Ndipo the DC sukunama anthu ma mmodzi mmene akuvutilila mhuuu ndaona ineyo kuno ku centeral region mene anthu akumudzi mmene akuvutilila mhuuu ndaona ineyo ndi maso angawa
Mmmmm kodi iwe boni kalindo ku mwela kumene ukunena zoti anthu akugona ndi njala kodi wayamba lero kugona ndi njala kodi dpp ikulamula anthu samagona ndi njala nthawi imene ija, ku mwela or vula itagwa bwino or boma litagawa fetreza khomo lililose matumba 100 sangakolole NDie u da matinamize ku mwela athu ake adazolowela za ulele
Never give up mr kalindo 😢
Mlungu azikusogoleran Mr president ❤❤❤🎉 boooon kalindo the dc❤❤
Osaopa mr president mulungu ali nanu
Umatimilira bon kalindo tell them,more 🔥 you my dear friend
More fire my president ❤❤❤❤❤
Musamasowe big up Booooon ❤❤❤🎉🎉🎉
Matiimilira mr dc❤
Please numbers mr dc tipatseni
God bless you always bon
More fire 🔥 mr president bon kalindo ulemu wanu this president chikangawa is nonsense president 🙄 😑 😒 😐
Uyu atakhala president eish dziko lathu likhoza kukhala lokoma
The Diiiiiiiiii ciiiiiiiiiiiiiiii❤🎉
DC my vote
Sitikhuta English ife
Achalume DC
Salute Mr president
Yr no. 1 the president for poor people bravoooo
Never give up Big
Zoonad Bon Kalindo amayankhul zoonad asogoleri alipo lerowa achuluka kumzikonda basi koma zoti anthu akuvutika sidzikuwakhuza koma Mulungu wanthawi uyu
Ndipo the DC sukunama anthu ma mmodzi mmene akuvutilila mhuuu ndaona ineyo kuno ku centeral region mene anthu akumudzi mmene akuvutilila mhuuu ndaona ineyo ndi maso angawa
Umaima pa chilungamo ❤
Kukanika kutilipila ma supplier ndalama zapita ku unga
My president 🎉🎉🎉
Bon Kalindo osaiwala Mulungu amakantha ena ndi aja adya nkhumba aja kuyamba kumeneko sikunati Mulungu sangalore kut munthu modzi adzizuza anthu osalakwa potenga misonkho yawo msiye n Mulungu adzathana nae
Amalawi tiwone dzina ATIPHA NDIMAMVUTO AMALAWI KUTSAMVA MCP YOYIPA AYI KA KA ENA PAKA PANO AKUTI MALAWI PANO ALIPABWINO iiiiiiii ufiti bwanji koma
More fire ngt bundle the dc❤❤❤
Thanks
DC woyeeeeeee ❤❤❤❤❤
Iwe usadzafe koma udzangosowa kkkkkk❤❤❤❤
Big úp bon
Ameneo ndye Booon kalindo
Koma kupha chilima ndi ena 8
❤❤❤❤ bon kalindo ❤❤ love you ulemuwanu boss ❤️ 😘
Awa ndanzeru
Abale ife tatopa naye munthu wankhaza ngati uyu sindinaone koma asogoleri akungoyangana osayankhula kanthu muchotseni akapitirize za ubusa basi.
Uyuyu muti president yu asatiphwanyitse mutu
Abwana muuzeni fitiyo chakwera avesese pomupha mzake chirima
Eeee ndili konkuno ku dar es salaam, magufuli was a real man and president ever in Africa. Tikumulira zedi kuno.
Blessed Bon the DC!!!!
Mmmmm kodi iwe boni kalindo ku mwela kumene ukunena zoti anthu akugona ndi njala kodi wayamba lero kugona ndi njala kodi dpp ikulamula anthu samagona ndi njala nthawi imene ija, ku mwela or vula itagwa bwino or boma litagawa fetreza khomo lililose matumba 100 sangakolole NDie u da matinamize ku mwela athu ake adazolowela za ulele
Wasowa nkhani ife timalima ndipo ngati mvula yagwa bwino feteleza so mkupezeka mosavuta timakolola ndipo sitipephetsa ife kwathu kuyakhula kopanda mzeru timadya kwanu ife nkhope za anthu akumwela tinabwera kwanu kudzapepha umfa ndiwe opanda mzeru poyakhula, tamasiyani ndale uko km ku makonda iwe Mzimu wa umunthu ulibe
Ndiwe Mulungu kt udziti sitingakolole umagwwtsa mvula ndiwe timakolola ngati mvula yagwa bwino komaso feteleza wapezeka osamayakhula ngati wapanila chigumu zaziii ku centre ndye makolo la chani fodya kt mudzisuta siwe Mulungu chaka chamawa tikolola Mulungu si james
Kodi bwanji kungomuchotsa chikangawayu tatopa naye watinyansa
Moto kuti mbuz!!!!
Km eee chingochi yavuta njala
ᴍᴜᴍᴀᴋᴡᴀɴᴀ ʙɪɢ ᴍᴀɴ
The dc
President adziyenda chifukwa kuyenda kumaphunzitsa kwambiri chifukwa English yako kalindo yomvetsa chisoni go back to school.
𝐢𝐧𝐮𝐲𝐨 𝐚𝐦𝐞𝐧𝐞𝐰𝐨 @𝐀𝐥𝐢𝐜𝐤𝐬𝐨𝐧𝐌𝐚𝐤𝐚𝐭𝐚 𝐦𝐮𝐥𝐢 𝐩𝐡𝐞𝐞 𝐨𝐥𝐨 𝐜𝐡𝐢𝐬𝐨𝐧𝐢 𝐦𝐮𝐥𝐢𝐛𝐞 𝐚𝐳𝐚𝐧𝐮 𝐚𝐤𝐮𝐯𝐮𝐭𝐢𝐤𝐚 𝐮𝐳𝐢𝐤𝐡𝐚𝐥𝐚 𝐧𝐚𝐰𝐨 𝐦𝐳𝐢𝐦𝐮 𝐰𝐚𝐮𝐦𝐮𝐧𝐭𝐡𝐮 𝐰𝐚𝐦𝐯𝐚 𝐚𝐧𝐭𝐡𝐮 𝐚𝐤𝐮𝐯𝐮𝐭𝐢𝐤𝐚 𝐮𝐥𝐢 𝐚𝐩𝐚 𝐤𝐮𝐲𝐚𝐤𝐡𝐮𝐥𝐚 𝐧𝐠𝐚𝐭𝐢 𝐮𝐥𝐢𝐛𝐞 𝐧𝐣𝐚𝐥𝐚
Asaa awaso ndye nda mbuli theretu mwamva tidya chizungu ife? Chizungu chosapindulisacho akolora kuyendayendako akuchoka 2025 ufune usafune ase
Mbuzi ya president yosakaza eeeeeh khululu yeni yeni
Rispect Mr BON kalindo
Mumakwala kwambili Mr ndikamanvetselama voice yanu ndimasa ngalala kuti president wathu wadabwa kenakake
Dc umatiyimila
Mbambande
Matiimilira mr dc❤