Panopa waona kuti chisankho chili pafupi akufuna kunamiza anthu kawiri amalawi chenjerani no mistake again chaka cha mawa anthu awa ndiokuthwa pakamwa nthawi yonseyi munàlikuti
Dzikoli sila DPP SI LA MCP SI LA UTM, UDF, KAYA AFORD AYI ndi LA aliyèse nde palibe chifukwa chomaletsela munthu kuti kuno usafike aaaaa zimenezo nde ndale zopusa inu a dpp, kugawanitsa anthu, or inu pa 2025 kupanda ukuvotelani anthu aku Lilongwe mungawine, or anthu aku mpoto mungawine panokha
aaaa, kuganiza ngati bakha Njala ya chilengederyo? If you have the powers to command God to give rains according to your wish why didn't you do so Leave the man of God alone
You instructed your ministers that they have to make sure every admarc deport must have maize with affordable prices but up to now this directive is not honoured. Poor policies can also contribute to hunger and poverty
Kod za commission of Inquiry simukulankhulapo bwanji munangomva zoti anthu akunena kut mwamwalila Munathamanga ku BT koma za kafukufuku wa imfa ya Biyen kuli ziii
Aliyense akudziwa kuti timadalila ulimi eya koma dzipangidzo dzafika pa dzina lako dzonse ndi dzinalako. Ukadabadwira ku American zinthu ku Malawi sidzikadafika pamenepa ayi. Munthu wakuba iwe
Kkkkk ndie anakupangirani chan apm? Kapena mukutengera ntundu? Nkakhara ine ndi mchewa koma bingu namuvoterapo chifukea Cha ntchito zake osat izimunenazi kut mumuve bwino chakwera yamban kugwira ntchito akulu chuma panopa chinthaka kulibe zoti one nilipa ntchito anthu piano ena asiya ntchito kuyamba ulimi
Kodi feteleza osika mtengoyo munalonjeza mu 2019 pa zaka 4 mwapeleka kwa angati? Ma mega farm aopindura ndi angati? Ife kwathu kuno tili ndi farm koma adangobwera oyendera adabwera kuzayendera ma farm 6 koma mpaka pano olo ndi modzi mwaife zatinathandizidwe mpaka pano
Thanks mr president keep it up
Iwende wantha ndikurumbira tikukhadzura 2025 nyerowako chikangawa😅
Balotani, dreaming is for free
Cheat yourself olo mutatukwana ziwalo million times, you will be surprised, shameless ppl
Kulankhula ngati munthu opemphela koma ndi mbuzi yaikulu komanso ziwa kuti ulamulilo wako mulungu akudananao
Says who?mmmmm, does God get orders from you?
Njala yinayamba ndikale chakwera sanabweretse njala ,,,,,koma womwewo akukanika kulima
Panopa waona kuti chisankho chili pafupi akufuna kunamiza anthu kawiri amalawi chenjerani no mistake again chaka cha mawa anthu awa ndiokuthwa pakamwa nthawi yonseyi munàlikuti
Kodi wadzukamso nthawi yanji kodi Mesa anafa uyu😂😂😂😂
nde chikundinyasa eti
Iwetu vincent samala pakamwa pako😂😂😂😂
Kuno tikumupokererani na mawoko yawiri chakwera my vote
Dzikoli sila DPP SI LA MCP SI LA UTM, UDF, KAYA AFORD AYI ndi LA aliyèse nde palibe chifukwa chomaletsela munthu kuti kuno usafike aaaaa zimenezo nde ndale zopusa inu a dpp, kugawanitsa anthu, or inu pa 2025 kupanda ukuvotelani anthu aku Lilongwe mungawine, or anthu aku mpoto mungawine panokha
Oooh MK110,000.00 ndiyochepa iweyo iweyo
Nthawi yantha inu, mwakanika
Bona ndilomweli basi
Mbori yako me nd chakwera emweyi😢
Congratulations ❤ you
Ndiye Kuyankhula kumeneko anthu akuba ndamane amadana ndi chakwera anazolowera kusolola ndikudya zaulele
Chikangawa iwe wakupha chilima iweyo machende ako
Achakwera zoona mungaime pachulu kunena azanu kuba pa nkhani ya fertilizer? Iwe ukudwaladitu sure😢
Chakwera nzeru zikukuchepera , last year MUNATITENGERA NDALAMA KOMA FETELEZA OSATIBWERESERA koma mwabwera kut mutiberenso?????
Anamizeni anthuwo😊
Osamaiwalira kuti vote is about numbers.The one who will get more numbers will carry the day
Pheeeee, watching from very far. Waiting for the results for 2025.
We love you Mr President Chakwera ❤
Ku Machinga kulibe azibale ako mkono wakufawo Ngati kuli azibale ako ndichifukwa chani ukuwasiya akuvutika ndi njala . Kwako ndi kukasiya bx
Ndikanakhala kuti ndimatha kutukwana ndikana tukwana ndithu
Kodi lweyo umachita kuwelenga chichewacho poyankhura 😂😂ndiwe Garu kwambiri
Osati galu. Koma sizikukhala bwino
Bola ukudziwa dza njalazo koma sitivotelaso mcp
Chakwela pa nsana pako.......... Kachipanda iweyo kukweza mitengo ya fertilizer ukuganiza mgat bwenz njala itafika apapa ???????
aaaa, kuganiza ngati bakha
Njala ya chilengederyo? If you have the powers to command God to give rains according to your wish why didn't you do so
Leave the man of God alone
Kkkkk😂...
Koma yea, munda ndi waukulu koma antchito ndi ochepadi.
Chomvetsa chisoni okumbera mmanja ndi aku Mozambique
Ine ndikusaka pomwe Pali VN
Iweyo nyani mashende ako ndi abwuyako amako
Mlimi akut mbori yako Chakwera😢😢
Alandila ndi angati ngongoleyo? Best way just drop prices
You instructed your ministers that they have to make sure every admarc deport must have maize with affordable prices but up to now this directive is not honoured. Poor policies can also contribute to hunger and poverty
Kod za commission of Inquiry simukulankhulapo bwanji munangomva zoti anthu akunena kut mwamwalila
Munathamanga ku BT koma za kafukufuku wa imfa ya Biyen kuli ziii
Asandithele bando uwu
Ineso iyaaa mbolo yake ndithu
Eya wabweretsa njala iwe,ukamutenga kuti fertilizer??
Chipanda chilima mmmm kaya pano ulikt ??
Ali kuchipiku kokatuwa
Kumangowelenga mfundo iliyonse?
Kkkk ndiwe galu kwabas😂
Kumnyero kwako galu iwe.ukanangomalidzika galu iwe,ife tikanapuma😅😅😅😅😅😅
Ndiye kwamene madelamwawo mulibezimene mwanenazi muwathandiza bwanji aaaaa madimaki munaseka aja ndiye njalayo
Kodi tivota liti.... Tione zina
Aliyense akudziwa kuti timadalila ulimi eya koma dzipangidzo dzafika pa dzina lako dzonse ndi dzinalako. Ukadabadwira ku American zinthu ku Malawi sidzikadafika pamenepa ayi. Munthu wakuba iwe
Amene azavotere mcp nd mbuli
Nsanje imeneyo Ife tikavotera Chakwera
Chitsilu cha muthu mesa ndalama ukoonongela zopusa malo mogawila anthu chakudya
Kodi mufuna tizayamikira zinthu zomwe aliyese akuona.God will speak Himself come 2025
Thank you my dream play there
Ndipo zoona mr president ndipo tikulandilani ndiinu president wa kuno ku malawi,,,president. Wachitukuko
Chemapwesa ma battery ako ndakwanu+ okusatilao
Kodi mulimi akolola bwanji fertilitizer ndalama mudatitengera fetiliza osabweletsa
Ndipo inu uyu namachendeyo eeee ayi ndithu
Chitsilu iweyo chakwela feteleza analipo osamalakhulatu ngati makhala pachimbuzi muku nyela ,mumaganiza koma achakwela
Time will tell
Chakwela una ndilakwila kwambili kumpa SKC 😭😭😭
Nthawi yatha koma😂
Kumupoto kulibiretu fetereza wa aip sankho limenelo
Kkkkkk agalu inu
Chitsilu cha president busy kupanga ma push up
Chakwera I want to tell u this 2025 u ll be nothing believe you me munthu wanji onga m'busa koma ili mbabva kunja nkhosa nkati mwako ndi fisi😢
Choka galu iwe tatopa nchitedze ifeeee
Nyini ya Monica chakwela komaso nyemba yache chakwela mboli nfi zoona wabweresa njala ndiweyo
Kungofuna kuzitukwanitsa basi ndiye ngati mukuziwa za njalazo ndiye mukupangapo chiyani?
Iwe ndiye nd phwala bas
Votsek Chakwera
Kkkkkkkkkkk kom iwe ndingalu kwa basi why why Malawi ukunama iwe kom ukundithela bundle
Iwe Chakwera palibepo chomwe ungatinamidzenso ife, Akulu akulu adati" Mpheche-peche mwa Njovu samadutsamo kawiri .. Ineyo ndim'modzi mwa anyamata a Moralo womwe akuyimbawo kuti ; CHAKWERA WATENGA VOTE YANGA .. Koma mmm ' 94% ya anyamata womwe watimva tikuyimba nyimbo yimeneyi" Ayi ndithu sitikukufunanso kuti ubweledzenso kutizunza , gulu lathu lonse ma vote athu akupita ku dpp basi,
Chikangawa galu iwe
Pepani malubino anaphukako pazaka izi simulufuna ulamuliro koma kupha malubino
Iye ngat kholo wachitapo chani kunthandiza anthu omwe sanakokore pot kumakhala budget yochuluka pachat yoti atha kugawa chimanga chifukwa chadyera angoononga ndalama ndimaulendo akunja opanda pake
Nanga pemphelo la ku ndirande lija munalimva kuti aliyense akukhuzidwa ndi ngozi ya ku chikangawa akuti apange stroke tu
Ndiye kulephelako kumeneko chifukwa munthu okonda anthu ake sasankha aliyese amayenela kulandila zili ndiye yo kuli a kapena kusalema ndiwe olephela ndakuona ndimomwe fundozako kukambilana aaaa km iwe,,, nifu ukukambayo kd ndi bugwe kapena ndi boma? Mesa ndibugwe kd loyima paokha iwe bwanji km,, ukudwala Chan kwenkwen,, usasekese odwala iwe 😂😂😂
Koma amalawi tulo chilichose bas yes bwana yes bwana tangolandilan 200 imeneyo eish fertilizer wakhizepela kkkkk
President wa dziko anthu amene abwera pa nsonkhano sakumaka nd omwe anabwera dzulo kwawo komwe kwa Mgona Gangata atauyatsa moto
USAMAYANKHULE CHAKWERA NGATI SUKUDYA KUKANYERA WAVA KUTI FETELEZA AFIKE YAPAPA MTENGO WAPANGA ZIMENEZI NDANI IWEDI OFUNIKA KUKUPONYA MIYILA DEMITI
Uwudi ndinyero wen wen mbuzi kod tikukonda bwanji ukutipanga khaza nanga biyeni atikut? Ndiwe ovetsa chison
ulibe malo mutima mwanga
APM my vote
Nde usamatsegule Pager imeneyo
Kkkkk ndie anakupangirani chan apm? Kapena mukutengera ntundu? Nkakhara ine ndi mchewa koma bingu namuvoterapo chifukea Cha ntchito zake osat izimunenazi kut mumuve bwino chakwera yamban kugwira ntchito akulu chuma panopa chinthaka kulibe zoti one nilipa ntchito anthu piano ena asiya ntchito kuyamba ulimi
Anakupangirani chiani apm basi kumangosatira chifukwa chamtundu basi eeeee zamanyazi
Malawi chison kwanbiri,mumasankhiranji president wopanda nffundo ngat uyu,koma kungokoma pakamwa basi
Njara yabwera chifukwa cha iweyo galu iwe feterizer akusowa chifukwa cha iweyo chikangawa galu iweyo onama iwe wakuba wakupha chisiru
Galu Mapwala ako wakuba ndiweyo waona mavoti ali pafupi galu
Mbuzi ya munthu iyi ....nanga mumalesa anthu kupanga nsomkhono ku central region chifukwa chiyani .....iyi ndi mbuzidi iyi
president wanji ameneyi anawaona anthu amene kwaoko kulibe donthi lo Lima kuno kumalawi ndipatipo anthu akukhala osalemekeza ulimi kumalawi 🤣🤣🤣 fundoless ndi chifukwa ena amati Chakwera mulibe nzeru ndizoona
Tamagiyani achinyamata kandalama akupatseni pamenepo ndikosakwanira kuti mukagule sugar zovetsa chisoni kwambiri kumaombera mmanja ndikumavina
Koma izi iwe kumat wanena za zelu koma mulibe mayaz ponena zopusazo
Aaah chikangawa ulibe mfundo bwera udzagawe kobiliyo koma ife voti yathu ndi APM osati inu akuba
😂😂😂ZOONA ZAKE NZOTI SITIDATHANIZIDWE. Ma stroke ndi nkamwa momwekkkkkkkkkko
Chakwera ndi odwala makanja akugwa ndi njara
🎉
Ndalama dzantukula pankhomo chakweuna unachita kupeza usaname😮kuwanyega athu
😮😮😢
munthu fetereza mukukafufuza ku pharmacy mukuti njala pamenepo yabwera ndi ndani?
Chisilu iwe mapwala akoso pat
Kodi feteleza osika mtengoyo munalonjeza mu 2019 pa zaka 4 mwapeleka kwa angati? Ma mega farm aopindura ndi angati? Ife kwathu kuno tili ndi farm koma adangobwera oyendera adabwera kuzayendera ma farm 6 koma mpaka pano olo ndi modzi mwaife zatinathandizidwe mpaka pano
Ubongo wako ndumene unaguga chifukwa umalankhula zopanda nzeru
Kkkkkkk guys aliyese alimbe kuti awone ngat akulandila nawo *4331# aaaaaapaaaa
Mumu ziwe yesu apure
Akutundu akulankhura tchelani khutu
Za ziii
Ukunamiza anthu akuneno omweyu anthu tikufa nd njala
Inu chakwela plz opani mulungu choyamba inuyotu manyaxi kulibe ai
MASENDE AKO CHAKWERA MILIMI AGULA BWANJI FETEREZA TIMAGULA K114 000 IWE NDIWE WABWERETSA NJALA MAKUTU YAMAKO
Ine ndukuyesa kutenga ngongole ku neef koma zikuvuta, nde zikatheka mwina ndipomwe nditazaone ubwino wanu bwana ndizakuvoterani kma ngat ai aaaaa ndekut ndizavitera amene ankandipasa muholo😂
Chakwela ndionama kwambili komano amalawi ndiopoila njala ili kumalawi iyeyo angamalankhule zopusa akulangulazo chimwendo machendache komaso chakwela akanamwalila kumene koma anthu tikuphemphela aona nyekwe
Chilima alikuti a president zoona adapita ndithu chifukwa chofuna kuti mupirize kulamula mpaka 2030
Bwanji musakupepha kuti akusiileni ndale kulekana ndikumuthamangitsira kumanda ana , abale ake ndi mkazi wake kusala pamasiye
Zokamba zake abale kkkk komatu mizimu ya anthu ija yakwiyadi palibe chomwe chikunveka apa