ZIKUCHITIKA POMPANO KU BALAKA SKEFFA CHIMOTO WAIMBA NYIMBO IYI PAMASO PA A PRESIDENT CHAKWERA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 16 окт 2024

Комментарии • 93

  • @WinerdShadreck
    @WinerdShadreck 2 месяца назад +4

    When u ar near to finish it's like this 😂

  • @michealchaomba9761
    @michealchaomba9761 2 месяца назад +1

    😂😂😂😂😂 ndalama ija ufiti ulimo

  • @EviChio
    @EviChio 2 месяца назад +2

    Olo Skeffayo, kungoimba kufuna ndalama ndithu. Zaugalu

  • @richardmasina5454
    @richardmasina5454 2 месяца назад +7

    Nyimbo ngati zakuthera skeffa ndibwino kungokhala osati kuyinba izi zikuonongerani luso , sankhani moyenera chonde

    • @SalaJawali
      @SalaJawali 2 месяца назад +2

      😂😂😂😂

    • @AntinHawile-rw9fj
      @AntinHawile-rw9fj Месяц назад

      km ndalama imaiwalisa mulungu iiii skeffa munayamba bwino kuchiyamb munali ndi mulungu mukuloreranj kuti satana atenge ulamuliro pa moyo mmmmmm

  • @ThokozaniBondo-em9fr
    @ThokozaniBondo-em9fr 2 месяца назад +2

    Amalawi sitichedwa kuyiwala lero tili busy ndi chakwera kuyiwala zakuchikangawa pompano abale 😢

  • @SalaJawali
    @SalaJawali 2 месяца назад

    Kodi mwayilemba Lero nyimboyi ndikuyimba so Lero kodi😂😂😂😂😂😂

  • @BeatriceNkhoswe
    @BeatriceNkhoswe 2 месяца назад +2

    Aliyense amene walandila ngongoleyi awone zomwe zikubwera kutsogoloku bola asadzakupheren Ana, coz satanic panopa nde yalowatu😢😢😢

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r 2 месяца назад +1

      Ndipo nde Simukunama. Anthu enanso akumalota aku saina ma contract akumidima 🙌🙌

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c 2 месяца назад

      Sister ndikugwilizana nanu

  • @SaloDavie
    @SaloDavie 2 месяца назад +1

    Dziko la malawi ndilovetsa chisoni kwabasi mukachoka kumeneko mukagona ndi njara 😂😂😂😂😂moti mr chikangawa adzigura chakudya kupatsa anthu akumamidzi anthu akufa ndi njara. Amalawi chonde khalani maso mukapusa titha tonse ndi chikangawa 😢😢😢

  • @GiboTakondwa
    @GiboTakondwa 2 месяца назад +4

    Ndimayiwake wandani ameneyi akudikulayi moti masiku omwewa waiwalilatu njalaija ine phee pajoni pano votelani agaluanuwo musazandipemphenso yabeseni azikupasani omwewo achakwelawo

  • @austindavid3601
    @austindavid3601 2 месяца назад +1

    Grace uja osazamuphwekesa

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 месяца назад

    Zaziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii zikuwonetseratu kuti mwadya nawo askeffa chimoto chisoni ndithu

  • @AntinHawile-rw9fj
    @AntinHawile-rw9fj Месяц назад

    panod ndye ndazindikira kuti skeffa naweno uli mgulu pa nkhanya kalata wa grace

  • @DevisonHala
    @DevisonHala 2 месяца назад

    ❤❤❤❤

  • @LovelyAntenna-jh8yh
    @LovelyAntenna-jh8yh 2 месяца назад +3

    Mboba timakukondani Koma pomwe mwafikapa manyi enieni

  • @YamzyNedson
    @YamzyNedson 2 месяца назад +1

    😂😂😂😂kod skeffa chimoto ndiye akuimba kut nyimbo yake yakumowayi??Ngat nyimbo zamuthela atha kungosiyatu kuimbako chamba eet.😢R.I.P Chilima

  • @mthawisakaunda
    @mthawisakaunda 2 месяца назад +2

    Malawi kumvetsa chison. Nthaw yonsey agalu amenewa anali kutiiiiiii. Skeffa wanga uja 😢

  • @mwaiwaobanda2691
    @mwaiwaobanda2691 2 месяца назад

    Ndipo malawi kumvetsa chisoni....ine still mourning chilima wanga Eeeeish...Ambuye atitsegule maso koma...😭😭

  • @ThokoLungu-tq6pw
    @ThokoLungu-tq6pw 2 месяца назад

    Zaziii askfa mwayamba misala mmmm onsala awa

  • @EdnahShantell
    @EdnahShantell 2 месяца назад

    Ndani atiwerengere kalata ya Grace chinga ija ☹️

  • @amoschisisi2070
    @amoschisisi2070 2 месяца назад +2

    Skeffa Chimoto you have lost a plot

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 2 месяца назад

    Skeffa chani Kama 😂😂😂😂😂

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 2 месяца назад +1

    Chakwera anthu akuziwa kare kuti iweyo ndiwe wasataniki koma iwowo anthu awa dyera rikuwaphweteka kwambiri iwo akati bolani dpp rero akurandira ndarama kwaiweyo chakwera sakuziwa kuti ningongore zimenezo ndipo azabweza mosavuta ayi ndipo uzawatumizire chigumura vula yayikulu izawathe kamozi uzangotenga magazi awo awo ndipo uzayambire kugwesa vula kumwerako azathe ose anthu ni vula

  • @GeraldMkwewu-gd5eb
    @GeraldMkwewu-gd5eb 2 месяца назад

    Kodi wadramayo ndibachara gogo Monica nthawi lkubwera mumakhara Pasi ndi mr chikangawa wanuyo mungoti kulikose londorondo mzaziwona zoona munagoneka chilima pano alipasipa ngt boza kumusiya mery muchison lnu kumanjoya mulungu akukantheni km serious

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 месяца назад

    Family yanga ndayiwunza kuti osachepensa ndalama zimenezo ndi zanthu kumachulusa kwambiri anthu awa asawukisa dala asaname ndipo awana nyekwe chaka chamawa awa anthu akuvina akufuna ndalama basi chifukwa mwasawukisa kwambiri ndipo mukapasa mundifunse chaka chamawa awa ine pheee vot yanga yawina kale inu mbizy kumayenda yenda malawi mukumuziwa inu

  • @StellahMsodoka
    @StellahMsodoka 2 месяца назад

    Paja Malawi tu sakhala mnyumba mwa munthu

  • @MaickJannah
    @MaickJannah 2 месяца назад

    @skefa bas ulendo uja uwu uyu nde bas wantha

  • @Paul-q2p
    @Paul-q2p 2 месяца назад +1

    Matongo yako

  • @ChancyMathuwa-w4d
    @ChancyMathuwa-w4d 2 месяца назад

    I follow you but zomwe mwayambazi sizikusungani bwana

  • @JesseKanjanga
    @JesseKanjanga 2 месяца назад +1

    Ife tidakalira muzimu9 ija,inu nukudya ndalamazo

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember 2 месяца назад

    Apa ndiye a Skeffa mwapala

  • @StellahMsodoka
    @StellahMsodoka 2 месяца назад

    Zaziii mukhalira kuyakhula azanu Ali busy kuzilimbikira...njalayo si onse ndi kwanuko kuzolowera zolandila zaulere basi....ena ubwino alinawo pano mukumbukire school ija mumkayithawa ija pano muli mu office yotukwa anthu basi

    • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
      @AbdulsharifulKalipinde-m6u Месяц назад

      All your family is rich
      Kuyankhula motumbwa basi
      Kumene anthu akuvutika ndi njala
      Ngati unapita ku sukulu iweyo ndiye family yako yonse ndiyophudzira

  • @PaulineKamwana
    @PaulineKamwana 2 месяца назад

    🙌 za ugalu

  • @spargomw
    @spargomw 2 месяца назад

    Skeffa apa nde wapala😂😂 tiona kut ufika nazo pati paja kunaliso zitsiru za ku 25 zija Symon and Kendall zidaimba kut Tivoteso pano ndim'mene palili pa ground sakuvekaso mau akungoimba za ZAKUDYA BAS😂😂😂😂

  • @WizeyManyozo
    @WizeyManyozo 2 месяца назад

    askeffa koma ndiiweyod kapena munthu wina eeee wandiliza saname ndipo ngat kunali munthu yemwe ndikamukonda kuno kumalaw ndiiweyo bc km pano ndamutuluka ndipo ndimakutenga wazelu kuposa oimba ambili ku malaw koma ndisathe mau mwina ndikulota ay zikom pangat kufuna kwanu paja munthu amasauka ndizelu amalemelaso ndi mzelu zikom

    • @AntinHawile-rw9fj
      @AntinHawile-rw9fj Месяц назад

      ndpo inenso ndazizidwa uyud nkan amafuna kumpha gibo pearson uyu

  • @JuvenileDebwe-bv8ow
    @JuvenileDebwe-bv8ow 2 месяца назад

    Akapusa skefa amumalize ndi awa a kongeresiwa coz iyeyunso ankaikonda ndiye kaya tiwona kkkk

  • @Peterchirwa-tf1ox
    @Peterchirwa-tf1ox 2 месяца назад

    😂😂😂😂... Kma

  • @LamequeSamuel-v6y
    @LamequeSamuel-v6y 2 месяца назад

    Ndi a kumidima okhawokha mukudabwa!!!

  • @YoweliChipapaChipapa
    @YoweliChipapaChipapa 2 месяца назад

    Inu mukudabwa za sefa Kuti ndiwasataniki chakwela Joice banda bushir NDI ena Otero, NDI anthu apasi pa nyanja pakufunika kupempha mulungu Kuti atichotsele falão ameneyu

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 месяца назад

    Sikefa uku kuntha wasowa zochita komaso sangawine uyu kusalima

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr 2 месяца назад

    Ulamuliro wa athu openga ,,,kkkkkkkk ziphuphu zakumaso?mwina sindikumva bwino ine,,koma amavinawo alindi ana ndithu?!! Ngati kutambatu!!!!! Koma abale.

  • @johnmponda9070
    @johnmponda9070 2 месяца назад +2

    Is Skeffa Chimoto normally or abnormal mind?

  • @johnmponda9070
    @johnmponda9070 2 месяца назад +1

    It seems like he is losing his mindset he must better go to Zomba mental hospital immediately.

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 2 месяца назад

    Koma ndekuvinatu anyamata achipani kujiya ngongole kodi?
    Akuti kuwasanglatsa apule.

  • @GiftKayembe-n9n
    @GiftKayembe-n9n 2 месяца назад

    Skefa watinamiz

  • @ZogoZeko
    @ZogoZeko 2 месяца назад

    Zopanda poke chip chipani magazine bakili muluzi antenna kale

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 месяца назад

    akuwona ngati anthu akumusatira koma sakuziwa kuti anthu agofuna kulandira ndalama yawoyo aketero pheee ndikumadya kokavota ndiwina

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 2 месяца назад

    pali ndalama amwene

  • @BenjaminKamanga-p8w
    @BenjaminKamanga-p8w 2 месяца назад

    Vuto ndine kusatira oimba ena, mbuzi zina zikuvuna asanazipase umphawi sizinthu

  • @KondwaniMamveka
    @KondwaniMamveka 2 месяца назад

    Km awa imeneyonyimbo

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON 2 месяца назад

    Nonsens 😂😂😂 kumeneko nde kumutemera ngolomera kuti Aziba bwino 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 2 месяца назад

    Kaninso iwe sikefa ndiwe chitsiru chotere.

  • @GracePhiri-f2u
    @GracePhiri-f2u 2 месяца назад

    Zovuta eBay akusangalal Mary akulira 😢😢

  • @AubreyWilson-j8w
    @AubreyWilson-j8w 2 месяца назад

    Nkhani ndi unduna wa Matumbi

  • @NyangwaKoma
    @NyangwaKoma 2 месяца назад

    Uyutu bas ulendo OK athela kundale😊

  • @CharlesGremu
    @CharlesGremu 2 месяца назад

    Skeffa apa basi titulukana

  • @imraanJafal
    @imraanJafal 2 месяца назад

    Nonsense in Malawi poor culture forever never changed

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 2 месяца назад

    Akuvinawo atakhala mayi anga mpaka nditawakakhapo sure

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 2 месяца назад

    Koma akadakayimbila ku msonkhano wa adad yooo malawi msanje .ndi bussines iyi kaya mzanu ndipo mukamuyitanitsaso inu kwanu atha kubwelaso kudzayimba.

  • @KingsleyJika
    @KingsleyJika 2 месяца назад +1

    Ndakutuluka skeffa ndimaona ngati uli ndi nzelu koma ndiwe mbola mmxxxxx

    • @GeraldChisamba
      @GeraldChisamba 2 месяца назад

      Even utamutuluka iyeyo aluzapo chani 😂😂😂😂😂 osauka kudelera ma biggy kkkkk

    • @KingsleyJika
      @KingsleyJika 2 месяца назад

      Iweyo ndiwe galuso pa mako

    • @GeraldChisamba
      @GeraldChisamba 2 месяца назад

      @@KingsleyJika mmmmm u too masapusa men

    • @KingsleyJika
      @KingsleyJika 2 месяца назад

      Nsunu ka nyoko

  • @MisheckKamwendo-w9n
    @MisheckKamwendo-w9n 2 месяца назад

    Pepani athu anga kuyamikila manyaka ziko lomvesa chisoni

  • @chimwemwechiundira6002
    @chimwemwechiundira6002 2 месяца назад

    😅😅😅😂

  • @MwanyaliLenzo
    @MwanyaliLenzo 2 месяца назад

    Asikefa mwatha basi

  • @wezzimoyo1Angera
    @wezzimoyo1Angera 2 месяца назад

    Musegule mabungwe athana ndi ziphuphu muzitipasaso ma number tizithulatso mavuto atnthu

  • @LiyayaNyamula-j3b
    @LiyayaNyamula-j3b 2 месяца назад

    😂😂😂😂😂

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 2 месяца назад

    Computer

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim 2 месяца назад

    Man skeffa apa ndye mwadzipha

  • @AmosScott-z9x
    @AmosScott-z9x 2 месяца назад

    Nyimbo yanji imeneyo a Skefa

  • @ABc-fk1uu
    @ABc-fk1uu 2 месяца назад

    Langizo language kwa Skeffa ngati ukosowa zochita Bola ungokhala pankhomo nkumacheza ndi Ana ako kusiyana zomwe wayambazi zikuonongela luso I see u have got crazy
    Pompano waiwala kuchikangawa ife tikanalilabe chilima nonsense

  • @DerickZiba
    @DerickZiba 2 месяца назад

    Devils MCP, skeffa satana

  • @HopeLiwonde
    @HopeLiwonde 2 месяца назад

    Wavuta ndi uphawi

  • @SAMUELOSMAN-h2o
    @SAMUELOSMAN-h2o 2 месяца назад

    Zosabeba

  • @WorriedNdhlovu
    @WorriedNdhlovu 2 месяца назад

    Zauchitsilu

  • @GiboTakondwa
    @GiboTakondwa 2 месяца назад

    Anthu alikuti

  • @EllenNamulu
    @EllenNamulu 2 месяца назад

    Zamakape izi

  • @HarrietMtenje
    @HarrietMtenje 2 месяца назад

    Zaziii

  • @BrotherPaul-ln2ld
    @BrotherPaul-ln2ld 2 месяца назад

    Skeffa kapena gopani? kkk

  • @KestonNGUBO
    @KestonNGUBO 2 месяца назад

    Mavi ako nakusik iwe

    • @LovelyAntenna-jh8yh
      @LovelyAntenna-jh8yh 2 месяца назад +1

      Koma ndalama NDI satanadi eti iyeyu anali oti angamaimbe zimenezi hahahaha skefa waphonya nsewu basi oimbawa osamawakhulupilila basi

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no 2 месяца назад

    Kodi mukamati , ayi manganya , ayi chakwera , kodi IFA zabwera mu ulamuliro wachakwera , ? Kunali bingu or Peter anthu samamwalira , ? Nanga anthu anafa kumcesi nyumba kusandutsa manda , nanga Ku area 24 kuwatenthera nyumba ? Nanga zopha alubino , kuli apitala , komaso kudikirila panjira , ? Tisaweruzane oweruza ndi yehova yekha wakumwamba ,