TAKONGOZA NDALAMA 100 BILLION PLUS | PHASE 2 IBWERA NDI MOTO |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 6 сен 2024

Комментарии • 28

  • @user-fz7fo8vr4l
    @user-fz7fo8vr4l Месяц назад +1

    Azimayi opanda nzeru kumangovinila zilizonse 😂😂😂🤗🤗

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu Месяц назад +2

    Lazaro chikangawa fiti lweyo mulungu akukanthene ndi agogowo Monica muzalavura 2025 ndalamazo amanganya nanuso mwafikapo mutamupereka chilima yudasi lwe mutu ngt chiboribori ngt nguli Galu bambo asikono

  • @TroubleKatsala-jp2li
    @TroubleKatsala-jp2li Месяц назад

    Palibe chimene ndatolapo akungozikolakola poyankhula kuyambankhani iyi kulowelanayokwina aaaaa

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft Месяц назад +1

    Kodi ilosatenga ndrama zomwe mukupeleka ngat ngongolezo kukalipirako Ku ma company omwe amagulis feteleza komaso mbewu Kut Ngati thumbs Lili 80k likhale or 40k

  • @EnelesKanyerere
    @EnelesKanyerere Месяц назад +1

    Koma pansonkhanopo analipo ndimmodzi yemwe analandilapo ngongole mu one hundred billion'yo? Kapena mwangongozana nokha nokha kumipandoko?

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft Месяц назад +1

    Nsokhano Ngati nthano Oro molalo Oro ka molaro kake kokakamiza

  • @LukeshadrickShadrick
    @LukeshadrickShadrick Месяц назад +1

    Yomweyo chikangawa iweeeee

  • @hesbaluku7281
    @hesbaluku7281 Месяц назад

    Mpaka.tidikire 4 yrs iwe next yr yomwey ukusweka # chikangawa

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Месяц назад

    Mulungu saywalla somwe munashita nkushikangawaw ashankwela asayelenkese nkupitha nkusiphe musapha sipheyosse akukuyu asinkalle ashimwendo

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Месяц назад

    Ndipo mapwala ake ife achewa atizolowera ndipo akuwona ngati tizamuvotera iyeyu akunama kwambiri

  • @happychavula4469
    @happychavula4469 Месяц назад +1

    Chakwela or ukanati usise fetriza motani kulibe zowinaso ayi pokhapokha fetriza ufike pamutenga wa kw 20,000 bag

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Месяц назад

    Anthuwo ukwayensa ngati nyawu

  • @user-hl1jt6eo3d
    @user-hl1jt6eo3d Месяц назад

    😂😂😂ee ata yemweyo chikangawa

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope Месяц назад +1

    Ine sindibwenza chifukwa ndikutenga ndalama za nsokho wanga nde zikomo kwambiri pondibwenzera zochepazi

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu Месяц назад

    Izi zipindulila anthu ochepa, koma akadapeleka ku makampani kuti katundu atsike.

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Месяц назад

    Mboli yako iwe chakwera ndambuyako amene

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg Месяц назад +1

    Mukanamakondwerera, mphindu lomwe ngongole yo yabweresa.Osati kut mwagawa ndalama.

  • @PatrickMtira
    @PatrickMtira Месяц назад

    Nanuso musamangotolera zili zonse enawa sitifuna kuwamva

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu Месяц назад

    Azimayi zeru mulibe nose munali kumeneko

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Месяц назад +1

    Ine ndikatenga zindibweza chivukwa ndindarama zatu zicomo

  • @BaldwinBanda-gd9zo
    @BaldwinBanda-gd9zo Месяц назад

    Iwe ukuyenera ku khala secretary not president mumutu Umu mwadzadza usi

  • @BaldwinBanda-gd9zo
    @BaldwinBanda-gd9zo Месяц назад

    Iwe ndiwe cha bodza kwambiri

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa Месяц назад

    Machende ako iwe chakwela mbuzi iwe

  • @MustapherLino
    @MustapherLino Месяц назад

    Chakwera panyopako wakupha iwe

  • @AbdulRashidKachala
    @AbdulRashidKachala Месяц назад

    Koma malawi ziko losabgalasa kwabas

  • @EvasArafredi
    @EvasArafredi Месяц назад

    Machende ako chakwera

  • @GiftSoko-w4h
    @GiftSoko-w4h Месяц назад

    Mumalo moti musise katundu mukubwerekesa ndalama ndiwe galu kwabasi