Brilliant research Joab. My interest is Banda's succession plan...this good work needs to continue even after his life; who is he training to takeover from him?
I'm right there with you buddy 😢 I lost my grandmomma last year September due to high blood pressure which resulted to stroke and I tried my very best with these herbal remedies but alas! And now I'm seeing this eee yandiwawa
Kuli kwina kwake mkuluyu Ali nao mu gulu lopeleka ma license ku anthu azitsamba. Mkuluyu ayenera alembe buku lake la zitsamba lomwe lizigwititsidwa ntchito mzipatara mdziko muno komanso kuphuzitsidwa masukulu just like Biology. Matenda wanena apawa ndi omwe akupulura a Malawi.
Ngani yabwino achikulilewa basi mulungu awadalidze miyoyo ya andu ambili ita kupulumuka kusela mwa abambo amenewa Ndiye aku akulu amene angakale ndi number yamadalawa chende andigawile kuti tikafikeko ❤
Brilliant research Joab. My interest is Banda's succession plan...this good work needs to continue even after his life; who is he training to takeover from him?
I've learnt some amazing stuff here with Mr Alex Banda, so awesome
Awa nde ma program oti munthu uzinvela ndithuu... thanks joab chakhaza ...tamphunzila ndikuziwa nawo zambili....
So inspired n motivated, what a gift, groly be to God
Akamuna awa, ndapeleka ulemu tidzacheze one day mwatsilizamo
President koma uyu.......imirani bwana muwina !!!
Tonse tivota🙂🙂🤜🏻🤛🏻
Why did we lost our grandparents so early just because of stroke while mr BANDA is there😭😭😭
I'm right there with you buddy 😢 I lost my grandmomma last year September due to high blood pressure which resulted to stroke and I tried my very best with these herbal remedies but alas! And now I'm seeing this eee yandiwawa
This guy (man) is well educated
Tatigayileni nr yawo abale
So we should hope that his number cannot be accessed? M'mene anthu ayambira kufunsa muja palibe akudziwa?
Very genious man, ndaphunzira zambiri
Tsiku lina ndidzabwera komko ,this man is very smart
ATI, mu airways muli obstacle imene yatseka,,, uyu ndi doro
Anthu timafadi chifukwa cha kusadziwa zamphambvu ndithu big man
I Listened to this twice - i have enjoyed it
Nanga tingalumikizanenawo bwanji pakuti simudatipatse ma number wawo?
Johnson Johnson Powder wandilira😂😂
Komatu mukanapereka ma contacts awo. He is God given natural doctor. Ndipo anachitaso kulowera nkalasitu zosangalatsa
Tatigayileni nr yawo
Chonde tigailen fon namba ya mkuluyu
Tonse onyamula zinyalala zambiri let's gather here😮😂
Tatigayileni nr yawo abale
Ulemu wanu wakulu. Uyu akutiuuza Kuti tizikonda kudya zinthu zomwe ife timaziona zopanda pake.
Amene mukusaka nambala tandipezani ku box kwanga ndugaileni ..komanso mutafika mu lilongwe abc clinic mutsetsereke pang'ono mupeza akabaza kunkono wamanzere from abc clinic ask them ngotchuka kwambiri akuuzani
Share me number Dr Alex Banda aku Tree of life
Hello boss,may you pliz share the phone number of the Doctor
Pls ndigawireni nambala?
tikuifuna
Help with Dr.Alex Banda's phone contacts.
Part 2 Please Joab
Please ndigailen fon number ya mkulu ameneyu kwa omwe ali nayo chonde.
Koma asthma ndi antibiotic zugwilizana?
I hope this skill amaphuzisa anthu ang'ono kut lusoli asazapite nalo
Reminding me of Dr Sebi
Dr sebi was great man
nambala ndiyemene ikufunika
Mkulu uyuyu simunthu wamba amatha. Respect DR
Engineer of human body.. Eeeh akaka kandiwaza heavy
Tatigayileni nr
Koma mukanandifusilako fuso lokuti....chimapangitsa ndi chani,kuti munthu amene akwa ma ARV azisitha maonekedwe athupi lawo? Umeza munthu akumwa makhwala bwino bwino koma thupi likusitha maonekedwe...khosi loneneka,misempha yatuluka...khopeyi ngati aidina ndinjelwa...aaah ine ndimazifusa mafuso ambili zedi.
Ugalu wako
@@JacquelineKanjedzatatigayileni nr yawo abale
Joab is the best journalist eee munthu umamva kalikonse
Nanga mwina sunakumanenaye wochilisidwayo ungatani?
Eeeeeeeeesh komatu tamva zinthu sure 🙏
mitu ngati iyi imazatchuka ikafa alimoyo ai ndithu
Sikunama ase
Koma ndipo man.... Luso ndi nzeru izi azapita nazotu izi
Genius
Boma bwezi likugwilitsa ntchito anthu ngat awa nzipatala zathu.....bwez zinthu zikuyenda mkumaseva ndalama timapita nazo ku india.
Mmmmm God is good all the time koma yeah
Kuli kwina kwake mkuluyu Ali nao mu gulu lopeleka ma license ku anthu azitsamba.
Mkuluyu ayenera alembe buku lake la zitsamba lomwe lizigwititsidwa ntchito mzipatara mdziko muno komanso kuphuzitsidwa masukulu just like Biology.
Matenda wanena apawa ndi omwe akupulura a Malawi.
Zolankhula zikuchita kundisowa this guy ndimdalitso kwa ife
Ndaphuzira nawo ndithu palibeso kugula baby powder apa
Siliza patipati map sir want to come ndikukhala Kwa senti around trading
Tatigayileni nr yawo
Ntchito yabwino neba
School siyithadi
Apa tomato ndikudya wachi seveni
😂😂
😂😂😂😂😂😂
Job please tifufuzireniko a Verson Idi,tidzawamveko
Hahahaha I like this guy 😂😂😂
Ku school anati mu cabbage mulibe Vitamin aliyese km uyuyu ndie akt ndie number medicin eishiiiiii awa anadya ma book with aximu omwe
Adawa ndi amzeru koopsa
This guy is a genius
Interesting story
Mmm I really appreciate the guy..
Awawa ndi madhala kuyankhura momveka bwino
Nambala yawo tipiteko bp yikutivuta
Asamudziwe2 uyu athera mchikangawa kkkk
koma number yawo simunasiye bwanji
Eti abale
EEE guys 😅 God bless you sir
Tatigayileni nr yawo
Ngani yabwino achikulilewa basi mulungu awadalidze miyoyo ya andu ambili ita kupulumuka kusela mwa abambo amenewa
Ndiye aku akulu amene angakale ndi number yamadalawa chende andigawile kuti tikafikeko ❤
This guy is genius
Share the contact info pls
Zikomo ndaphunzira kwambiri
Zikundiwaza kwambiri
Uyu ndi katundu
Koma number ya mkulu uyu ndingaipedze motani😢😢
Tatigayileni nr yawo abale
Akulu akulu alindinumber ya akuluwa ndan plz
Koma joab na pa nyimbo pokhapa umatinamidza
Kuopa kutalikitsa nthawi bwa🤣🤣, nane ndimadandaula mwee
Ya live zimakhalapo on zodiac
Number please!
Moti asthma ndiyochizika ndithu abale😢
Eya ndiyochizika umboni ndili nawo ine ndinachira
Why sanayike number yawo kod why
Km number yo😢
Tomato ndizidya ngt sweet
Apapa ndizingodya bonongwe ndi mpiru basi
Tingawapeze bwanji
Just go pa mtsiliza take wanjinga and tell him ukupita Ku Tree of Life
Zosangalatsa kwabasi. Tubwela komko
Eee ineyo sindinayembekezele kut mulungu anatidalisa ndima chiliso mu dziko lathu lomwe
Komatu phone number ndye smunasye nanga tkakufunan tztan???
Korma dzikoli kuli anthu azeru koma saonekela Mr Banda is very interigent man mmmmmm number yawo ndiyofunikira kwambiri
ndipotu sadasiye number timaifunadi imeneyi
Dolo katatu
Share number amene angayipeze nanzani stroke yanditsautsa
Zilibwino ndthu number yawo bwanj abare
Tiri komweko abanda
Shasha kwambiri uyu eesh eee physician katundu
Johnson Johnson Powder wandilira basi
Apopo mumkamwa mankhwala aji amene ali mkapumo
Tigairen number yawo Dr wo
Mulibwanji achimwene tandigayilani nr ya Dr
This is Malawi
Koma number mutipatseko
Kma pa tomato po.... Men..!!
Dolo ka 10🔥
which country is this?
Malawi my dear
Spain
😅😅
😂😂😂😂😂@@patrickmasa7145
Powerful
Dolo❤
Mkulu uyu ningampeze kuti ine
Mexa akuti kwa nsiliza kulilongwe
Muzanditenge ine nkakuperekezen
@GiftBanda number yawo bwanji bwana
@@MikeFaititatigayileni nr yawo abale
Tatigayileni nr yawo abale
Number yawo bwanji
Ali ndi number yawo share
Ndaponya number zao... Read comments
@@johnmanganya2886number mwaponya pati Chief? Ife sitikupaona, ponyaninso tipeze chithandizo.
Tigaileni number abale
Number yanu Mr Banda sure please please please 🙏
Brilliant research amwene
Mdaphinzirapo zambiri
Number bwanj
I stay opposite to his hospital
mukatitengeleko # plz
Can u share his contacts
Where exactly in Mtsiliza
@@chikumbutsobanda504 it's after gateway mall as if we going towards area 49, before tisanafike pa mtandire