BRIAN BANDA NDIYEMWE WAWERENGA NKHANI ZA LERO, INU KOMA ZIKUCHITIKADI KU MALAWI KUNO IZI ZOONA?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 16 дек 2024

Комментарии • 30

  • @AnkoloAkutsidya-kn7gc
    @AnkoloAkutsidya-kn7gc 2 часа назад +3

    BRIAN BANDA Ndiwe Dolo kwambiri umatha ngakhare kuwelenga Nkhani respect to U Boss

  • @MusaAman-r1z
    @MusaAman-r1z 2 часа назад +2

    Malawi let's pray all together our lord is most merciful

  • @BadmanbBeesca
    @BadmanbBeesca 2 часа назад +5

    Chimwendo tionesana poti ndiwe dolo anthu 6 sangalimbane ndi anthu 20milion uziona kunali anzko pano alikuti uzimfunse

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 2 часа назад

    Thanks BM TV HISTORY UMAYITSATHA 🎉🎉

  • @AustinMhone-r3s
    @AustinMhone-r3s 2 часа назад +1

    Malawi is lacking good leadership that's why is the poorest country in the world.

  • @DavisSeyani
    @DavisSeyani 22 минуты назад

    Kodi mukukakamila maudindo mufuna kuti muzipha anthu?

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p 3 часа назад +1

    Kupusa kotani nanga kuganiza kuti mabungwe athu achinyengo omwe a Afro barometer ananena, alibe nawo gawo pakusankha kumeneku. RCB aikuganiza kuti Amalawi ndi opusa.

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 10 минут назад

    Nanga ku Rumphi katumbi Hewe enaso nyumba inagwela ana atatu awiri Ali ku chipatala pa Rumphi district hospital chifukwa cha mphepoyo zili patipo? Mwina mmango ona ku mwera kokha? Fufudzani Kuti muone chilungamo

  • @MwaiHillso-p6b
    @MwaiHillso-p6b 2 часа назад

    Abela kale mavoti nde lero akuyankha ntuxu cos mbali yawo athana nazo

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 3 часа назад

    Koma nde zakwera heavy .....tilibe kothawila chilichonse .... Chikungo....kwera eeeeish😢

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 4 часа назад +1

    Wanthu wokupha aziwanda,mbava Za MCP Chikangawa pamtumbo pa mawo

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 3 часа назад

    Ndikuti ndibwerera zeni zeni ku MCP kulibe wanzeru ngakhale pang'ono kaya chipani chimenechi ndingachifanizire ndi chani kaya? Kuvunda kwenikweni Kwa chipani

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p 3 часа назад

    How silly to think that the corrupt institutions don't have a hand in this selection process. RCB really thinks malawians gulable and naieve.

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 3 часа назад

    Ayi asamuchose ayi sitirora ife chakwera aramurireso ndipo azigwesa vula azitumizaso vula aizipha mesatinamusakha tokha chakwera ndeno tikuriraso chabi

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 4 часа назад +1

    Kkkkkk mcp mitu zao mulibe zelu alowelabwanji pomwe ndi awo omwe

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p 3 часа назад

    Then they all failed in the selection process or it was deliberate. They failed to note the compromised positions and their affiliation to MCP.

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 3 часа назад

    Achoke sitikuwafuna ...ife Amalawi.....

  • @djthembizo265
    @djthembizo265 3 часа назад

    Koma Jane Ansa nde munatipanikiza kuti tizichemelela kuti achoke eti?

  • @AdamAhamad-k2i
    @AdamAhamad-k2i 3 часа назад

    Kumtumbo kwanu agalu a MCP anthu okupha

  • @ChrispineJonathan
    @ChrispineJonathan 4 часа назад

    Atukedi pasi maudindo awo sitikukhulupilila

  • @wilsonchimtikaphiri9496
    @wilsonchimtikaphiri9496 4 часа назад

    Apatsidwa ndalama ku mafumu pomatizunza nkumaitanisa ziphaso

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 4 часа назад

    Ngati akulaphela kuyendetsa bwino amayenela kuchotsedwa basi

  • @wilsonchimtikaphiri9496
    @wilsonchimtikaphiri9496 4 часа назад

    Konse kuno ku Lilongwe

  • @Hendersonspoon
    @Hendersonspoon 3 часа назад

    Statistics onama ameneyo Mene zikukwerera kumati zikusika shame on you

  • @IgnatiousKaombe
    @IgnatiousKaombe 3 часа назад

    Ntchito yawavuta

  • @ChuluMsounds
    @ChuluMsounds 4 часа назад

    Atulepansi maudindo antuwa

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 3 часа назад

    Chimwendo yo asatsewele ndi amalawi.judicary,imuchonse ameneyo.ife,monga aweni ziko,osati la mcp,ifeyo malawi ndi wa ife tikuti,achonsedwe,ameneyo.judicary,ya ziphuphuyi ichonse anthuwa mwa changu olo tidzakutidzimulani,koko.

  • @NicolasKamunga-rv9vr
    @NicolasKamunga-rv9vr 4 часа назад

    Azipita sitikuwafuna