EXCLUSIVE INTERVIEW WITH PATRICIA KALIATI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 ноя 2024

Комментарии • 32

  • @GiftJossam-if2gt
    @GiftJossam-if2gt Месяц назад +5

    Muzipanga upload za latest!!! Ngati ayi basi siyani.......times is overtaking u guyz

  • @Dan44-x5b
    @Dan44-x5b Месяц назад +4

    Yes focus on development like Chilima not of nepotism. These foolish parties let them continue to eat their foolish nepotism politics in their own ignorance

  • @KhooMadex
    @KhooMadex Месяц назад

    Ngati mwatopa ku zodiak ko tsekani 🎉muzikalima gondolosi

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 Месяц назад +1

    Zodiac mwayamba kupenga apa 😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @richardarmittage1693
    @richardarmittage1693 Месяц назад

    Doesn't matter kuti ndiyakale kale koma zimene zikunenedwa m'menemu is real
    And ngakhale itamapabwela day by day zitha kukhala bwino . Pamenepa pakukambidwa tsogolo leni leni la dziko La Malawi

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h Месяц назад

    Zodiak munali kale pano nd mbuzi zeni zeni,,,ndale zakuonongani

  • @justicenyirenda2049
    @justicenyirenda2049 Месяц назад +11

    Interview ya kale kale you are uploading now 😂 No wonder Times is doing well than you.

  • @richardarmittage1693
    @richardarmittage1693 Месяц назад

    Sizokakamiza kuti munthu amvetsele interview imene yaponyedwa
    Koma Mfundo zimene zikunenedwa m'menemu ndizaphindu zotukula dziko la Malawi

  • @sadockkapesa8139
    @sadockkapesa8139 Месяц назад

    Inali wayilesi kale, panopa ndi chinzache cha wayilesi😅😅😅

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka Месяц назад

    Kavotedwe kosankhana mutundu kakugwesadi dziko lathu aMalawi, tiyeni tisenthe tivotele anthu amene angakweze ziko lathu

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 Месяц назад

    Program yakale iyiii times has overtaken you

  • @MathaNamanja
    @MathaNamanja Месяц назад

    Inu mesa izi tinaonera kale kodii????

  • @MaliGomani-z4k
    @MaliGomani-z4k Месяц назад

    Zakaletu izi😅😅😅

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td Месяц назад

    Alonwe tatopa nawo konaso UTM natama kudzimva mwini chipani samadzikonda koma atidye nao Moyo ngati finye

  • @JohnMota-jd1gt
    @JohnMota-jd1gt Месяц назад

    Kodi mulibe Zina zokamba koma zandale basi?

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska Месяц назад

    Mwayamba zobweleza mwatipa eti

  • @MaryNyirenda-nq3mh
    @MaryNyirenda-nq3mh Месяц назад

    Mayo data langa

  • @gkay-striker
    @gkay-striker Месяц назад

    Zakale izi

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 Месяц назад

    Nonsense, musatinyase agalu inu