DR KABAMBE NDI KATUNDU KWAMBIRI MVERENI ZOMWE WALANKHULA |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 8 ноя 2024

Комментарии • 12

  • @ChrissieNyasulu
    @ChrissieNyasulu 7 часов назад

    Muzabwereze kumene anthu ambiri sanalembetse chifukwa Cha ziphatso Cha unzika.

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 2 часа назад

    Kabambe is answer muli SKC and Bingu traits....tiyeni timunyamule atipatse tsogolo lowala

  • @edgarmbewe7009
    @edgarmbewe7009 6 часов назад

    Kodi ndekuti ndiwachibwibwi

  • @YuzzeGowero
    @YuzzeGowero 6 часов назад

    Osamanga mpanda wina bwa be serious

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 7 часов назад

    Awa ofuna kugulisa chipani.

  • @ChrissieNyasulu
    @ChrissieNyasulu 7 часов назад

    Bwalo la ndege losateramo ndeege.

  • @AustinChabinga
    @AustinChabinga 7 часов назад

    Tikufuna kabambe 4:33

  • @felistasbunu9824
    @felistasbunu9824 7 часов назад

    1:25

  • @josephalfred5138
    @josephalfred5138 8 часов назад

    Iwe usatipute galu iwe sambo get out

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 7 часов назад

    Kabambe wa kuthyolo kwathu wazeru koma opanda chitukuko kudera kwanu

    • @OmarManjawira-up3ns
      @OmarManjawira-up3ns 6 часов назад

      Not only him but also Bakili Muluz komanso Atupele muluzi kulibe chitukuko cholozeka kuMachinga atupele he was a nember of parliament by then and Bakili Muluzi he was a President,,, imagine?

    • @MosesDicostar
      @MosesDicostar 6 часов назад +1

      @OmarManjawira-up3ns athu amenewa ndokuba even mp wakwanthu mery thomu navicha ndi galu weniweni koma akamalakhula matama thooo