KWAYAKA! DZULO NKHANI INALI YA ANTHU AWA PA HOT CURRENT ~ 15 SEPT WITH BRIAN BANDA, WONDER AND JONA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 сен 2024

Комментарии • 97

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 3 дня назад +16

    Pa nkhani ya Dr. Kabambe, yes amapanga zimene amanena, muone kuti Economy yinali bwino , kwacha siyinagwepo pa 6yrs.

  • @AlexMphalasa
    @AlexMphalasa 2 дня назад +8

    Guys Times TV no 1 indeed keep it up Brain Banda, Wonder Msiska & Pankuku very Childish

    • @TsArKhaii
      @TsArKhaii 2 дня назад +2

      These guys are living machines for real😂🎉

  • @DannielOnions-fy3dc
    @DannielOnions-fy3dc 2 дня назад +4

    Nice Nice one thanks brother's keep it up please we need people like u in malawi 🇲🇼 who can make malawi good 👍

  • @mikesangano6624
    @mikesangano6624 2 дня назад

    Big up TTV big guys, mumatiimilira kotheratu. You stand for the real truth for Malawians, not even favouring any political party. Good to go,, Bravo!!!

  • @PeterMwale-e5w
    @PeterMwale-e5w 2 дня назад +2

    hot current yabwino mwatiunikila za zelu gyz kep it up

  • @JamesMangani-s1y
    @JamesMangani-s1y 40 минут назад

    Keep the fire burning Mr Brian Banda

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 3 дня назад +7

    Apapa wonder,,mukanandilola ndilankhule voice note pankhani la nyazi limozi

  • @VicentMalopa
    @VicentMalopa 2 дня назад

    New Generation Alpha Rules Our Country

  • @IOSARBX
    @IOSARBX 3 дня назад +3

    BS Malawi, My guy, your content is on point. Collab in the future?

  • @VicentMalopa
    @VicentMalopa 2 дня назад

    Bravo To You All❤❤

  • @Edwinsanga-zh4yv
    @Edwinsanga-zh4yv 2 дня назад +2

    Kunena chilungamo anyamata a MCP adalakwisa chifukwa president amakhara ngati kholo la ana ndiye bwanji amakachosa ndembera za DPP asiye kupanga zinthu ngati zimenezo nthawi zambiri zizabwelesa chisokonezo muziko

  • @MatridaChikaphonya
    @MatridaChikaphonya 12 часов назад

    Love you guys

  • @EliasPaul-z6q
    @EliasPaul-z6q 2 дня назад +2

    Kabambe is another lion whom we are expecting to rule malawi

  • @Nthambi-zg4nu
    @Nthambi-zg4nu 11 часов назад

    Amen 🙏

  • @ArronBenson-g6d
    @ArronBenson-g6d День назад +2

    Waukape chikangawa

  • @TonyThompson-u3o
    @TonyThompson-u3o 2 дня назад

    Gonzalez Kimberly Martin Kimberly Thomas Donna

  • @user-wl4nd7ic1s
    @user-wl4nd7ic1s 2 дня назад

    I lovee uu guy's 🔥🔥🔥

  • @EnockMsusa
    @EnockMsusa 11 часов назад

    Amapanga thus why Enomony was stable

  • @chisomomatola5463
    @chisomomatola5463 День назад

    What a !!🎉

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 2 дня назад

    Fire guys...!..

  • @RodgerChaula-r5z
    @RodgerChaula-r5z 2 дня назад

    You are pushing guys 💪💪💪💪

  • @rodwelldaudi7386
    @rodwelldaudi7386 3 дня назад

    For sure

  • @MusaLion-os1lx
    @MusaLion-os1lx 3 дня назад +3

    Ndevu zamwayi umayankhula bwino kwambiri ndipo mwayankhula bwino

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 3 дня назад +2

    Wawatu wonder,,great work

  • @VincentAndrew-p8l
    @VincentAndrew-p8l 18 часов назад

    Siza Ndale zimenezo,Uchitsilu umenewo

  • @LumbaniKaunga2
    @LumbaniKaunga2 2 дня назад

    Looking forward kuzamva za Likoma

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 3 дня назад +3

    Kabambe number one ❤

  • @EmmanuelSambani
    @EmmanuelSambani 3 дня назад +1

    Anthu inu mukumanga Malawi titayendera zimenezo Malawi apita patsongolo

  • @WesleyKalimwayi
    @WesleyKalimwayi 2 дня назад +1

    Grezeda asowa chochita manyazi alibe

  • @mustafasimika1275
    @mustafasimika1275 День назад

    Hot current ipatseni dzina la Chichewa ndi program ya mchichewa

  • @ChrispineSteven
    @ChrispineSteven 2 дня назад

    Mr Pankuku muzitolele
    You better make short Comments than kumangozungulira mophatikiza nkhani

  • @paulvimbamvula9508
    @paulvimbamvula9508 3 дня назад +1

    Komano kugenda koohako convoy ya president kunalakwika heavy ...than kuzula mbendela

  • @FrankJumah-l7f
    @FrankJumah-l7f 3 часа назад

    Pankuku walowa MCP bwanji akunyengelela😅

  • @louisbonongwe8537
    @louisbonongwe8537 3 дня назад +1

    Kkkkkk amen pastor
    2 timoteyo 4 v 14-15

  • @TonneyLucius
    @TonneyLucius 3 дня назад +1

    Milandu iyi tiziweluza tokha coz chilungamu sichiwoneka tikachisata nanusa atolankhani be serious on ur job coz kwachitika ma voilonce zinathela pati

  • @StellaMichael-s4d
    @StellaMichael-s4d 2 дня назад

    Tizigendabe chikangawa

  • @PrinceJMpaso
    @PrinceJMpaso 2 дня назад

    Nsanje

  • @WorshipMangandale
    @WorshipMangandale Час назад

    Mvuto la anthu anda amapanga za mamvuto. Aoo

  • @LucyMagombo
    @LucyMagombo 3 дня назад +1

    Wonder amafuna anthu amutame kuti ndi abwana

  • @RuthMkangala
    @RuthMkangala 3 дня назад +2

    Kabambe Ali kuthekera koti atha kupanga zosithika

  • @SymonChiyamwaka-zt6mi
    @SymonChiyamwaka-zt6mi 20 часов назад

    Komano pena pake anthu atundu achilimwe akufunika school post ina iliyose ya president kutukwana maphuzo eish

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 дня назад

    Ife kuno Ku nsanje sitipembeza mafano and tell chakwela he must not come again here za manyi sitipanga Ife mumuwuze asazabwelenso

  • @HajiraMustapher
    @HajiraMustapher 2 дня назад

    Times TV palibenso

  • @RachelMbvundula
    @RachelMbvundula 3 дня назад

    Very interesting keep it up

  • @georgephiri4181
    @georgephiri4181 2 дня назад

    Amuchita bwino ameneyo ndithu

  • @andreabanda7838
    @andreabanda7838 3 дня назад

    Mmmm guys. Don’t look good bodza bodza apa. We know what you are up to.

  • @DicksonLashars
    @DicksonLashars 2 дня назад

    Zowona ndemvu zamwayi awo ndi amcp

  • @MsaiwaleMatanje-hy7hq
    @MsaiwaleMatanje-hy7hq 5 часов назад

    Kkkkkk vn ndzambuli

  • @ChifundoChicco
    @ChifundoChicco 3 дня назад +1

    Anyamata inu mwayamba mwano kachezeren uko you must be serious plz

  • @ConlardNkhoma
    @ConlardNkhoma 2 дня назад

    Tikagwetsa pampa akabwela ku chigao chapakati

  • @AaronSumana
    @AaronSumana 2 дня назад

    💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥

  • @DykeMasho-u8g
    @DykeMasho-u8g 2 дня назад

    A ma VN ndosatha kulemba 😅😅😅😅 achna kalindo mbuli zaathu😊

  • @LinlyKokani
    @LinlyKokani 2 дня назад

    Andale akumalawi dyera akufuna kuba nawo ndalama zapweka ku mcp

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 дня назад

    kkkkkk kuyakha ndimiyala yesi

  • @PeterAkidu-h9r
    @PeterAkidu-h9r 2 дня назад

    Auzen

  • @IbrahimkDyman
    @IbrahimkDyman 2 дня назад

    Anachita bwino kumugenda

  • @MartinLikachuwajr
    @MartinLikachuwajr День назад

    Koma maguys inuyo mumatha

  • @BistonMacheso
    @BistonMacheso 3 дня назад

    Kulibe amene angakukonde onse olo mpingo kulibe amene amakukonda inuyotso anthu sangakukondeni onse koma osafoka kuli nyimbo nambar 18 yachisisimutso

  • @GanizaniCmbewe
    @GanizaniCmbewe День назад

    Kma awa amat uku apita uku apita musamalenawo

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 3 дня назад

    Apankuku adya banzi

  • @EdwardChapola
    @EdwardChapola 2 дня назад

    Yankhulani mosanyengelela

  • @muhammadjuma3317
    @muhammadjuma3317 3 дня назад

    Zakunyasanitu achina Brian Banda kulowa kwa achina mtaba ku mcp

    • @TsArKhaii
      @TsArKhaii 2 дня назад

      Sizinawanyase pitani uko inu

  • @BistonMacheso
    @BistonMacheso 3 дня назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂 Timoteo koma ndakomoka alipodi alisathera

  • @TanazioUziyele-v6k
    @TanazioUziyele-v6k 2 дня назад

    Tiye nazoni

  • @user-gs9vr1lc9d
    @user-gs9vr1lc9d 2 дня назад

    Wonder kkkkk wayankhulatu bwino apa

  • @VictorBarratt
    @VictorBarratt 3 дня назад

    I totally agree with the gentleman if said that the office of the president must be respected regardless of the person in office, but I feel he fell short of completing the truth.
    The truth is the person in that office must also respect the office of the president and not take it as his bedroom or his personal farm, charity begins at home, the president must be the first one to respect the office of president as the father of the nation, then the nation follows suit, no ody is above the law must start from the president himself, in that office you become a president if the whole nation and not for your political party. Malawians we need a lot of change, especially our women who spoil our politicians by their tendency of over praising the president over nothing, Bona!! What does this mean?
    I forgot one would never allow my wife to go and dance for a president when she doesn't dance or sing for me a man who feeds her and takes care of her.

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo 3 дня назад

    Andale atengerapo mwai wa umbuli wa achinyamata kuti aziwagwiritsa ntchito

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 3 дня назад

    Imene ija ndinjila yabwino yoti atsogoleri aziwe kuti athu akwiya,,asilikali onse aja agendedwa bwanji

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 дня назад

    😂😂😂😂 koma dada wang'aluridwa za ndiiiii

  • @OwenJACKSON-sm4yl
    @OwenJACKSON-sm4yl 3 дня назад +1

    Kabambe Atha kusitha zinthu.

  • @EdwardChapola
    @EdwardChapola 2 дня назад

    Kkkk koma ndiye ziko lelo

  • @muhammadjuma3317
    @muhammadjuma3317 3 дня назад +1

    Iweyonso Barian Banda udzikhala ndi manyazi

  • @OwenJACKSON-sm4yl
    @OwenJACKSON-sm4yl 3 дня назад

    Zoonadi

  • @GerilsonLort
    @GerilsonLort 2 дня назад

    Voice note ndiya anthu osadziwa kulemba like born kalindo

  • @GiftNyamulani
    @GiftNyamulani 3 дня назад

    Mmmmmhu

  • @blessingsmandiwa4840
    @blessingsmandiwa4840 2 дня назад

    Nyazi limodzi kkkkk

  • @RodgersMtonga
    @RodgersMtonga 3 дня назад

    😂😂😂😂burfools

  • @BlessingsNambaya
    @BlessingsNambaya 3 дня назад

    😂😂😂😂

  • @IsaacRichard-o3y
    @IsaacRichard-o3y 3 дня назад

    Enao alibe umunthu mumanena zona paja chilungamo ndimwano

    • @user-lp8wj3vq4x
      @user-lp8wj3vq4x 2 дня назад

      Ndaonera antaba ndi jeff ubongo wao asungiza ku dpp abwera ndi mutu okha ku mcp

  • @EdwardChapola
    @EdwardChapola 2 дня назад

    Tiyenazoni

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 3 дня назад

    Mcp ndi chipani cha mtopola basi cnanga ndi cha magazi chokupha ndie mkawona chimapanga khaza kwambir kwa anthu 😂😂😂

  • @MartinLikachuwajr
    @MartinLikachuwajr День назад

    Koma maguys inuyo mumatha