AKUTI OLO KAMBA ATADIKULA DPP SINGALOWE M'BOMA ~ WATERO JESSE KABWELA PA MSONKHANO WA MCP PA 15 SEPT

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 17 сен 2024
  • AKUTI OLO KAMBA ATADIKULA DPP SINGALOWE M'BOMA ~ WATERO JESSE KABWELA PA MSONKHANO WA MCP PA 15 SEPT
    Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
    Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
    Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
    #MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

Комментарии • 224

  • @LastbornEnd-r9c
    @LastbornEnd-r9c День назад +3

    Ku Mangochi kuno kulibe vote ya mcp
    Yiwalani
    Ife ndizingokudyerani ndalama koma vote ndiya APM

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 3 дня назад +11

    Pa mtumbo pako wazobwirabwira iwe

  • @HappinessKapombeza-ut9mo
    @HappinessKapombeza-ut9mo 3 дня назад +8

    Miseu,kaya chani?Ndi ndalama za Misonkho yathu.

  • @EstherZintambira-sq3yy
    @EstherZintambira-sq3yy День назад +3

    Jessy galu amwa mafutao anthuo DPP boma

  • @JusticeKawilira
    @JusticeKawilira 2 дня назад +2

    Malawi ndizomwe adzasankhe sipakamwapo ayi DPP boma

  • @benardalfred786
    @benardalfred786 2 дня назад +2

    Ndanena ndanena mufune musafune koma dpp ili pa pando kare or ma vote asanaponyedwe koma dpp yili boma

  • @JovitastoloBridane
    @JovitastoloBridane 3 дня назад +5

    Achimwendo ndinuopusa komanso ndiwembuli msewutu sithandizo pezani zochita

  • @smartjilamu8026
    @smartjilamu8026 2 дня назад +1

    Chakwera akusiwa mavuto amalawi😢😢 koma ndalama

  • @SaimonSaimonmw
    @SaimonSaimonmw 15 часов назад

    It's treu m c p is going to Winn again,

  • @GraceMasiye
    @GraceMasiye 2 дня назад +1

    Mcp imandinyasa bwanj😢😢

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 2 дня назад +2

    Boma lake liti
    .
    Boma la mbava komanso zigawenga

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa 3 дня назад +3

    May iwe panyopako ndichakwela ndiwe opanda zeru patumbo machakwela ndi iwe womwe

  • @MaggieBanda-ft5tu
    @MaggieBanda-ft5tu 3 дня назад +6

    So sad, dzimayi olimba ntima kuyakhula kwa ndinthe ndithe ,tidzavelaso vidio iyi chaka chamawa🙏🙏

  • @AlexMakawa-j9f
    @AlexMakawa-j9f 3 дня назад +3

    Chikangawa

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 3 дня назад +3

    Mcp kupha , kuba , kunama .
    Mcp out , no more chance
    Only savages can say kwachaaaaa 😂😂😂

  • @Hamilton-f2q
    @Hamilton-f2q 3 дня назад +2

    Opusainu mcp yokupha komaso yodalila usatanic

  • @SAMARTEDWART-b1j
    @SAMARTEDWART-b1j 3 дня назад +9

    Uyu sinakubala uyu
    chitsilu cha chiwanda ichi

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd 3 дня назад +2

    Nonsense the government that fails to make passport and license...

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 дня назад +1

    Uyu asandipalamulise agalu okupha wa shupiti

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 3 дня назад +2

    Amayi awa ndiachitsiru kwambiri akachita thupi kusawa ngati amamwa matokoso kuli kusamva mafuta ngati amadzola mchere.

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 дня назад +1

    Zaziiii mukuwona muwina never

  • @RobertsNyirongo-o7u
    @RobertsNyirongo-o7u 3 дня назад +2

    koma bwanji mawi amenewa kodi mwaredzela zipaseni ulemu mai

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef 2 дня назад +1

    Kabwirayu Mutuwake sugwira,

  • @FrezerJangiya
    @FrezerJangiya 3 дня назад +2

    Vomekezani kuti chakwera walephela,kabwila ma pilisi amukwana

  • @ChifundoKabichi
    @ChifundoKabichi 2 дня назад +1

    Paja amatamika mmalankhulidwe awa

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 18 часов назад

    MCP singawine

  • @YamikanChirwa-s1n
    @YamikanChirwa-s1n 3 дня назад +2

    Mmmm iwe

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 2 дня назад

    Useless government

  • @chikaonekarh
    @chikaonekarh День назад

    Ukamba nonsense Kabwira, just tell them you want money ku MCP end story

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 4 часа назад

    Jeassy Kabwila Ovotaotu ndi Amalawi

  • @TrensChikaluma
    @TrensChikaluma Час назад

    Zimenezo ndizale tizaziwona po kolola musiyeni tiligu nasongole akulile limodzi

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g 2 дня назад

    MCP ingozilimbitsa mtima achimwendo banda muli ndi thumazit ndipo MCP ikupita olosera talosera kale MCP is going for good DPP iri mudzit osati town olo mutamanga nsewu wakumudzi sakukumvani Iwo angoti chakwera sitivotera , makhwala zipatala anenamo mulibet makhwala. Ndipo MCP yationesa Malawi muno 2025 pitani kapumeni for ever .

    • @TracyBanda-i2g
      @TracyBanda-i2g 2 дня назад

      Nyimbo yasenderayo tailekani achakwera sikuwakhala imakhala BINGU IYOOOO OSATI MANYAKAWO

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 12 часов назад

    Akudalile kubela mavote namachende amenewa

  • @HaliJana
    @HaliJana 3 дня назад +1

    Tikufuna tikuveni kwakonda kwanu amalawi anakusisani kuti ndege yazaza ndindani pano kwasala masiku4

  • @MosesSolomoni
    @MosesSolomoni 2 дня назад

    Amasuta chamba kabwila mudzimuona mayanthulidwe akewo

  • @FarookYahaya
    @FarookYahaya 2 дня назад

    Walandira 2000 ameneyo ..DPP my vote

  • @AngelaMphinji
    @AngelaMphinji 11 часов назад

    Ndinu. Opusa. Mayi. Muzinamiza. Amalawi. Ngokwiya. Tsegulani. Maso... Akudikira. Kukutuludani. Boma.. 2025.DPP. Boma... Muziyamika. Chilima.... Simungawine. Nokha. Opanda. Alliance mukapuma. Mpaka. Muyayaaaaa!!! '

  • @user-iz5ui3xm4g
    @user-iz5ui3xm4g 3 дня назад

    Boma ndilomweli abrayan mungochitika ngat mburi bwanji

  • @MiracleDamiano
    @MiracleDamiano 17 часов назад

    Zaziii mayi opusa kwmbri iwe

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 дня назад

    Tiona 2025 JESSY ndindaniso uyuyu kape kwambiri

  • @twaibupatrick-k1n
    @twaibupatrick-k1n 2 дня назад +1

    Inu mwapha chilima

  • @NickNyilendachisengah-p4u
    @NickNyilendachisengah-p4u 2 дня назад

    Mumayakhula mutamwa Makhwala ozunguza ubongo eti kapena mutamwa mowa azimayi ophika mowa

  • @user-pc7hj7hs5v
    @user-pc7hj7hs5v 3 часа назад

    DPP boma

  • @user-pc7hj7hs5v
    @user-pc7hj7hs5v 3 часа назад

    Uyu ndiwankhunyu

  • @SaimonSaimonmw
    @SaimonSaimonmw 15 часов назад

    It's treu mama

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g 2 дня назад

    KOMA AMZIMAI OSASAMBA AMCP NDIOMVESA CHISONI KWAMBILI ,KUMUONA MZIMAYIYO ARI MBUUU KHOPEYO , KHUNGU , NGAT PANSANA PA NG,AZI AWA ALIRA 2025 DPP IKUTENGASO M,BOMA NDIPO KAMBAYO AZADIKULA KUONESA MCP KULUZA TILI PANO IFEE

  • @HaliJana
    @HaliJana 3 дня назад

    KODI INU MSEU WAKE UTI AKUMANGA CHAKWERA CHIMWENDO UYU ANALI KUNJA INU DPP MOMWE YAMANGILA BLANTER LILONGWE INU UYU AKUONA NGATI IFE WANA ETI

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 3 дня назад

    Kodi inalikuti mcp inu minali ku opposition for 26 years kapanda chilima ukadakhala muli ndani inu

  • @HaliJana
    @HaliJana 3 дня назад

    INU IFE AMALAWI SITIKUFUNA NKHAZA ZOPHANA ZOGWESA NDEGE AAA INU CHAKWERA SITIKUMUFUNA

  • @user-bw2cv9sd7x
    @user-bw2cv9sd7x 2 дня назад

    agaluu awanthu a mcp aziona 2025

  • @robertkalima874
    @robertkalima874 День назад

    Mkwiyo paja ndi ufiti. Tisayiware

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 2 дня назад

    Kabwira mbuziyako wamva ndi chikangawa team yakupha nonse agalu n okha

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 3 дня назад

    Akuopa mgwirizano wa dpp ndizipa zina akuziwa zangawine 50+1 chipani chilichoze chikuopa kukapanga ndi gwirizano chifuka ochewa ndale zawo kumapheto ndikupanda akamutenge nakhumba ka nakhumwa akuganiza angawine mcp chitukuko chomwe akunena chakulilongwe only ife kuno kuzimba kulibe mcp komweko kulilongwe ife ikabwela mcp ndikudyelani ndalama koma voti zimungathole kd misewu yomwe ukunenayo ilipalipotse kuti mukanika msewu wabalaka to ntchewu

  • @HaliJana
    @HaliJana 3 дня назад

    AMALAWI AKUKUGENDANI AMALAWI MUKUNENAWO NDI ATI SOPANO

  • @RajahKanjera
    @RajahKanjera 4 часа назад

    Zawugalu zenizeni

  • @Patgregorymanyumba
    @Patgregorymanyumba 10 часов назад

    Chinsiru cha mzimayi ichi

  • @KondwaniGumba
    @KondwaniGumba День назад

    Koma na khani ya misewu adpp imawabaya kwabasi.

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi 3 дня назад +2

    Kulibe njanji kumalawi

    • @HappinessKapombeza-ut9mo
      @HappinessKapombeza-ut9mo 3 дня назад

      Kkkkk...koma yah!Mai uyu ali ndi NZERU dzopusa.Koma mukanadziwa Mai,ayi musandilakwitse.

  • @adammnonyele4263
    @adammnonyele4263 3 дня назад +1

    Misewu yo yenda mnyawu

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 2 дня назад

    Adamuona kamba kuti sadikula, chitsilu

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe 3 дня назад +2

    boma ndilomwali ❤❤❤

  • @GibsonMithi-n4y
    @GibsonMithi-n4y 2 дня назад

    Maziko ndikupha munthu ngakhale chikhulupiriro changa ndi chofowoka koma ndimaziwa Kuti kumwamba kuli mulungu achimwendo banda muziwe

  • @AmirGhafoor-bk2le
    @AmirGhafoor-bk2le 6 часов назад

    Koma amabwereka ameneyu chisiru cha zimayi

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 дня назад

    Komatu mukayakhula zindikilani kuti mawa limafika mulungu si Lazaro

  • @esthergweje4038
    @esthergweje4038 2 дня назад

    Aaaaa Mcp izawine ndithu kuzakhala nkhondotu njala yake tikudya chitedze

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 3 дня назад +1

    Kabwira wamisala chimwemdo wamisala palibe chazeru chimene akulakhulapo pamusokhano kungokamba za ena basi ndani angabotere tambala wa black wakumudima tizaona yakhulani chilichose chabwera mumutu wanu koma amalawi akuona ndi maso awo 2025 ikubwera

  • @KingDavedNkhata
    @KingDavedNkhata Час назад

    Malankhulidwe awawa mwandilakwitsa dala panyopako mayi osasamba komanso galu iwe Chimunthu Banda chitukuko chake chiti chokuba ndikupha ndikunama
    Boma lake liti lingodziwa mfundo zokha pa ground 0 pa 10 mbava zokha
    Chitukuko chake cha m'makomo mwanutu masatansm fake government

  • @JoseKeyaton
    @JoseKeyaton 17 часов назад

    Ndihule ameneyo alive fundo chifukwa amawafuna apeter kudikula uhule bwasi walowa liti MCP huleyu

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 2 дня назад

    Hule ameneyo bwanji kodi akuganiza ngati kuti azawinaso mcp. Osangonena kuti kwinako munaba ndalama iwe ndi hule kwa basi
    Azibeans wukuikila kutiko beans yovundayo iwe wamva

  • @FrankMachiwi
    @FrankMachiwi 2 дня назад

    Tionana chaka chamawa uzayankhileso after zisankho

  • @TiyanjaneMkwate-we8gu
    @TiyanjaneMkwate-we8gu 4 часа назад

    Tiwavotera kuti tizadye chitedze, fertilizer 200,000.

  • @RafickAmiduh-r8f
    @RafickAmiduh-r8f 2 дня назад

    Amai awa ndiwopusa zedi.mmene akuvutikila amalawi osamva chisoni

  • @makomberodgers3791
    @makomberodgers3791 2 дня назад

    Mai amenewa alezera

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 3 дня назад

    Hule kwabasi APM

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 2 дня назад

    Kamba yo asanadikule udzayamba ndiwe Jessy Kabwira kudikula mpamene udzadziwe Kuti unatha mawu.
    God created heaven and Earth and everything living in it. Dzikoli si la MCP . Udzingodya ndalama za magazi akupasazo.
    History is the best teacher.
    Mbiri yanu a MCP ngakhale mwana akuyidziwa.
    You are Evil 😈👹👹😈🐊🐊

  • @TiyanjaneMkwate-we8gu
    @TiyanjaneMkwate-we8gu 4 часа назад

    Moti maso mulibe kuti muone zoti takutsikani.

  • @JovitastoloBridane
    @JovitastoloBridane 3 дня назад +1

    Ajese kabwila anthu akudya nyika inumubweretsa mafuta palinzulu auze bulaani

  • @user-cl5kx5cy2m
    @user-cl5kx5cy2m 3 дня назад +1

    Lehu iwe

  • @user-ov6jl8br7p
    @user-ov6jl8br7p 2 дня назад

    Akulu akulu ngati mwamuonetsetsa azimayi a mcp akumayamba ndi kumwa mowa kokeni ndi chamba Jesse kabwira ndi ena akumapanga ngati osungulira mutu

  • @KassimWilson-g6m
    @KassimWilson-g6m 4 часа назад

    Kulakhula zakachaso azimayi akachaso amwaso pamenepo

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 13 часов назад

    Panyinipako mai iwe ......😂 uzavota ndiiweyo we ll vote 🗳 u ll wait and see

  • @ArronBenson-g6d
    @ArronBenson-g6d День назад

    Za ziii

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 12 часов назад

    Mayi inu mutu wanu sukugwira ma Rv akudzungudzani

  • @JulietKapata
    @JulietKapata 2 дня назад

    Mulungu akupase moyo wautali galu iwe

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k Час назад

    Iweo kabwilabwila kaya ndi hule wako umenewo iwe ndichisilu kwambiri hule iwe kwachela amanu agalu inu muonanso 2025 DPP ikubweranso APM our vote ana a satanic inu iwe ndi chakwera wakoyo ndinu dzisilu

  • @juruEzra
    @juruEzra 2 дня назад

    𝙸𝚌𝚑𝚒 𝚌𝚑𝚊𝚗𝚍𝚒𝚔𝚞𝚖𝚞𝚍𝚠𝚒𝚝𝚜𝚊 𝚔𝚠𝚊𝚖𝚋𝚒𝚕𝚒, 𝚘𝚕𝚊𝚗𝚔𝚑𝚞𝚕𝚒𝚝𝚜𝚊 𝚝𝚒𝚘𝚗𝚊 𝚗𝚎𝚡𝚝 𝚢𝚎𝚊𝚛, 𝚠𝚎 𝚊𝚛𝚎 𝚑𝚎𝚛𝚎 𝚝𝚘 𝚔𝚞𝚘𝚗𝚎𝚕𝚊

  • @edsonwolemba3011
    @edsonwolemba3011 2 дня назад

    Anyani aku dpp kubwebweta anga ali mtulo

  • @ThokoGomeza
    @ThokoGomeza 3 часа назад

    Izi utha kulakwa Mai ochomwitsa okulakwisa

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 дня назад

    Kod chakwera wapanga chan akukhalira kuba ndalama kupha ndpo wagulisa Malawi palibe wapanga ndpo anthu akufa ndi njara Mai iwe galu iwe

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 12 часов назад

    Iwe mayi opusa kwambili pa nyapanu inu mayi

  • @HappyBirchForest-zy8nq
    @HappyBirchForest-zy8nq 2 дня назад

    Komaso ukunena kuti mwapanga zitukuko misewu zosezo ndi misonkho ya amalawi zitukuko siza president ayi iwe ndimisonkho ya amalawi palibepo chitukuko cha president mu malawi

  • @MuhammadInack
    @MuhammadInack 3 дня назад +2

    Hule wachabe chabe iwe galu et

  • @user-wb3us4pg4b
    @user-wb3us4pg4b 2 дня назад

    Azizinyenga choncho ...nde ngt akukufunani bwanji mwabwerako ndi miyala

  • @MikeFalasiya
    @MikeFalasiya 32 минуты назад

    Oky

  • @ElizabethKumwenda-f5h
    @ElizabethKumwenda-f5h 2 дня назад

    Mukuyakhula ngati kuti mulibe ubongo bwanji tikumana 2025 usathe mau kabwira

  • @TiyanjaneMkwate-we8gu
    @TiyanjaneMkwate-we8gu 4 часа назад

    Yokagwa nayo kumanda ndi ya mcp mboni ndi anthu 9 aja.aliyense anaona yekha.

  • @user-iz5ui3xm4g
    @user-iz5ui3xm4g 3 дня назад

    Chimwendo ndi ( tilembe mchichewa) kompyuta mwava kodi

  • @CharityGondwe-bw9gs
    @CharityGondwe-bw9gs 2 дня назад

    Mayi uyu amagwa chifufu sabereka ndichisiru cha zimayi. Panyapako wava

  • @FELIXMAJAWA
    @FELIXMAJAWA 2 дня назад

    ndipo pa ntumbo Pako chabwera

  • @adammnonyele4263
    @adammnonyele4263 3 дня назад

    Chimwendo kod zipatala zomwe akumanga achakwera zopanda mankhwala akhala ma gest house zupusa