In our country Malawi need people like this guys let's support this guy if we love our country seriously on me just saying my Allah plz protect this guy
Katundu uyu ali ndi mzeru zamnanu - mnyamata uyu amatsakatula zinthu za deep zot olo a president amabalalika nazo mutu kudabwa kut zimezinso zilipo mukayendetsedwa ka dziko?😂😂😂 Mahata ndi katundu 💪💪
I agree with u but mfundo zabwino koma it's risky as u said kuti anthu ena akupindula kuvutika kwathi Khani ndi pull out there policy like Burkina faso
Denis Bakiki TV DC DK APM Kakiati Suleman Norman Chisale Namiwa Plus ineyo kuli bwino tipange chipani Koma osatila ena Monga jappy mhango ndi uyu vitumbiko akubwera bwino advisor azakhala Ras chikomeni 😂😂😂
Uyutu ndi katundu, Mulungu atipasa mpulumusi, osati kumangosintha ma act Let's put every law straight forward ⏩ not this law says this,the other in the same talking different
Makape amadana ndi chilungamo anthu opusa, lets support this man.
God bless my brother Dennis Mahata,,,he is a genius guy uyuyu azungu nd andale wa sakumuonera kukondwa
Ndikugwirizana nanu kwathunthu Mr Mahata. Tsogolo la Malawi likudalira anthu a maganizo abwino ngati Inu. Chosangalatsa mulipo ambiri ndipo chatsala ndikukwaniritsidwa. ❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉
Ena uthengau autenga ngat olakwika km mmmmm... mahata❤❤❤
Genius full of confidence and wisdom ❤❤❤❤
In our country Malawi need people like this guys let's support this guy if we love our country seriously on me just saying my Allah plz protect this guy
To understand this guy you have to be intelligent, politically sober and patriotic. This guy is a genius
This is my captain ❤
Mkuluyu ndi big deal,o Lord protect this young man
Ndagwilizana nawo aMahatha ndipo ndawavesa bwino
Bwana mahata mulungu akutetezeni
Our Ibrahim treolle...I'll vote for you for better Malawi.
Powerful words 💪! We need people like him in this country 🙏
Building new Malawi 🇲🇼 ✊🏽💪🏽❤️
We are behind you brother keep it up
This guy is very genius
You're the best bro
❤❤❤❤❤❤❤ viva traore mahatma
Ndakwela iyi 💪
Osawopa boss mulindintchito yokonza malawi
I wish this massage was heard by many n impact them the way it is impacting me.
Whenever he speaks, I just go wow! In him, we have got a visionary leader
Am very willing to join this team NRC💪
My man my vote my Malawi, Bola musamukhomelele
Katundu uyu ali ndi mzeru zamnanu - mnyamata uyu amatsakatula zinthu za deep zot olo a president amabalalika nazo mutu kudabwa kut zimezinso zilipo mukayendetsedwa ka dziko?😂😂😂 Mahata ndi katundu 💪💪
❤❤❤
Boys let's sit down en understand the guy ..uyutu uyu mulichachikulu mwa iye
My vote Dennis!!!❤2025 MULUNGU akuteteze kwa adani andalewa.
Big up 🔥🔥🔥🔥🔥 this guy is a genius
❤❤❤❤ much love you mr president mahata
vote yanga mahata
❤I aim sport with them
Dennis mahata my vote ❤❤😂
I need to get in touch with this guy...
This guy deserve a chance
You're a set of this country by any means necessary you need to be protected
Truly, he is a great asset to the Malawi nation. May the good Lord above, protect him always.
And we need to join hands together to support him
Munthu uyu ndiwqnzeru zodabwisa mpaka lero sindimvesa nzeru zake akamalongosola woyandikilqko ndi kamangila basi
Malawian freedom fighter
Bola asamusowetse akanganya awa
We need to support this guy please
I agree 💯 %
Komano ada achitolirowo eee ndimbambande
I agree with u but mfundo zabwino koma it's risky as u said kuti anthu ena akupindula kuvutika kwathi
Khani ndi pull out there policy like Burkina faso
Akamuna ogona kukhomo kosaseka viva NRC viva thanthwe Mahata
This guy plus kamangira can save malawi
My pulezedent. Muli zelu umu akumawagwila manja mangochi anjadi ndi athu okuda😂😂. Paka kushola chiseko chimuthu okuda zawo
He's a genius guy
Denis
Bakiki TV
DC
DK
APM
Kakiati
Suleman
Norman Chisale
Namiwa
Plus ineyo kuli bwino tipange chipani Koma osatila ena Monga jappy mhango ndi uyu vitumbiko akubwera bwino advisor azakhala Ras chikomeni 😂😂😂
I will vote for him Kodi sizitheka kuvotera anthu awili ?😃😃😃 APM Ndi NRC Denis???
You're great mahata
Ulemu wanu a Mahata 🙏
Uyu nde msogoleri woti angatukure malawi, fundo izi ndizimene akuyendera msogoleri waku Burkina Faso
Biggy inuyo amene mmapelekera za Denis Mahata inu mmandipeza zedi Denis mahata uyuyu tsiku Lina adzatiombola I doubt not
Awa ndi machine traore wathuwathu mulungu akusungeni ndi moyo
He is very very right nkhani ya Block of discoveries
Uyutu ndi katundu, Mulungu atipasa mpulumusi, osati kumangosintha ma act
Let's put every law straight forward ⏩ not this law says this,the other in the same talking different
Denis Mahata must be protected at all costs
Ayise I love you
He may be like Traore of Burkina Faso
Katundu uyu❤
Tizimpemphelera uyu ndi bridge yamthesa umphawi
🎉🎉
God sent
Nyali yawala , nthawi yakwana
Support you man❤❤
Zonad uku ndye kuyankhula momveka bwino apolisi asilikali akumalawi ndi omvesa chison makape omvera Chakwera 😮
ichichi ndichilombo guys
Ine uyu ntangomumvera koyamba pompo nnagwa nae mchikondi
Mahata ft muthalika bomba
Ma yes bwana nde azisogoleri athu
Mawo
Chakwera ali ndimantha asiye udithu atenge akamuna awa ndi 1
Mahata for life
Zeru zilipo apa
Machine eeeeeeeh!
Am in
ngati kulanda boma sikutheka panga chipani ndipo udzawina
Osati zochokera ku busa basi kukhala msogoleri wa ziko
Uyu muli mzeru
Eish koma kuli anthu oganiza bho
Uthengawu upite kutali makamaka kwa anthu a m’midzi yathu. Zabwino kwambiri kwa Mr Mahata. Zipani za ndale zimenezi zikugwirizana ndi mavuto athu. Tiyenera kukumana pamodzi ndikusankha anthu omwe ali ndi ndondomeko zabwino kuti akonze dziko lathu.
Following
Malawian sankara
Kodi action itengedwa liti?
Kuteteza ndi kwamwini mulungu timusiyile ngati akukawombela Trump kumalawi ndiye kachqniso
❤
❤❤❤❤
Following