put Allah first zinazo pambuyo but one more thing don't forget that any good or bad coming from God almighty ndakonda momwe mwayankhulira

  • @AlexHanyana
    @AlexHanyana 7 месяцев назад

    Mr president I love your sepich god bless you 🙏

  • @fatsanijere-r1g
    @fatsanijere-r1g 7 месяцев назад

    The speech is very fine congratulations Michael usi

  • @StevenMjMbama
    @StevenMjMbama 7 месяцев назад +1

    All the best Mr usi plz do ur best for malawians ndipo ausi finyani onse amene akutsokoneza Malawi ndikatangale plz muma office aboma Mr usi awonetseni nyekhwe onse opanga zibwana muma public sector plz plz our people are suffering

  • @ronexlouiskamangeni
    @ronexlouiskamangeni 7 месяцев назад

    I just pray for the protection of God, to be with you on that risk you have taken!

  • @meekmsuseni3108
    @meekmsuseni3108 7 месяцев назад +1

    Pallbe cha nzaru chimene ndanva.... all i heard is devil voice. Rest well Mr Chilima

  • @LatifahDavid
    @LatifahDavid 7 месяцев назад +1

    All the best Mr Michael Usi❤❤

  • @CharityAlex-r3v
    @CharityAlex-r3v 7 месяцев назад

    ❤❤❤ motooo kuti buuu congratulations Bambo asikhono

  • @trytizankhoma2871
    @trytizankhoma2871 7 месяцев назад +6

    Vanity upon vanity
    .
    Chilima will always be my vice president

  • @stevenkaombe8737
    @stevenkaombe8737 7 месяцев назад +4

    Congratulations Dr Michael Usi. You are a blessing!

  • @Adamkandulu
    @Adamkandulu 7 месяцев назад +1

    Chenjeran a VP oyipayo alipompo akusekerera

  • @BrendaMalunga
    @BrendaMalunga 7 месяцев назад +2

    Nice chining'a

  • @moffatzgambo9722
    @moffatzgambo9722 7 месяцев назад

    Mr usi do what God has direct you i love you sir

  • @TryceMagombo-sh7kb
    @TryceMagombo-sh7kb 7 месяцев назад

    Ur our celebrity manga we love u ulibe mbiri yoipa yako ndi Geri basi umatha kucheza

  • @SlajihMeria
    @SlajihMeria 7 месяцев назад +4

    Malawi ziko lomvesa chisoni kwambiri 😢😢😢😢😢

    • @lillynhlema9656
      @lillynhlema9656 7 месяцев назад

      Kwambiri.....ngati tinatembereredwa😢

  • @rashirdbanda8204
    @rashirdbanda8204 7 месяцев назад +7

    Chilima tikusowani chifundo chinaphesa

  • @JamesMushinge
    @JamesMushinge 7 месяцев назад

    Well spoken. Put God first

  • @ChisomoKandikole
    @ChisomoKandikole 7 месяцев назад +4

    Xoopsa masiku otsirixa 😢😢😢😢😢😢

    • @DuniaMalinga-gw7of
      @DuniaMalinga-gw7of 7 месяцев назад +1

      Pa dzana nyumba yomweyi timalila lelo zomsezija taiwala we don't focus on here after 😢

    • @bernaphiri
      @bernaphiri 7 месяцев назад +2

      Athu amamuiwala muthu ngat sanali naye limodzi kuvesa chison 😢 mzimu wachilima uziusabe nd mtendere

    • @ChisomoKandikole
      @ChisomoKandikole 7 месяцев назад +2

      Ndipo inu week osantha aiwara Kare eee miximu yao anthu amene anja ibweze in the name of Father, son and the horysprit

  • @DytonMission-iz5rn
    @DytonMission-iz5rn 7 месяцев назад

    All the best Mr usi🎉🎉

  • @ChristinaSukwambe
    @ChristinaSukwambe 7 месяцев назад

    Ndchimodzimodzi kusakha olongolora class😂😂😂😂😂

  • @StephenwMbuzi
    @StephenwMbuzi 7 месяцев назад

    May love and peace be with you all Malawians in this difficult time and may God continue blessing you Amen!

  • @LazarousMwanza-de4ro
    @LazarousMwanza-de4ro 7 месяцев назад

    Manganya, God is with you.

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 7 месяцев назад

    Lord have Mercy .
    " Mulingati Abwino😭😭😭
    Malawi wangaaaaa 😭😭😭

  • @clesheinvestments
    @clesheinvestments 7 месяцев назад +5

    In Micheal Usi there is Wisdom.
    Wishing him all the best

  • @PatienceAmigu
    @PatienceAmigu 7 месяцев назад +3

    Nyumba yomweyi timaliramo dzulo dzuloli lero ndimu tusekeleramo mmmmmm 😢😢😢😢😢😢

    • @DuniaMalinga-gw7of
      @DuniaMalinga-gw7of 7 месяцев назад

      Wicked world 😢

    • @SindisiweMendu
      @SindisiweMendu 7 месяцев назад

      Afiti awa

    • @KepherChinyama
      @KepherChinyama 7 месяцев назад

      Ndilo dziko munthu akafa basi watha palibeso chifukwa chsachitira zinthu zina ayi life goes on

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 7 месяцев назад +4

    😢It seems the plan of MCP to put Chakwera on ballot are working😢Chilima was killed by MCP😢84

  • @EphraimJoevino
    @EphraimJoevino 7 месяцев назад

    All the best, politics munayamba pakanthawi big..pakamwa mukutulusa funds zanzeru

  • @adrianobrigida3402
    @adrianobrigida3402 7 месяцев назад +1

    Wampheranji Chilima, Manganya? Unkafunadi udindo?

  • @JosephNgona-f9v
    @JosephNgona-f9v 7 месяцев назад +3

    Rip my vice president chilima mudalibe ulemu wa u vice President .kkkkkomasesa mu church haaa rip

    • @AishaChibwana-b8o
      @AishaChibwana-b8o 7 месяцев назад

      Aaaa kuyankhula kwa bwanji ngakhale bible linalemba zichesepeseni pa maso pa mulungu u vice president ndi mau a mulungu chachikulu ndi chani kodi???

  • @OwenDoctor
    @OwenDoctor 7 месяцев назад

    Amighty God please help Malawi and put your mercy in Malawi chilima may your soul rest perfect in peace 🙏

  • @IvyViyuyi
    @IvyViyuyi 7 месяцев назад

    Yes abwana mwayankhula. May auzimu ndipo kwanilisani chimene mulungu akulamulileni sitiziwa chimene mulungu akuitanilani

  • @OwenDoctor
    @OwenDoctor 7 месяцев назад

    Amighty God please help Malawi and put mercy in Malawi 🙏

  • @MarkManyowa
    @MarkManyowa 7 месяцев назад +1

    Ndakatulo ikhale ya Robert Chiwamba "Muzafa Imfa Yowawa"
    🇹🇿

  • @IMRANSHUKURANBEDI
    @IMRANSHUKURANBEDI 7 месяцев назад

    It was so nice

  • @lastondaniel6697
    @lastondaniel6697 7 месяцев назад

    Anga👁️👁️

  • @EdwardChiwaula-g5j
    @EdwardChiwaula-g5j 7 месяцев назад +8

    Izi akungomphimba Maso utm usi ndiwa Congress asatipusitse

  • @stewardmbele7385
    @stewardmbele7385 7 месяцев назад

    Mmmm great speech by Dr Usi

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 7 месяцев назад +2

    M c p zomwe imafuna zatheka,,, mmmmh koma ifah😢

  • @JoyceBanda-k8t
    @JoyceBanda-k8t 7 месяцев назад +2

    Manganya sekerera kucola lwa achilima 2 days yomweyi mwamuiwala chilima rip chilima asiyeni manganya akondwe

  • @OsmanChisi
    @OsmanChisi 7 месяцев назад +6

    Usapiteso Ku UTM galu

    • @amourvido8027
      @amourvido8027 7 месяцев назад

      Chifukwa chani🤷‍♀️

  • @pamelachirwa427
    @pamelachirwa427 7 месяцев назад +2

    Amen! Man of God.

  • @CHITENZE_EMPIRE
    @CHITENZE_EMPIRE 7 месяцев назад +1

    Mr jokes amenewo 😅😅😅

  • @Nya-Jeka
    @Nya-Jeka 7 месяцев назад +1

    Pepa Saulos. Mzimu wanu uwuse mu mtendele 😢

  • @PeterKimani-e5n
    @PeterKimani-e5n 7 месяцев назад

    Congratulations from Nairobi Kenya.
    Take over from where Chilima left.

  • @LinahNgulube
    @LinahNgulube 7 месяцев назад

    Family ya chilima yikumva bwanji😭😭Malawi💔

  • @doreenchirwa-ry5yt
    @doreenchirwa-ry5yt 7 месяцев назад

    All the very best sir ....May God guide you

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l 7 месяцев назад +7

    Mavuto mu Malawi alipo

  • @FaithKanyoza
    @FaithKanyoza 7 месяцев назад +1

    Chizikhake ng'omachicho ku kuomba manja mwa mphamvu.....mxieeeee

  • @FelixAndreFrancisco
    @FelixAndreFrancisco 7 месяцев назад

    Mery chilima soleeeee😢😢😢😢😢💔💔😔😔

  • @OwenMajoni-qv3eg
    @OwenMajoni-qv3eg 7 месяцев назад +3

    Dr. Usi ulemu wanu. Zabwino zonse pa ntchito imeneyo. Ambuye akhale nanu baba.

  • @chiccochimwaza4791
    @chiccochimwaza4791 7 месяцев назад

    Big up Manga, umatha daily

  • @TalazanGamah
    @TalazanGamah 7 месяцев назад +4

    All best work manga Many Allah be with u n work hard like the first one rate chilima

  • @ZainthwaSikelo
    @ZainthwaSikelo 7 месяцев назад +9

    Akamalumbira chonchi with Bible zimaoneka ngati pali uMulungu km ndithu ndithu ndithudi,palibepo Mulungu pamenepo

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 7 месяцев назад +10

    Ndikulumbira,pali Mulungu .
    Sangalalani kwa kanthawi kochepa
    Ife amalawi ena tilibe atsogoleri
    Km a MCP.
    Mulamulira mpaka chaka cha 20000000000000000000000000000000000000000000000
    MCP WOYEEE

    • @GodwinKatunga
      @GodwinKatunga 7 месяцев назад

      😢😢😢😢 Malawi tizikhala ndi umunthu Mary chirima afila bwanji? 😢😢😢😢

  • @JusticeBornNdhlamini-fp7ic
    @JusticeBornNdhlamini-fp7ic 7 месяцев назад

    Kuchokera ku masewera lero akukathera as Vice president koma moyo uwu

  • @evaromeo1897
    @evaromeo1897 7 месяцев назад

    Congrats Dr Michael Usi, wish you best

  • @amonfriday630
    @amonfriday630 7 месяцев назад

    Great speech boss

  • @DoctorStaniel
    @DoctorStaniel 7 месяцев назад

    Thanks Lord 🙏🏽🙏🏽🙏🏽🔥🔥🔥

  • @eunicemacdonaldkaipsa9705
    @eunicemacdonaldkaipsa9705 7 месяцев назад

    Tsiku lachiweruzo nde osaomba mmanja kwambiri tu aphunguwo😂😂😂

  • @KondwaniLungu-x5l
    @KondwaniLungu-x5l 7 месяцев назад +2

    VC ameneyu ndi wa MCP si wa utm. Asankhana okhaokha

  • @RobertJosias
    @RobertJosias 7 месяцев назад +1

    I wishing you all the best vice president

  • @JoannaGadabu-el5og
    @JoannaGadabu-el5og 7 месяцев назад

    Ine kumangolulutila🎉🎉🎉🎉

  • @FatsileniKwakwata
    @FatsileniKwakwata 7 месяцев назад

    Powerful 🎉

  • @alicejonny7990
    @alicejonny7990 7 месяцев назад

    Do best all over Malawi not only kumwera. Even us we need chitukuko kumpoto

  • @PhillipMaalo
    @PhillipMaalo 7 месяцев назад

    True African leader.... Chichewa

  • @AntonyKalenga
    @AntonyKalenga 7 месяцев назад

    Wakalamba usi 😅😅😅 osadandaula tikupatsa ndodo uziendela.

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 7 месяцев назад

    Kufuna Kwa Mulungu kuchitidwe ..we are the kapolos in our own country

  • @WisdomKapawo
    @WisdomKapawo 7 месяцев назад +1

    Zachibwana basi pa Malawi 😂😂😂😂😂

  • @LeendaDeborah2005
    @LeendaDeborah2005 7 месяцев назад +1

    Zokhudzatu kwabasi 😢😢

  • @DalitsoKaunda
    @DalitsoKaunda 7 месяцев назад

    okay dxinali zogwilizana Kuti munthu uja muphe ayi khalani pampandopo tikuoneleni 🤭🤭

  • @JamesWandari
    @JamesWandari 7 месяцев назад

    All the best my vice

  • @AgnessLudzu
    @AgnessLudzu 7 месяцев назад +1

    Manganya sadzathekanso😅

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 7 месяцев назад

    What l knows mukudziwapo kathu pa imfa ya Chilima kondwerani ndithu nyadani posangalala ndi imfa Chilima anakapanda kufa inu simananjoya mmene zilimu zili bwino ndi moyo wanu😭😭😭😭😭😭

  • @DorothySailesi-vh1mh
    @DorothySailesi-vh1mh 7 месяцев назад

    Lero 1 kumaona nkazi wakeyo,,,,, happy for them

  • @robsonmanyesa1110
    @robsonmanyesa1110 7 месяцев назад

    Malawi politics is between the president and his/her deputy vice president. Very soon, we will hear that these two are now fighting. Only time will tell it all.

  • @KepherChinyama
    @KepherChinyama 7 месяцев назад

    Uyuuu sadzatheka uyuu kkk😂😂😂😂😂😂😂 mbambande AVP

  • @Jerry-vm6mo
    @Jerry-vm6mo 7 месяцев назад +3

    Ukuyankhula zopusa ndizomwe umafuna

  • @GraciousBeyard
    @GraciousBeyard 7 месяцев назад

    Once Evance Meleka sung (adzakuiwala,
    Utasanduka nyatsi
    Adzathamanga nawe kumanda kokakutaya, bwanji udzipemphera)