ZOMWE ACHITA ANA A KU MZUZU UNIVERSITY PRESIDENT CHAKWERA ATANGOFIKA PA KATOTO MADZULO OMWE UNO

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 сен 2024

Комментарии • 234

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i Месяц назад +20

    Malawi is a very sad country, where did such a stupid president come from?

    • @PhillspicJere
      @PhillspicJere Месяц назад +2

      Zikuvuta ithought uzinena zakupusa Kwa bambo ako pobeleka mwana ofuntha ngati iwe?

    • @user-si7po9sd5i
      @user-si7po9sd5i Месяц назад

      @@PhillspicJere ntumbuka opusa iwe galu,ukununkhaso nkamwa pamodzi ndi mtundu wakwanu onse.

    • @user-wi9pe2hz7e
      @user-wi9pe2hz7e Месяц назад +1

      Akuluwa amatha kuyankhula mopeleka chiyembekezo kma pa ground 0%😂

    • @user-qq1uj7ct6n
      @user-qq1uj7ct6n Месяц назад

      This is Mr Chikangawa

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Месяц назад +14

    Kkkkkk atumbuka kkkkkkk simuzatheka angakhare Sinomse komabe zitsiru zachuluka😂

  • @user-bl2ee4zk4n
    @user-bl2ee4zk4n 22 дня назад +1

    Simunati MCP Ikubwera mwa nkokomo,mpoto yonse ndi ya Mcp.Bwana president mtima pansi ,kumpoto kuno chomwe tagwilizana chimakhala chimozi.Bwana president ma constituency wonse komanso mpando wa u president zikupita ku chipani cha MCP ndi president Dr Lazarus maccarthy chakwera 2025.❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Месяц назад +15

    😂😂😂 amalawi amangoombela mmanja zilizonse lululu mukagonabe ndinjala what a shame chakwera simunthu othandiza

    • @MatthewKanyenda
      @MatthewKanyenda Месяц назад +1

      AMALAWI Mitu yathu ndi yofooila, dziko lathu palibe chomwe chidzasunthe chifukwa choombera mmanja ndi zopusa zomwe

    • @zimmekapachika6784
      @zimmekapachika6784 Месяц назад

      Ndipo sitichedwa kuyiwara,akutinamiza uyu cholinga anthu amuvotele​@@MatthewKanyenda

    • @AshrafMasese
      @AshrafMasese Месяц назад

      Malawi sizatheka mwachuluka mbuli kuomba mmanja ndi kululuta for 50 years palibe phundulake

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg Месяц назад

      Ndipo live, maiko anzathu amakwiya zenizeni osati zibwana tikupangazi.

    • @FelixMachika
      @FelixMachika Месяц назад

      Zikundibowa Z, kumangolulutira zilizonse. Palibe mfundo apa😢😢eshiii Voti ikuchedwa bwanji? 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢Za chamba basi😢😢😢😢tilinso ndi mtsogoleri muno? For sake! Nditukwana kwinaku😞😞😞😞😞😞😞😞😞😞😞

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn Месяц назад +10

    Atumbuka ndi ochenjera AKUFUNA achidyele amva kuti chikungomwaza ndalama

    • @hezelchavinda9817
      @hezelchavinda9817 Месяц назад

      Munaonako pule wachitumbuka ndiye tisankhalenji atsogokeri andale

  • @mphatsokuwali6389
    @mphatsokuwali6389 Месяц назад +1

    boma koma ili till 2030 mzuzu yatukuku very fast during this president 💪💪💪😘🔁🔁 chakwela my vote.

    • @user-ms8tm3yf7d
      @user-ms8tm3yf7d Месяц назад

      Wapangako chani chakwera ku mpoto osamangosapota zopepera nanu inu

  • @RollentFrank
    @RollentFrank Месяц назад +1

    Chakwera is good leader

  • @giftkayome3568
    @giftkayome3568 Месяц назад +3

    A very sad country indeed kaya nchifukwa cha umphwawi, ndikukayika ngati mabvuto azatha machitidwe ake ngati amenewa..

  • @ubs7030
    @ubs7030 Месяц назад +1

    I am kaliton Mbuna and I say: let chakwera keep developing this country till 2030.

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад +3

    Si za value nanga DPP ingayamikile chakwera tamapangani za value zanuzo koma chakwera yemweyo boma 2025

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад

      Ndipo srs wa dpp sangayamikile ayi paja amaziwa kutukwana zilizose😅😅😅

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад +3

    Za ana a dad leroso ayi sitikufuna zomayenda opanda insurance no number plate kumamenya a traffic kupha ma lubino takana ife DDP ayi kuno kumpoto

  • @DucePerez
    @DucePerez Месяц назад +6

    President anali bingu

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td Месяц назад +2

    Akuluakulu sindikuona ogwetsa bwana chakwera kumalawi mwina akadzapuma 2030

  • @MeriaMasinga
    @MeriaMasinga Месяц назад +13

    Gwenembe anapha bale wake

    • @HappyFlipFlops-di5gg
      @HappyFlipFlops-di5gg Месяц назад

      Mlemekezeni president wanu a Malawi

    • @user-wi9pe2hz7e
      @user-wi9pe2hz7e Месяц назад

      ​@@HappyFlipFlops-di5ggmunthu oipa uyu osamaimbila mfit mmanja😮

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 Месяц назад +1

      Anapha Chilima uyu mothandizidwa ndi Usi

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад

      ​@@henryphiri6100nsanje ikuphani or mutatani simungafikile paiwawo or harf kunyoza olemela sikungakupase mwayi

  • @SiphiweTonnyChidumayo
    @SiphiweTonnyChidumayo Месяц назад +2

    Batumbuka banyane mwanigongoweska aaaaah😢😢👐

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад +1

      Wananga vichi akulu ine nkhuwona wapanga makolaso wanthu awa wose wakuyana waka kumupoto kwithu woganizilako yay ni uyu pera chaa

    • @SiphiweTonnyChidumayo
      @SiphiweTonnyChidumayo Месяц назад

      @@user-nv3rf7bl7r wanangiska kulutako apo he's feeling entitled anakapanga ngati zaku zomba

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад +1

    Eni Ake Mzuzu yake iti chitsilu iweti eni ake Mzuzu ndamene amulandira iwe ndi mlomwe ku Mzuzuko

  • @hopesato
    @hopesato Месяц назад +5

    Zaziiii zopanda ninchere omwe

  • @benjaminmvuma-rk6mu
    @benjaminmvuma-rk6mu Месяц назад +2

    The more mukuti wanthu wakumupoto zeru yilije the more we love mcp

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i Месяц назад +8

    Nothing of value has been said

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад +1

    Zonyoza atumbuka zimandinyasa ineso nditumbuka be careful

  • @MuyaoComedies
    @MuyaoComedies Месяц назад +1

    I'm following Salam alaikum

  • @OMEXTWAIBU
    @OMEXTWAIBU Месяц назад

    MCP my vote ❤

  • @lightchimbalanga
    @lightchimbalanga Месяц назад

    Ena sangamvepo kanthu apa chifukwa adazolowera atsogoleri omangotukwana opposition mpaka pa MBC radio panali pa program special otukwana basi ena akamva zimenezo amati ndi mfundo

  • @thomasbotha9790
    @thomasbotha9790 Месяц назад +7

    Vindere nadi vitumbuka kumpoto kumpoto vikululutira vinthu zwaziiiii

    • @MgGondwe
      @MgGondwe Месяц назад

      Vindere nad nga boza or mwamwazga mutima ngambachewa kululutila vili vose uwo wachita mbumbulina

    • @thomasbotha9790
      @thomasbotha9790 Месяц назад

      @@MgGondwe ine or picture ya chakwera kuti yiimunyumba mwane namotcha pamoto

    • @MgGondwe
      @MgGondwe Месяц назад

      @@thomasbotha9790 kkkkk ine or kupulika mazgo yake nkhukhumba yy mnthu uyu

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад

      Mukujisuzga pala mukulimbana wandale ninja walikuvwilako kumupoto kula or muti musinthe pulezdent ndiyo wazakumuganixilani ngati uyu ngwakwamba chaaa wa dpp ndiwo awo wanthu wakwithu walikufwa so pawemi nimphani kuchimbilila kuyowoya uheni wamunthu chaaa kwe mubekengeso uku munthu wafuma ine nindavotepo mukuvotela chakwera ine kukawa kulije kare or pala mungate muwone ulamulilo wa uyu wakumana nimasuzgo vandale vilekani tiyeni tilimbane waka Nanyang izo tilimo kweniso kukhumbila viwemi charo chithu no matter tili kwithu yay

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi 14 дней назад

      So. Yaaah

  • @eliasemmamoyo8225
    @eliasemmamoyo8225 Месяц назад +1

    Ma guys anali ndi ka hope koti atolako kena kake paja anava zoti akukaga ndalama akungo choka ngati pama lilo 😂😂😂😂

  • @BlessingsBanda-ol2pg
    @BlessingsBanda-ol2pg Месяц назад

    Atumbuka azanga mwatani kumulandila chikangawa 😢😢😢😢😢😢😢 nose munali uko ndnu zisilu

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Месяц назад +1

    Ifetonse mbanva yoyoyoyo 😂😂😂😂😂

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад

    DPP amalemba army commander mulomwe wachiwiri wake mulomwe inspector general of police mulomwe deputy wake mulomwe za umve basi

  • @CosmosLuciano
    @CosmosLuciano Месяц назад +8

    Panyapake garu ameneu

    • @PhillspicJere
      @PhillspicJere Месяц назад

      Sizikuthandiza zomwe ukutukwanazo ndale zisakupangise kukhala chisiru, Ife titha kuktukwanila mai ako ndi bambo ako Ndiye usiiletu zakozo

    • @ernestnyirongo3962
      @ernestnyirongo3962 Месяц назад

      Iweso abambo ako pawo

    • @MicaelGraciano
      @MicaelGraciano Месяц назад

      Kkkk

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад

      Kkkkkk iwe ulibe kodi ngati ulibe pepa

    • @ubs7030
      @ubs7030 Месяц назад +1

      Iwe ndiwe was misala osanyoza president wa dziko, udzatembeleledwa ndithu.

  • @user-dn8pt4uz3q
    @user-dn8pt4uz3q Месяц назад +6

    Fundolesi 😂😂😂😂za ziiiiih

  • @MerryWayson
    @MerryWayson Месяц назад +10

    Ife tonse ndindani wakoyo munthu wachabe iweso ukuzimva kut ulowaso m,Boma unya Bola walawa U President

    • @PhillspicJere
      @PhillspicJere Месяц назад +1

      Iwe tangokhala komwe uliko, ovota ndife tilipano ndipo uyu alowaso unya ndiwe

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td Месяц назад

      Chinyezi kubafa wekha sukuona Kuti ndiowinawina akadzangotenga North Central basitu south tidzagawana patala watha

    • @MosesSolomoni
      @MosesSolomoni Месяц назад

      Oipa uyu

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td Месяц назад

      @@MosesSolomoni Palibe wabwino ngakhale iweyo ndiwe oipa chitsanzo waobetsa kale

  • @JohnBanda-k5y
    @JohnBanda-k5y Месяц назад

    Osati nvula yanzuza koma mulungu wakwiya mawu achimulungu koma muntima monyasa ine siwandale koma naneso ndizalolela kufera mbendera imeneyi.

  • @MosesDzonzi-em5px
    @MosesDzonzi-em5px Месяц назад +1

    Mcp si ya pa social media, musamanamizane pa social media pano kuti Mcp sidzawina, mudzakhumudwa Mr chikangawa akulamuliraso mpakana 2030 woooo, balongolorani apa zimene zachitika ku mangochi kuja zikupatseni mphuziro, mudzakhumudwa

  • @IshmaelNesta-rb8dx
    @IshmaelNesta-rb8dx Месяц назад +1

    Ndangoononga bundle yanga ine mayo 😭😭😭

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh Месяц назад +1

    Ntumbuka paja amapita ku school cholinga akaone double decker ku Blantyre. Anganya muli uli

  • @JuliusSikamawawe
    @JuliusSikamawawe Месяц назад +2

    Amalawi simuyamika ntchito ndikunyoza present ndale zanji choncho

    • @BlessingsNyirenda-ru7ss
      @BlessingsNyirenda-ru7ss Месяц назад

      What does it mean bro
      Don't support no sense bro

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад

      ​@@BlessingsNyirenda-ru7ss vazeru kapangeni imwe pera adumbu 😅

  • @user-wi9pe2hz7e
    @user-wi9pe2hz7e Месяц назад +1

    Awa azingopakila bas nzeru zatha

  • @carllewis2744
    @carllewis2744 Месяц назад +1

    I've never loved this dude.. Guess am not the only one 😋😋

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад

    Mudya bwibwi MCP my vote

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Месяц назад +2

    Kalindo akuti adalowa u president kamba ka mademo 😂😂😂😂😂😂 . Boma😂

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад +1

    Chakwera boma

  • @ThomNkhoma-no5rt
    @ThomNkhoma-no5rt Месяц назад +1

    kape nfiti

  • @user-rk3jx3kg8i
    @user-rk3jx3kg8i Месяц назад +1

    Anthu akumalawi ndife womvetsa chison,

  • @tingamasi106
    @tingamasi106 Месяц назад

    Anthu awa akanyamuidwa kuchokera karonga Rumphi Nkhatabay ndikwina they are not from mzuzu township 😊

  • @lydiananyiza9125
    @lydiananyiza9125 Месяц назад +1

    My Malawi a blessed land

  • @AbelBlack-f9q
    @AbelBlack-f9q Месяц назад

    Mcp my vote

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 Месяц назад

    He ddnt even bother to sho up at SKC plane crush site...fishy....

  • @karenn2969
    @karenn2969 Месяц назад

    Something is very out of kilter, both the crowd and the one speaking

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад

    Atumbuka timapanga ndale za school osati alomwe za umbuli basi

  • @user-vk4jf1bg8f
    @user-vk4jf1bg8f Месяц назад +1

    My vote

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov Месяц назад +1

    Wanthu wakwithu mbaya mwakondwachi chitima chikukolana uli echi

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад

      Imwe mwate wachite uli adumbu yaliyose uyo watemwa 😅😅

  • @hanifazuwaja1300
    @hanifazuwaja1300 Месяц назад +1

    Kkkkkkkk atumbuka polani moto mudzingoti kulowela uku kulowela ngati ndinu mbuli zosalowa kukalasi

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 Месяц назад

    Zaziii he has done nothing and Ambuye Kumwamba akumbukule Thukuta la a Chilima kuti iye apezeke ali pamenepa.

  • @JohnBanda-k5y
    @JohnBanda-k5y Месяц назад

    Kunoko tinazolowera kunamizidwa mchifukwa amkati lowani mkalasi muzagwila tchito ndiangati ophunzila lelo Ali patchito koma andale ayi zikomo.

  • @Stevebanda-p1t
    @Stevebanda-p1t Месяц назад

    Palibe ndamvapo chamzeru apa... Bundle yanga mmene ikuduliramu ndangoononga😢😢😢😢

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f Месяц назад

    Inu mukuyimbira zokuti Kwachazo? ndiye kuti mukamamusatila ameneyo simumadzimvera chisoni

  • @TIDEscom
    @TIDEscom Месяц назад +1

    Koma atumbuka

  • @hagayichiluwe
    @hagayichiluwe Месяц назад +1

    Uyu mpaka 2099 wooooooooooooooooooooooo

  • @voicedumathindwa
    @voicedumathindwa Месяц назад

    Anthu ifeyo kumasatilabe chisilu cha president ichi

  • @macmsiska2937
    @macmsiska2937 Месяц назад

    Ku malawi njala yawa balalisha mitu waku lulutila waka chilichose vindeli ivi

  • @Enock-c9l
    @Enock-c9l Месяц назад +1

    Why do malawians clap hands .... for what

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Месяц назад

    Koma amalawi ndife anthu omvetsa chisoni mukuimbira manha munthu okupha

  • @benjaminmvuma-rk6mu
    @benjaminmvuma-rk6mu Месяц назад +1

    We will support our ministers from the northern and mcp vibes

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d Месяц назад

    Mumadziwaso Mulungu iweyo

  • @DevisonHala
    @DevisonHala Месяц назад +1

    Manganya ndi chakwera alibe fundo koma kupha anthu

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад

      Usatenge ufiti wa abambo ako kupasa wina ukuwona ngati sitikuziwa iwe zoti abambo ako atha anthu osamatchuka pa social media pano chosecho makolo anu anthu amawawopa mumizimu 😅😅😅😅😅😅

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h Месяц назад

    Km takambani fundo imeneyi waimba ndindani athu akufa ndi njala osakamba zotsitsa katundu oloimodzi osanena kkkkkkk tiziona kutsogoloko

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад +1

    Alomwe muva bebe DDP bolaso bakuwaku paja last election anakupondani ku kalonga

  • @PatrishaHamish
    @PatrishaHamish Месяц назад

    Pali mfundo zanjinpamenepo abale km ma presedent enawa kaya ndipo kaya

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад

    DPP ya Quarter system kufuna kuthana nafe wene mpoto sitinayiwale

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад

      Awuze amenewa amafuna chakwela asamulandile azinyoza bwino pano agwa nayo amenewa 😅😅😅😅

  • @MussaMasuku
    @MussaMasuku Месяц назад +1

    Uku ndi ku mpotodi zitsuri za anthu

  • @eliasjohnsonkamanga3715
    @eliasjohnsonkamanga3715 Месяц назад

    Your headline is not giving chief.

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад

    Kuchotsa JCE zowona alomwe koma zeru ngati bankha

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo Месяц назад

    Let action speak louder than words.

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg Месяц назад

    Mesa ukulemba anthu ntchito pachibale ndiwe

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h Месяц назад

    Km naine mundibwezele bandle yanga palibepo chazelu cho ndikuimba kkkkk fundo palibepo apa

  • @ISHMAELCHITENJE-ri9rq
    @ISHMAELCHITENJE-ri9rq Месяц назад

    Uyu ndigalu chuma chake chiti,,,kugwetsa kwacha

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад

    All directors and principal secretaries during DDP government are from thyolo and Mulanje mukuwona ngati tayiwala

  • @leganzuze3004
    @leganzuze3004 Месяц назад

    Ufiti ku Malawi no. 1

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад

    Tumbuka sanakhalepo mbuli yenda ma office uwone mbuli ndi alomwe kumalowa tchito ndi certificate ya JCE

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h Месяц назад

    Km zingovelani muzazisunge muntima mukuziwa chomwe muli

  • @BaldwinBanda-gd9zo
    @BaldwinBanda-gd9zo Месяц назад

    Chimunthu chopanda manyazi ngati ichi komaso atumbuka mbuzi zawanthu

  • @DucePerez
    @DucePerez Месяц назад +1

    Boma ilo

  • @KingfrahMachado
    @KingfrahMachado Месяц назад

    Palibe mau anzelu amene ayakhula ngt President galu 🐕🐕🐕kwabasi mau oti tikanatha tonse akunena chan komas Anthu aku Mzuzu kuomba manja pazopanda nzelu😢😢😢

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h Месяц назад +1

    Koma azimayi kululutila chindele ichi nthena asa chilijeso fundo

  • @ArnoldPhiri-u9w
    @ArnoldPhiri-u9w Месяц назад

    Saononge bundle ine

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Месяц назад +1

    Abusa kupusitsa a Malawi poti ndi anthu okhulupilira mulungu.zovetsa chisoni ife ndi anthu opusa kwambiri

  • @samchibenene4458
    @samchibenene4458 Месяц назад

    Perekaniko ndalama nawowarweko

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Месяц назад

    Za ziiiii chisiru cha president

  • @HaliJana
    @HaliJana Месяц назад

    MUMUUZE CHAKWERA PANYO PAMAKE MBOLO YAKE

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад

      Iwe yako wayipanilatu koma anthu mikamatukwana ine ndimaseka over y malawi 😅😅😅

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 Месяц назад

    Atumbuka ndi anthu oti sadziwa zomwe amafuna

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад

    Alomwe tsako too much munatizuza thawi ya DPP pakana kupha athu kuno kumpoto sitinayiwale

  • @user-eh1gn1nj9d
    @user-eh1gn1nj9d Месяц назад

    Ndale ndizovuta mukafuse anthu aku Mangochi

  • @chauncychauncy1683
    @chauncychauncy1683 Месяц назад

    Uyuyu mapwala ake sure

  • @henrymasamba3627
    @henrymasamba3627 Месяц назад

    Ulibe manyazi kumati Kwacha kwacha shame on u

  • @EvanceKapondeni
    @EvanceKapondeni Месяц назад +3

    Kumapeto Kwake Pauline chazelu wayankhula.

  • @nelsonkajawo5176
    @nelsonkajawo5176 Месяц назад

    Ameneyu mpaka 2030 wooo odyeledwa akubwera muwawona

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Месяц назад +1

    Koma amalawi mkuombera manja kkk😂😂😂😂 koma mumagona ninjara kupusa amalawi pomwe chakwera akadya kakatu zanuuyo

    • @user-ol1hf7ru1v
      @user-ol1hf7ru1v Месяц назад

      Malawi ndidziko lovesa chisoni kwambiri aa

  • @berthamigodi6529
    @berthamigodi6529 Месяц назад +2

    Kod athuyinu mukuona mmmm uyusangaruze bas nazituluka zandare

  • @user-ow5zo4cn1m
    @user-ow5zo4cn1m Месяц назад

    Ma green intellectuals awooooooo

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h Месяц назад +1

    Chikangawa chikangawa