Komatu tiyeni tiyakhule chilungamo inde imfa inalakwa chifukwa anachita kuphedwa km chilima anali wamwano and ozikonda mumayakhulidwe ake mphuma linamuphesa uyu koma poti ndi imfa that's why tikumilira kwambiri poti anafa imfa yangozi koma kt anadwala sibwezi tikumulira chocho
On this fateful day, an individual seemingly embraced their imminent demise by inscribing their name upon the document of mortality. Reflecting upon the poignant passing of the esteemed Sadic Mia, one might discern the wisdom in deriving lessons from such an event. 😢😢😢😢
Biyeni mzimu wanu uziusa mu mtendere, something keeps telling me that your death will not be in vain.... Pangatalike Malawians will be saved and tsogolo lowala lifika
Koma Chakwela chimene wamupangira muzako 😭😭😭 ndipo udzafa naweso imfa yowawa
Chilichose pano chinadula, km chilima anali munthu guys, km lelo alikumanda kamba kozichepetsa, cakwela iweyo mulungu 🤲 ndikungopempha akuyendele pawekha ndiwesatana kwambili
Onse anatenga mbali apa minyama izakusatani mpaka kale😅😅
Koma Mulungu ,hmmmmm.awoneni amene anaphylaxis this gentle soul, I will forever be behind your idealogies
Lero zilipati guy's mgwilizano wanu unali wakupha chilima
Mphuno salota zobwera m'mawa, mukanadziwa biyeni, simunakavomereza mgwilizano umenewu!! 😢
Mnmn Kona BIYENI anatilakwira pogwilizana ndi anthu awa mmmmm zosakhalabwino kumangotiliza mayiineee 😢😢😢
Anthu awa popanga ngwilizano wawo kutiika m'mavuto mm ukanaziwa kuti muli Infa khalimo sukadachita kumuthawa Peter onani relo anthu andale siyani dyela zochepa zomwe mapeza km mmm kutiika pa mavuyo ife
Phuma. Chilima. Linakuphesa... Ndi. Apm.. simunayambane... Unachita. Kukaziponya. Wekha. Ku. Ng'ona.... Ayi. Pepa
Akuti looksharp zogona zenizeni
Kuombela mfiti manja kunali komweku Malawi wanga let's hope anthu ovatafe tikavote mwadzeru
Ngoni ozikumbila zenje yekha biyeni sanje kwachitila apita tona lero akadali angwiro kupusa 😢😢
Eish
Zoona dyera limapha eeeisiii
@@KingDavedNkhata kumakhala bwino ndi anthu mawa siliziwika
Munatipweteketsa Inu,taonani lero munaphana nokhanokha ,dyera ndi kudya mfulumidza zinakuphetsani
Kuyankhula kosaganiza
😭😭😭😭😭😭😭 Tawonadi kusintha njala ndi iyi ndikugona nayoyi chakwela ndi iwe galu basi watizuza mokwana 😭😭😭😭😭😭
Anakumba zenje kt agweremo peter koma agweramo okha ..peter a nali phe kuma stand kuonelera nyasi zanu, Mulungu amenyera nkhondo pano muli ndi mau 😮😮😮😮ubwino wake sakakuyankhan anali phe ngati nkhosa yopita kokaphedwa ... Zanu izo mwadyana nokha
Komatu Chakwera ngat uli ndi umunthu chikumbumtima chikupeze,
Onse anazichepetsa nthawi imeneyo anamwalidi.... Eeeiisshh
Munthu akamafika pofela akuti mumayamba ndi khutu kugonda kutandauza kuti chilima adagwilizana ndimikango yanjala et
Heeee. Akweni.kaliati!!! Mukawonerenso. Ka. Clip. Ka. Mulira. Sure... Dziko.ndi lozungulira. ili... Ayi. Zikomo!!!!
Ko dziko limasintha kulankhula ngati ngelo koma lero ndiawa akulimba ntima ngati nfitiwa kumangosankha ntundu wakwawo munthu oipa 😢 kwambiri
Iwe Shikangawa ndi galu kwabasi😮😮😮😮
Vuto lomakhulupilira chilichonse a Malawi moti zimenezi mwakhulupirila.muchedwa nazo iziiiiiii
Chilima ndi munthu ekhayo anatisakila mavuto dziko muno
Ntchito zako zinakusata
Dyera limapha chilima dzenje anali kumba yekha lero watisiya amalawife pa moto mmmmmm
Ukakhala pabwino poyipa pamayitana ..... Ziganizo zomwe anapanga atsogoleri awa ndizongofuna udindo osati kusamala za ife ...... Nanga look us now
Gwirizano ofuna kuthana ndi Peter mmmmmm lero ndi izi Mulungu simunthu ayi
😢😢😭😭😭😭🙌 nothing to say only God knows R I P chilima
Munatipwetekasa athu Inu eshi 😮😮😮
Na ntindi yenseyi ndithu kukasainira mabvuto mmmmmm
Koma dziko ili🙌🙌🙌🙌🙌😢😢
Rest in peace my boss Dr souls chilima ❤love you 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢❤
Dziko la pansi😢😢mukumutseweretsa mulungu
Tikanaziwa sibwedzi zonsezi zili choncho lero lino, this should be a reason learned to malawians.
Chihana anati chibakera mwamba koma abale 😢
Forever in our hearts ❤
Zomwe anayakhula chinga zimu wake uwuse muntendere ..anthu akumpha mwamuwonano bushir uja pano
Achakwala mukuva bwanji apa Shem with you
Chakwera ndi dulu, Joyce munthu wachabe tonse tisamila mkono soon and very soon we are going to him
Dont forget that this world is not our home Gotan,chimwend and chakwera what do you feel God is watching !!! 5judges
Boma ndilomweli osasintha amalawi mpaka 2060 mcp woyeee
Ase izi mungoyakhula mwachibwanabwana kusakonda dziko lanu ife monga a mcp sitikuwina ndipo sizitheka
Imfa ya Biyeni inawawa komabe kusaona kwake ndi ndi diso la. Uzimu lero zamuubwerera yekha.
Zinthuzi tiziyang'ane mbali zonse nkuluyu amayankhula monyang'wa zedi
Dyera limapha onse oipa chilima, chakwera ndi joyce ana asatana🧞
Mayi Joice Banda akuti ufiti samaudziwa Ali mfiti yaikulu ya chikadzi ndipo odala yemwe adasiiratu mwachangu atadziwa Kuti adalakwitsa Mulungu awakhululukire Koma onse amene akuonongabe Mulungu Moto ukuotcheni ndithu agalu kwabasi
Komatu tiyeni tiyakhule chilungamo inde imfa inalakwa chifukwa anachita kuphedwa km chilima anali wamwano and ozikonda mumayakhulidwe ake mphuma linamuphesa uyu koma poti ndi imfa that's why tikumilira kwambiri poti anafa imfa yangozi koma kt anadwala sibwezi tikumulira chocho
Mfiti zovala masuit ,ndinkhangomva kuti kunja kuno kuli ufiti apa ndiye ndikuona mfiti zeni zeni.
Palibe umayakhula pamavuto akukumana nawo Malawi
Biyeni shuwa, kufela mbendela yaMalawi chifukwa chaChakwera
Koma chakwera muzako unamurakwira kowophya uzisamara mabanja awose unawaphawo munthu wopanda chisoni kape iwe
Ine ndilemba chiyao chining'a kusosa ndamo kusima nisyausyo
Iweyo September 2025 watipheraso SADIC MIA ALI KUTI NANGA
Watiphera chilima ndiwe chakwera galuwe lero chilima alikuti
Munawononga Malawi anthu inu,,tonse alayasi ndiyomwe yabweleaa mavuto ku malawi,,chipanda ngwilizano wanuwu sakanawi a mcp,,a dad ananenatu kuti AMalawi muzalila muzawona nyenkwe 😢😢si izi apa😂
Koma chilungamo nchakuti chakwera ndi munthu oipa mtima kwambiri komanso alibe chifundo.ukumva bwanji ukaonela zotele pomwe chilima kulibe ? Moto upita kwatsala Chile
Abiyeni anafera malawi kulimba mtima, continue rest in peace abiyeni.
Koma anbambo awa zomwe akuyankhula ngati munthu Ali mukango osaganizira mwana wa nzawo ufiti umenewu a Malawi votani moganiza bwino .
Ma advisor onse a chilima must be arrested in logical sense this agreement was impossible basing on African politics
Sidik mia kulibe, achilima kulibenso, koma chakwera uli ndi mano ankhuli
Chele chele adafa ndi M'chimba mudawa pusitsa a Malawi.
Ichi chakoma ichi chakoma pusi adangwa chagada.
Nsabwe yoyenda yenda idakoma ndichala,
Lero Zomwe mudawalonjeza a Malawi mukupanga.????????????
Konseku kunali kufuna kumuonesa nyenkhwe peter munthalika iiiiiiiii mphuno salota ndithu lero nyenkhwe zakufikisani kumanda amalawi nkuwasiya pamabvuto iiiiiiiimmmm
Chowawa ukamuona chilima zoona mlungu wanga koma achakwela mmavabwaji mkakumbuka
Kkk Nanga lero chimanga tikugula zingati?
On this fateful day, an individual seemingly embraced their imminent demise by inscribing their name upon the document of mortality. Reflecting upon the poignant passing of the esteemed Sadic Mia, one might discern the wisdom in deriving lessons from such an event.
😢😢😢😢
Chimanga ankalira 20 000 sau pano mulira mokweza 50 000😂😂😂😂
Kkkkk Dc boni kalindoooo
Kuzisainila imfa + kuwampha amalawi ndi njala qnthu inuyo mmmmm
Chakwera ndimunthu oipa kwambir kupha nzake chifukwa cha udindo
Game yonse inafoilaà pamenepaa.
Vice kusainilanso kuti akhalenso vice mmalo mwa u President.
Skc Rest in peace.
Kuzichepesa iwe analibe omugulisa munthu uja 😢
Muziyankhula mokwezako mawu.
Koma ngati mzimu sumafadi plz plz akhaulise anthu amene anakupanga chipongwe
Monica chakwela kumaso kukwinyika ngati chisetero. ,,a chakwela zoona kumupha mnzanu chifukwa cha u president mufika nazo kuti? Msambi.
Nthawi mkachitsiru
Mmmm mavuto
Koma iwe ndy unazilodza wenkha ndithu kukupha kuja ndiwenkha unaliika dziko pamoto taona tsopano athu mene akumvutikira tsopano wazilanga wenkha ndthu mulungu kukuseka ndithu chimanga athu akangula ma twety sousandrd ndy lero athu akufa kudya zinkhawo shame on you chilima.
Dziko siliramulidwa ndi mfiti kodi? 😂😂adabaya mwana koma mmmmm chosadziwa
Adatenga mbari kumupha chilima zimutsata ndinthu cz mulungu ndiwamoyo sanafe ndipo zonse amaona ndithu ndipo amamva kulira kwa anthu
Onse analankhula ndasatana😅😅😅
Chilima was born to save malawians
Dyera silabwino ndakhulupilira
Ndimene sinalli ok skc munatenga mballi yanji
Unazipha wekha mphuma
Koma kunali zinthu ,,but why achakwela ,,ndi anthu ena mumapanga zakumpha chilima why ,,,,,,,,,,,ndiyetu. History siwola muziona 😂
Anthu andale ndi anthu oipa kwambiri
Mr manganya alikuti patsiku ili .. Sakuveka pamaulemupa
Okumbatu dzeje amagweramo yekhaaaaaaaaa
Kkkkkkk
Zitsiru zokhazokha zinangokumanapo apa
Zovuta ndithu😭
Mphuno salòta ndiwòlotse ndikakutafune mmmmmmm
Kkkkk nthawi imeneyo mukuti chimanga chinali 20,000 koma chinali chochuluka aliyense amadya ndi kutaya nsima
Biyeni mzimu wanu uziusa mu mtendere, something keeps telling me that your death will not be in vain.... Pangatalike Malawians will be saved and tsogolo lowala lifika
Chilima adayezekedwa ndiadzawo chakwera manyaka enieni basi 😂😂😂
With a handshake mukumpereka mwana wa munthu kodi
Eish komaaaa
Mphuno salota lero udindo wakoma kuiwala pangano mcp yakamuphera chilima ku chikangawa ,bwana chilima munkaona ngati ng'ona za mcp adazigulula mano mukadalota bwana izi sizikadachitika😢.
Mayi kaliat apangen tag 😂😂
Mulungu ndi wamphamvu,
Koma chilango chilipodi mmmmm
Kkk akweni sopano
Pemphero la anthu osakhulupilira,
Alliance yabwino pano tikufa ndi njala mmalo mokudya katatu.
Unatisiya mmavuto galu iwe
Ndipo ndi galudi dyera linamuphesa
Kkkk the DC sopano
😢😢😢 Jesus 😭