MZUNGUYU APA MCHOTSENI |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 6 сен 2024

Комментарии • 256

  • @emanuelphupha19
    @emanuelphupha19 Месяц назад +15

    If we had leaders like Mr Usi before! Aaaaa Malawi would have been a beautiful country. Let's support him to transform our country.

  • @user-ro1pl7rv7z
    @user-ro1pl7rv7z 21 день назад +3

    Michael usi loves his country... AND jealous people are feeling painful to see him doing this 😅😅

  • @InnocentChimemya
    @InnocentChimemya Месяц назад +5

    This what we are looking for our leaders to do. Go to the ground yourself sometimes and a look on your own. May you strength the leadership spirit to be like this. Bravo Dr Usi

  • @kensonmbewe6692
    @kensonmbewe6692 Месяц назад +7

    Zomvetsa chisoni kwambiri, dziko silingatukuke chonchi, Koma Michael Usi Ambuye akusungeni ndi moyo. Izizi anthuwa amapanga dala, they make them to be loops for cash gate leakages. Wish long life Dr Usi

  • @AaronNyirenda-v5p
    @AaronNyirenda-v5p Месяц назад +3

    You have started well Dr Usi may God be with you , we need courageous leaders to transform our nation. This is a servant leader not a boss one

  • @Twaya-ds7tf
    @Twaya-ds7tf Месяц назад +15

    Uyu ndiamene akufunika kukhala mtsogoleli wadziko osati zinazi kumangokhala mu offers ,my vote for usi

  • @Zionefaith
    @Zionefaith Месяц назад +21

    Zinazo zili apo
    Koma chilungamo apapa malawi akhoza kusitha zitapitilira zoterezi

    • @victorauwana7258
      @victorauwana7258 Месяц назад

      Vuto ndiwe mwana ku ndale .. mcp imafuna munthu oti sangawapase mpeshupeshu kundale .. why sanamupase chilima this chance

    • @CharlesPhiri-ds1rk
      @CharlesPhiri-ds1rk Месяц назад

      100%

    • @MeruMitha
      @MeruMitha 23 дня назад

      they are not talking about the pope kkkk😂😂😂😂

  • @user-de6dz3yv5l
    @user-de6dz3yv5l Месяц назад +11

    Mukamaliza.... Muwaitanitse ma contractor Omwe anapasidwa ntchito yomanga bridge ya Mulanje mkando

  • @peterchiutsi
    @peterchiutsi Месяц назад +2

    People can you see that this guy has an ability to deliver something to this Malawi guys lets stop kuyang'ana zinthu mwa ndale and lets spot chilungamo he has something special that Malawian politicians are lucking

  • @EnerstBanda-m4s
    @EnerstBanda-m4s 29 дней назад +2

    Dr Chilima ankapanga zimenezo ndipo Anthu anakamuuza president kuti akushaina mpakana kumupezera zifukwa zambiri mbiri till kumuchepetsera mphamvu kenako milandu later kumupha

  • @chiccochimwaza4791
    @chiccochimwaza4791 16 дней назад

    Mr Usi , Continue monitoring development we need your leadership. I salute you Mr vp

  • @LaurentNewa
    @LaurentNewa Месяц назад +7

    Yes that is magufuli spirit,

  • @Stephanogube237
    @Stephanogube237 12 дней назад

    Michael usi zachbwana sakupanga nawo that's what we all need in Malawian leadership

  • @user-kn9jz4qp9h
    @user-kn9jz4qp9h Месяц назад +9

    Bwana Usi ndakukondani alesi sakufunika zikomo

  • @shafiemalobvu
    @shafiemalobvu Месяц назад +13

    ndipo zikamakhala choncho bwenzi Malawi alipena pake

  • @AicyGlance
    @AicyGlance 12 дней назад

    Where were you Utsi?
    This is greatful movement. Osamasekerera zoputsa ...being a leader zimafunika choncho ndithu

  • @Standwell78
    @Standwell78 Месяц назад +7

    Ku immigration please zibwana zichepe chifukwa ndimbali yimozi yimationongela kwacha yanthu

  • @CharlesBainett
    @CharlesBainett 20 дней назад

    🎉good leadership, keep it up our VP

  • @deborahngwira724
    @deborahngwira724 Месяц назад +6

    Izizi ndi zabwino, chabe kuti next term sakutengaso, safuna anthu otere.

  • @innocentmanda7885
    @innocentmanda7885 21 день назад

    Usi Can be a good President. He can deliver

  • @DanielMengesi
    @DanielMengesi Месяц назад

    Zabwinobwino. Kumeneko ndiko kulikonda dziko lathu, sianakalipe. Aaaaa! Zina zimawonjeza.

  • @MCLoudZeka
    @MCLoudZeka Месяц назад

    Michael Usi iiiii beautiful leader

  • @thomluciouss7360
    @thomluciouss7360 Месяц назад +1

    Kkk let's start what you have not done simple then we will start from there well done Mr vice president

  • @ChipiliroKasakula
    @ChipiliroKasakula Месяц назад +1

    I like the fact that Mr VP you are dedicated to serve the interest of Malawians not yours alone big up

  • @isaacchagwa2917
    @isaacchagwa2917 Месяц назад

    Usi this is a way to go.I like you that you dont pay attention to politics,but real development.You will never be loved by selfish politicians who cherish in rallies

  • @SOSTENLPHIRI
    @SOSTENLPHIRI Месяц назад +1

    KOMA bwana VP mwachemetsatu

  • @SamsonChilonga
    @SamsonChilonga Месяц назад +2

    That's what we want Malawi politicians and leaders to be

  • @GiftCMlangeni
    @GiftCMlangeni Месяц назад

    Ididn't know that Dr michal usi is that serious oooh my God. This kind of head is out of Malawi education system indeed. And he don't tolarate nonsense which means it also pains him as aleader. Just imagine if we have such leaders.

  • @ManzyMassa
    @ManzyMassa Месяц назад +2

    Outstanding 😊

  • @ngindechikalodza8051
    @ngindechikalodza8051 Месяц назад +1

    Ine usi ndimadana naye Koma izi zokha nde zandisangalatsa

  • @FatimaRehemah-gi4mp
    @FatimaRehemah-gi4mp 14 дней назад

    thus zomwe amafuna chilima but amakhomeleledwa ...mpaka mmanda ..mwayi kusiyana ...rest well chilima ...

  • @ShurahimWyson
    @ShurahimWyson Месяц назад +1

    Good VP asamangoti apita kunja apita kunja kumangotha ndalama za zii no yenderani zonse bwana apa mukapitiliza mope a ma voti ochulu ka

  • @user-re7fo3be2z
    @user-re7fo3be2z Месяц назад +2

    VP don't forget immigration sector

  • @ShurahimWyson
    @ShurahimWyson Месяц назад +2

    Suimba anthu timakawakaziwili kumeneko ndikumawalimbikitsa km pano yo no way to go

  • @user-ps8vq5co8n
    @user-ps8vq5co8n Месяц назад +3

    Excellent usi

  • @vitumbikocobysinyiza-5116
    @vitumbikocobysinyiza-5116 Месяц назад +1

    Very nice koma MCP payokha ayi situyifunaso

  • @AndrewNjikho-ne1le
    @AndrewNjikho-ne1le 23 дня назад

    Good work the VP koma azungu muziwakalipira mwa ukathyali kuwopa kunyula mu njira zina.

  • @FarookStambuli
    @FarookStambuli Месяц назад +2

    President ukhale iweo bwana usi more fire

  • @Yamikani-q6s
    @Yamikani-q6s Месяц назад +1

    Good job,,, big Mr VP

  • @sungirenikampu8630
    @sungirenikampu8630 22 дня назад

    Uyu avutika naye anthu , that's how agood leader work's

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o Месяц назад +1

    Good job Mr Usi, tangowathamangitsani abolingo awa

  • @omarduwa3441
    @omarduwa3441 Месяц назад +1

    Muwumiseso nyanja ya rake Malawi kuti nsomba tizigwila mosavuta

  • @DavieKumbanga
    @DavieKumbanga Месяц назад +3

    Mudzaendeleso mseu wamkati mwa town ya balaka from ngwangwa filling station to balaka escom house ka mseu kosakwana 3kms chaka chino chachiwili sakumaliza

  • @allanlouis6235
    @allanlouis6235 Месяц назад +7

    Izi zipangitsa kupanga chithu chosalimba

    • @innocentmanda7885
      @innocentmanda7885 21 день назад

      Poor thinking capacity, in Japan or China they can build that in less than a week. But they infrastructures are way much too strong than ours omangidwa 10 years iyo

  • @olobodokatwaha5947
    @olobodokatwaha5947 25 дней назад

    Malawi akuoneka kuti mbuyomu munalibe anthu
    Ngati usi chifukwa usi akufuna kuti
    Ife amalaw tikale ndi zochita uyu ndi
    Leadership wabwino kwa ife amalaw
    God bless you usi God bless Malawi

  • @user-ke2dp7vk7x
    @user-ke2dp7vk7x Месяц назад

    Nice vp watching from mgubudu 🇿🇲 Chipangali

  • @user-pb6wb3iz7z
    @user-pb6wb3iz7z Месяц назад +1

    Usi keep it up kkkkkk you're the game changer

  • @georgegondwe4636
    @georgegondwe4636 16 дней назад +1

    Ma PC mumapangira dala kuti muziday ndalama you cant change the design while the contracter is building

  • @user-zf4ij4vs3d
    @user-zf4ij4vs3d Месяц назад

    I wish the president also to be crc like manganya you are well done keep it up

  • @FanscioDancun
    @FanscioDancun Месяц назад

    Remind him of immigration departments people are just ducking around there

  • @kenmadan5350
    @kenmadan5350 Месяц назад

    Big up bwana vip ,this is powerful ,my vote of thanks

  • @PeterKhumbilaZimba-ql9ue
    @PeterKhumbilaZimba-ql9ue Месяц назад

    Yes my president if we were having you b4 our country could be somewhere.

  • @ronaldflitwick3383
    @ronaldflitwick3383 Месяц назад +4

    Uyuyu bola akanakhala ku utm osati mcp yakeyo

  • @ndagomaMagalasi
    @ndagomaMagalasi Месяц назад

    That's awesome mr vice keep it up

  • @adamashrafi5875
    @adamashrafi5875 Месяц назад +2

    Kuti apezeke a Usi atatu malawi akhoza kusintha

  • @kamenakedrick7644
    @kamenakedrick7644 28 дней назад

    Usi ulimutu sana keep it up

  • @IzzyAsir
    @IzzyAsir Месяц назад

    my freedom fighter mr usi keep it up

  • @stevenmwiinga165
    @stevenmwiinga165 Месяц назад

    Very powerful vice president 💪💪💪💪

  • @MikeNkhoma-jm6uu
    @MikeNkhoma-jm6uu 27 дней назад

    Awa ndiye awona chomwe chidameta nkhanga mpara

  • @TrophyMwafulirwa
    @TrophyMwafulirwa Месяц назад

    You are the right leader, continue to do so

  • @NoreenNaituri
    @NoreenNaituri Месяц назад

    Wonderful job Mr VP,I ministers must lean something

  • @paulonipuecha8760
    @paulonipuecha8760 Месяц назад

    Nsogoleli wa Chisanzo. I m here in mozambique and as well a Mozambican

  • @gracemiranzi3780
    @gracemiranzi3780 Месяц назад

    Mpasa mulandu mungoti pheee mcp ilibe zimenezo

  • @AsanteMungu-d6b
    @AsanteMungu-d6b 14 дней назад

    My vote to usi❤❤❤

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg Месяц назад +1

    Usi wayamba bwino kwambiri malawa atha kusintha ndithu

  • @Edwinsanga-zh4yv
    @Edwinsanga-zh4yv Месяц назад

    😊mupitekoso kuma offence yama passport akupanga zibwana kwambiri anthu azidikira passport mupaka chaka wosatenga passport

  • @AnneJenalaMbale
    @AnneJenalaMbale Месяц назад

    That's awesome our VP keep it up

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Месяц назад +1

    😂😂😂koma yaaa mwayamba boza chakwera akutumani

  • @jomochirwa
    @jomochirwa Месяц назад +1

    But ine ndikuwona ngati kuti amupatseso agriculture ministry .ameneyo akuwonetsa kuti alibe dyela atha kuthandiza ku zamalimidwe njalayo mwinaso kuthelatu.chifukwa zonsezi ndi chabe koma dziko lili ndi njala anthu akufa ndi njala.kuyambila muluzi gv,bingu,joice ,peter mpakana lelo chakwela palibe boma limene lapititsa patali zaulimi kuti njala ithe.

    • @HendresonTafatatha
      @HendresonTafatatha 26 дней назад

      Zoona sabsidy ija anakamapanga zinenezi Kwa ma contractors zinakayenda bcz panali ma contractors adyera oipa Moyo Koma anasekeleledwa kwambiri

  • @GeoLikwanya-cb9gn
    @GeoLikwanya-cb9gn Месяц назад +1

    Komaso tiyeni tiziyang'ana mbali zonse... Iyeyu zaka ziwiri zonsezi anali kut osabwera kuzaona ntchito yomwe anayamba... fotsek!

  • @user-et3il7pi7t
    @user-et3il7pi7t Месяц назад

    Usi. Yes you can make this country change and we need you to check our mbelwa university why are we not on the ground work regards swank Ibrahim mzimba pelekezi constuency

  • @thokokankhunda7725
    @thokokankhunda7725 Месяц назад +1

    mulungu amapanga njira uyuy sikape blv me

  • @hawardmkandawire673
    @hawardmkandawire673 Месяц назад

    This guy is so intelligent ❤❤❤

  • @GiftCMlangeni
    @GiftCMlangeni Месяц назад

    That contractor guy why is he whispering when responding to the VP?? Is he like that or kudelera kapena manyazi kuti wagwidwa ufiti??

  • @alfrednkhata-vt9qb
    @alfrednkhata-vt9qb Месяц назад

    God bless Usi for being aggressive to shake people in offices. Too much being wasted.

  • @Fravor95
    @Fravor95 Месяц назад

    mukatha kumeneko mutapitakoso mu mzinda wa Lilongwe they are playing too much🤨

  • @JerryNcube-gt3te
    @JerryNcube-gt3te Месяц назад

    ❤❤❤❤ Mr VP mukuesetsa Kumbali yanu

  • @ewn-mc6jv
    @ewn-mc6jv Месяц назад

    Bwana Usi amatha kugwira bwino koma vuto ali pa kaliyala. Pajatu wokwela Ku kaliyala siimba beru

  • @JrAlfeoLungu
    @JrAlfeoLungu 20 дней назад

    Wangokhala kathyali koma ntchito yake ndiyonthandiza Dziko

  • @chiefmitengo
    @chiefmitengo Месяц назад

    Makina vice President usi

  • @user-mb8ye1ve5w
    @user-mb8ye1ve5w Месяц назад

    The former Veep wasn't aggressive

  • @JuliusMtekele
    @JuliusMtekele Месяц назад

    Our vise president did it well 🎉🎉

  • @IshumaerWazakile-u5d
    @IshumaerWazakile-u5d Месяц назад

    zonse ndi zanu km ine ndikungofunako chisot ndi make sikono ndi maglass bs chonde avice president

  • @GonçalvesXavierOrlando-m8m
    @GonçalvesXavierOrlando-m8m Месяц назад

    Ine sindine malawian km a vp ndawakanda magwilidwe ao a ntchito

  • @graciannkumba-rb8qt
    @graciannkumba-rb8qt Месяц назад

    Thus good Mr Micheal usi

  • @NatashaMkumba
    @NatashaMkumba Месяц назад +1

    Sangazumalize ameneyo mavuto alipaliponse taikani chimanga kwa ADMARK apa osati zaziiiizo

  • @PeterMukhori
    @PeterMukhori Месяц назад +1

    Izi nzomwe ankafuna Chilima koma akati atere amamkhomelera

  • @user-hc9hc3dk5o
    @user-hc9hc3dk5o Месяц назад

    Micheal "manganya" USI.litle did I know you're that brilliant

  • @geoffreymugawa8632
    @geoffreymugawa8632 Месяц назад

    Maganizo akupanga manganya ndiabwino koma vuto chinthu chitha bwanji ndalama asanapereke zokwanira ndiye zichani ungamange nyumba ulibe ndlama yokwanira wasewero uyu😂😂😂😂

  • @EstherZintambira-sq3yy
    @EstherZintambira-sq3yy Месяц назад

    Akunenepatu bambo asikono mpando wa VP ngonona

  • @RalphZambezi
    @RalphZambezi Месяц назад

    Kugwa mowilikiza kwandalama ya kwacha kwasokoneza ntchitoyo,simukumvetsa pati Bambo asikono😂😂😂😂

  • @LusandaZuma-i3q
    @LusandaZuma-i3q 19 дней назад

    That changes was just part of stealing money

  • @FrankChindimba-j5v
    @FrankChindimba-j5v Месяц назад

    Osapanga zamolalotu komanga ngat mkupanga zimenezo muchoonadi Mulungu akudaliseni

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 Месяц назад +2

    Uyu ali ngat maguful
    Koma posachedwap mumva amabungw akt auful kt sakuchit bwino asiy

    • @CharityMhone-uk9ym
      @CharityMhone-uk9ym Месяц назад +2

      Sangafanane ndi magufuli..never magufuli samamwaza ndalma amachita zitukuko zoopsa kufuna chabe vote ya Malawi kt azavotele Mr chikangawa

    • @PrinceBlessings-bv5bs
      @PrinceBlessings-bv5bs Месяц назад

      ​@@CharityMhone-uk9ym ndipo ngati amalawi tipuse mukamphindi kochepaka komwe akubweresa tokoma 😂😂😂😂❤ Mcp will lead again Next year....

  • @SuzgoMkandawire-ss4kh
    @SuzgoMkandawire-ss4kh Месяц назад

    Believe me if hes a president we can change for sure

  • @JamesMatambo-x7q
    @JamesMatambo-x7q Месяц назад

    This is great 😂🎉😂🎉Mr Vp

  • @user-ve7rx7vj1g
    @user-ve7rx7vj1g Месяц назад

    He is doing the needed

  • @mikefoster3828
    @mikefoster3828 Месяц назад

    Zofunikira zimenezi go ahead

  • @FisherAction
    @FisherAction Месяц назад

    Time out nothing happens failing to organize his source as UTM leader not well organized original UTM leader was starting doing as such but cruel mcp leaders stop him now they realize and regret too late stop it it's no sense

  • @FrancisNyasulu-v3b
    @FrancisNyasulu-v3b Месяц назад

    Kma apapa amaitha kwambiri ndie zikufunika Ku Malawi izi