Mau amenewa Chakwera akava apuma bwa. Chikangawa alibe mtendere wamtima

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 11 сен 2024

Комментарии • 28

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 23 дня назад +4

    Chakwera bas watapo wolo atachoka lero alobe ntchito ndive

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 23 дня назад +1

    Kufotokoza Kwa mnzeru ndikuganiza kuposa Chakwera😂😂😂

  • @NaomiMagoha-uw7rm
    @NaomiMagoha-uw7rm 16 дней назад

    Adamwera tea ndalama zafodya sangapezeke nazoso😂

  • @Sammy-vb1ed
    @Sammy-vb1ed 23 дня назад +1

    Chakwera zamukanika, chimene akudziwa katangale, kupha, kukweza dzinthu, tsankho komanso kumangomanga anthu osalakwa. Chakwera akuipitsa mtundu wachewa, achewa siopa koma oipa ndachakwera ndi cabinet members yake. Chakwera he will not pass elections ndimunthu oipa komanso osayamika pazimene alinazo.

  • @JosephyMussa-f5e
    @JosephyMussa-f5e 20 дней назад

    Munthu opanda umunthu ngati uyo sindinamuone kumangokwedza zinthu opanda kuganizila osaukafe mmmm ai watitopetsa

  • @StevoZimba
    @StevoZimba 23 дня назад +1

    Mr chikangawa akupita ku Germany kukasokoneza za report ya ndege😢😢😢😢

  • @user-gd7ce7fc6p
    @user-gd7ce7fc6p 19 дней назад

    Kufotokoza mwanzelu ndipo eshii athu maganiza sure

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 23 дня назад +2

    DPP iyoooooo❤❤❤

  • @MarryUnyolo
    @MarryUnyolo 19 дней назад

    Zoonadi anthuwa akunena chilungamo thumba la fateleza kuchoka pa 18000kufika 100000 amene akuona mavuto avota mwanzeru. Koma tikafuna mavuto kuti apitilire tivotera chakwera

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 23 дня назад +2

    Kkkkkkkkkk fatereza yemweyo

  • @PreciousBandah-l2r
    @PreciousBandah-l2r 17 дней назад

    Brain iwey mcp itenga boma osaopa osatopa mcp anthu awo nd a dpp iwens

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 23 дня назад +1

    Achewa mbambande zed ❤❤

  • @Elson-cf1gy
    @Elson-cf1gy 23 дня назад

    Anyamata amzeru kuyangula mbambande.osamuikilakumbuyo chikangawa.

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 23 дня назад

    Ochewa omweo kkkk fotoleza yemweyo kkkk yomweyo 😂😂😂

  • @fatsanichibwana9438
    @fatsanichibwana9438 19 дней назад

    🎉

  • @HarryKandani
    @HarryKandani 23 дня назад +1

    Munthu oli ulakwa 😂😂😂

  • @KelvinKapalamula
    @KelvinKapalamula 21 день назад +1

    😂😂😂😂

  • @rachidepitamuhamedmuhame-jg9id
    @rachidepitamuhamedmuhame-jg9id 23 дня назад +1

    Koma brain fatereza kkkkkk einteni nfaifi

  • @kantayeniphiri4016
    @kantayeniphiri4016 20 дней назад

    Mbuz ya munthu iwe

  • @paulkatunga5738
    @paulkatunga5738 23 дня назад

    Ine ndalama yafodya ndilinayo ngati akuyifuna abwere adzatengeko

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o 20 дней назад

    Fateleza

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 21 день назад

    Fateleza 😂😂😂😂 brain

  • @CrytonMalunga
    @CrytonMalunga 23 дня назад +1

    Koma eeee ochewa mwayitha

  • @HarryKandani
    @HarryKandani 23 дня назад +1

    Olumbwita

  • @EagerBulldogPuppy-fb3hf
    @EagerBulldogPuppy-fb3hf 23 дня назад

    Naye Brian amafuna zomwezo

  • @user-ww9rj2wx8d
    @user-ww9rj2wx8d 23 дня назад +1

    Kkkkkkkk

  • @user-ji4xn6me8d
    @user-ji4xn6me8d 23 дня назад

    😂😂😂 odi ukooooo

  • @Mrsusumila
    @Mrsusumila 21 день назад

    😂😂😂