The drum beats are so soothing to my soul, each time I listen to them I feel much better with my mood swings and the clinical depression. Greetings from North London UK, your sense of humour and acting experience script is so amazing mfumukazi the matriarch queen of the lomwe❤🎉
Ndikuntha kuona mkazi wa marilo Ovilila😅😅😅😅 akuyanda ndi Ngiling"ande😂😂😂😂
Amfumi kazi muli ndi mwano😂😂😂
The drum beats are so soothing to my soul, each time I listen to them I feel much better with my mood swings and the clinical depression. Greetings from North London UK, your sense of humour and acting experience script is so amazing mfumukazi the matriarch queen of the lomwe❤🎉
Ateng ma ngenge ..ma wholesale😂😂😂😂😂 km mulizithu umu😊
Amfumukazi mpaka kuba ufa 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣ndiye athu angakuveleni chochi
Kkkk kwini akubera ufa afumu kazi 😂😂😂😂😂umandisangarasa kwini
Amfumukazi aba Ufa 😂😂😂😂
Kodi mayi chokochoko mmm misala yakwa adyangu mwabwera nayo Kwa mfumukazi😅😅😅😅
😂😂😂😂 komatu amfumukazi ndiamunaawo😂😂😂
😢😂😂😂😂 kwavuta afumukaz kubawufa zowona
Ma holy center😂😂😂
Nafuneya mwana pretty wa kalanka 😂😂😂...Maliro ati anangowatengera cha mpunga mkati😂😂😂😂
Mangengeeee kkkkkk ma wholesaler kkkkk Kalanka❤
Ulendo uno mfumukazi yayaka moto🤣🤣🤣🤣
Anyamata awirirwa ah..bola gututu ndi nzake
Ndakuwona kwathu kwalosa abale💃💃💃✔️
Amfumu kazi mtopora wabwanj uyu musiyeni kwini akafike bwino ku chigayo kkkkkkkk
Mfumukazi maboza mmm😂😂😂
Musandiyang,aneso ngati undiyang,ana matumbo ayi
Koma Apadela amandiwaza kobasi 😂😂😂
Eeeh koma ndaseka zili umu 😂
😂😂😂 Km mfumukazi eeeee
Mumakwana bwana malilo kkkkk
This has to be the best drama in malawi manje
it's better today ndinakusowani Queen ndi mayi shoko shoko mumakwana 💪
Mfumukazi maboza kwambiri 😂😂😂
Banja la a Mfumukazi limandisangalatsa .kaya bwanji?
Koma queen ndiopsesa mtima 😅😅ufa amunela
Tea ndamwa osati ndadya 😂😂😂
Kudya osat kumwa😂😂😂😂
Amfumukazi mumandindisangalasa❤❤❤
Proud of you people
Ndakusowan Joshua naaa nkhani yaufayi Joshua asalepherepo
Welcome queen & mai shokoshoko to mfumukazi
Brings chisangalalo❤
Mtopola Fumukazi
Paja a Queen abwelera ku Mudzi
Nanyoni uziporamoto
Mfumukazi ❤
Dilikisi yemweyo😂😂😂
Ati mangenge😂😂
Yachedwa bwanji
Koma mlomwe zanga 😂😂
Koma queen ndimachini
Mfumukazi amatha..
giling'ande😂😂😂😂😂😂😂😂
Khwin wafuka kumuzi sopano kkk ii
Kkkkkkk champunga Mkati
Kwathu kwa Losa kwayaka motooo
Kuno nikwina mai shokoshoko misalayayi aqeen ulemu niwabwino
Afumukazi ayamba Kuba mmmm
dilinkisi
Mfumu yatopola iyi eeeehh 😡😡😡😡😡
Anyamata ajuga awa sakumbemba
Awiriwa aaaaa kaya
Those who were waiting kandigulileni dilinkisiyoo
Koma fumukazi
Ngenge
Oyamba ndine
second its miiikkkk
Kkķk kulawilira tuu