Chibadwileni Sindinamvepo Dziko Likujudula Ma Passport - Comrade Ntanyiwa
HTML-код
- Опубликовано: 4 июн 2024
- There are rumours that some members of the First Entourage to Switzerland had their visa denied by the Swiss Embassy in South Africa due to the quality of the Malawian Passport. So, On Nyasa VoiceBox, we have Comrade Ntanyiwa commenting on the same.
Pali mphekesera zoti mamembala a gulu la First Lady kupita ku Switzerland anakanizidwa visa yawo ndi ofesi ya kazembe wa dziko la Switzerland mdziko la South Africa chifukwa cha kachitidwe ka Malawian Passport. Ndiye, Pa Nyasa VoiceBox, tili ndi Comrade Ntanyiwa akufotokoza zomwezi.
Indeed we have the president but we have no leader we need someone to lead our country
M'Malawi Boma tilibe
Kkkk Monika wazionera ekha ..omuperekeza kubwezedwa amalawi akamadandaula kumaona ngati akunama Malawi wanunkha
More fire
Amenewadi ndi akanyimbi man eish!,
Ndipo mulungu atimenyera nkhondo sanati antanyiwa amenewo ayaluke zeni zeni kuti awake pambala mbanda
Pa nkhani imenei ndiganizo langa kuti ndalama za passport ya fec zizilowa mthumba la acipani.
Chilima ndi chakwera ndi mabi enieni MBAVA
Boma ili ndila fake,chinthu ukachita kulanda ndichoncho.boma ili anachita kulanda m,'manja a DPP
Ndipo koopsa zedi, upresident siu group admin, ndimakape.
Ulamuliro wa MCP ndi wa fake ndichifukwa akupanga zinthu za fake apangiletu c u 2025
Komatu anthu wa simadolo ayi,, ndi anthu opanda nzeru chabe coz anakakhala ma dolo sibwezi ma deal awo akumenyawo akungogwidwa,, zopoila
Ambuye atithandize 😢😢
Boma la mtundu wanji lopang ma passport afeg boma lopanda nzeru
Kumalawi kuli so makhoti
Boma lomvesa chisoni zedi mcp
We need to have reader
Anthu onse amene amayankhula pa nkhani za ulamuliro wabwino ali chete pamene Dziko lathu likuyendetsedwa mwa ukatchali chonsecho tili ndi President mdziko,, Chakwera tulani Pansi udindo mwationongera dziko.
Kumalawi kulibe boma
Mr mtanyiwa mumatiyimilila
Kunkuyu apeza choyankha, crook sasowa choyankhula
Sheeeeee!!!!!
Achakwela mizimu ya kwiya 😂😂😂😂😂😂😂
Akulu akulu zoona mpaka zinthu zizitere m'dziko lathu koma tili ndi police and army ?
Police ndi army zakumalawi amazionetsa udolo kwa ife tomwe . . Koma kudya ndikunyela basi
Dziko lopusa lomvesa chisoni worst government in Malawian history shame on u chakwela
This Government is fake, mwinanso tingonena kut tili ndi Chifanifani cha Boma,,,,, Chilima unandilakwisa pondiuza kut ndikavotere Boma ili.
Ndipo chilima ndi mfiti zedi