ZIMENE PATRICIA KALIATI KOMANSO DALITSO KABAMBE AYANKHULA LERO......TAMVANI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 сен 2024

Комментарии • 92

  • @user-xo8ms5wh2s
    @user-xo8ms5wh2s Месяц назад +4

    Kaliat anakonza mai wochenjera kwambiri Mmalawi muno atapezeka azimai awa awiri kungabvuti zedi umatha Pati i love you❤❤❤❤❤❤❤

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi Месяц назад

      Tili nao koma amaopa apasaneni ma boord gurdz 😅😅

  • @DoYouKnow3838
    @DoYouKnow3838 Месяц назад +9

    Koma Kaliati ndi machine opangila machine anzake 🤗😂

  • @BoysonNgwenya
    @BoysonNgwenya Месяц назад +9

    Kaliati wadya ndalama from 2006 thawi ya bingu koma ndalama sikhutika respect madam kaliati proud of you 😂😂😂

  • @user-vi5qn7fj7z
    @user-vi5qn7fj7z Месяц назад +3

    Iweyo Patricia kaliat unabwera kuzakhala pa ndale keep it up

  • @DoYouKnow3838
    @DoYouKnow3838 Месяц назад +7

    Chakwera ndi Kaliati apikitsane pa debate eeeeeeee Chakwera akhoza kudwalatu😂

  • @AlexMatemba-r4w
    @AlexMatemba-r4w Месяц назад +2

    PK you deserve to be the president of utm and Malawi nation

  • @wisemanjere6572
    @wisemanjere6572 Месяц назад +3

    As it is, I vouch for mai Kaliti for UTM president. Go for it mama. Obwerawa asatinamize

  • @dzikomwahara4811
    @dzikomwahara4811 Месяц назад

    What a strong woman ever seen . Proud of you keep it up

  • @kadijachilwan967
    @kadijachilwan967 Месяц назад +4

    Never trust politicians onse ndiamozi amangofuna kutiyuza

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r Месяц назад

      Exactly. Anthu opusa andalewa ndithu

  • @falesiwillas-k8r
    @falesiwillas-k8r Месяц назад +3

    A utm ndikhalidwelawo lonyoza komwe akuchokera. Pitani kwinako nukayese ngat mtendere uliko. Zisankho simuwinaso agalu.

  • @EmmanuelChiwaka
    @EmmanuelChiwaka Месяц назад +1

    My brother Salambula mumatiyimilira

  • @PatriciaNabanda
    @PatriciaNabanda Месяц назад +1

    ❤❤❤❤my name

  • @user-vh1pf9kv8v
    @user-vh1pf9kv8v Месяц назад

    Akuti CHIKANGAWA😂 siinetuuuu osandisakasaka ai

  • @ophlexmkondowe8107
    @ophlexmkondowe8107 Месяц назад +4

    Manifesto ya UTM akanaikwanitsa ndi Chilima yekha basi no one else

    • @BoysonNgwenya
      @BoysonNgwenya Месяц назад +1

      Exactly and I don't trust these people

  • @hi-profileltd
    @hi-profileltd Месяц назад +2

    Mcp boma 2050 woooo

  • @Lingstone-r3z
    @Lingstone-r3z Месяц назад

    ❤ Unity with love all of Malawian people and activities with faith thanks for every one

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd Месяц назад +2

    Usi better kaliyati....wangowona kunkhala zimayi....

  • @SaviourTepu
    @SaviourTepu Месяц назад +1

    Usi is indeed not amember to UTM. Even ma speech onse amasonyeza ndithu kuti ndi wa mcp. Koma akungofuna chabe kubalalitsa anthu mitu

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Месяц назад

    You are the best mama at UTM

  • @RuthBinali-b8c
    @RuthBinali-b8c Месяц назад +2

    Mama ndinu one

  • @GladesMhango
    @GladesMhango 12 дней назад

    Monga wachinyamata ti vote pati UTM oyeeh

  • @user-vh1pf9kv8v
    @user-vh1pf9kv8v Месяц назад

    Mama awawa ndikatunduuu

  • @virginiakanjala6310
    @virginiakanjala6310 Месяц назад +2

    Nsaluzo zituluke kuno ku South. Tikukufunani pa Njamba

  • @StoneckJali
    @StoneckJali Месяц назад +2

    Very unforyunate speech

  • @user-mm4sr9gy5j
    @user-mm4sr9gy5j Месяц назад

    More fire kaliyati

  • @Dalitsozingani
    @Dalitsozingani Месяц назад +4

    Kabambe wabwera kudzaba UTM. Ma factory ikuyika MCP. osatinamizapo apa. Mwadziwa liti a Kabambe kuti UTM ndichipani chabwino.

  • @ChikondiSmart-rz2vf
    @ChikondiSmart-rz2vf Месяц назад

    Kaliat wa bodza ufuna utinamizepo apa a mtsogoleri wanu nd amene anangoculutsa kulonjeza km osakwanilitsa chakwera my vote

  • @VictorThemba
    @VictorThemba Месяц назад

    Ur super mama

  • @EmmanuelChirwa-z3n
    @EmmanuelChirwa-z3n Месяц назад +2

    Akaliyati azinamiza ana ama 2000, mpoto wake uti munamudzutsayo🤣🤣

    • @jestinanamkonda1495
      @jestinanamkonda1495 29 дней назад

      you just talk too much without principles. Chikagfawa issues will not give you votes rather the truth.

  • @williamsalexmbonga
    @williamsalexmbonga Месяц назад +2

    Inuyo simunawauze bwanji amzanuwo kuti asakwele ndege coz kuli chivungacho hahahahaha nde tsopano mwayamba kutsutsana ndi Michael Usi? Mmesa Chilima amati ayamba kuyimba bell tsopano

  • @ganizanitembo1492
    @ganizanitembo1492 Месяц назад +1

    Tell people what you will do to improve the economy madam provide alternative leadership

  • @sarahchimwaza5647
    @sarahchimwaza5647 Месяц назад +1

    Kaliatii umatha iweyo.

  • @BlessingsMaheya
    @BlessingsMaheya Месяц назад +1

    Skc anasankha Mai olingalila

  • @TiyamikeJobe
    @TiyamikeJobe Месяц назад +1

    Kaliyati anatha anthu anasiya ukukhulupilila

  • @user-om7yf5tq6g
    @user-om7yf5tq6g Месяц назад +3

    Crook ya munthu iyi ngati pali ma minister anaba ndrama za boma she is one of them. She could even use a Government truck to buy goods from Tanzania uyu.

    • @tingamasi106
      @tingamasi106 Месяц назад +1

      Nanga osamumanga bwa? Kupusa

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r Месяц назад

      @@tingamasi106amangidwa bwanji when oyenera kuchita ntchitoyo are corrupt like any other politician?? Palibe wandale yemwe azatukule dziko la Malawi

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge Месяц назад

    😂😂😂😂😂🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @LukaThawe
    @LukaThawe Месяц назад

    Zakumpoto ndiye musanene Mai ndiboza limenelo amene Azusa mpoto ndi chakwera. Ndiye akuziwa Kuti ku mpoto ndikumalawi not mbuzi inu ndizanu Peter machende anu

  • @yamikanimalunga8451
    @yamikanimalunga8451 Месяц назад +1

    SKC RIP

  • @LuciusByson-z7u
    @LuciusByson-z7u Месяц назад

    Aaaaaa athila kuwiri inu mesa mumkat tambala nde dzichan idzi hiyaaa dpp boma

  • @MarionMwenifumbo
    @MarionMwenifumbo Месяц назад +1

    Aaaaa Patricia pena umasongoneza zinthu

  • @ShalifRoma
    @ShalifRoma Месяц назад +1

    Akabambewa mulibe mfundo muli ziiii awa ndiye achita kutumidwa

  • @williamsalexmbonga
    @williamsalexmbonga Месяц назад +1

    Kabambe chavuta chizungu proboka pro eish limbikilani Chichewa chomwecho basi

  • @stephennyirenda8809
    @stephennyirenda8809 Месяц назад

    Ubwino wake a Malawi anatsekuka maso.
    It's up to them to decide in 2025.Talk is cheap.

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi Месяц назад

    Ku gender kumakunkharani mama

  • @ReubenGama
    @ReubenGama Месяц назад

    Mayiwa adayenera kutsogolera chipani utm

  • @joycemagalasi2207
    @joycemagalasi2207 Месяц назад +2

    Same lies

  • @frankmzomera2798
    @frankmzomera2798 Месяц назад

    Koma a kaliati😂😂😂😂😂

  • @williamsalexmbonga
    @williamsalexmbonga Месяц назад +1

    Kodi mmesa utm inalindi ma mp 4 okha

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana Месяц назад +1

    Koma kumeneko mwamuminitsa usi wanyaaa manyii

  • @ChristinaSimwaka
    @ChristinaSimwaka Месяц назад

    Kkkkkkkkkkkkklkkkk😅😅😅

  • @danieleneya808
    @danieleneya808 Месяц назад

    Koma mukuziwa kuti ena ali ku Israel 🇮🇱 Chipani chanuchii timachikonda apa nde mwanyereratu takutulukani ndinu anyapapi apapa 😢

  • @FranceQongwane-ro5yr
    @FranceQongwane-ro5yr Месяц назад

    😂tizasiya katangale according to kabambe,and utm believes him

  • @ChidaPhiri
    @ChidaPhiri Месяц назад

    Michael Usi akulakwa zedi ayenela kuchotsedwa

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o Месяц назад

    Abiti makandulo yauzimu mukutokota heavy

    • @AmoTiamo
      @AmoTiamo Месяц назад

      Iwe ndoomvesa chisoni chikanakhala Kuti mu ndege munali mbale wake am sure sukanalankhula matuzi akoo

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 Месяц назад +1

    Akwen kachaso bibida too much

  • @BoysonNgwenya
    @BoysonNgwenya Месяц назад

    A before jesus christ 😂😂😂😂

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx Месяц назад

    Chonde osavotera Dr chikangawa chonde munthu oipa

  • @user-pc3jg6pd1h
    @user-pc3jg6pd1h Месяц назад

    Uku nde kung'alulatu

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Месяц назад

    Tamuwuzani usi asiye kunyoza chilima please

  • @josemoises7742
    @josemoises7742 Месяц назад

    A LUTA CONTINUWA koma amalemba A LUTA CONTINUA....
    ZIKUNDISANGALASA ZA NFUNDO YA UTM NDITI KU MOÇAMBIQUE NDIE KUATO MAPUTO

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb Месяц назад

    Zomwezi zoweta agaluzi mpaka kukondela

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx Месяц назад

    UTM moto usi apanika ndi chitseko Yudasi

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 Месяц назад

    NDIKUFUNA KUKUWUZANI IZI PLESASE OSAMULOLA MAGANYA KU UTM CHIFUKWA CHOTI MANGANYA SIKUTI NDI WA UTM AI MOWOPA MULUNGU IZI NDIKUNENA MOWOPA MULUNGU AKUFUNA KUKUPUsiTSANI KUTI CHAKWERA apeze mpata wakupha anthu amene ndinu wodalilika ku chipani chanucho komaso mukuwoneratu kuti ndamene anapanga ma pulani wamupha Achilima pamodzi ndi gulu lachakwera nsimukutha kuwona pamenepa nokha manganya ndichitdilu kwambili

  • @muyabasamson
    @muyabasamson Месяц назад

    Phavu osatakgwanika nigalu usi

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw Месяц назад

    Makaliati zukani pano ndifundo zanu zili bwino

  • @solobertkamunga2826
    @solobertkamunga2826 Месяц назад

    Kabambe ndi zero EQ

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere Месяц назад +2

    Kodi akabambewa adziwa liti kuti UTM ndichipani chokoma?

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi Месяц назад

      Namga chilima anaziwa bwanji kut mcp inali ya bho ndale us dirty game

  • @mathewschifya764
    @mathewschifya764 Месяц назад

    Yongo wayongo anali chipani chanji?

  • @EnockMuyaya
    @EnockMuyaya Месяц назад

    Musarore kubwerara kuthiko

  • @hopesonmumba1056
    @hopesonmumba1056 Месяц назад

    zaziii😂😂😂

  • @FavourAmos-rx5fl
    @FavourAmos-rx5fl Месяц назад

    Ndinyambo akufuna kukola msomba tikamadzazinfikila madzi afika nkhosi

  • @dawsonwaya4722
    @dawsonwaya4722 Месяц назад +1

    Zaziiiii numadziwa kuti mukhala pa kaliyala ,ndikumayankhula zoti kudya katatu,komanso fertilizer otchipa,lero mukuti samaimba belo, hahaha malawi wake siwalero,muname zina,izo ayi,anzanu ayendetsa boma movutikira chifukwa cha manifesto anu abodzawo ,shut up ,patricia

    • @PearsonYonah
      @PearsonYonah Месяц назад +2

      Choka iwe ukunyoza Mai Kaliyati Kaliyati akunena zoona otsutsana naye ndi nfiti mwazolowera kupha anthu inu

    • @florachizungu
      @florachizungu Месяц назад

      Ndipo zoona anthu akupha inu...Mukumunyoza kaliati kuti watani zopusa basi mukhara choncho afiti inu