BON KALINDO LERO__ZACHITIKA KU CHIKANGAWA __17 December 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 16 дек 2024

Комментарии • 86

  • @SimonChuungula
    @SimonChuungula 14 часов назад +2

    The DC
    Always behind you love you 😍
    From livingstone Zambia 🇿🇲 ♥

  • @chrissyamanda5510
    @chrissyamanda5510 12 часов назад +4

    Presdent oyipa
    Chichitikileni ngozi sindinamvepo kuti wapita ku site kukawonapo pomwe iyeyu anaphera anthu 9 aja
    Akuwopa kukapenga misala eti
    Chonsecho ndichizindikilo choti akudziwapo kanthu ndetu Yehova amakuphimbadi ku maso kuti uwonekèle uchitsilu ndi umbanda wako

  • @OfwaMwambila
    @OfwaMwambila 13 часов назад +13

    Still can't come to terms what made the president not to go visit the site where CSK died he was just within the same area 😢😢.it doesn't add 🤔 up to me.21 questions??

    • @besterlumbe4404
      @besterlumbe4404 12 часов назад +6

      Kuti apiteko misala ikayambila pomwepo ndi nkona akuopa kupitako

    • @jowiemhango5058
      @jowiemhango5058 12 часов назад +5

      He has a fear kut somthing might happen to him uyuyu. He knew kut he contributed to the their death

    • @anniekachale
      @anniekachale 11 часов назад

      The DC🔥🔥🔥🔥

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 11 часов назад +1

      Mwina akuopa anapanga zizimba💔💔💔

    • @MandalaChaona
      @MandalaChaona 10 часов назад +2

      He was the master planner for those who were killed on that Area. Ndiye poti kunali kukhwimira Udindo akuopa akasemphanisa zizimba.
      That is Mr Smartmatic Chakwera evil Man

  • @OscarKathumba
    @OscarKathumba 14 часов назад +5

    Mwayakhulako za nzeru lero Mr Kalindo,,,lero ndayamikra

  • @RuthTimothyChirwa
    @RuthTimothyChirwa 7 часов назад +1

    Amen the Dcccc❤❤❤❤ from Cape Town ♥️🙌🙌♥️🎉🎉

  • @billybanda7280
    @billybanda7280 10 часов назад +1

    Very nice voice of singing Mr kalindo!!

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 13 часов назад

    Amen Amen Amen !!! The DCCCCCCCC CCC CCC CCC CCC may God be with you inetu I don't even understand am confused .God is watching us us from a distance.Booooooooon kalindoooooooooooo mwana owopsyaaa kwambiri from njeza village mulanje southern Africaaaaaaaa malawi

  • @JohnSoweso
    @JohnSoweso 12 часов назад +1

    The best choirmaster ever
    Born kalindooooo
    Lazarus killed Saulos
    Lazalo waumphawi adapha Saulos wa ku damasiko
    Kandiolotse mkakutafune

  • @BernadetteKapito
    @BernadetteKapito 11 часов назад +1

    Congratulations bwana Kalindo posutsa zolimbikitsa zophana.

  • @abdikariincolow3531
    @abdikariincolow3531 14 часов назад +3

    Mulemu wanu bwana Dc❤❤

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 14 часов назад +4

    Chakwera asamara bwanji za chilima munthu anamupha ndiye mwa masamu

  • @chrispinechisaka9121
    @chrispinechisaka9121 15 часов назад +5

    Aja alibe nazo ntçhito pano akumva kukoma alibe nazo komaso alibe umunthu

  • @JessypaulBeauty
    @JessypaulBeauty 13 часов назад +1

    Ameeeeeeeen bwezi utamkonda Yesu nyimbo yosuntha iyi

  • @aaronbamusi9802
    @aaronbamusi9802 12 часов назад +3

    Apita bwanji kukaona malowo, pomwe chikumbumtima chikumusutsa

  • @chiccosuliwa
    @chiccosuliwa 14 часов назад +2

    Ulemu wanu bwana DC❤❤

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 14 часов назад +1

    Muyanjanitsi Bon Kalindo . Amalawi , posawerengera ntundu ndikochokera kwa munthu ndi ife a Malawi .Ma judge anthu opuma , Mulungu awateteze munyengo yoopsyayi . Anthu mpando olamulira dziko aumva kukoma kufikira pomapha anthu kuti asachokere pa udindo .

  • @IdrisahChuma
    @IdrisahChuma 12 часов назад +2

    Mulungu azikupasa zabwino the DC

  • @Maxielyies
    @Maxielyies 13 часов назад

    That's our beloved president, the Dddddd Cccccc talking the truth and spreading free advice ❤❤❤❤

  • @ChikondiKunjawa
    @ChikondiKunjawa 12 часов назад +1

    beautiful singing

  • @prettytambala5687
    @prettytambala5687 11 часов назад +1

    Asing'anga anamuuza kuti akazangofika pamene paja azapenga

  • @Dellingsmunthali
    @Dellingsmunthali 13 часов назад +1

    Kodi umaimbaso bwana DC👋👋

  • @JamesSuman-if2xo
    @JamesSuman-if2xo 3 часа назад

    Mbambande a DC ✴️

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 11 часов назад +1

    Ndipo live zolimbikisa nkhondozo ai DPP isamapange zimenezo

  • @HildaMbizi
    @HildaMbizi 14 часов назад +5

    Fundo iyo meayowoya adpp nawo wakunanga Nadi UTM my vote Kabambe yemweyo

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe 9 часов назад +1

      🎉🎉🎉UTM my vote ❤❤❤

  • @ZuzaPrecious
    @ZuzaPrecious 8 часов назад +1

    Nyc singing

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 14 часов назад +1

    Dpp Mcp onsewa alibe khumbo Lotukula Malawi....
    UTM BOMMAAAA

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe 9 часов назад

      Indee UTM my vote ❤❤❤

  • @RulerChriss
    @RulerChriss 12 часов назад +1

    Now it's no longer the warm heart of Africa 😩

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni 14 часов назад +1

    Bonkalindo sanakaone mtengo koma anakapamga makwala pamalo anafera Chilima

  • @euwarttawakali4320
    @euwarttawakali4320 5 часов назад

    Booooooorn Kalindoooooooooo🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @godfreyalberto7425
    @godfreyalberto7425 14 часов назад +1

    Dpp musamabwezere zolakwa Za MCP .Aloreni a MCP adzipanga misonkhano kumwerako.

  • @ChristopherSiliyako
    @ChristopherSiliyako 13 часов назад

    Iwe adapanga palibeso congratulatio to you the DC

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs 12 часов назад +1

    I think you are posessing power from the ALMIGHTY

  • @tabunelbig1586
    @tabunelbig1586 7 часов назад

    This also puzzles me,kuti mpaka pano utsogoreli osakaona pomwe anafera vice wake..😢

  • @DorothyKamanga-l9j
    @DorothyKamanga-l9j 9 часов назад +1

    Zoonadi kalindo😂😂

  • @MercyTasherah
    @MercyTasherah 6 часов назад

    Utm my vote

  • @HarryMakwale
    @HarryMakwale 12 часов назад

    Anganga ulemu wanu ❤❤❤❤

  • @petermasenti2084
    @petermasenti2084 11 часов назад

    The D.C. amakupha ndiwodya naye mbale imodzi mvuto la a malawi sitichedwa kuyiwala tinkawona ngati tikusitha zinthu tikutenga njoka kulowetsa nyumba

  • @JosephyMaloya-h6q
    @JosephyMaloya-h6q 14 часов назад +2

    Mumakwana akalindo

  • @DigleDafter
    @DigleDafter 11 часов назад +1

    The DC nfana omvuta kusunga pamuzi 😂

  • @ElizabethMwale-z3s
    @ElizabethMwale-z3s 11 часов назад

    Malangizo abwino the DC mwanena za umodzi. Zipani zotsutsa tiyeni pa nsonkhano tiwauze anthu mfundo zoti tikatenga boma anthuwa avutika tidzawatani. Musatchingire kuti chipani ichi kuno chisabwere, koditu zokha zikuoneka or enao akukana kuti sangakhulupilire za aja analosera kt ena ali pa 46% 29% etc. Misonkhano ife tikuona tokha kwina kopanda anthu, akabwerako ochulukirapo ndiye kt agawa ma 5 pin, kwina sanagaweko kanthu koma anthu phwiii. Mulungu atithandize masankho ayendetse yekha.
    The DC ee mumaimba ndakutayirani kantengo kk

  • @gracemaluwa4674
    @gracemaluwa4674 8 часов назад

    Nyc song

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 8 часов назад +1

    Zomwe akuchita a DPP ndizomwe a Chilima ankanyasidwa nazo. This is the reason I can not vote for dpp neither mcp. U T M my vote

  • @InnocentKavalo
    @InnocentKavalo 8 часов назад

    Good mr dc

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 9 часов назад

    Ndizoona. Azingoyankhula fundo pa misonkhano not kunyoza

  • @JustinPhiri-kq2bb
    @JustinPhiri-kq2bb 13 часов назад

    Arrest iyambe ndi a president kenako a ndi zake UTD ikanakadandaula ku ICC

  • @HessiLimani-n2o
    @HessiLimani-n2o 13 часов назад

    Winiko your number one

  • @prettytambala5687
    @prettytambala5687 12 часов назад

    The DC let's collaborate 😢😢

  • @JamesJonkha-y7t
    @JamesJonkha-y7t 4 часа назад

    Chakwela ndifiti

  • @austingsmaganizo
    @austingsmaganizo 10 часов назад

    Lero borani uthenga wabwino.

  • @IdrisahChuma
    @IdrisahChuma 12 часов назад

    Man of the moment the DC

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 14 часов назад

    Inenso mkulu ameneyu anayankhula ku ndilandeyu anandinyansa kwambili

  • @MadaloUsen
    @MadaloUsen 11 часов назад

    Atiuze atibwanj kod

  • @Fatima-db8ut
    @Fatima-db8ut 8 часов назад

    Amaopa nkhalango yowirira

  • @JazakaPhiri-j3h
    @JazakaPhiri-j3h 13 часов назад

    Mwana obadwa masiku okwanila samasowa pitilizani kutilangiza amalawi wakumva azimva osamva asamve koma chomwe ndikuchiona ine monga mwana obadwa mma 90 MCP ndichipani chopanda manyazi zoona mmmmmmm

  • @MemoryMteketi
    @MemoryMteketi 13 часов назад +1

    Chakwera amangidwe basi

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly 14 часов назад

    Nyimboyo ibwelezedwee kkkkk

  • @lameckkaudzu2287
    @lameckkaudzu2287 9 часов назад

    Umatha kuyimba

  • @JacobMsukwa-q6v
    @JacobMsukwa-q6v 14 часов назад

    Komanso a DPP asaiwale Ali kale ndi kambiri konunkha😢😢asamaoneke ngat nda ngel pano iyahhh tinkavutika ndi Jane Ansa

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi 14 часов назад +2

      Bola ddp koma mcp mbiri yawo ikunukha dziko lonse la pansi

    • @GodfreyWhayo-hh1dm
      @GodfreyWhayo-hh1dm 13 часов назад

      Mphechempheche mwanjobvu samitamo kawiri . Amalawi Tiyeni tiyese tisanazinonzi .

    • @CharlieChirwa
      @CharlieChirwa 13 часов назад

      Jane asah analakwa chiyani

    • @JacobMsukwa-q6v
      @JacobMsukwa-q6v 12 часов назад

      @@CharlieChirwa I guese you are not in Malawi so will elaborate everything in my comment around 4pm

    • @MandalaChaona
      @MandalaChaona 10 часов назад

      With Or Without DPP leadership will Change.
      Mkhamza, Tsankho, Kupha, kungodzudzula Boma kukumanga so Ng'ona party Will never rule again.

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 11 часов назад

    ❤❤❤❤❤🔥🔥🔥

  • @WizahChawinga-xu5pd
    @WizahChawinga-xu5pd 13 часов назад

    Inde the DC ulemu wanu

  • @LumbaniNeba-d9n
    @LumbaniNeba-d9n 14 часов назад +1

    The DC the great
    Proud of you brother

    • @DavisSeyani
      @DavisSeyani 13 часов назад

      Mzimu owukira ndi umene ukutipwetekesa kumalawi

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 11 часов назад

    Uncle Bon

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p 13 часов назад +1

    😩😫😭

  • @daudphiri7578
    @daudphiri7578 13 часов назад +1

    Winiko ndikadakonda ukadakhala msilamu bwelera ku chipembedzo chako ndithu ndiwe okamba zoona ndithu. Touching words for sure.

  • @DorothyKamanga-l9j
    @DorothyKamanga-l9j 9 часов назад

    Kkkkkk😂😂😂

  • @SlajuMajawa
    @SlajuMajawa 11 часов назад

    Timakunyadila kwambili

  • @MoreiDipuorice
    @MoreiDipuorice 12 часов назад

    Amen

  • @dorothymkandawire
    @dorothymkandawire 12 часов назад

    Zoona zokhazokha

  • @HassanGift-z7r
    @HassanGift-z7r 14 часов назад

    😢😢

  • @godfreyalberto7425
    @godfreyalberto7425 14 часов назад

    Zoonadi

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 14 часов назад +1

    Chisankho cha fake plus opposition yopepela