Mcp ikuyandama chavhikulu kuswa kuphwanja smartmatic mcp tikayilanda smartmatic muoona matama wose atha ana wadowado mimba zipwa chifukwa akadzaluza ose azabwera kuno ku mzuzu prison or ku nkhata bay prison
Koma ndizoona chakwera mumapanga ma push ups koma mmalawi muno muli president ngati ....nanga president kumapanga ma push ups koma kulamula ziko kulilephela ....chisilu cha munthu iwe chakwera ....munthu wopusa kwambili
Amene anathawa kumudzi kupita ku town kufuna kuti azikalandila mbale ya ufa yosagwilila ntchito chifukwa cha ulesi ndi amene amangofuna kutola zosagwilila ntchito, wa ulesi asadye
Mwauzeso a mcp apiteso kwathuko ku chinsapo koma asapite ndi oyimba😂😂😂😂akapita ndi Dan-lu,,,ndiye kukadzadzadi chinsapo imakonda ma Dance😂😂😂😂koma awa ndiye madolo osayenda ndi oyimba,,,
Popanda kubera chisankho aaaaa Trump wathu wathu akuwina
Kuonera from Majuni , Mozambique
Long live Apm❤
Dpp more fire 🔥 2025 boma my vote
Koma ngat osawina dpp izakhala kut chikangawa wabela
Let's pray my dear palibe kubela awa azipita basi mulungu wakana
@@RemitterFlik1130live let's pray
Ku Dpp posankha Alfred Gangata kukhala Vice president wa Central Region, sitinabetse❤❤❤❤❤ tilipambuyo panu Gangata. Dpp my vote forever❤❤❤
me too dpp my vote
@moureenmolesi Thank you my sister
APM my vote 💙💙💙💙💙💙
abrian banda ndi DPP bas
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Nankha akazabwela pangolini APM kuzazaza bwanji ❤
Utm my vote ❤
My vote 💙💙💙
APM my vote 🔥🔥
APM akhalise ❤❤💙💙💙💙
Adad omwewo
Adadi wwww
Thanks times group mumatiimilila
Chikangawa ,wadowado BP yashuta
Tramp wanthu APM
Lilongwe oyeee agangata oyee ambuye akhale nanu aDPp
More fire DPP l love u Dad
Live from Durban
Congratulations dpp
Manyazi bwa kubetsa vote 😂😂😂
Chiyembekezo cha amalawi dpp
Kuonera from Cape town.
DPP iwina next year trust me am listening from RSA
Mukamati kung'alula kukhala ngati okhoza kulankhula kapena wanyanyala
Panopa ting'alule kaye, fundo tikupatsani campaign ikayamba. Paja Apm amanena zomwe achite osati kuti atamike.
My vote is for Dpp under Apm osati akuti chakwera mbuzi yeniyeni .....katundu akukwera daily ...mafuta agalimoto akusowa ....njala ndiye ndi imeneyi ..ndingavotelenso chakwera chifukwa chiyani .....chakwera walephela ndipo sitimaziwa kuti chakwera angawononge ziko chonchi
Agangata mukufuna abusa alowe pansi ? Mwagwedeza centrally region
Ndipo Kwambiri
Dpp oye
Mcp kwakwe nkumpa kuba ndi koononga, King nkong muthu oipaa kwambili, 2025 achokee mazila aoo oseeee!!
Koma gangata akugwira ntchito kwambiri
chikangawa watitopesa achoke
Mcp ikuyandama chavhikulu kuswa kuphwanja smartmatic mcp tikayilanda smartmatic muoona matama wose atha ana wadowado mimba zipwa chifukwa akadzaluza ose azabwera kuno ku mzuzu prison or ku nkhata bay prison
Eeeesh
Koma ndizoona chakwera mumapanga ma push ups koma mmalawi muno muli president ngati ....nanga president kumapanga ma push ups koma kulamula ziko kulilephela
....chisilu cha munthu iwe chakwera ....munthu wopusa kwambili
MCP apakire basi
Amene anathawa kumudzi kupita ku town kufuna kuti azikalandila mbale ya ufa yosagwilila ntchito chifukwa cha ulesi ndi amene amangofuna kutola zosagwilila ntchito, wa ulesi asadye
Apm my vote komanso sitidya Zolandila
@@AlexanderYovatiKhumalo sitidya Kwanu nzanga phunzira kupanga zako iwe nda mene umadya zolandira kukasiya kwanuko chitsilu iwe 😝😝😝😝
Tiyeni tiuze boma litipatse ma solar pump olimila mbewu za m'thilila kumakolola kawili katatu pa chaka njala osaiona, boma lithandizile kudikila kuti lidzitipatsa chilichonse Cha khomo lathu mkovuta tiyese kuyamba kudzithandiza tokha masiku ano mbewu iliyonse imene munthu ungalime ndi ndalama mitengo ya mbewuzo ilibwino.
Malawian politics
Katundu omanga mmawaya dpp ikulamulaso
Ngangata and chisale ipatseni Moto kuti,buuu kwa chinsapo kwavuta
Kodi mumkung'alula mulimfundo zanji pliz,
Tamawauzani anthu mfundozo ❤
Iweyo ndi amene uli ndi vuto sinanga mutu mwakomo mwazaza mamina okhaokha ndi thoovu thooo laku kasiya chikangawa
@AmoTiamo 😃😃😃
Odi uko! DPP 2025 pa chiongolero
Koma kuli ntchito 🩵🩵🩵✔️✔️
Peter wamtharika ndi McDonald Trump wa kumalawi 2025 Boma ilo
Koma gangata wadya one
Zabwino zonse apm
Dpp waboma 2025
Apm boma 2025
Chibwana chimalanda
Chizolowezi cha nankholowa chinazulitsa mbatata ya pansi
MCP Wake up
DPP chaka chamawa boma
Amanyengeza a mcp
Kwavuta kwambiri
Kwanthu mkobeba
careful with the numbers the crowd is full of children to them it is Sunday intertainment
Ana ake a mnyumba mwako, kavaleni mazenela muone bwino bwino, osangovomereza kuti mcp yakanika kuendetsa boma bwanji
Mwauzeso a mcp apiteso kwathuko ku chinsapo koma asapite ndi oyimba😂😂😂😂akapita ndi Dan-lu,,,ndiye kukadzadzadi chinsapo imakonda ma Dance😂😂😂😂koma awa ndiye madolo osayenda ndi oyimba,,,