Za meeting yoyamba ya UTM atamwalira Chilima yemwe anali mtsogoleri wao zili motele

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 июл 2024

Комментарии • 13

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 15 дней назад +7

    Chakwera kupha munthu kamba ka udindo? Ayi ndithu Mulungu akukhathe.

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 13 дней назад

    Nkhani imeneyo ndi yabwino, koma Manganya awatangwanikitsa chabe, mwamunva mzimai uja, Usi ndi wa independent, awapusitsa chabe apa.

  • @BrunoChakukuma
    @BrunoChakukuma 14 дней назад

    Usi ndi crook musiyeni ameyo pangani zanu a utm plz

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 15 дней назад +4

    Moto buuu akaliyati tiyeni nazo poti inu ndi omwe mumakhala pafupi ndi chilima

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 15 дней назад

    UTM ikakamila chingalawa chá tonse alliance ngati m'mene anachikakamilila Cláuds Chilima , ndithudi chipani cha UTM chizathela pomwepo mu 2025 , 😊

  • @UsenLashid
    @UsenLashid 14 дней назад

    Ulemu wanu akaliyati team yonse ya UTM pitiliza kusunga ulemu wanu komaso ndi kukweza mbendela ya Malawi komaso mokomela amalawi chezezo la ndilakuti samalani kwambiri musagulitse chipani chanu Ku MCP Ayi foundation ya UTM chakwela sakuyidziwa Ayi, chomwe akudziwa iye tonse alayasi koma zofetsa chisoni Kuti chakwela Anantchola bridge yowolokela tonse alayasi zomwe zikutathauza Kuti chakwela sakuwelengaso Za tonse alayasi chonde chonde ndalama zimene akukoza a MCP including president Kuti akupatse inu ndikuopa mulungu wanu Musalandile Ayi chifukwa zimenezo sindalama ayi Koma ndi mwazi wa president wanu komaso Kuti Ife amalawi tipitilize kukusapotani , ndi mbili ya bwino inuso mukuona amalawi ndi Mene alusila musakhale mu gulu lonyozedwa ndi amalawi chifukwa cha ndalama mudzakhala wosowa mtendele Moyo wanu , tikumbukile Kuti silikali wa kuzomba uja Anati ine ndinali komweko Ku chikangawa ndipo tibapatsidwa ma 10,000000 Koma ine ndenkha ndikulemphela kudya ndalama iyi chifukwa cha mwazi wa chilima Muthu wosalakwa god bless UTM party including all the members

  • @DalitsoMbalanje-n2p
    @DalitsoMbalanje-n2p 14 дней назад

    Osanyengela yudasi kut adye nafe imfa ija ikutiwawa.

  • @AyamMkango
    @AyamMkango 14 дней назад

    Kd mesa kuli vp kumeneko

  • @MisheckNtanbalika
    @MisheckNtanbalika 15 дней назад

    Atuluke kaye ku tonse kut fundo zawo zikhal zamphavu km akapanda kutuluka akhozelaso maplani ngt president wawo chilima tsogolo labwino la utm liyime palokha osati ndi mcp

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 15 дней назад

    Awa adziwona kuyipa kowombela fiti manja UTM Iithela pops asaganidze kuti .MCP yasekela aaa ngati sanalemekedze chilima awa asalawa adzingodikila kuchosedwa limodzi ndi MCP 2025 UTM adzathela popo basi dziiiii

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 14 дней назад

    Chakwera phudzo lelo Chilima kulibe

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg 15 дней назад

    Chakwela nd fiti

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi 15 дней назад

    Zitakuchitikitala zimenezi ja ndizokaikisa ngati mungakhale ndi zonveka Kaya simuli ku chipani chakuphacho 😭😭😭😭😭😭😭😭😭