Only evil fools will not like what Mtanmbo said but he speaks with love and dedication to his country....zinangochitika but yhis guy wanted the best for the nation....
Mbambande bwana a mtambo don't give up my bro big strong we need your help plz my allah guide and protect you all the time allah akbar respect to 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🤲
Congratulations to our opposition chifukwa cha mgwilizano wanu pobwera poyera ndi mtima imodzi uku ndiye kukonda anthu ndi dziko lanu musasiyire pomwepo pitilizani ❤❤❤❤
Mtambo unali chete the time you were a minister should we trust you now because anakuchosani unduna why you were defending the government while you were a minister
Uyu ali ndi nzelu izi lero?? He is one of the guy amene anatiika mmavuto omwe tili nao pano ,,anthu inu pamsana panu you are fighting for your bellies not poor people,,MCP ,DPP ,UTM and AFORD onsewa si anthu abwino
Chief mwayakhula mwadzelu kwambiri but remember nomwenu u will eat chibadzi then muzakhala chete osayakhulaso please please less fight for our nation this country is not for one person
Only evil fools will not like what Mtanmbo said but he speaks with love and dedication to his country....zinangochitika but yhis guy wanted the best for the nation....
Mtambo chigewenga
Bakili muluzi tv ndimachini ananena kuti kwabwela smart matic
Exactly amwene
Mr Ntambo yomweyo...... Moto buuuu🔥🔥❤️
Never give up Mr comrade we fear no death but defeat (this is not 1964 this is 2024)
Mbambande bwana a mtambo don't give up my bro big strong we need your help plz my allah guide and protect you all the time allah akbar respect to 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🤲
M one of a big fun of you Mr, koma osatengela zotukwanazo timawerengera kuti tili Ndi anthu a mphamvu u are one of them..
Muzichangamuka chonchi osati zopusa zija, we love you guys more than you know ❤️ ❤❤❤
Powerful speech mr mtambo keep it up
Keep it up guys,,God b with yu all our leaders,,nkhani iyi ndiyosakambiranadi iyaaa
Which God. Wa Baal Mtambo mkhito munaphetsa anthu osalakwa.
Mtambo waiwala Nkhani yaku karonga
Bravo Comrade. Osaopa osafooka osatopa
Let's work together all opposition parties keep it up good work 😇
Thank u Mr mtambo your speech is very powerful
Mtambo is back Moto undi Timothy 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
We are speaking from experience not just a say big up Mr ntambo🗣️
Paja you always fight for your pocket. Zikakuyendera ukamadya ndalama umakhala ziii
When I meet fearless Malawians...I feel proud to be born this era
I was waiting for you Mr mtambo, more fire
Mr mtambo you should be AVP indeed
Powerful speech Mr mtambo
More fire akatundo umakwana Mr Ntambo.
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 mkwiyo ochotsedwa ku boma mademo tinayambitsa ndife ndipo tinatseka zimenezo tamalimani tidye makobidi next year
Yes yes powerful speech Mr mtambo ❤
Thats Original Comrade Mtambo more fire Comrade
Our country needs peoples like you.
powerful speech comrade Mtambo
leaders unite !!
Vote ndiyanu kale mtambo❤❤❤😂😂😂😂
ng'alulaaaaaa koma amalawi munalusa😂😂😂😂😂
Iyi si mec koma cikangawa electro comission.mumakwana a mtambo tiyeni ku mademo basi Anabelo, Nrb,mec,cikangawa onsewa acoke!
Congratulations to our opposition chifukwa cha mgwilizano wanu pobwera poyera ndi mtima imodzi uku ndiye kukonda anthu ndi dziko lanu musasiyire pomwepo pitilizani ❤❤❤❤
Mtambo man of the moment
Tili pambuyo panu Mr ntambo❤❤
thanks mr mtambo for your speech
Smart Matic musayilore imabera ndikuziwa ine ku Kenya sizinali bwino
Bwana mtambo timenyereni nkhondo maso anthu ali kwa inu bas❤❤❤
Going forward ❤❤
The Boy Who Harnessed National Unity
Ntambo adaziyeretsa kunyatsi pano ndi woyera ndipo anthu akumuimbira mmanja. Ndipo mukanyozera zomwe wanenazo, uyu mumumva kuyabwa muja adachitira dzana. Bola asagulidwenso ndi mcp, otherwise kudzakhala kubwerera mundowe.
Mtambo unali chete the time you were a minister should we trust you now because anakuchosani unduna why you were defending the government while you were a minister
Remember anali wa UTM and analibe mphamvu
Tiri mbali yanu bwana maso aa malawi akuyang, ana pa inu ngat ntdogoreri olimba mntima
The real problem mtambo.kaliati wanted to be Minster forever if even dpp win today will lebel again if not given any possion
More fire Ntambo
Pajaso munthalika amakaniza jane answer kutula pasi udindo😂😂😂😂😂😂😂😂😂mwanyela mmadzi mwakhaula
Malawian we will be power to people not to government
Osaopa
Osafooka
Osatopa
Bwana mtambo timenyeren nkhondo
Can try to show the reality of this story 👍👍👍👍👍👍
Kungoti a Mtambo anthu samakumvetsani kuti inu mangofuna za chilungamo regardless of which party it is
Powerful words Mr mtambo
Mtamboyu amakhalad nd amalawi just imagine my fellow youth ❤
Mmakwana bwana timothy
one of the reasons why us malawians are suffering is you mtambo..you fought for MCP and now wayamba kupanga against..you are very panyopatic
Noooo he was fighting for better Malawi woyipa ndichakwera and his cabernet
He fought for change unfortunately to deliver requires a certain mentality which has perpetually lacked in all our leaders with one exception.
Uyu ali ndi nzelu izi lero?? He is one of the guy amene anatiika mmavuto omwe tili nao pano ,,anthu inu pamsana panu you are fighting for your bellies not poor people,,MCP ,DPP ,UTM and AFORD onsewa si anthu abwino
Ndipotu anthu awa satikonda olo mpang’ono
Better dpp inkaba koma zinthu zinkayenda awa akuba mwachimbulimbuli
Kaliati is not enough and much in mtambo legacy
Ndakusowani galu iwe Timothy mtambo
Mtambo ineyo wandimaliza ndi mau oti sakufuna kuti wina akondeledwe angakhale aopposition koma will ichite prevail kkkkk Izi ndezoona
Thanks mr mtambo nice speech
Chakwera anapha Chilima full stop or atani mzimu ukudikira nayes adzafa siku lina Chakwera sakudziwa kuwawa kwa imfa ili ndi dziko adzaziona
Zoonadi Zokha Zokha💪💪💪
Tamachangamukani guy's. Amalawi. Tabwelani maiko achizathu kuno kuyendesa dziko lokomela winaaliyese osati Malawi guys kaya dziko lathu lisitha liti guy's
Zoona a mtambo zomwe zinacitika nthawi ya boma timadya ka 4 pasiku lija, zicitikenso panopa Acoke!
Uyuyu ndie ndiwachibwana akanamumanga ameneyu mesa ndi amene akasapota mcp nthaw yazisankho ija
Kodi judge uja anayendetsa chisankho cha re-run mu 2020 uja analakwitsa chani???
Zodabwitsadi kwambiri akunena a mtambozi 🙌🙌🙌
Contract inatha
@@MCAnthonyNdau ok ok
Congrats good team mu matiyi milira
Thanks Mr mutamba sure 10:54 😂
Uyo nde mtambo ndimaziwa ine good job
Congratulations mtambo ❤❤❤❤❤❤
Following bro caryon❤❤❤❤
Dats my Comrade Timothy Mtambo I salute you
This is Comrade I know Mtambo anapha msilikali ndi mwala sapanganazo za phadazo Anakuikani pa mpando akuchosaninsoni
Big up Mr Timothy 👏
Thanks mtambo you help us to remove dpp chipani chogawa Malawi chipani chokomela alomwe
😂😂😂😂😂ayamba kale kulira ndíe akazaluza 2025 muzalira bwanjiiii😢😢😅
Wachibwana mtambo iwe sitidzakukhulupiliraso or utayakhula motani sitingave ife
Now Mtambo you are ready to fix the country are you serious?
Makwana keep it up
Maputo osewa chifuka chamtambo manyazi ulibe ukufu uzi use a malawi tsoka anakuzindkra kuti ndiwe ofun kumause amalawi iwee uziona wenkhe umanyoza petr munthalira relo uzitiuzaso zimenezoo wajerasi iweee tinakutuluka amalawi iwee
Bravo opposition lets unite to make a better Malawi
We gonna die because of our country, kulibe kuopa
Mutambo good speech❤❤❤❤❤
Malawi needs prayers indeed
Chief mwayakhula mwadzelu kwambiri but remember nomwenu u will eat chibadzi then muzakhala chete osayakhulaso please please less fight for our nation this country is not for one person
MCP mulimmwamba padzana mumadandaula zomwezo, from next year Muonetsetse musaluze muzafinyidya koopsa a MCP
Love you guys don't keep guite
Nice speech
Dziko mudaliwononga kale mcp my vote
Kķkk
MCP no Chance.
System yomwe MCP ikuchita ndikuba
Iweso pako ukunyoza Mtanbo muziona ana achikangawa anjoka inu mumayesa Kuti ndinu ochenjera mwagwa nayo 😂😂😂
Mbava nzosezi inu, simulators basi azingokunamizani zopusa, analikuti iyeyo poyamba? Amalakhula nchiyani?
Omwe aja anatinzuza Aja MCP itawalonjeza zonona abweraso lero koma mavuto sadzachepadi
Ulemu wanu brother Timophy osaopa osafooka osatopo chilungamo
Mtambo usandilakwise iweyo ulibe nzeru iweyo unali patsogolo kuwononga dziko lelo uzinena zamanyi zakozo usandiyakhulitse pambali
Good job
Ineyo khumbo langa ndiloti ndikangoona bere lomwe anayamwa Mtambo.Munthu uyuyu ndiofunika mu mbiri ya Malawi
Good massage 🎉🎉🎉🎉
Amtambo boma labwino kwa inu ndi litiro?
Nde azisekelera zopusa
Let's learn from our past else history will be repeated and the world will Lough.😂😂
Very good boos
Amayo ku mtonso komweko auze ntambo🎉😂😂
Palibe chomwe mngatiuze coz ndinu nomwe mkatimema kut tipite Kuma demo ndye pano zikukubowaniso ife tili busy kusosa kumunda bwana zinazo mthana nazo nokha
Powerful man
When it comes to this mtambo
Your the best.atrue patriot...
Iweyo tiyenawo agaru