Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Pasewerori mwanvapo achulapo ntumbuka ngati okay muzifuse nokha
Kkkk
Kkkk apa nde mwatikumbusatu wayilesi yakwanu ikatha mabatire mpakatu kupita kwa neba kukhala mukhonde kumamvera nao ayini ake alinyumba 😅😅😅😅
Ndamvaso muli chilima umu 😭💔RIP Achilima 😢❤
Continue resting in peace Mr John chilembwe freedom fighter ❤
Thanks for reminding us about that beautiful song and play. Like JETU said, changing the date from 3rd March to 15 January confused people.
Thanks for listening
Koma kare kare mavuto analipo mm Jon zimu ukare mutendere kwa muyaya ❤🎉 🙏
Nice keep it up. I'm hearing from Capetown
🎉Thanks broh Appreciate it
Mwatikumbusadi Koma EEE kumavutatu Ngati tikumuona j ❤❤❤
Freedom fighter RIP
Freedom fighter my homie unfearing man
Sewero ili limakoma koyambaku komalizaku limalilitsa
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
This can be good movie
Tinkadzunguliradi wyless mithawiyo wish 🎉🎉🎉🎉
Ndipo akamathamangisa mene ndimalililo😢
Good mwandikumbutsa kale tikizungulir wayires
The great work of Lucius Chikuni.
They fought for freedom 👏 MTSRIP😥😥
I miss John chilemdwe
Nthawi imeneyo hollywood kulibe
Great work done by muyao all the way from chiladzulu .
Big up
Chiradzulu
Kodi family ya John chilembwe still exists in chiladzulu chifukwa nsinabveko Boma likuti tinakathandiza akubaja
Futso kabwino
Ineso ndufuna ndidziwe ngati abale ake alipo.
Muyao ❤
Usandkumbutse kale ndalira😂😂😂
Congrats to all participating, beautiful ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
😂😂😂😂😂 komatu zidali bwino kale lathu
Mwandikumbusa kale tikumvera wayilesi
Thanks 🎉
Which platform is streaming the new movie of John chilembwe? Any one with an idea?
Tikamamvera timakhala ngat tikuona zikuchitika
Nice mwatikumbutsa kale
❤❤❤❤ thank you so much
You are so welcome
❤❤❤❤❤❤🙏🙏
Freedom fighter
Ndakuthokozan ndikuvera pano ndpo ntchito ikukoma kwambiri uku ndkuvera sewero kuno ku south Africa
Wow that's nice Thanks Biggy ❤❤🎉🎉
History is the best teacher.. thanks Malawians cameras mwatikumbutsa kale lathu watching from Kimberly
Qq
Good mwatikumbusa
May his soul continuasly rest in peace
Those days
Tikuvela apapa kuno ku SA😢
Thanks brother 🎉❤
We miss you chilebwe
Kodi family ya John chilembwe ikadalipo?
Timazungulira Wireless titasambasamba tonse mmm koma kale lathu😂Flora Suya alimotu.mu Sewelori
😂😂😂 Yes alimo kale kumabeba
Zikomo kwambiri watikumbutsa
Muyao
❤❤❤
Umasiya zose paka nsima simakomaso 😂😂😢😢
❤❤❤❤❤❤❤❤
❤❤❤❤❤
❤❤❤❤❤❤

They fought for freedom 👏
MTSRIP😥😥