MUKAMVA TIMESTV YASEKEDWA MUSADABWE PROGRAM YAKE NDI YA HOTCURRENT YA DZULO ANG'ALURA MOSANYENGELERA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 22 сен 2024

Комментарии • 101

  • @ChimsyUlemu
    @ChimsyUlemu 16 часов назад +12

    Well speaking men, chikangawa mwamuyankhula koma samamva za wanthu

  • @KeraMkandawire-pn5lx
    @KeraMkandawire-pn5lx 15 часов назад +2

    I can say bravo to the directors of security for both parties of MCP and DPP of what happened in Mzuzu, that was true exercise of a good Democracy. Let peace reigns this is nice. Zikhale choncho Ku madistrict onse especially South and Central regions Ma campaign akhale aufulu. Political tolerance a way to go.👏👏

  • @MosesLeckson
    @MosesLeckson 17 часов назад +3

    Ku Mzuzu kuli anthu ozindikira zimenezi ku Lilongwe sizingatheke and always pamakhala special team ya ziwawa so amadutsanawa zaziwawa sizimawakhudzudza.Alipo ma baunsa amene amayenda ndi zikwanje aja

  • @JeanfatsanJere
    @JeanfatsanJere 16 часов назад +4

    Good idea times yendani mudziwe zoona ndazikonda❤

  • @shenwaahabdulhakim
    @shenwaahabdulhakim 17 часов назад +9

    Ku mzuzu ose ndi a DPP awo mukuona ndi amodzi ena angopita ku mcp kufuna ndalama koma vote yawo ndiya Dpp

    • @frankkalambule
      @frankkalambule 15 часов назад

      Hmmmm ili nde bodza ili

    • @RuthBeyala
      @RuthBeyala 10 часов назад

      𝐞𝐲𝐚 𝐱𝐨𝐨𝐧𝐚 𝐚𝐥𝐨𝐧𝐝𝐚𝐤𝐨 𝐧𝐝𝐚𝐥𝐚𝐦𝐚

    • @AndrewKaira
      @AndrewKaira 10 часов назад

      Bola MCP DPP ayi tu kumpoto kuno

  • @geofreydzinyemba6107
    @geofreydzinyemba6107 7 часов назад +2

    Well done guys mumalankhula chilungamo keep it up

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 14 часов назад +3

    Kungong'alura zilungamo pwiiiiiiiiiii!

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf 12 часов назад +10

    Kuyankhula kofunira zabwino dziko lanu, zikomo.

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 16 часов назад +9

    I could be much impressed if all sensitive positions in the country were approved by a parliamentary commission where all parties are involved .

  • @mtenderemitembe3433
    @mtenderemitembe3433 16 часов назад +3

    Amadanitsa anthu ndi ma politicians. Zinachitika ku mzuzu ndizabwino

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka 5 часов назад

    Congratulations 🎉 Northern region this is what we call democracy

  • @LehmanManere
    @LehmanManere 13 часов назад +3

    In that commission of enquiry you should also include some of Chikangawa villagers please anthu akumeneku Aliso ndimau komaso umboni wabwino

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 17 часов назад +2

    Pasakhale ndipo pasapezeke ntundu wa anthu ndi umodzi omwe odziona kuti ndiye oyenera kutsogolera dziko la Malawi .

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 11 часов назад +2

    guys yehova akusungeni pobisika mwaima pa chilungamo mokonda dziko lanu mosatengela mbali pitilizani

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka 5 часов назад

    Bravo Times TV continue kuyima pachilungamo

  • @williammandhlopa
    @williammandhlopa 7 часов назад +3

    North is special

  • @LastonThelele
    @LastonThelele 16 часов назад +2

    Ma top positions should not be appointed by the president but should be appointed through parliament like mec chairs, inspector genal , nrb chairs not by the president because president belongs to a certain political party.

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 6 часов назад

    It always pains me when we Chewa tribe are taken like fools or all mcp funs. Some Chewaz are exceptional. TTV big up!! Osagawa ma sweet no!! We need leaders who love our Malawi through right decisions and good governance.

  • @BersonChidziwe-yu9jb
    @BersonChidziwe-yu9jb 14 часов назад

    Nice speech with very good logic

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka 5 часов назад

    Kachali is a gentleman ❤

  • @PollyLysonLutepo
    @PollyLysonLutepo 11 часов назад +1

    Tipex yili ndi zolinga ziwili.
    Kwa oipa kubera.
    Kwa olungama kukhozera pomwe paonongeka.
    Koma cholinga chenicheni ndi kukhodzera pomwe pa wonongeka.
    Pa nthawi yija anali kukodza momwe m'naonongeka

  • @Allan-bk1
    @Allan-bk1 14 часов назад +4

    😂😂😂😂😂 guys mwathira nchenga mumpunga wagulu

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole 14 часов назад +1

      Apapa sungadyeke olo kumezanso ayi😂😂🎉

  • @clementmondiwa2128
    @clementmondiwa2128 14 часов назад

    Waiting for them in southwest and 😊😊

  • @GerraldSolomon8
    @GerraldSolomon8 17 часов назад +1

    Dpp yokhayokha iyi agendana bwanji awo akungopita kukatengako ndalama basi

  • @LangsonNyambalo
    @LangsonNyambalo 12 часов назад

    Gentlemen,khalani serious munkhanizi.Mwina chifukwa mulibe Brain.
    Mukuonjeza kutseka kwambiri.

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 13 часов назад

    Powerful massage

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 8 часов назад +1

    Ayitanise ndithu aaa asazembe

  • @EddieChan-hj2ql
    @EddieChan-hj2ql 17 часов назад +3

    We can say mzuzu is the most civilized city.

  • @MikeSymon-si8dw
    @MikeSymon-si8dw 15 часов назад

    It was nice indeed yoooh..😊😊

  • @AboudujanahMawulidi
    @AboudujanahMawulidi 17 часов назад +2

    Chigawo chapakati sangapamge zimenedzi kwanyawu kumene kuja zitsilu za anthu

  • @SqueyaHosmane
    @SqueyaHosmane 2 часа назад

    Congratulations 🎉 wana wakukaya

  • @GodfreyKamphiripiri
    @GodfreyKamphiripiri 12 часов назад

    Nice speech ❤❤❤

  • @JustinMpunga-c8b
    @JustinMpunga-c8b 15 часов назад +1

    Kmanso mmene mwayamikila ma supporters a MCP ndi DPP apangira liwudzeninso bola la MCP kuti kalembedwa ka ma ID zikhalenso chimodzmodzi ma boma onse mMalawi muno

  • @SamuelBillon-i2f
    @SamuelBillon-i2f 9 часов назад

    Very good

  • @CharyLand
    @CharyLand 11 часов назад +1

    Yah Kung,alula

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 15 часов назад +1

    Amai aja ananena choncho chifukwa Mcp ndi imene imayambitsa za chiwembu ndinkona ananena kuti Mcp isadzapangitse ku phalombe

  • @BrendaDimba
    @BrendaDimba 8 часов назад

    Koma nde kung'aluratu no mantra times kip it up

  • @GreenBadani
    @GreenBadani 8 часов назад +1

    💓💓♥️♥️💪

  • @frankiechasokoneza5802
    @frankiechasokoneza5802 12 часов назад

    Mayi Yolamu akugwilitsidwa ntchito ndi Chakwera yemweyoi nothing can change as mcp they are commanding Malawi police to favour them

  • @TamaraSamidu
    @TamaraSamidu 10 часов назад

    👋👋 kuyakhula komatu uku

  • @HassaniKhenge
    @HassaniKhenge 7 часов назад +1

    ine ndi chewa koma mawu oti dziko ndilachewa nde mmm musasalalkhule wangokhala kuti mtsogoleli uyu ndi onyasa mtima ndipo sakukhalaso pampando

  • @MikeMwale-bw1xw
    @MikeMwale-bw1xw 6 часов назад

    Achita manyazi aDpp nthawi zonse kuyipaka mbiri zoipa MCP anthu akuonetsanitu.

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 3 часа назад

    Kodi zikutheka kubela masankho? Ndizowina tipex 2019 MRs jean assah Tipex

  • @TaweniChavulaKamwendo
    @TaweniChavulaKamwendo 15 часов назад +1

    Kkkk Koma anthu Inu pulizi 😂😂😂😂😂😂

  • @PatrickMailos-j6u
    @PatrickMailos-j6u 11 часов назад

    Kwathukuno kummwela sitingalole Kuti MCP tidusane ndimagazi amenewo

  • @KONJEC-m8o
    @KONJEC-m8o 14 часов назад

    I think ikhale Dpp yomweyo zinazi ndizakupha, Kuba .chomwe tikudikira ife Peter akangolowa Ayesetse Anthu amenewa amangidwe basi

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer 9 часов назад +1

    Km kumalawi kuli ntchito eeeesh ai zikom

  • @rashidpoul502
    @rashidpoul502 3 часа назад

    Enafe tinapitila kukapeza 2 pin yandiwo koma ife tikavotela dpp

  • @EdsonChisale-r4y
    @EdsonChisale-r4y 16 часов назад

    Palibe wandale amene azakufere iwe mpanda dzina wakunchira okonda chipani ngati cha mnyumba mwako. Support a party responsibly.

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 14 часов назад

    Umu nde asambwazadi

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 16 часов назад

    Kusekedwa ndi kutsekedwa ndi zinthu ziwiri zosiyana .

  • @YusufChipojola
    @YusufChipojola Час назад

    Kosdi zoti ndege idafika ku mzuzu amamvana ndichani kuti ndege izathele? Nanaga mawu amenewo ku control alipo ngati Mundege mudalibe box ,,,yaku control ilikuti sound

  • @AratonManda
    @AratonManda Час назад

    Ndikuona ngati malamulo adziko amakhwila tchito kumpoto kokha, chifukwa chake mmaboma Ena ake kumakhala chikulilano

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 4 часа назад

    Ine ndimawayamika anthu aku north amakondana

  • @AndrewChawinga-t1v
    @AndrewChawinga-t1v 4 часа назад

    Ndazikonda kwambili zimenez

  • @HedgensChisale-n4b
    @HedgensChisale-n4b 5 часов назад

    Week ya mawa abishop azakhaleposo

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 14 часов назад

    Kodi imu mesa a ndevu zamwayi milati simutenga information ya social media mde za kumangidwa kwa mtambo munazitenga kuti? Inuyo mukudziwa kuti imali plan ya mvp yomwe imafuna kuipitsa mbiri ya dpp bwanji simukunena?

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 3 часа назад

    Kumpoto amantha

  • @MercyDzonzi
    @MercyDzonzi Час назад

    Mmmh mukudziwa zomwe akuchita kuseriku awa asakupusitseni ndithu 😂

  • @GuejendraMk
    @GuejendraMk 15 часов назад

    Zmukamanyoza mudziyamba kuon kut chatsitsa dzaye nchani kut njobvu ithyoke nyanga. Shhaaaaa abale

  • @Peter-yz8tm
    @Peter-yz8tm 13 часов назад

    Dpp ndidye obera zisankho. Only dpp and their team b utm amakamba za chiavhine.

  • @ecksonnjoloma8713
    @ecksonnjoloma8713 2 часа назад

    Onsewa akuzavotera chipani chimodzi,alipo akudyeredwa apapa.akudziwana. sizingatheke kungodusana kumalawi kuno.kkkkkk ku mpoto kuli atambwari😂

  • @MikeMwale-bw1xw
    @MikeMwale-bw1xw 6 часов назад

    Kumpoto kuli anthu ozindikila kuti ndale zisawadanitse.

  • @RichardChirwa-em6qj
    @RichardChirwa-em6qj 7 часов назад

    Chiripo akubisa anthu akuphawa anapha chilima ndi anzake

  • @PatriciaChiwerenga
    @PatriciaChiwerenga 2 часа назад

    Mpaka ena ayedzedwe 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @donbastora854
    @donbastora854 8 часов назад

    Ife si akumwera okonda ziwawa kapena a pakati

  • @kelvindickson
    @kelvindickson 13 часов назад

    Amachita ziwawa ndi agule Aku lilonnge

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya 14 часов назад +1

    Ndinu amanyi nosenu kuli pitala kunalibe nkhaza ? Ndinu zitsilu kwambili mcp singapange naw zaugogo ai

    • @MiracleDamiano
      @MiracleDamiano 12 часов назад

      Hahaha 😅😅😅 yabayatu mwana wa njoka iwe ndye uphulika chfukwa simunat achikangawa party tikukhwekhwezani asatana inu

    • @giftmabuka3589
      @giftmabuka3589 9 часов назад

      Chikangawa ichooo😅😅😅

  • @ShaibuSmart
    @ShaibuSmart 4 часа назад

    Northern Region ndi anthu ozindikira sapanganawo zopepera

  • @MercyDzonzi
    @MercyDzonzi 2 часа назад

    Koma akumanyegererabetu kuwatengera ku china kodi tiwakhulupilire bwanji anyamata wa

  • @FadwukeAfoso
    @FadwukeAfoso 5 часов назад

    Boma sitikusintha mwayambakale kulira

  • @FloraBanda-w7t
    @FloraBanda-w7t 13 часов назад

    Kod a bishop aja sadzabweraso ??ine amandsangalasa akamang'alula 😂

  • @AlickJam
    @AlickJam 14 часов назад

    Anyamatawa mpaka uniform ku ntchito

  • @rashidpoul502
    @rashidpoul502 3 часа назад

    Kuyankhula kopusa achewa zikoli ndamene amaliwonga

  • @YusufChipojola
    @YusufChipojola Час назад

    Kodi ukakwarila azimayi awili akadwala mozi kumawula ungapitise mzakeyo ?

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 14 часов назад +1

    If the government wanted a fair and transparent election they could have reappointed Mr Chifundo Kachali because he did the last election religiously. But because the current government is aware that they can not win without kubela that's a Ntalimanja was appointed.

  • @MasterMwandira-d3k
    @MasterMwandira-d3k 12 часов назад

    This is northern region, it'll never happen in central and southern region

    • @rodglae6657
      @rodglae6657 11 часов назад

      Tisayiwale koma kuti Chakwera was attacked in Mzuzu pa Katoto pompo when MCP was an opposition party. Ku Karonga was almost a no go zone area mpaka was nicknamed Bengazi for its terror nthawi ya DPP. Ndiye Northern Region is not as a holy region as is being speculated.

  • @ManualCar-d9z
    @ManualCar-d9z 13 часов назад

    😂😂😂😂😂😂😂 kung'alula

  • @PaulMalunga-i5i
    @PaulMalunga-i5i 16 часов назад

    Vuto samamvatu awa mmm

  • @AndrewChawinga-t1v
    @AndrewChawinga-t1v 4 часа назад

    Ku mpoto kuli anthu abwino okha okhatu

  • @KingKambuku
    @KingKambuku 15 часов назад

    Koma yah

  • @FrankMsiska-i9j
    @FrankMsiska-i9j 14 часов назад

    Anthu a kumpoto ndiozindikira

  • @JeniferKananji
    @JeniferKananji 14 часов назад

    Analipo azako akati nawo amuyaya anampita kut zaziiiiii

  • @JaimenadrenadreJaimenadre
    @JaimenadrenadreJaimenadre 17 часов назад

    Alinse voti ilimuntima komachipani chamcp mmmmmm. Chopanda chisoni

  • @tracybennie7783
    @tracybennie7783 16 часов назад +2

    Koma. Thawi. Ya. Piter. Kunalibe. Khanza

  • @RaheemMogoya
    @RaheemMogoya 17 часов назад

    Chakwela ndi galu wa muthu sazatheka satanic wamagazi anapha zake chilima nyan amene uja

  • @FadwukeAfoso
    @FadwukeAfoso 5 часов назад

    Kudanitsa amalawi basi

  • @JhadahLeafs
    @JhadahLeafs 9 часов назад

    Pankuku

  • @JohnMalupia
    @JohnMalupia 17 часов назад

    Zitsilu zili ku mmwela agalu eni eni mbuli mbalame za chabe chabe ,dziko ili ndi la achewa ndipo lidzakhala la achewa mpaka muyaya

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 15 часов назад

      Achewa ake ati Ali ndi dziko mwana wahule iwe, uku sindiko kubweresa chisokonezo kumenek mmalawi muli mitundu yambirimbiri mchewao wapambana chani kt dziko likakhale la achewa kupusa basi kuzolowera kumangogwiritsidwa ntchito ndi andale kt muzikhapa azanu in the name of mitundu

    • @JohnMalupia
      @JohnMalupia 15 часов назад

      @MzadziWanga mukafuna kunyoza muzinyoza munthu osati mtundu wa anthu chifukwa mutation achewa mumanena aliyese ndiye zimatinyasa mchifukwa chake tikuti alomwe nonsense ndinu agalu kuphatikiza ayao ndinu zitsilu ndipo boma simudzaliwinaso agalu ,inu osamadabwa kuti chiyankhulidwe chathu chachikulu m'dziko muno ndi chichewa agalu mbalame dziko ndi la achewa ndipo tikupanani munya muona

    • @DoYouKnow3838
      @DoYouKnow3838 7 часов назад

      ​@@JohnMalupiandiwe munthu omvetsa chisoni kwambiri.