Yoyoyo Mr namiwa muopa mulungu kupotsa abusa achakwera yoyoyo my allah protect and guide you mr namiwa be longest mr azibale anu akumvutika mmalawi please please my allah bei with you all the time allah akbar respect to u
Allah azikuyang'anirani thawi zonse mpaka mcp atiuze basi kuti chakwera ndi amen anapha athu aja amalawi akuziwa zimenezo ndiye iyeyo akubisa koma thawi ikubwera
NAMIWA SIDEDI..NDIYE IYE ANALAPANGA ZAKEZO NDIPO ENAWO A CEDED ANAKAPITILIZA KUPANGA MADEMO A NKHANI MADANDAULO A MALAWI AMBIRI.@ MADANDAULO AKUGWA JET PLANE @ MADANDAULO A KUKWERA KWA ZINTHU..KATUNDU WOSIYANA SIYANA .NDI KUKWERA KWA AKATUNDU @ KABQEREZA BWEREZA WA " DEVALUATION YA KWACHA KATUNDU NKUMAKWERA.@ KUMANGANA MANGANA NDI APOLISI POPANDA MULANDU @ A MCP KUPHA IPHA ANTHU POPANDA CHIFUKWA. NDIPO OMANGAWO A POLISIWO NDI ANDALEWO OSAIMBIDWA MULANDU .NKUMANGIDWA.AYI .CHIFUKWA IWO NDI A MCP ANTCHTITO A CHAKWERA LAZARUS @ KUKWERA KWA MAFUTA KONYANSA @ A MCP KUBERA KALE MAVOTI NDI KUWAPANGA A MEC NDI NRB NDI A SMARTEC COMPANY KUTI ABERERETU ZISANKHO .ZISANKOZI ZISANACHITIKE ETC @ NDIYE MADEMO AJA AMATI AKHALE PA 30TH OCTOBER 2024 MITU YAKE INALI YAMBIRI. SIZINALI ZA NDEGE ZOKHA AYI. KOMANSO KUDYA CHITEDZE MMALO MWANSIMA. CHIFUKWA CHANJALA YOIPANGA A CHAKWERA KUTI ANTHUFE TIZIANJENJEMERA
NAMIWA SI SIDED AYI SIDEDI NDI GULU LA ANTHU AMBIRI NDIYE ASAMADZITENGE KUTI IYEYU NDI SIDEDEDI. NDIPO IYE AKACHOKA ENAWO ADZITENGA MAUDINDO OSATI IYEYU AZILETSA PROGRAMES ZA BUNGWELI..SIDEDEDI SIKUNYUMBA KWA NAMIWA. . .ZIKOMO.SIDEDI NDI CHIGULU CHA ANTHU OK..
Namiwa maso amulungu ali pa iwe ndipo akutetezen mulungu mwini moyo . you are a man of truth pa iziz
God bless you Mr Namiwa
Namiwa you are the best citizen. Ife tikufuna zonse zikhale live on camera palibe zobisa.
Shadreck misheck ndi abidinengo anakana kurambira fano reroso namiwa wakana kurambira fano ❤❤❤
Mr namiwa mulungu akudaliseni pa ichi thandizani tundu wanu mulungu akusungeni ndimoyo akutetezelleni
NAMIWA AKUFUNIKA CHITETEZO CHAMPHAMVU CHIFUKWA MCP ILINAYE MASO NDITHU🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔
❤❤❤❤ Congratulations Mr Namiwa mumatiimilira pachilungamo
Powerful speech Mr. Namiwa, 100%.
God be with mr namiwa always that's it's our prayer
Perfect talking
Say allahamdulillah mr namiwa muziwe kuti chilungamo chanu allah mulungu wakumwamba alinanu ambiriwa ndalama zatsocheletsa akuona ngati ndiamuyaya viva mr namiwa🙏🙏🙏🇲🇼🇲🇼💔
Zelu zimenezo pitilizani anamiwa tikuva kuwawa amalawi
Perfect Mr namiwa 👌👌👌👌👌
Namiwa ndiwazeru koma vuto la anthu chilungamo sachifuna
Namiwa is a patriotic Man,,,,and commission imenei palibe mayankho omwe tipeze
MR Namiwa mumauwona umphawi wathu chonde pitilizan kutikonda ife amphawi musalore Chakwera akupaken mbiri yake yoipa
Good citizen Brother Naniwa Brave Man don't go back More fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
🔥🔥Namiwaaahhh!!!
Inuo anamiwa nd biggy ndpo mulungu aptlize kukusamaliran nzeru zanu zsathele pomwepa ai
Yoyoyo Mr namiwa muopa mulungu kupotsa abusa achakwera yoyoyo my allah protect and guide you mr namiwa be longest mr azibale anu akumvutika mmalawi please please my allah bei with you all the time allah akbar respect to u
Nayeso ofusa mafuso amafuna azimusokoneza namiwa kuti asafotokoze molondola koma wanena chilungamo wakana zachibwana
Namiwa ndimuthu
Mr S. Namiwa mumayima pa chilungamo
A Namiwa kumenya kugwetsa moto buuuuu💪💪
Anamiwa ambuye mulungu akhale nanu kwambiri kmaso azikusamalilani kwambiri
Mwachita bwino kuzisiya chifukwa akanakakupatsani kafele kwanu
Namiwa Namiwa kuyankhula mosabisa kkkk nkukuyu amati chani amafuna akudyese chibanzi eti 😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂 ameneyu di wakana chibanzi
Mpakana Mbelwa osakuvoterani with that good point eeeish dziko ili bwanji?
Mtolankhani uyunso, hmm alindi vuto pang'ono mafunso ake wotsokoneza munthu akulankhula bwino bwino koma akumudula.
Pena akumadzakhala ngat ndiwa mcp 😂😂
Congratulations namiwa ❤❤❤❤God bless you all the time please musabwelere mmbuyo
Allah azikuyang'anirani thawi zonse mpaka mcp atiuze basi kuti chakwera ndi amen anapha athu aja amalawi akuziwa zimenezo ndiye iyeyo akubisa koma thawi ikubwera
Ngati mukuiva khani imenei bwino lomwe fatsani ife ku school tinapitako alipo akumpanga chakwela chipongwe koma iyeyo asakudziwa ngati munava akuti report yochoka kulikulu linane kuti zayokhula zikhale live ngati mene ananenela namiwa koma anakana pamenepo Pali question mark alipo menemo akukhudzidwa kungoti president luso lofufuza yekha payekha alibe anthu amene akuwagwilitsila tchito ndiye oopsa
@LastonBezeni Koma iyeyo ndi wankulu akuyenera kumazifunsa yekhanso payekha,,kut uyu Bwanj akupanga Izi,,, In short iyeyo Ali ndi Vuto
Namiwa ndi munthu wamzeru amaziwa chofunika kuyakhula.
Mafunso enawo ndiye ali irrelevant
Mtolankhani akuzimva kufusa mafunso Koma akumudula Namiwa kut afotokoze bwinobwino
Ndipo nde akunditopetsa bwanji.
ANamiwa mukhale pompho musachoke mulungu akudalitseni ndikukupatsani nzeru zochuluka
U did well mr Namiwa they wanted u to put in evil system
Akanakuphaa wachita bwino kutulukaa
Namiwa wuli ndi zelu❤❤❤
Iyi ndembuzi yeneko
Ulemu wanu namiwa
Namiwa Namiwa Namiwa❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Namiwa I salute u
Bravo Sylvester Namiwa
Apa pakumana akamuna okhaokha,oziwa kufusa wina oziwa kuyankha mafusao, zamphavu kwambiri❤❤❤❤❤❤❤
The line of questioning 😂😂
Ndindani kodi ameneyu?
My point is, aziwerenga news or zanyengo. Otherwise 🗑 🚮
Manganya akunama ndi kulu ameneyu
Mene ndikuivela khani imenei achakwela akuyenela akhale osamala kwambili chifukwa pali anthu amene akhoza kukhala kuti anapanga zimenezi mwaseli iwowo asakudziwa
Km namiwa akuesesa pa ntchito yake ndipo kunena mosabisa chakwela ndi nduna zake anapha chilima ndi kasambala
Mbambande Mr namiwa
Ukanyamula mbendera ya chilungamo uzilimba mtima, mulungu amakhala ku mbali yanu koma chinyengo,sichabwino akuphawa azipita
Mudziko lathu mukanakhala anthu achilungamo oopa Mulungu ngati inuyo Anamiwa,,bwenzi tili penapake.
Zoonadi simukunama
Ndiponso inuyo
Zoom
Mulungu wake uti ?
Viva namiwa
That's good news namiwa
Achokeeeeehh kumenee ose atchulidwaooo
Namiwayu amaganiza guys ndipo sikape
Akulu mafunso enao opanda mayankho musamubvutise muthu
Those questions to Mr Namiwa are not important. Ask relevant questions.
MrC
Mulungu asikudalisani pachilungamo chanu
Alimo mdzikoli anthu a mzelu, koma Vuto ndiosauka
A Namiwa akufuni okhale ambiri kuti dziko liziyenda bwino
Ndye olakwisa ndiomwe anayitana Anamiwa anayitana mitani
APATU NAMIWA WAKWIYA DZENI DZENI UYU MWANA WATEMBO ACHOKE KU MEC AMALAWI SIFE DZISILU TOTSE AYI PAKA KUYIKA MWANA WAMUNTHU WA MCP AAAA CHIYANI ICHI NKHONDOTU AYI AMALAWI
Mr Namiwa mwachita bwino kutulukamo mmenemo
Zakukomera bwanji kufunsa funsolokutuma akunkuyu kulephera kutumikila anamiwa atkutuma ukanilamji
akufunsa zopepela ameneyo amwene asatitayitse nthayi
Mtolankhani uyu adyesedwa banzi nditu but anamiwa akulongotsola momvekha nditu
Kodi apule mmene amamuyika uyuyu mu comment imeneyi, samamudziwa kuti iyeyi amadya msima ndiwo zake chilungamo😅😅😅😅😅😅
Uyuyu anabadwa nduumunthu ulemu wanu a namiwa
Wishing you a long live Mr Namiwa
Anamwa ndinu katundu omanga ndi mawaya osawanyengelera amenewo
Anamiwa inu ndimuntbu wankuru ulemuwanu
Anamiwa samphweketsa
Namiwa munthu wamkulu iwe
Decision yazotsatira za inquiry anapanga kale agulukunyinda awa
NAMIWA SIDEDI..NDIYE IYE ANALAPANGA ZAKEZO NDIPO ENAWO A CEDED ANAKAPITILIZA KUPANGA MADEMO A NKHANI MADANDAULO A MALAWI AMBIRI.@ MADANDAULO AKUGWA JET PLANE @ MADANDAULO A KUKWERA KWA ZINTHU..KATUNDU WOSIYANA SIYANA .NDI KUKWERA KWA AKATUNDU @ KABQEREZA BWEREZA WA " DEVALUATION YA KWACHA KATUNDU NKUMAKWERA.@ KUMANGANA MANGANA NDI APOLISI POPANDA MULANDU @ A MCP KUPHA IPHA ANTHU POPANDA CHIFUKWA. NDIPO OMANGAWO A POLISIWO NDI ANDALEWO OSAIMBIDWA MULANDU .NKUMANGIDWA.AYI .CHIFUKWA IWO NDI A MCP ANTCHTITO A CHAKWERA LAZARUS @ KUKWERA KWA MAFUTA KONYANSA @ A MCP KUBERA KALE MAVOTI NDI KUWAPANGA A MEC NDI NRB NDI A SMARTEC COMPANY KUTI ABERERETU ZISANKHO .ZISANKOZI ZISANACHITIKE ETC @ NDIYE MADEMO AJA AMATI AKHALE PA 30TH OCTOBER 2024 MITU YAKE INALI YAMBIRI. SIZINALI ZA NDEGE ZOKHA AYI. KOMANSO KUDYA CHITEDZE MMALO MWANSIMA. CHIFUKWA CHANJALA YOIPANGA A CHAKWERA KUTI ANTHUFE TIZIANJENJEMERA
Ndinane ine kt namiwa siwogona.
NAMIWA SI SIDED AYI SIDEDI NDI GULU LA ANTHU AMBIRI NDIYE ASAMADZITENGE KUTI IYEYU NDI SIDEDEDI. NDIPO IYE AKACHOKA ENAWO ADZITENGA MAUDINDO OSATI IYEYU AZILETSA PROGRAMES ZA BUNGWELI..SIDEDEDI SIKUNYUMBA KWA NAMIWA. . .ZIKOMO.SIDEDI NDI CHIGULU CHA ANTHU OK..
Kodi uyoyo ndintola nkhani kapena akuimila mcp sindikumunvetsa chimene afuna munthusanamalize kuyankha akufunsa zopandanzeru pantumbopako Pako
Ndipo nde Akutopetsa koopsya pena akumadzakhala Ngat ali mbali ya mcp. Ndiobowa bwanj mxiiii
Mulungu azikudalisa
God bless you mr namiwa