Innocent Mutholo On The State of Good Governance In Malawi

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 28 сен 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Innocent Mutholo comments on the Court ruling regarding Kalumo's position as Director General of Immigration and Citizenship Services, as well the state of Good Governance in Malawi.
    Ku Nyasa VoiceBox, Innocent Mutholo anenapo ndemanga pa chigamulo cha bwalo la milandu pa udindo wa a Kalumo ngati Director General of Immigration and Citizenship Services, komanso za ulamuliro wabwino m’Malawi.

Комментарии • 34

  • @YasmeenYalabi-b2c
    @YasmeenYalabi-b2c 3 месяца назад

    I salute you Mr I mutholo

  • @Ushermchebe
    @Ushermchebe 3 месяца назад +3

    😢😢😢😢😢

  • @BilalAliyah-k1f
    @BilalAliyah-k1f 3 месяца назад

    More fire big auzeni kuti apm ikulowaso

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 3 месяца назад +1

    Pro Arther Peter Mutharika ndi munthu wanzeru not zi abulutu zili panozi

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 3 месяца назад

    Ine boma limeneli likundivesa kuning'ina kwambir Mr... Timenyereni nkhondo inuyo pamodzi ndi DC Kalindo kuti anthu ena asakomedwe ndi zomwe angawachitire panoz nda apapa ndi ndale ya nyooo kuti ena aiwale padzana mkukumbuka lero ndipo sangazindikire konse tsogolo lawo... More 🔥🔥🔥 APM bas

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 месяца назад

    Awuzen akanganya amenewa malume!

  • @Ushermchebe
    @Ushermchebe 3 месяца назад

    😢😢😢😢😢

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 3 месяца назад

    Mmmmmm

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita 3 месяца назад

    ngati kuli kotheka Born kalindo ndi ena nonse mukutiimilila chonde ku mec marthah chizuma uja abwelekoso ku mec

  • @LamekiMawindo-kl2cw
    @LamekiMawindo-kl2cw 3 месяца назад

    Maulemu

  • @Maxwell-e2d
    @Maxwell-e2d 3 месяца назад

    😂😂😂😂😂 voice 😂😂😂😂

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 3 месяца назад +2

    Makamaka ma passport kulipila ndrama ndikudzidya ndrama tikuzileza movutika zochita kukongola athu olemela kutidyela ife athu ovutika ndithu adzalilipila ndithu

  • @EnockMuyaya
    @EnockMuyaya 3 месяца назад +1

    Peter mutharika boma

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 3 месяца назад +2

    More fire more fire Mr muthoro ulemu wanu❤

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 3 месяца назад +1

    Apm wooooyeeee!!!!

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 3 месяца назад

    Tili Pano kuchosa Chakwera pa U President mwayankhula mfundo Mr Game Changer

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita 3 месяца назад

    listern from RSA zipiteso ku mec kukonzedwe akhumbo katchali achokeko pampando

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 3 месяца назад

    Chakacha mawa kukala ngondo chakwera avuneasa vune akuchoka 2025 agaluwa achokwe sitikwavunaso olokupedwakumen boma likasinda ndikandakona atapedwa sindinga dandauleso eetu💪💪💪chatap agalu

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 месяца назад

    Ndipo mulanduwo si umodzi okhatu oti azayankhewo, ilipo migolomigolo , mitolomitolo ya milandu

  • @emmanuelalbertbotolo
    @emmanuelalbertbotolo 3 месяца назад

    President akuononga dziko ,aiwala anasakidwa ndi anthu

  • @MathewsChitsulo
    @MathewsChitsulo 3 месяца назад

    Ndi zoona Pali kusiyana kwakukulu si nkhwali zili m'boma lelozi

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 3 месяца назад

    More fire azasa ndalama zathu

  • @FelixBoss-yn9pe
    @FelixBoss-yn9pe 3 месяца назад

    Nde mwati asanza misonkho iiiiii koma sono

  • @FranklinNdovi
    @FranklinNdovi 3 месяца назад

    Two blind persons will mislead each other vonsequently they will follow into a ditch.

  • @CharlieAmosi
    @CharlieAmosi 3 месяца назад

    God bless you game change

  • @andrewchirwa2193
    @andrewchirwa2193 3 месяца назад

    Thanks God 🙏🙏🙏

  • @uchizJoelMumba
    @uchizJoelMumba 3 месяца назад

    Alomwe inu mulilaso 2025 mukhaula simunati chakwela sakuchoka

  • @AishaChibwana-b8o
    @AishaChibwana-b8o 3 месяца назад

    Zaziii

  • @Ushermchebe
    @Ushermchebe 3 месяца назад

    😢😢😢😢😢

  • @morgansilungwe
    @morgansilungwe 3 месяца назад

    iyayi innocent mussati DPP ndi APM anali bwino ayiiiiiiii.akuluwaotu anatikwanansotu.onsewa awonnga basi.ukakwatira mkazi osabeleka banja likatha nkukwatira wina nayenso osabeleka baba sumabweleranso ku mkazi wakala uja noooo.APM was sleeping on duty.kambani anthu ena man.again APM has no new blood in his team to run the country.iiiiiiiii nooooo its the same people that massed up last time aaaa man izozo ayiiiiiiii

    • @DouglasDazuKamwendo
      @DouglasDazuKamwendo 3 месяца назад

      You don't know what you're talking about, it's better to be quiet than to demonstrate your ignorance.

  • @wilsonfelix6559
    @wilsonfelix6559 3 месяца назад

    Amen brother mutholo