A NAMIWA AYING'ALULA _17 December 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 16 дек 2024

Комментарии • 45

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo 5 часов назад +3

    Romans 12:19
    Never avenge yourselves, but leave it to the wrath of God, for it is written, "Vengeance is mine, I will repay, says the Lord.Dear friends, never take revenge. Leave that to the righteous anger of God.
    KUMWAMBA KULI MULUNGU
    SKC forever In Our Hearts

  • @NickeshNdagama
    @NickeshNdagama 2 часа назад +1

    Namiwa he didn't run away commission of inquiry
    He come out bcoz of he wanted to be live and public, buy members they refused to admit public
    That's why he come out

  • @SaimonDavide
    @SaimonDavide 5 часов назад +2

    More fire Mr Namiwa timakudalirani

  • @EmsAdam-c1i
    @EmsAdam-c1i 4 часа назад +1

    Yomweyo comrade agalu amenewa atitola achoke

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 2 часа назад

    Kupha nyani nkusayang'ana nkhope . Olembedwa ntchito asamayankhulidwe mopsyatira ngati akulakwitsa ntchito .

  • @JacquereenPereira
    @JacquereenPereira 35 минут назад

    Zoonad Achakwela analakwitsa kupha chilima amene Anawaika pampando Eish chikumbuntina chikusowetseni ntendele ntendele Achakwela chilima anali phwanu amakukondani chilima athu amamuuza kuti akufuna akupheni koma sama zitengela pachikondi chake Mwana opanda mwano

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 56 минут назад

    Chakwera ndi wakupha ndi amene anapha chilima basi,amene mukutsutsana ndi namiwa ndi a mcp😂😂😂

  • @AhmedJali-xf3rw
    @AhmedJali-xf3rw 3 часа назад +1

    Namiwa ndiwedi olimba mtima kwabasi

    • @chipilirolikatho3572
      @chipilirolikatho3572 3 часа назад

      Not kulimba mtima koma uchitsiru umpawi umampweteka uyu, komanso sadamangidwepo, sakuziwa kuti cello imawawa bwanji amufunse Winiko

    • @NoelKhwimba-bh3ts
      @NoelKhwimba-bh3ts 2 часа назад

      ​@@chipilirolikatho3572 umphawi wake uli pat munthu wamulungu chilungamo chimawawa munthuyu akunena zoona 😢

  • @Nadeon-y2k
    @Nadeon-y2k 4 часа назад +1

    Ulemu wanu comrade Namiwa

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI 4 часа назад +1

    Achakwela munaphelanji chilima soka ndi thembelelo likhale pamutu panu

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 2 часа назад

    Osalimbananso ndi umboni wina Chakwela anapha chilima full stop..

  • @MwinkhulanaLulu
    @MwinkhulanaLulu 51 минуту назад

    Ndili ku mbuyo kwa Namiwa

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 5 часов назад +2

    Mu report mulibe chomwe chamveka akungosintha ma statement always

  • @BlessChilita
    @BlessChilita 27 минут назад

    Chibwibwi chamugwira nthawi yino

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 2 часа назад

    Ndege ija sinali yaufiti, potengela ubale wa chakwela ndichilima umene unalipo yankho ndiyoti chakwela anapha chilima kuti Aimenso 2025,

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 2 часа назад

    Asembles of God mumati munali ndi m busa kumanena chakwela mitu yanu imagwila? Simumaona kuti chakwela ndi ozelezeka, Chakupha, chinyau? Nonse assembles of God Pantumbo Panu.

  • @StefanoBinwell-f6x
    @StefanoBinwell-f6x 2 часа назад

    Mbuzi ya munthu iwe ngati anthu omakanika kubweletsa umboni kuseli kulibwanji live ndiwe mbuzi fwetsiki

  • @OliviaKhan-z2m
    @OliviaKhan-z2m 2 часа назад

    Kd inuyo munatulukilanji atakusakhan mumafuna mudzidzatsutsa ngat amzeru bwanji nde inuyo muona kt anachita kutan

  • @JoyceMoloya
    @JoyceMoloya 2 часа назад

    Akuti mwakhutila ndi report nu mukhale chete mwina simukuva bwino.

  • @zachariakhunkhu5093
    @zachariakhunkhu5093 10 минут назад

    Namiwa didn't run away but Chakwera and his entire members are murderers

  • @altonchikaoneka-6848
    @altonchikaoneka-6848 2 часа назад

    Anamiwa mukufuna kuoneka dolo ndinu opusa musanamize mtundu wa amalawi iwe unathawa chani ngati umakonda mtundu wa amalawi

    • @NoelKhwimba-bh3ts
      @NoelKhwimba-bh3ts 2 часа назад +1

      Ngat report mwakhutira nalo nkhalani chete osati kuyakhula motumbwa apa

    • @altonchikaoneka-6848
      @altonchikaoneka-6848 Час назад

      @NoelKhwimba-bh3ts amwene tizimva ziti ngati namiwa anali dolo sakanathawa musamatipusitse mukuphatikiza ndale ndizangozi anthu akafukufuku muyika angati chilungamo mukuchidziwa kuti ndingozi mukufuna mpaka ziwawa ife tili ndimaudindo osamala miyoyo ya anthu , mukufuna payifa imeneyi pafe anthu ambili chifukwa chozunguza mitu anthu ngati ndinu madolo ndinu amabugwe ndikudziwani mukudyera momwemu ma funding.

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 3 часа назад

    Amalawife mdi anthu ogona ndithu

  • @MaggieJsinkaika
    @MaggieJsinkaika 2 часа назад

    Kodi iwe ndindani koma ulindizelu kapena umadya ndalama ya amcp umanfinyasa macometi ako

  • @HappyMajo-l3q
    @HappyMajo-l3q 4 часа назад

    More fire malume

  • @Harrychokanda
    @Harrychokanda 4 часа назад

    Amalawi ndife ogona

  • @GabrielJosua-r2y
    @GabrielJosua-r2y 5 часов назад +1

    Akuona ngati amalawi ndi zitsiru amcp.Bwezi labwino limaoneka pamabvuto.koma report anapanga mokakamizika komanso alimbe chidwi bwino ndi ifayi.anthu akufa akupezeka alimbe magazi zikulalika chani😎??Tulani pasi achakwera udindo zauchitsiru tatopa nazo

    • @CharlesMatete-h6n
      @CharlesMatete-h6n 3 часа назад

      Mutu wako sukugwira iwe chomwe unachokela mu enquiry mo ndichani ungofuna kusokoneza anthu ulibeso ndi fundo zomwe ukungolankhula ngati wadzuka kumanda

    • @NoelKhwimba-bh3ts
      @NoelKhwimba-bh3ts Час назад

      ​@@CharlesMatete-h6nKodi report za black box mulibemo bwanji poti ofalitsa nkhani ananena kut zonse zilipo ndy mukutipo chani apa

    • @GabrielJosua-r2y
      @GabrielJosua-r2y Час назад

      @@CharlesMatete-h6n mukasuta Chamba nkumaonera amako ndi baba wako osandiputa ufiti umaposa pamenepa iwe ndi Chakwera wakoyo PA

  • @HassanOmar-n3s
    @HassanOmar-n3s 3 часа назад

    Kumalawi kuno palibe amene ali seve

  • @AlakheDumile
    @AlakheDumile 4 часа назад

    Zoona achoke atitopetsa akadzare fodya kwawo

  • @MikeMagwira-ed3ih
    @MikeMagwira-ed3ih 3 часа назад

    Boma ili ndi la mafia

  • @emmanuelnyirenda3289
    @emmanuelnyirenda3289 2 часа назад

    This is just planned argument, why did u run away in the first place?

  • @ChristianSimlemba-p5s
    @ChristianSimlemba-p5s 3 часа назад

    Namiwa ndi chitsilu, ananthawilanji,, iyeyo ndiye akanabwela, ndi zeni zeni, osati zopusa akuyankhulazo,,, @alibe fudo, ife tinayika chinkhulupililo PA iyeyi, koma anachoka, wakwatiwa kwa mphezi saopa kung'anipa,, ndi chitsilu Namiwa asatipusitse a Malawi,, mzimu WA chilima, uzadzuka, tsiku ndilimodzi,, galu namiwa,

  • @chipilirolikatho3572
    @chipilirolikatho3572 3 часа назад

    Namiwa do you want u president, ? just join politics pls

  • @chipilirolikatho3572
    @chipilirolikatho3572 3 часа назад

    This guy is arrogant, he is a coward, he thinks Chilima was for him only, tonse tidaluza leader wachinyamata,

    • @DavidPeter-e2o
      @DavidPeter-e2o 2 часа назад

      U do know anything dude jst keep or including those people who lost their direction?

  • @chipilirolikatho3572
    @chipilirolikatho3572 3 часа назад

    Namiwa alibe nzeru zomwe, kweni kweni akufuna chani, anthu awa ndiomwe akubweretsa chisokonezo mdziko, nkhondo imayamba chonchi, those people died they will not rise from death, let them rest in eternal peace, Namiwa you can do better focus on other agendas, let's move on as a country, everyone will face death, koma munjira zosiyana, anthu akukutumani akulu akupweteketsani

  • @AubreyShaba-b5d
    @AubreyShaba-b5d 3 часа назад +1

    Anamiwa, it will be very difficult to believe in you now... You run away to be part of the Commission of Inquiry ya ndege ku Chikangawa...It doesn't make any sense for you coming again from your hideout and start pointing at what you term faults of the report when you had all the privileges to counter on such you deemed filtered report within the Commission of Inquiry you dumped down... People follow whatever arguments you make but it will make people who follow you to trust you...Tell us if you want to score a political mileage... You should learn to know many people who follow your trajectory comments think with a depth to scrutinize comments you make...I hope it's not just a hullabaloo... Some of us had lots of hope in you but you've veered away from the direction we believed in you..Are you another politician in disguise...

    • @GodfreyWhayo-hh1dm
      @GodfreyWhayo-hh1dm 2 часа назад

      Namiwa declined to join the commission of enquiry after noting that there were prepared guide lines for the commission to follow .

  • @OliviaKhan-z2m
    @OliviaKhan-z2m 2 часа назад

    Kd inuyo munatulukilanji atakusakhan mumafuna mudzidzatsutsa ngat amzeru bwanji nde inuyo muona kt anachita kutan