BON KALINDO LERO PA 16 DECEMBER WAMUNG’ALURA PRESIDENT CHAKWERA ZOKHUNZA IMFA YA SAULOS CHILIMA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 17 дек 2024

Комментарии • 125

  • @CosmasKaunde-i7y
    @CosmasKaunde-i7y День назад +11

    The DC anakhuzika kwabasi kumapetoku he nearly cried
    Mumatimirira

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale День назад +3

    MCP will never be forgiven for what they have done to Chilima😢😢 The guys has reached the unreached areas to campaign for a change, He was the only hope for the hopeless...He was hated by selfish and greedy leaders who has no passion for the welfare of bare and hungry poor people ...Chilima is only leader that Malawi will never have , he was man who never tolerate nonsess😉 Chilima will still be in the heart of no people for a prolonged time..Continue resting in peace My President😢😢😢

  • @replacefruittreenursery
    @replacefruittreenursery День назад +2

    Very sad and unbelievable the history of malawian for ever. R I P chilima .

  • @JessieNgwira
    @JessieNgwira День назад +9

    Bon is very right I salute him

  • @samsonchitseko-w5q
    @samsonchitseko-w5q День назад +2

    Your right bigboss

  • @kittymalambo1853
    @kittymalambo1853 День назад +1

    Mmmh waliratu Kalindo simmene amamalizila Booon Kalindo the DC, ndizowawa koma abale anthu aja anafa imfa yowawa kwambiri 😢

  • @JanetKangoma-x1k
    @JanetKangoma-x1k День назад +12

    Ndalira kwambiri kulilira Malemu Dr. Chilima president amene ndinkamudikilira kuti asintha Malawi, mzimu wawo upitirize kuusa mu mtendere

    • @RodgersMwanakhu
      @RodgersMwanakhu День назад +1

      Ndipo inu mmmmm 😭😭😭😭😭🕊️

  • @clementzintambira4796
    @clementzintambira4796 День назад +1

    There's no hospital report n people who were talking or eye witnesses are nowhere to be found, what Malawi do we have now 🤷‍♀️🙆‍♂️
    The army which used to defend us, quite now 🇲🇼🇲🇼😭😭😭
    God deliver our nation please in history of this nation we have never seen this, first of its kind. 😭😭😭😭

  • @quincyswart1884
    @quincyswart1884 День назад +4

    The ending part. So painful Mr DC😭

  • @DamaliceWamalanguluko
    @DamaliceWamalanguluko День назад +2

    Achakwera adalakwitsa kusainila kuti chilima aphedwe ichi ndichosantha pa moyo wa amalawi

  • @paulganizani7392
    @paulganizani7392 18 часов назад

    It's sad development,will never heal as a country 😢

  • @BrendahNaphiri
    @BrendahNaphiri День назад +2

    ndipo ndizonvetsa chisoni mpaka pano sindukhulupilira hmmmmm anapitadi SKC😭

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz День назад +3

    Chakwera must resign chakwera achoke

  • @RodgersMwanakhu
    @RodgersMwanakhu День назад +2

    Chilima wanga ine mmmmm rest well Bhiyeni 😭😭😭🕊️

  • @SusanZulu-k1q
    @SusanZulu-k1q День назад

    The DC cried at the end, very sad indeed.

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i День назад +1

    Yoo! DC walilira malawi inenso ndimanena kuti mmalawi muno mulibe presdent mudzikhlupilira panopa ndife nkhosa zopanda m'busa.Presdent tikhala nae 2025 amene adzatiuze cilungamo cha ndege mcp ndimene inapha 9 aja sangatiuze cilungamo.DC umatiyimilia ife a malawi ofuna cilungamo timakunyadila.

  • @patsonkumwenda456
    @patsonkumwenda456 День назад

    Kumapeto the DC made cry 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani День назад +1

    Amalawi tikulirabe koma panopa tiyeni tilire tikuyang'ana kwa Mulungu kunena zoona anthu onse omwe ikuwakhuza pa imfa imene ija adzalandra chilango pansi pompano

  • @IsabelLuka-i8f
    @IsabelLuka-i8f День назад +2

    Namadrama anaona nkhondo, mumanenaditu zowona Mr DC ulemu wanu osatopa,osafowoka osaopa

  • @BazukaChikungaM23
    @BazukaChikungaM23 День назад +4

    Akamati anthu anafa Ndenge ikali mmalele ndiye kuti oyendetsa Ndegeyo amayendetsa wakufaifa😂? Ngat anthu anafera mmalele onse ndiye ndegeyo imalunjika bwanji ku chikangawa😮? Anthuwa anafa alibe Magazi Mmalele ndiye magazi anapita kut kapena anthuwa analibe magazi ngat Chiwala? Anthu ayenda bwanji akufaifa Zonse anakamba zija sizikuveka its Nonsense manyi ya Chakwera. Anthuwa aja awuse mumtendele.

    • @jamesFoster-dx4ur
      @jamesFoster-dx4ur День назад

      Ndipo manyi nsete zenizeni ndipo zosamveka koma anthu oyipa mtiti ndipo chonena kutha ambuye ndamene akudziwa

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni День назад +1

    Usi udziwe kuti tsiku Lina adzakuumisa magazi ndimkozo😢😢

  • @MuhammadAyatu
    @MuhammadAyatu День назад

    Tili pambuyo pan Mr bon kalindo udalisike kulikonse komwe uliko❤

  • @austinvincent773
    @austinvincent773 День назад +1

    Kalindo ndiwe wabodza umaidziwa ngozi ya ndege ukati akanangovulala ukuona ngat galimoto kupulumuka pa ngozi ya ndege ndichisomo chamulungu chabe koma sizimachulukila ai

  • @vittazomba
    @vittazomba День назад +2

    VN iyi mmene yathera zandimvesa chisoni Bon kalondo samayankhula choncho kumapetoko😢

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august День назад

    Ndipo zoonadi Mr Bon Kalindo kufikira panopo sindikhulupirira kuti ku Malawi kungachitikedi zimenezi Ambuye woziwa chilungamo apitilize kuipasa chiusiro chositha ku mizimu imene inafa pangozi ya ndege imeneyi 😭😭😭😭😭

  • @austinvincent773
    @austinvincent773 День назад +1

    Kalindo ndiwedi wamisala samanama anthuwa iwe president akadzimange yekha 😂😂😂😂😂utanena kuti ose amene amamunamjza president kuti ndege inafika kumzuzu anabwezedwa ndamene amayenela amuchotse osati izo zoti president adzimange yekha ndiwedi wamisala hvy

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l День назад +1

    Amen 🙏🙏🙏🙏

  • @PrinceAmanson
    @PrinceAmanson День назад

    Don't cry God is watching

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 День назад

    Zoona zeni zeni Kalindo, Dzamalala sapereke umboni pazifukwa. Tisinthe boma tidzadziwa zoona zenizeni.

  • @TamboChaps
    @TamboChaps День назад

    Bon kalindo is very true on that why chilima why and the of the people who were in plane crash to face this

  • @ShiraKasekaNyirenda
    @ShiraKasekaNyirenda День назад

    Zikomo the DC🔥🔥🔥

  • @LennieblessSimbi-q2r
    @LennieblessSimbi-q2r День назад +1

    Tiyeni tikangomasha tiyeni panseu tiyeni tikamuchotseko Kodi ife tinamuika pampando Kodi timangodziwa kuika munthu pampando koma kumuchotsa sizimantheka inu ngati uyu sitimuchotsa oyipangati ameneyi ine ndikuvakuwawa

  • @martinkhozombah
    @martinkhozombah День назад

    First comment,🎉 2024😊

  • @JrAlfeoLungu
    @JrAlfeoLungu День назад +1

    Koma nde watizudza chakwela 😢

  • @gertudebandah1758
    @gertudebandah1758 День назад +1

    😊😊😊😊kumvetsa chisoni kulila kwa munthu wamkulu Ambuye atithandize dziko lathu likuvutika 😮😮

  • @GeorgeSathula
    @GeorgeSathula День назад

    Koma guys chakwera chilichose angapange amalawi angomukuwira. Kod minyamakapena chani koma the DC bon tawaitaniren pambari achakwera kutheka mukama zuzula. Amapanga manyazi kuti mumazuzulila pagulu chakwera wamisala anaonankhondo mumamusha namadiramayo Ndiamenewo angakuomboleni bola ndanena

  • @TundeMarry
    @TundeMarry День назад

    Katswiri DC✊️

  • @JosephMakatha
    @JosephMakatha День назад

    The ending is painful..this guy feel our pain .....🥺🥺😭😭

  • @jamesFoster-dx4ur
    @jamesFoster-dx4ur День назад

    The DC mpaka kulira ayi zomvesa chisoni kwambili ndipo achilima anatisiya pamavuto ambuye odziwa kuweluza aweluze aliyense amene anatenga gawo pa imfa chilima

  • @Martha-x8z
    @Martha-x8z День назад

    Pepa DC moyo ukupweteka zoonadi mabala asusulidwanso

  • @CarolynLuwemba
    @CarolynLuwemba День назад

    Zonadi kalindo

  • @AliceJere-k9v
    @AliceJere-k9v День назад

    This is sad....zandikhudza

  • @GodfreyKamphiripiri
    @GodfreyKamphiripiri День назад

    ❤❤❤Kaswiri DC

  • @GOSH-c8y
    @GOSH-c8y День назад

    KOMATU MUKADZATENGA BOMA KALINDO OLO KU EMBASSY INA YAKE MUDZMPITITSE OSATI ADZIDZAKUONERANI MUKUDYA BWINO IYE AKUFA NDI NJALA, NDIYE TIDZAMMENYERA UFULU CHIFUKWA SAKUFUNIKA KUDZAYIWALIDWA

  • @lucymsiska5903
    @lucymsiska5903 День назад +1

    The end💔

  • @InnocentHassan-m3r
    @InnocentHassan-m3r День назад

    Boooorn kalindo ❤❤❤❤

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 День назад +1

    Ndipo zoonadi bwana kalindo ife tinalozedwa kwambili chilungamo chikuoneka koma anthu tangokhala amayenela kuchosedwa afitsi amenewa

    • @jamesFoster-dx4ur
      @jamesFoster-dx4ur День назад

      Ndipo kaya tudikila chani ?? Amayeneradi kuchoka pa mpando masatanic amemewa

  • @KambonaDaud
    @KambonaDaud День назад

    Ing'aluleni munthu wamkulu

  • @GodsFavourite1
    @GodsFavourite1 День назад

    Its really painful 😢
    ...my country ndakulila shuwa😢😢

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni День назад

    Shame kulakwa abale , may their souls continue to rest in peace😢

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 День назад

    Mcp chipani chamagazi basi kuyambira Kare

  • @DadyPatrickMtondo
    @DadyPatrickMtondo День назад

    Boma limeneli likangochoka pa mpando,kudzamanga everyone including those in this called commission of enquiry.

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 День назад

    malawi ndindziko lamanyi lamanyi kwambiri. Failed state

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl День назад

    President wil do nothing bcz he's also involved in the incidents

  • @BazukaChikungaM23
    @BazukaChikungaM23 День назад +1

    Komaso Funti ziwili zimatani mundege Muja MCP ndinu akangalu akuluakulu ndinu Fiti zoopsa jwambili koma zopemphera

  • @GiftKaziyambe-u4p
    @GiftKaziyambe-u4p День назад

    So painful and takes time to heal 😞

  • @JohnfosterNkusengwa
    @JohnfosterNkusengwa День назад

    Zoonadi and this report is not clear ndipo mr kalindo ineyo ndalila zedi report ili akanangosiya kuti president wina atabwere 2025 azaing,alule yonse mcp ku ndende plus onse amene appanga comition of inquiry iyi kundende ndipo iziz fun asafune zizachitika receive my condolences again malawi eshii mmmm All the way from cape Town pa boma mr kalindo ❤❤❤❤❤

  • @GeorgeSathula
    @GeorgeSathula День назад

    Komaso munthu wamzeru ndiamene amamva malangizo munduwina wake kukuuza kuti akolo ndila imeneyo musaduse iwe kuti ndidusa kukapezako makolo apolice kukapezapo iwe ukuchokera pompo apolice kukutenga Kodi amakuuza uja ungamutenge kuti wamisala izindapangira chakwera samamva

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar День назад

    God bless Malawi

  • @smartchisoni2143
    @smartchisoni2143 17 часов назад

    Report lenileni lowona lizamveka MCP ikazachoka pa ulamuliro wina azanena plot yonse mmene zinayendera

  • @MaryMalemia
    @MaryMalemia День назад

    Tsono inu osapanga yanu inquiry yolondola bwanji? A lot of issues: musamaike mawu mkamwa mwa achibale, inuyo ndi amene mudzayambitse Nkhondo, tsono inu mwatani kuchoka pa easy, Kodi APM m'mesa anebera chisankho kumubera Chakwera? Nkona suli president iweyo, maganizo Ako amenewo, ulu ndi mantha ndiweyo, tsono zikutheka bwanji kuti iweyo ulibe information ngati wanzeru? Mumafuna report lotani? Choka iwe! Nfuti zakuti? Bola pano mukuoneka bwino nkhopeyo, poyamba umaoneko ngati chitubuwa iweyo, wasalala ndi ndalama zaboma. Sudziwa nkhani anzako Ali ndi nkhani zogwirika osati zam'maluwa

  • @vinceynyone6693
    @vinceynyone6693 День назад

    Ndege sinaphe Chilima ayi, Koma MCP inapha Chilima may his soul rest in peace 🕊️

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s День назад

    SDA YANGA YAPUSRATU NDI ZOTSALA ZA REPORT LOTERERI.

  • @HenryJamson-c1d
    @HenryJamson-c1d День назад

    the dc

  • @GOSH-c8y
    @GOSH-c8y День назад

    EMOTIONAL BON KALINDO

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 День назад

    Zoonadi the dc chakwera akuziwapo kathu basi koma thawi yako iwe crocodile ikwana pompano usaone ngati dziko ndi rakwanu

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO День назад

    Ngati mdziko muno muli chizolowezi choti atsogoleri olo anzunze a Malawi chotani, koma akapuma amakhalabe a fulu zithe! Uyuyu ndiye akaone Maula Basi.

  • @Chiss-w3e
    @Chiss-w3e День назад

    Musazafe inu abon kalindo

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi День назад

      Mesa kodi ankat anamwalira chifukwa chakulekeledwa pansi nde pano akut afa mwamba ahhh izizi pena zikumabalalisa anthu bwanji

  • @wilsonchimtikaphiri9496
    @wilsonchimtikaphiri9496 День назад

    Ndipo zomwe mcp idachita mmmmmmmhhhh , no piece in democracy

  • @AndyWilliams-b3x
    @AndyWilliams-b3x День назад

    The end is hurting

  • @princephilipmasambewa6410
    @princephilipmasambewa6410 День назад

    Boss mumakwana

  • @MaryMalemia
    @MaryMalemia День назад

    Kodi iwe sunatope!

  • @ahmedsema2149
    @ahmedsema2149 День назад

    Chilungamo chidzadziwika nthawi imakwana pangatalike motani

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni День назад

    Live

  • @JonaSato-j8e
    @JonaSato-j8e День назад

    The D.C. ❤

  • @AlexKamfosi
    @AlexKamfosi День назад

    Ausemutendele chilima ndiazizaoose. Chakwela azayakha. Sikulina. Likuzalo

  • @Nelliembite
    @Nelliembite День назад

    Ngati mukufuna Kuti mizimu Yao iuse mupeleke repoti Yoona Komatsu bwalo lakumwamba mukayankha

  • @MayamikoMlenga
    @MayamikoMlenga День назад

    Ndipo zimadabwitsa kwambiri kuti amalawi amangovomeleza chilichonse

  • @Fkaymw1Kadango-by5mu
    @Fkaymw1Kadango-by5mu День назад

    Ndipo simakhulupiliradi

  • @lusayomathiya6551
    @lusayomathiya6551 День назад

    Uyu akufunika kumangidwa

    • @gospelsuleman3072
      @gospelsuleman3072 День назад

      Paja samaopa kumangidwa, you can even go and arrest him today

  • @RajaAlicky
    @RajaAlicky День назад

    Tangogulira kusinjayo

  • @AlexKamfosi
    @AlexKamfosi День назад

  • @issahmaloto9141
    @issahmaloto9141 День назад

    Vuto tafasa kwambili chakwera akupha anthu mu njila zambili

  • @BlessingsHarneck-p3y
    @BlessingsHarneck-p3y День назад

    COME ON COME ON

  • @RuthKaunda-tc5qd
    @RuthKaunda-tc5qd День назад

    Painful indeed

  • @Mirriumkamwendo
    @Mirriumkamwendo День назад

    A kalindo mukutiimilira , chimwendo Banda afunsidwe amene anamuuza kuti asakwere ndege yazaza

  • @StevenMasiku-xe4zx
    @StevenMasiku-xe4zx День назад

    😢😢😢😢

  • @violetkamfose6693
    @violetkamfose6693 День назад

    😭😭😭😭😭😭😭 So many questions????????

  • @lolinichitute
    @lolinichitute День назад

    😭😭😭 🙌

  • @gospelsuleman3072
    @gospelsuleman3072 День назад

    😭😭😭😭😭💔💔

  • @AliceChipeta-pc3nb
    @AliceChipeta-pc3nb День назад

    Zoona timaonangati abwelaso mmmmm chilima iwe ilikuti

  • @trifoniachilunda6263
    @trifoniachilunda6263 День назад

    Zovuta ndinthu Koma chakwela zoona kumupha chilima chifukwa chaudindo wapaziko lapasi Mmmm. Ayi mulungu achitenawo ose anatengapo Mbali kupha chilima

  • @HenryChapweteka
    @HenryChapweteka День назад

    Black box ili Kuti owe chikangawa

  • @JoeKay-o2s
    @JoeKay-o2s День назад

    Koma ndaseka😂😂😂😂

    • @JafarWiati
      @JafarWiati День назад

      Uzaseka ali m balewako

  • @JimmyMhone-b5p
    @JimmyMhone-b5p День назад

    Lazaro watinyasa ungofa bwanji?

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d День назад

    Boma lamwazi😂😂😂😂

  • @InnocentNgulube-f5c
    @InnocentNgulube-f5c День назад

    Apo mukuwapasa njira yot zivute zitan 2025 awineso basi kuopa kukathera kundende abera ndthu chisankhochi

  • @stormchatepa134
    @stormchatepa134 День назад

    Waliratu uyu

  • @JamesPhiri-h7p
    @JamesPhiri-h7p День назад

    Zovuta kwambiri eish Boma ili

  • @JudieBanda
    @JudieBanda День назад

    Hhhhhhhuh zomvetsa chisoni kutulutsa report la bodza