DEAR EX SERIES SEASON 2 EPISODE 3

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 3 окт 2024

Комментарии • 47

  • @YusufMatias
    @YusufMatias 15 дней назад +6

    Kma ikumachedwa kutuluka mpaka tinaiwalapo kut kuli dear ex series2

  • @GivenMvula-k5k
    @GivenMvula-k5k Месяц назад +7

    Komanso mupange ubale ndi ma tv akumalawi muzionetsa kumeneko

  • @GrantNorman-ir6if
    @GrantNorman-ir6if 15 дней назад +6

    The writer of this serie is more than genius 🔥🔥🔥🔥

  • @Hasha2.
    @Hasha2. 14 дней назад +1

    Ine Chaka chino ngati kuli kulakwa mayeso ndi inu😂❤

    • @christhepoetTV
      @christhepoetTV 13 дней назад

      iwe nde sunaiphonye tilakwa ambrit apa

  • @dominicmphepo-jk8lk
    @dominicmphepo-jk8lk 13 дней назад +1

    Big up guys the whole team ili perfect,,
    Aliyense Ali mwala.
    Bwana ignicious Kaphinde AKA Scott mumatha sure

  • @GivenMvula-k5k
    @GivenMvula-k5k Месяц назад +7

    Koma mkuchedwa kutulusa anthu ayamba kukuberani nzeru ndaonanso ena ayamba kupanga ma series ngati anuwa so better you release them fast

  • @andrewmeki8718
    @andrewmeki8718 12 дней назад

    🔥🔥🔥🔥🔥🙌 this just got more interesting

  • @JussabRobert
    @JussabRobert 6 дней назад

    Koma uncle Jimy nawoso e ndinyambalotu😂

  • @estherkamwendo7971
    @estherkamwendo7971 14 дней назад

    Ngati DR Chimango ali ndi zinsisi zawo, ndakaika ngati alipo wa innocent umu 😂😂

  • @CathyPhiri-m2g
    @CathyPhiri-m2g 13 дней назад

    Ine fiona amandisangalatsa ati ndi abambo ako awawa 😂😂

  • @FannySibale
    @FannySibale 8 дней назад

    Koma mukumachedwesa kutulusa mpaka miyezi yambirimbiri

  • @ChikondiMpate
    @ChikondiMpate 15 дней назад

    Komatu a chikondi nawonso sanaithe, m'bale wao kumwalira osalira or kuonetsa kukhumudwa mmalo mwake nkumakamba nkhani zofuna kukwatirana ndi Scott.

  • @JulianaChinangwa
    @JulianaChinangwa 13 дней назад

    Koma asing'anga ake abale 😂😂😂😂 ayooo inee kkkk

  • @CliveChikaphonya
    @CliveChikaphonya Месяц назад +1

    Mpaka 21hrs eeeee kmabe tidikira ndthu

  • @AllieKaterra
    @AllieKaterra 13 дней назад

    Km ikuchewda kutulukhatu guys bwanji ❤❤❤

  • @lilybanda4605
    @lilybanda4605 15 дней назад

    Hear my silence if you want 🤣. Chikondi just give up . Chikondi sakaka

  • @nana-aka9ka
    @nana-aka9ka 11 дней назад

    Kuchedwa mpaka after 4 months😏

  • @eliyakaudzu
    @eliyakaudzu 15 дней назад

    Ndinu madolo kwambiri 🔥🔥🔥

  • @MartinMasumba
    @MartinMasumba Месяц назад +1

    Ma hours onsewa why???😮😮

  • @Kelvin-hj5qv
    @Kelvin-hj5qv Месяц назад

    Am wait mativetsa kukoma

  • @ElizahKachulu
    @ElizahKachulu 17 дней назад

    Mpaka kumupha Hamid???😢😢😢😢 ohoo ai zikomo uncle Jimmy

  • @EuniceChabvuta-e6z
    @EuniceChabvuta-e6z 17 дней назад

    Dr chimango nawo Ali ndi zisisi asaaa

  • @miraclebanda
    @miraclebanda 16 дней назад

    Waiting

  • @ClaudinaAugustoAugusto
    @ClaudinaAugustoAugusto 10 дней назад

    Kkkkkkkkkk vamos

  • @CliveChikaphonya
    @CliveChikaphonya 15 дней назад

    Jimmy akuoneka ngt chigawengad 😂😂😂😂

    • @ChikondiMpate
      @ChikondiMpate 15 дней назад

      Ndipo nde part imeneyi akuitha 😂😂😂😂

  • @NallahBriston
    @NallahBriston Месяц назад

    🔥🔥🔥🔥🔥 waiting

  • @JacquelineLidamlendo
    @JacquelineLidamlendo Месяц назад

    Waiting

  • @RhodiWhite
    @RhodiWhite Месяц назад

    Waiting ❤❤

  • @giftpenjankaungah8104
    @giftpenjankaungah8104 15 дней назад

    Mbambande🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @charlesRajabu-cc4bx
    @charlesRajabu-cc4bx Месяц назад

    Bola osayichosaso ngat last tym ija

  • @DominiqueMejere
    @DominiqueMejere 15 дней назад

    Kwachema 😂😂😂

  • @amosgoliat4472
    @amosgoliat4472 Месяц назад

    Zamwasing’anga esh😂

  • @ChifundoEleson-i7d
    @ChifundoEleson-i7d 16 дней назад

    Ikumachedwadi kutuluka

  • @Malambia
    @Malambia Месяц назад

    Apa kwachema

  • @AishaSidreck
    @AishaSidreck Месяц назад

    Kuchedwa koma