BON KALINDO LERO PA 17 DECEMBER WATHA MAU NDIPO WASAMBWANZA AKUTI NTHAWI YOOPA MUNTHU ALIBE

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 16 дек 2024

Комментарии • 64

  • @OfwaMwambila
    @OfwaMwambila 11 часов назад +18

    I was deeply surprised by the attitude of chakawra to not go visit the site where CSK died.such low thinking of a leadership of this government so inhumane 😢😮. Power can indeed corrupt a man's soul to be come so blind to reality

  • @RichardAlick-o8k
    @RichardAlick-o8k 12 часов назад +6

    Guys uyuyu akuyankhula chilungamo a dpp tonse tiyeni tipange zomwe akunena mkuluzi tisamalimbane ndi ndale zachimidzi zokangana tiyeni tikonze campaign wabwino osati zopoilazi i love dpp two much

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 9 часов назад +3

    The DC Boooon Kalindo president wa aphawi Malawi kutiyankhulira ife amene tilibe mau 🙏🙏🙏🙏

  • @elvienyirenda-ln3dm
    @elvienyirenda-ln3dm 10 часов назад +7

    The DC mwayimba bwinotu nyimboyo. Keep it up.

  • @MirriamChakanza
    @MirriamChakanza 4 часа назад

    Chilungamo chosayang'ana nkhope. Bravo the DC. Keep it up🎉🎉

  • @YankeazyMws
    @YankeazyMws 9 часов назад +1

    Chakwera kungoyelekeza kuponda pomwe anafera Chilima chachikulu chngathe kumuchtikr even kufa kumne munthu oipa kwambri ndpo Mizimu imukanthe mtendere asazaupeze konse😓😓

  • @THOSI-d1l
    @THOSI-d1l 2 часа назад +1

    Machine ounikila dziko la malawi the Dc

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 11 часов назад +4

    Misala koma a Chakwera mutu sukuyenda bwino mizimu ikuwakantha awa ndithu ayenda maliseche asiyeni mulungu ndiwadongosolo atimenyera nkhondo chilungamo chioneke

  • @BealiniaLangultone-jk5nj
    @BealiniaLangultone-jk5nj 12 часов назад +2

    The DC mulungu azikudalitsani mwalankhura bwino

  • @MercyNkhoma-b6h
    @MercyNkhoma-b6h 12 часов назад +3

    Ine ndi wa dpp koma nanenso ndinaona kuti dpp sinayankhule bwino ku Ndirande. Mwachita bwino kuwadzudzula, anthuwa pena samayankhula bwino.

  • @CourtexNzima
    @CourtexNzima 10 часов назад +2

    I understand you Bon Kalindo, one thing that I don't understand is what is behind your courage to do all this.
    Your analysis is in both truth and speculations. I think you should as well forward some truth and evidence that may condolence the groves.

  • @BujuWhyson
    @BujuWhyson 9 часов назад +2

    the most deadly child of T.A Mabuka .

  • @MphindiraChimwemwe
    @MphindiraChimwemwe 9 часов назад +1

    Keep it up kalindo umakwanira

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 9 часов назад +1

    MCP zamanyi izipanaga ku lilongwe konko....panya pawo
    Ku ndirande zopusa ayi iwe kalindo

  • @giveuslumbanishaba3079
    @giveuslumbanishaba3079 6 часов назад +1

    Every time I get a like,
    I will be doing 10 pushups.

  • @mathewssimbi3052
    @mathewssimbi3052 11 часов назад +2

    Ukunena zoona let's avoid any violence

  • @DannyDaka-t7z
    @DannyDaka-t7z 8 часов назад +1

    Bon kalindo timakuyadila

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 6 часов назад

    The DC amatha kuimba si wamaswelo ekha, akufuna azayambe kuimba atakalamba ngati Jetu.

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 6 часов назад

    The DC'S mwana woooopsa kwambiri akhalise Malawi chilungamo chiyende ngat madzi

  • @BrieMajoni
    @BrieMajoni 9 часов назад +1

    Bwenzi utankonda yesu indeee😊😊

    • @ChimwemweMajoni
      @ChimwemweMajoni 8 часов назад

      Hahahaha akuposa kuimba nabanda

    • @BrieMajoni
      @BrieMajoni Час назад

      @ChimwemweMajoni andiposaditu😂😂😂

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda 6 часов назад

    Kalindo afunseni kuti chimwendo sanakwele ndege bwanji? The DC the great

  • @BealiniaLangultone-jk5nj
    @BealiniaLangultone-jk5nj 12 часов назад +2

    Kung'amba kung'alura😂😂😂😂😂 kma DC anakonza

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 9 часов назад +1

    The dc 🔥🔥🔥

  • @HENZBYMakanjira
    @HENZBYMakanjira 6 часов назад +1

    The Dc mwana oopsya kwambiri😂

  • @KondwaniPhiri-l2z
    @KondwaniPhiri-l2z 7 часов назад

    You can sing brother kalindo

  • @likoyamakoka
    @likoyamakoka Час назад

    Is this one Bon kalindo whom I know

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 10 часов назад +2

    Kodi Yama vote amanyo ilipati

  • @CosterMustafa-m6h
    @CosterMustafa-m6h 11 часов назад +2

    🎉🎉🎉🎉Bon mmakwanila bas

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 9 часов назад +1

    The Dc 🎤🎤🎤🎤🎤

  • @AbdallahDaniel-q3x
    @AbdallahDaniel-q3x 4 часа назад

    ❤😅😅mumatiimililabwana dc

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 9 часов назад +1

    Uyambe wamuuza chakwera ndi azinzake

  • @amosnyongo6565
    @amosnyongo6565 9 часов назад +1

    Pajatu sing'anga wa chakwera ndi mkaz wake uja

  • @naomiphiri2228
    @naomiphiri2228 44 минуты назад

    Ndi zoona Saulosi basi 😭😭😭🙌

  • @FrankChitengo
    @FrankChitengo 11 часов назад +1

    Ndichoncho 🎉🎉❤

  • @ChristopherChilambe-g4z
    @ChristopherChilambe-g4z 6 часов назад

    Mawa akalindo wa ku studio basi inenso mdayamba kugula oyimba ndiyambila pa MR DC😂😂😂😂😂😂 umakwana more fire

  • @JonaSato-j8e
    @JonaSato-j8e 11 часов назад +1

    The D.C. zoona ❤❤😂😂😂

  • @WisdomJeremiah-s3y
    @WisdomJeremiah-s3y 11 часов назад +1

    Ukapha munthu ku maliro ake sapitako

  • @FelixJumby
    @FelixJumby 9 часов назад +1

    😂😂😂😂 the DC mwana opwa

  • @PillianiMekelani
    @PillianiMekelani 11 часов назад +1

    Bon ❤

  • @LimitedKasambala-k5c
    @LimitedKasambala-k5c 7 часов назад

    Ankamuna pachilungamo🔥🔥

  • @KondwaniGulonyonyo
    @KondwaniGulonyonyo 11 часов назад +2

    Kkkkk umakwana bon ati achite mwayi mwezi uno apita pa earia 30

  • @DavidKanyemba-n2s
    @DavidKanyemba-n2s 6 часов назад

    The DC Bon Kalindoooo

  • @AbdullahFyson-l3j
    @AbdullahFyson-l3j 9 часов назад +1

    Ayankhula ngt activist 😂😂

  • @Itemsworld
    @Itemsworld 8 часов назад

    I only believe that God isn't dead, and whatever happened, next year u will see the anger of God over those who took a hand a d those who are busy covering the truth from being heard publicly, God will show a true Himself, to these pple, whatever our big boss is doing,, even though his kids or his wife can't push him to be so remorseful over vising CHILIMAs plane cars point, I see him not being on the ballot paper, and our friends who are happy with CHILIMAs death will cry beyond as thier God will face death also not matter what

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 9 часов назад

    Zikulakwitsa panopa zofunika kulimbikitsa fundo zolimbikitsa mtendere n kuwalimbikitsa athu kuti zavote mwazeru

  • @KelvinMkholi
    @KelvinMkholi 9 часов назад +1

    Dc

  • @IbrahimIsmael-h2w
    @IbrahimIsmael-h2w 7 часов назад

    DPP ndi yowinawina kale koma mupewe kumalankhula mau oopsezana

  • @AnthonyChilinkhonde
    @AnthonyChilinkhonde 10 часов назад +1

    Kalindo asazafe

  • @KockoMunyapa
    @KockoMunyapa 2 часа назад

    Makes sense

  • @RoseChakwamba
    @RoseChakwamba 10 часов назад +3

    Abwana simuyangana mbali mukafuna kuzuzula keep it up mumakwanira

  • @EmmanuelkpPraise
    @EmmanuelkpPraise 5 часов назад

    Keep it up the good work the dc😢

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 8 часов назад

    Mwayimba bwino DC mwatitsutsimula.Tikudziwa a dpp amalankhulira kupya mtima potengela ndizomwe a satanic awa akucita(MCP); komano tisawatengele ife tilalikile dza mtendere.Ma jaji amenewo abwere pamodzi cikangawa amangidwe.DPP 2025 BOMA! APM 2025 BOMA!

  • @danielswaleyi9776
    @danielswaleyi9776 10 часов назад +1

    Bon, the initiative you are putting on is very good. My request is don't force him to visit that place

  • @McfastonMkhala
    @McfastonMkhala 9 часов назад +1

    Kalindo is just a very good noise maker, no any substance, no any take aways.

  • @annievitumbikonkhoswe770
    @annievitumbikonkhoswe770 6 часов назад

    I don't understand kuti iyeyo alipaudindo wanji?? Alimbali itiiii?? Afuna anthu titani??😮

  • @gladysmanthimba7851
    @gladysmanthimba7851 12 часов назад +1

    The best man mwana woopsya kwambiri 🎉

  • @dalitsonambazo
    @dalitsonambazo 7 часов назад

    Kkkkk km uyu akanakhala mbusa alindimau alibwinotu Mr sss DC

  • @FlorenceMainga
    @FlorenceMainga 6 часов назад

    Nyimbo imenei agula imeneyo aboma 😂😂