Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
My best Malawian series ever❤
Mmmm koma Scot iweyo🙌🙌Koma chonde episode 5 musachedwetsenso kwambiri
Eshiii series ili nyatwa hvy but two things,is too short and it takes long periods to releases new episode. That's all matter I see but to say truth ili mwala hvy
Ndipo nkhaniyi yoona
Kwabas ikumatenga nthawi kwambili bola itakhalako 1 week koma ikumatenga mwina miyezi itatu kuiwalaso , koma kunena zoona ilibwino kwambili
Beautiful movie
Komatu mankhwala ake nde achanguchangu eh eh!😹😹
This series its🔥🔥🔥🙌 how can we sponsor this series coz wow 🔥🔥🙌
Koma ada Scott nde adyedwa mwa easy tu e😂😂😂
Ine ndili ndi chidwi kwambili i love this move
Achikondi mwaiphulatu nyimba yabwino😅😊
Series ili bwino kwambiri but the one thing I want to say is it takes long time to release another new episode
Yeah kaya bwaji
Guys this is too much previously mpaka kutenga episode yonse kuiika mu ep ina pliz chan zaonjeza
Movie iyiyi ndiyabh kwambilit timava kukoma km kuchedwa kutulutsa
But it always take long period to release
Koma movie iyiyi ndiyokoma eeeeehhhhhh🔥🔥🔥🔥🔥koma mukuchedwa
Koma nde mankhwala ogwira pompopompotu eh eh😅😅
Kkkk zatenge
Asing'anga achikondi😂😂😂😂😂😂
Can't wait for the nxt episode.... This is dope 👏🏾😎
Sound track nyatwa ❤❤❤
Next please
Konda ine uja wagwiratu🤣🤣🤣🤣🤣🤣kungodya kampunga mutu balaka a scot🤣🤣🤣
I was waiting for this
Jealous down this is best moviefrom mw
Previous ikukhala yambili kwambili abale kapena vuto ndine sindikuona bwino😢
We will sort it out.
Zoonaditu previous ikutalika kwabasi
Mukudziwa chani ku malawi kuno anthu aluso tilipo, koma nkhan ya zachuma ndimene imativuta
Mankhwala popo ayambilatu kugwira ntchito
Komatu ndaseka 😂😂😂 Kodi mankhwara amagwiladi ntchito eti???
Nice koma imachedwa hevy eeishyyy😢
Scot mpunga akuti waphikidwa bho umodzi umodzi lkkkkk kuli kathu kokathula nd sidzasi
Ili bho kwambiliDzuwa art palibeso🔥🔥🔥
Apa nde mwabwerano sopano❤❤
Next ❤
Kani zakudya zamankhwala zimakoma chonchija Scot 🤣🤣
Please if possible try your best kupqnga release fast MA episode this is Malawian best series ever
Best Malawian series💥💥💥
😂😂😂 China chizandithilire Mtera🤣🤣🤣🤣
Koma scot😂😂nde nyimbo yasintha bwa😂😂
My understanding is anamaliza kujambula kma inaseweredwa pa MBC 2 on go then imaponyedwa pamudzi pano
Can't wait for next season 😂😂 chiko wainyumwa
Asululanso mankhwala aja😂😂😂😂 zosayendatu zinthu zake😂😂 Dan alikuti komaa
Ili bwino kwambiri pitirizani 🔥🔥
😢😢❤❤❤ love this series
This episode is best one
Filim iyi yandisiya mmalele
❤ keep up guys ilove it
Mumatha guys zimenezi muzipanga after 2 days inayiliyose muzitulusa sewelo limeneli ❤❤❤❤
🔥🔥🔥
keep it up
Nice movie maguy
Nakusowani guys 🎉🎉
I like. It
Chfkw chn mumatenga nthw yaitali kuponya episode???
@@AdzafunikaMwale pangani check pa Facebook page ya Scot or Ignatious Scot Kaphinde. Mayankho onse Ali pamenepopo. Thank you
Inu tatulutsani wotsalawo🙄🙄
Malawi muli acting mwene ee😂🖐️
iiii Scott uja wapita basi 😂😂😂 . Ali m'botolo basi🤣
❤❤❤❤❤❤
Ifé timakukondani komano mmmmmmm nanga kusowa kwake kumeneko bwanji
💯
Mmmmm machedwa kwambr aaaa but keep it up
❤
Km Scott 😂😂
🤣🤣🤣🤣Scot kupengeratu
Following
Koma amatha !!!😂😂😂😂
Akuchedwesa km ili mwala
Nice movie
🔥🔥🔥🔥
Next
687 Cortez Hill
LOVELY🥰
waiting for 5 ife tikusowa zochita 😢😢😢
Kom Scot wapepeladi etiii mmhmh Kom this gender ai zikomo
Chiko waithatu😂😂😂
Wait for next part 😂😂
😂😂😂😂 the sing'anga at the end kkkk😅😅😂😂 ati 'uleketu kuyankhula zako zopusazo' 😂😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣
Koma scot😂😂
Next plz
😂😂😂mankhwala Aja usazawatole
Muzibwenzimu timazidyeratu kkkk
Waonatu et athufe eee
Next pls ilibho
Good series kma kut atuluse episode eeeeh chakatu😂
Inayo osachedwetsa plz kmso ikufupikitsa
Aphabas ndi makhwala aja uku
Malizani comedy imeneyo tione kut ana aja anathawila kut
Scott ukuvomera???😅😅😅😅
Bwanji ka kungokhalatu kochepa
Tikhalireee iziiiii kodiiiii
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
🔥🔥🔥🔥🔥
Zodikirazi sizabho 😂
movie iyi ili bho hev
Next kuchematu
Iiiii previously Mpana 10 minutes guys 😂
😂😂😂😂
Eish kongolawisa🥲
Scot kudyatu
Eeh
My best Malawian series ever❤
Mmmm koma Scot iweyo🙌🙌
Koma chonde episode 5 musachedwetsenso kwambiri
Eshiii series ili nyatwa hvy but two things,is too short and it takes long periods to releases new episode. That's all matter I see but to say truth ili mwala hvy
Ndipo nkhaniyi yoona
Kwabas ikumatenga nthawi kwambili bola itakhalako 1 week koma ikumatenga mwina miyezi itatu kuiwalaso , koma kunena zoona ilibwino kwambili
Beautiful movie
Komatu mankhwala ake nde achanguchangu eh eh!😹😹
This series its🔥🔥🔥🙌 how can we sponsor this series coz wow 🔥🔥🙌
Koma ada Scott nde adyedwa mwa easy tu e😂😂😂
Ine ndili ndi chidwi kwambili i love this move
Achikondi mwaiphulatu nyimba yabwino😅😊
Series ili bwino kwambiri but the one thing I want to say is it takes long time to release another new episode
Yeah kaya bwaji
Guys this is too much previously mpaka kutenga episode yonse kuiika mu ep ina pliz chan zaonjeza
Movie iyiyi ndiyabh kwambilit timava kukoma km kuchedwa kutulutsa
But it always take long period to release
Koma movie iyiyi ndiyokoma eeeeehhhhhh🔥🔥🔥🔥🔥koma mukuchedwa
Koma nde mankhwala ogwira pompopompotu eh eh😅😅
Kkkk zatenge
Asing'anga achikondi😂😂😂😂😂😂
Can't wait for the nxt episode.... This is dope 👏🏾😎
Sound track nyatwa ❤❤❤
Next please
Konda ine uja wagwiratu🤣🤣🤣🤣🤣🤣kungodya kampunga mutu balaka a scot🤣🤣🤣
I was waiting for this
Jealous down this is best movie
from mw
Previous ikukhala yambili kwambili abale kapena vuto ndine sindikuona bwino😢
We will sort it out.
Zoonaditu previous ikutalika kwabasi
Mukudziwa chani ku malawi kuno anthu aluso tilipo, koma nkhan ya zachuma ndimene imativuta
Mankhwala popo ayambilatu kugwira ntchito
Komatu ndaseka 😂😂😂 Kodi mankhwara amagwiladi ntchito eti???
Nice koma imachedwa hevy eeishyyy😢
Scot mpunga akuti waphikidwa bho umodzi umodzi lkkkkk kuli kathu kokathula nd sidzasi
Ili bho kwambili
Dzuwa art palibeso🔥🔥🔥
Next please
Next please
Apa nde mwabwerano sopano❤❤
Next ❤
Kani zakudya zamankhwala zimakoma chonchija Scot 🤣🤣
Please if possible try your best kupqnga release fast MA episode this is Malawian best series ever
Best Malawian series💥💥💥
😂😂😂 China chizandithilire Mtera🤣🤣🤣🤣
Koma scot😂😂nde nyimbo yasintha bwa😂😂
My understanding is anamaliza kujambula kma inaseweredwa pa MBC 2 on go then imaponyedwa pamudzi pano
Can't wait for next season 😂😂 chiko wainyumwa
Asululanso mankhwala aja😂😂😂😂 zosayendatu zinthu zake😂😂 Dan alikuti komaa
Ili bwino kwambiri pitirizani 🔥🔥
😢😢❤❤❤ love this series
This episode is best one
Filim iyi yandisiya mmalele
❤ keep up guys ilove it
Mumatha guys zimenezi muzipanga after 2 days inayiliyose muzitulusa sewelo limeneli ❤❤❤❤
🔥🔥🔥
keep it up
Nice movie maguy
Nakusowani guys 🎉🎉
I like. It
Chfkw chn mumatenga nthw yaitali kuponya episode???
@@AdzafunikaMwale pangani check pa Facebook page ya Scot or Ignatious Scot Kaphinde. Mayankho onse Ali pamenepopo. Thank you
Inu tatulutsani wotsalawo🙄🙄
Malawi muli acting mwene ee😂🖐️
iiii Scott uja wapita basi 😂😂😂 . Ali m'botolo basi🤣
❤❤❤❤❤❤
Ifé timakukondani komano mmmmmmm nanga kusowa kwake kumeneko bwanji
💯
Mmmmm machedwa kwambr aaaa but keep it up
❤
❤
Km Scott 😂😂
🤣🤣🤣🤣Scot kupengeratu
Following
Koma amatha !!!😂😂😂😂
Akuchedwesa km ili mwala
Nice movie
🔥🔥🔥🔥
Next
687 Cortez Hill
Next
LOVELY🥰
waiting for 5 ife tikusowa zochita 😢😢😢
Kom Scot wapepeladi etiii mmhmh Kom this gender ai zikomo
Chiko waithatu😂😂😂
Wait for next part 😂😂
😂😂😂😂 the sing'anga at the end kkkk😅😅😂😂 ati 'uleketu kuyankhula zako zopusazo' 😂😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣
Next please
Koma scot😂😂
Next plz
Next plz
😂😂😂mankhwala
Aja usazawatole