ZOMWE ZACHITIKA KU MALAWI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 12 сен 2024

Комментарии • 20

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 20 дней назад +3

    Penapake gayz mulungu timamulakwila izi vuto nditokha Malawi achina kalindo akhazula kuchikamwa paka kutopa so don't blame god please 😢😢😢😢😢😢😢

    • @KingDavedNkhata
      @KingDavedNkhata 20 дней назад

      Mulungu izizi zoziyanba dalazi Koma akulu akulu tiyeni Pena tizikhala serious
      Anthu ambiri alankhyladi ndikutopa kunikira ndikutopa nsiyeni Mulungu

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 19 дней назад

    Lack of philanthropy and genuine patriotism in Malawi has brainwashed divers leaders into thinking in very negative and limited terms.

  • @MabvutoSembo
    @MabvutoSembo 20 дней назад +2

    Mulungu atithandize

  • @AlickjoiceMatchipisa
    @AlickjoiceMatchipisa 19 дней назад

    Gwetsaso kwacha

  • @sweeneykamwendo6251
    @sweeneykamwendo6251 20 дней назад +1

    We are cursed as a nation

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 19 дней назад

    AAA mavito ku Malawi ochita kwakozawo

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 19 дней назад

    Mbaleme iwe wabodza nanga mchifukwa chiyani anthu mukungomanga?

  • @YaqoobStandwell
    @YaqoobStandwell 18 дней назад

    Kunkuyu ndiye palibe zomwe amayankhula bas oyankhulana zake zomunyengelela chakwela kut aziwoneka kut ali mbali yake kubisa chilungamo kut ziko lamalawi bwana sili kuyenda bwino bas kumangokwakopa ndimaboza alibe zelu kunkuyu

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 19 дней назад +1

    Kkkkkk pamenepo ndipamene mungadziwe kuti mcp onse ndi anthu oononga ndipo kulibe Utsogoleri.

  • @AndrewjemesJemes
    @AndrewjemesJemes 20 дней назад

    IMF must go

  • @RobertGalatiya
    @RobertGalatiya 20 дней назад +1

    Tsogolo logwetsaso kwacha layamba kunukhila a Malawi tili pamavuto akulu

  • @josephgabriel5941
    @josephgabriel5941 20 дней назад +1

    After mutamwanza ndalama zankhaninkhani....

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 20 дней назад +1

    We are not crc as country 😭

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 20 дней назад

    Guys tiyeni tidzuke mwa mphamvu coz izizi zitiwonongera Malawi wanthu

  • @onesterabayo1871
    @onesterabayo1871 20 дней назад

    Corrupt minister

  • @MussaZakeyu
    @MussaZakeyu 20 дней назад +2

    Mulungu atithandiza