Terima kasih untuk penjelasannya! Saya butuh saran: Saya memiliki dompet SafePal dengan USDT, dan saya memiliki frasa pemulihan. (alarm fetch churn bridge exercise tape speak race clerk couch crater letter). Apa cara terbaik untuk mengirimkannya ke Binance?
Mwagundika mabodzatu mukuona ngati Malawi wakale ujatu. UDF mmmm will never win the general election 2025. Us as Malawians we don't want yellow again in government
Terima kasih untuk penjelasannya! Saya butuh saran: Saya memiliki dompet SafePal dengan USDT, dan saya memiliki frasa pemulihan. (alarm fetch churn bridge exercise tape speak race clerk couch crater letter). Apa cara terbaik untuk mengirimkannya ke Binance?
Atupere atenga Boma. Ndilinaye patsogolo.
Akufziwa sangakhale president
Mu nthawi ya being humble .....tinamizeni basi....
A P M alipo ndithu
Apm
Mumanama anthu andale inu mumangofuna anthu akuvoteleni
Dpp will get 64 %
Ulamuliro sumayenda ngati ufumu.kwatu sitimadalira anthu andale, zinthu zativuta chifukwa cha chilala.ine ngati mlimi ndimadzichitira zonse pandekha. Koma kusagwa bwino kwa mvula sizinandiyendere.Nde wina sangandinamizepo apa.
Ena akut azizayenda wapasi kk😅
Ndizaboza zimene akulankhula ndiza boza nchito azazichotsa kuti kodi mvula mene yavutila umu chakidwa cizacokela kuti?
Akunama ameneyu
Boma APM akutenga
12:09
Those promises are meant children.
Ife sitifuna ndale ya phada. Don't take it after your father.
Liluen de moz
Zabodza zimenezo, andale amalankhula bwino akakhala kunja kwa boma , kungolo m'boma aiwala!. Za ziiiiii zimenezo.
Atupele tinene zowona inuyo simungawine,tinene zowona,panopa anthu akuwedzekani kaye,chifukwa inuyo ndi bambo anu mukudya limodzi ndi chakwera oloko mukunenazi zoti tima tokha mphamvu zonsezo akukupasani ndi chakwera,ndiye musavutike kumati udf iwina aaaaa mukuzinamiza
Koma ziliko
Ukunamatu iwe tobacco sangate koma ndalama za tobacco akudya chakwela ndi bambo ako
Mwagundika mabodzatu mukuona ngati Malawi wakale ujatu. UDF mmmm will never win the general election 2025.
Us as Malawians we don't want yellow again in government
Munthutu uyu alindibodza ngati bambo ake
Kkkkkkkkkkkkkkk zaziiiii
😂😂
😂