Nkhondo Yolimbana Ndi MCP Si Ya APM Ndi Atupele Muluzi Koma Ife A Malawi - D Phiri

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 13 сен 2024
  • On Nyasa VoiceBox, D Phiri says that the battle to get rid of the MCP is not dependent on one particular politician but is a group effort that must be undertaken by all Malawians.
    Ku Nyasa VoiceBox, D Phiri wati nkhondo yochotsa chipani cha MCP sikudalira wandale m'modzi koma ndi gulu lomwe Amalawi onse amayenera kuchita.
    #malawi

Комментарии • 89

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 Месяц назад +6

    Anthu opanda nzerunu mumkati muone Zina, lero bwa? Osamunamizira APM ndi Atupele Muluzi, anatiuza koma kusamva. Tiyeni nazoni.

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw Месяц назад +6

    Vuto sii Atupele kapena APM ayi..vuto ndife ovota ..2020 anatiudza ndipo anazungulira dziko lonse kuti Ana anga musavotere idzi koma sitinamve .nde mukufuna kuti APM ndi Atupele atani

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera Месяц назад +3

    Amalawi vuto ndiwunkhutukumve APM ndi Atupele ananene lelo wina azibwela pano kunenazopusa boma munapereka ku Chikanga Congress party.

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz Месяц назад +3

    Ndizoona don't point them fingers because its malawians who voted for chakwera even themselves they did not vote him its malawians

  • @InnocentChikhwazaNkhoma
    @InnocentChikhwazaNkhoma Месяц назад +3

    Zoonadi amene watulisa vedio imeyi yoti APM ndi Atupele ndi odzikonda ndi wopusa kwamniri akuyesa amalawi ndi omweaja a 2019 Amalawi a lero 2024 ndi odxindikira. APM Atupele staya away from Malawi politics until 2025. Osamvera afiti a ku Malawi

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf Месяц назад +2

    Mwalankhula bwino.God bless you

  • @CharityChirwa-t1e
    @CharityChirwa-t1e Месяц назад

    Zowona osalimbana ndi atupele kapena APM zofunazathu ndizimene tikukolola ulemuwanu achimwene apa nde mwandifikapo god bless you always ❤

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i Месяц назад +4

    Pamenepo ndiye wayankhula bro point taken amalawi tokha tinawakana anthu awa 😂😂😂

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Месяц назад +1

    Good points mumatha broz Zofuna iziiii.. Tidikile 2025 achotse basi olakwa ndamene Ana votera chikangawa 💔💔💔

  • @user-mi3fw1zg8b
    @user-mi3fw1zg8b Месяц назад

    My brother kulankhula uku kokha may God bless you 🙏 ndiyeno uthenga wanga mmawa uno upite kwa Mbuzi yomwe imalankhula kuti a APM ndi At.M ndi ozikonda mumuuze kuti mapwala ake

  • @VincentNyabanga-dw9uj
    @VincentNyabanga-dw9uj Месяц назад +2

    Very true, it's our fault APM 2025

  • @mosysi324
    @mosysi324 Месяц назад +3

    Kuganiza mwakuya uku...

  • @KennethJack-un2wf
    @KennethJack-un2wf Месяц назад

    For sure brother yr true, ndipo Malawi ndi otengeka ndizithu zopanda pake .chakwela ngat anakwanisa kupha nzake kwa asembules mukuganiza ngat angakhale ndichison ndi munthu.

  • @muhabaulen7912
    @muhabaulen7912 Месяц назад

    Ulemu wanu mr d phiri munthu wazeru mulungu akupatseni moyo wautali🇲🇼

  • @Ghama-k4i
    @Ghama-k4i Месяц назад

    Totally agree 100% Malawians we are crazy tnasakha achakwera tiyeni tilimbe nazo bas

    • @SalaJawali
      @SalaJawali Месяц назад

      Kkkkkkkk anangendedwa Kale awa apume basi

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Месяц назад +2

    Akunena zoona nkuluyu.

  • @user-mj3ms4jt3b
    @user-mj3ms4jt3b Месяц назад +2

    APM ndi atupele ndi ana achepa kwambiri sangalimbane ndi MCP

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms Месяц назад

      How did mcp win tel me?

    • @MjombaMjuba
      @MjombaMjuba Месяц назад

      APM ndi Atupele Muluzi wonsewo pamtumbo pawo, nyini zamawo, mkongo wa mawo, sangapange china chili chonse. Atupele Muluzi mbolo yake ya jando sangalhale president wa Malawi. Zapamtumbo basi

  • @WistonMphande
    @WistonMphande Месяц назад

    I totally disagree with the one accusing APM and Atupele Malawians who voted for MCP are are blind. APM and Atupele are humble leaders .

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko Месяц назад +1

    Kuyankhula kwanzeru ndithu kp it up boss

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt Месяц назад +1

    Zoona bwanawe ameen

  • @damianokachingwe3531
    @damianokachingwe3531 Месяц назад

    Ndie APM wakakamira bwanji pa president nkhondoyi ndi yake basi komanso Atupele ukunenayo paja adalephera ndi u mp omwe kwawo

  • @stevietungama9775
    @stevietungama9775 Месяц назад

    100% True bro wayankhula facts ndipo anthu mumaganiza 👏👏

  • @yusuflifa2923
    @yusuflifa2923 Месяц назад

    Bro mwayankhula za nzeru.

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 Месяц назад +1

    Very true

  • @AgrementShadreck
    @AgrementShadreck Месяц назад +1

    Zoonazake malu

  • @EstelleChilemba
    @EstelleChilemba Месяц назад

    Very true boss

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho Месяц назад +1

    Correct

  • @retirementtoafrica
    @retirementtoafrica Месяц назад

    Mau achilungamo. Auseni. Oponya voting ndi amene amasankha ntsogoleri

  • @user-po6ir6eh4z
    @user-po6ir6eh4z Месяц назад

    Zoona broz walankhula bwino anthu akafuna kuona kusintha lero ndi zimenezi mabvuto amalawi munachita kufuna. Mwayi mulinawo osinthaso zinthu mu 2025 mukazafuna kupitiriza zizakhala ndi inu

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Месяц назад

    Yes ndipo ana kosamva Andi a tupele ndi a Peter amayankhula koma kosamva ndiye mukubulema anthuwa and ine ndikutukwana amene akuti anthu akuzikonda no don't blaming them you must blame your self

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt Месяц назад +1

    Ddp kapena UDF akareso limosi 2025 inshall allah

  • @FridayH.pontio
    @FridayH.pontio Месяц назад

    Iweyonso nyasi zako zileke

  • @saidimwanyali8969
    @saidimwanyali8969 Месяц назад

    It's true brother

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms Месяц назад

    Indeed bro

  • @AlieNkalapwagaNkalapwaga
    @AlieNkalapwagaNkalapwaga Месяц назад +1

    ❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-xt2gu9yt9q
    @user-xt2gu9yt9q Месяц назад

    Sidzingatheke voti yamuthu mozi kuwinisa muthu dzikufunika Ife amalawi tigwilane manja amalawi mcp itipha those tinsamale komaso tichenjele may akulu akoma akagonela kumalawi tasala ndiathu awili apm ndi atupele Basi tikangoaludza away Tanya kumaganiza

  • @NaziruWapete-j8l
    @NaziruWapete-j8l Месяц назад

    Ndipo mwayakhula zoonad bro zofuna za Malawi bas

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Месяц назад

    Ameneyo khansara wa MCPigs amenyedwe kotheratu.

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma Месяц назад

    Inu mukulimbana ndichakwela iye akumumenyela nkhondo ni ambuye

  • @KendrickLuckyc
    @KendrickLuckyc Месяц назад

    Zoonadi mavutowa ndi chisankho chathu vuto si APM kapena Atupele

  • @FaheemChipojola
    @FaheemChipojola Месяц назад

    D phiri mulungu akudalitseni pa mawu anu anthu ena wa kuganiza kumawavuta ndipo mene anatikondela ife apita muthalika mmmm amalawi tinataya udzu omwetamweta

  • @amosnyirenda-pl1ss
    @amosnyirenda-pl1ss Месяц назад

    chisilu iwe galu ndi madala ako okalamba wo Malawi siyikufuna zinthu zokutha kale

  • @FatimaUmali-pc8sy
    @FatimaUmali-pc8sy Месяц назад

    Kulakhula koma ndi kumeneko me phiri zikomo

  • @HamiltonSinosi
    @HamiltonSinosi Месяц назад

    That's true

  • @EdsonKamwendo
    @EdsonKamwendo Месяц назад +1

    Point bro

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 23 дня назад

    Ayi atupele anationetselatu pa chiyambi, kuzikonda kwake atani awuzeni mfumu a malawife kusamva , chilipo apa tigwilizane tichotse manyiwa basi, tisatonse zala awawa, koma ngati udf , dpp, utm, boma

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw Месяц назад

    Zoona blz wel speach. and kuvutika tukuvutika ndife .

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga Месяц назад

    Thank you my boss audio yanu ndiyovek

  • @ChrisEnos-to5uv
    @ChrisEnos-to5uv Месяц назад

    Zoonadi tinakana tonkha ndiye lero tisayakhule moipa ndani amene saziwa kuti mcp sichipani chochi votela mavuto tinabwelesa tonkha timavota ndi ife lero zinthu zafika ponunkha ndiye sisatenge peter ndi atupele kukhala anthu ozikonda ai mavuto osewa akubwera chifukwa Cha kusava kwatu ndiye tisayakhule morakwika

  • @JamesChimera-hw1nv
    @JamesChimera-hw1nv Месяц назад

    Chachitikacho ndichiweruzocha amalawi eniake amavota masana sizokokelanazo ayi anthu akuonaokha Chilungamo musapangilezoipa ngati umadana ndichipani zikuvutani ife sitikuyang'ana chipani koma chitukuko mukaluza muzivomera osamangomenyana nokhanokha palibe amafunakuluza koma mukaluza vomelani

  • @idris6597
    @idris6597 Месяц назад

    Zoona zokha zokha boss mavuto awa tinazilowetsa tokha

  • @user-wh2my2ey3l
    @user-wh2my2ey3l Месяц назад

    Iwe ndi.munthu wanzeru Apm ndi a tupele ndiosalakwa vuto ndife timafuna kuona zina nanga taona kale zinazo?, ngati apm oyipayo angamalimbane ndi kutsutsa zomwe timkafuna? Poti timkafuna izi. Tiphunzire kulemekeza zomwe tili nazo apm akabweranso tizaziwano ku wapatsa ulemu ndipo sitizanamizidwa ndianthu adyera

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Месяц назад

    Vuto si azisogoreli awa ayi koma thokha ndimen tinasakhir

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j Месяц назад

    Ndizoona amalawi sitimachedwa kuiwala timakopeka ndi zinthu zosakhalisa poononga nazo zinthu zomwe zikanatithandiza mavuto tawaonawa takhaulatu tisinyuke tisachitenso masewera anthu omenyera ufulu sakugona siku ndi siku kukulangizani anthu oti muzawabvotere tibvomereze boma lina Lili lonse linali ndi mavuto ake koma izizi zanyanya amalawi timakuuzani kuti ngati simukwanisa kukana zopasidwazo chifukwa cha mabvuto landilani koma muzawabvotere

  • @hagayichiluwe
    @hagayichiluwe Месяц назад

    Izi ndiye ziti?nkhani ya chisankho kumangochi uyu akukamba zina,,,,,kupanda manyazi.Chakwela my vote

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Месяц назад

    Zoonadi brother

  • @AlasonPaulo-ht7zb
    @AlasonPaulo-ht7zb Месяц назад

    Ukunena zoona broo

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p Месяц назад

    Congratulations 🎉🎉

  • @user-st6bt5vv9c
    @user-st6bt5vv9c Месяц назад

    Zoona zache siboza ai tooonse ambiri ndiamene tiwachose pampando

  • @AkbarAllih-ln6ky
    @AkbarAllih-ln6ky Месяц назад

    Ndichoncho big man

  • @user-ni4nw1ee2f
    @user-ni4nw1ee2f Месяц назад

    Otiuza analipo Koma kusamva kwanthu mayoooooo

  • @ShavickMzula
    @ShavickMzula Месяц назад

    Mzoona mbuyanga mtokha tinaika mcp

  • @Edson-sj8vn
    @Edson-sj8vn Месяц назад

    Man penapake mukunama ife sitizawavoteranso

  • @LumbaniMthala
    @LumbaniMthala Месяц назад

    Ndipo wachinyitsa chigoli mkumati couche walephera kkkkk koma adha

  • @AlomweWathu
    @AlomweWathu Месяц назад

    zowona zake okanika ndife anthu

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 Месяц назад

    Kikkkk kodi wakuuzani ndani kuti APM/Atupele atsogolele nkhondo??? Kubwera ena tiyeni tipemphere otherwise pair imeneyi sangayithe MCP zinakanika kaletu paja....

  • @Freedomchennl47
    @Freedomchennl47 Месяц назад

    Zoonad ife anthu awa tinawada nde lero tikwafunaso

  • @LuhangaLoti-k7l
    @LuhangaLoti-k7l Месяц назад

    Palibe chanzeru walankhulapo apa

  • @WatsonAmon
    @WatsonAmon Месяц назад

    Wanena za nzelu ase

  • @MjombaMjuba
    @MjombaMjuba Месяц назад

    Ukunama iweyo, mboro yako. Who is Atupele Muluzi

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 Месяц назад

      Ma scandal a Chakwera
      1) Atangolowa kumene anapita ku nsonkhano wa virtual koma iyeyo anapitakobe ndi anthu 10. Chi hall chonse analimo yekha ndi mwana wake; ankolo ake; mpongozi wake
      2) Anakagula fetereza ku butchery
      3) Analemba ntchito munthu oti apapanga kale retire mthawi ya Kamuzu ku immigration
      4) Anapha Chilima, Shanir, Sidik Mia, Raph Kasambala
      5) Anamanga Chizuma. Kenako anakhazikitsa commission of enquiry yomwe inapeza kuti Chizuma ndi olakwa
      6) Anagwetsa kwacha ndi 100%
      :
      :

  • @JafaliChiwimbi
    @JafaliChiwimbi Месяц назад

    Mbambande

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os Месяц назад

    Mukunenadi zoonadi

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Месяц назад

    Awaso ndi achisilu kusephana ndi nkhani

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Месяц назад

    Koma ndizoona atupele komanso DPP akugona iya

  • @damianokachingwe3531
    @damianokachingwe3531 Месяц назад

    APM odzikonda kwambr kaka pa udindo

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 Месяц назад

      Chakwera ali pa 3rd Term ku MCP pomwe APM ali pa second term. Mitu yanu simaganiza musanaphwise ndi pakamwa panu.

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 Месяц назад

      Chakwera mthawi yake ku MCPigs inatha kalekale koma akufuna kukhala president wa muyaya.

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Месяц назад

    Mcp kuwina ku mangochi?ndafabwatu ine

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Месяц назад

    Ndadabwatu

  • @ManifoldPhiri
    @ManifoldPhiri Месяц назад

    Palibepo chamzeru apa!!
    Za zii!!!!!!!

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 Месяц назад

      Chamnzeru koma kugwetsa kwacha ndi kugawa ndalama mmisokhano. Pamtumbo panu a MCP afiti nonse

  • @OretarbadrBwanali
    @OretarbadrBwanali Месяц назад

    Zoonad ndithu