TAMVANI PA TIMES RADIO KUCHEZA NDI MUNTHU AMENE AMAKAKA MIZIDWA KUGONANA NDI MWENYE 15 SEP 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 12 янв 2025

Комментарии • 97

  • @LovenesskNali
    @LovenesskNali 3 месяца назад +4

    😢😢😢😢 amayi amenewo anali ankhaza iiiii

  • @charleschij524
    @charleschij524 3 месяца назад +4

    Ndalama zili kumalawi konkuno nkhani ndikuganiza booo

  • @MphatsoTolaniLindiweh
    @MphatsoTolaniLindiweh 3 месяца назад +2

    Imeneyo sinkhanza mwene mtendere umenewo 😅😅😅😅munakaberekera mwana

  • @ConnexKhomba
    @ConnexKhomba 3 месяца назад +3

    Amai amenewa kuwabela kunali ize bwanji asshhh

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 3 месяца назад +2

    😢😢😢kulakwatu uku eeeeish

  • @FunnyFishWaffle-oo7bd
    @FunnyFishWaffle-oo7bd 3 месяца назад +4

    Zaboza izi magazi mpakana miyezi 4 kkkkkkkk chidangopeka ichi chisatibowe kkkk

    • @WisdomMwale-j9h
      @WisdomMwale-j9h 3 месяца назад

      😂😂😂, Etii??🤲🙌🙌🙌

  • @macknesslovenesschisambi-ms1iu
    @macknesslovenesschisambi-ms1iu 3 месяца назад +2

    People are wicked,alot of evil things are happening in this world.lets be careful

  • @JohnPhopho-ut3ot
    @JohnPhopho-ut3ot 2 месяца назад +2

    Chitsilu iwe. Osajambula galimoto or nkhope yamunthu okutenga. B4 kupita kwa bwana aliyese timauza anthu komwe tili komaso emwe tili naye.

  • @Yossefeanodi
    @Yossefeanodi 3 месяца назад

    Osamuonetsa yachikuda amwene😊😊😊😊

  • @HawaMamo-q2v
    @HawaMamo-q2v 3 месяца назад +2

    Mmmm SA eshii 😢😢😢

  • @Rhoda-g1y
    @Rhoda-g1y 3 месяца назад +2

    Pepan brother 😭😭😭🙏🏻🙏🏻

  • @MussahBlackberry-z4h
    @MussahBlackberry-z4h Месяц назад

    Good idea km msogoleri Ali kunoku mmmm ndi chi

  • @GeraldBiliat
    @GeraldBiliat 3 месяца назад +1

    Akuluwa dyera likanawapha😂😂😂

  • @LuciusMaison
    @LuciusMaison 3 месяца назад +2

    Zosayenda kusaka ndalama kutiwonesa zinthu!!

    • @annamazingashaibuh6276
      @annamazingashaibuh6276 3 месяца назад

      Eish inu zovutatuu

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy Месяц назад

      Ndipo inu ine ndili ndi mulamu wanga amamuyamwa mweye mbolo yake akatero amugone komatu anawonda bale wanga nditava ndinangowauza abwana anga tinapita ndi abwana anga kukamutengako

  • @YusufuChalamanda
    @YusufuChalamanda 2 месяца назад +2

    Aaaaah mpakamyezi4 popanda kupeza plani yothawla uku ndiye kupepela ndithu

  • @IshmaelFrank-f7c
    @IshmaelFrank-f7c Месяц назад

    Khani ya boza iyi aaaa

  • @JIL-m3j
    @JIL-m3j 3 месяца назад +1

    Wishful thinking

  • @MussahBlackberry-z4h
    @MussahBlackberry-z4h Месяц назад

    Ndipo sunalakwise kuvaya jonz ndipo usabwereko chikangawa watigurisa

  • @RobertChikawonda
    @RobertChikawonda 3 месяца назад +1

    Mudakafelandi mapenate nanga mwanyimboyo

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 3 месяца назад +1

    Osati mwaiwo unabwera chifukwa chogonana ndi amaieo
    Unatenga magazi amwai achuma😂

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 3 месяца назад +2

    Eish 😢😢

    • @GrecianWyson
      @GrecianWyson 3 месяца назад

      Ayi napepe napepe.nabora muli ndimoyo. Ambuye akwezeke ndithu

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 3 месяца назад +1

    Amwene inunso nde munali otengekatu mchifukwa munakumanazo

  • @NaomieBanda-t6g
    @NaomieBanda-t6g 3 месяца назад

    Aaaaaaa osapita kupolice bwanji

  • @Cathysoza-o1m
    @Cathysoza-o1m 2 месяца назад +1

    🤣🤣🤣mwapakula zachimwenye

  • @innocentmaiden3711
    @innocentmaiden3711 Месяц назад

    Bodza lebileni iye anali ndi phone bwanji samaimbira azinzake or kuimbira ku police. And nthawi yomwe amatulukayo bwanji sanapite ku police akanatha kumupasa ndalama zochuluka

  • @BraveMunyanga
    @BraveMunyanga 3 месяца назад

    Ati kundigwira pyeee 😂😂😂

  • @PRECIOUSMKUTE
    @PRECIOUSMKUTE 2 месяца назад

    Unadya uli ndi bala lampeni 😂😂😂

  • @JeseGwile
    @JeseGwile 3 месяца назад +2

    Muziphunzira kaye mkumapitakaye kujon naweso umkafuna imadzukabwanji 😂😂😂😂😂

  • @annamazingashaibuh6276
    @annamazingashaibuh6276 3 месяца назад +1

    Sambi uhmmmm eish abale moyendamuuu ai zikomo

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 3 месяца назад +1

    Osamupatsa mimba bwanji

  • @khoviwaedward
    @khoviwaedward 3 месяца назад

    Damn bro, malodza awa

  • @TinaKazembe-l7d
    @TinaKazembe-l7d 3 месяца назад +1

    Akanakupha kaya

  • @CementAsher
    @CementAsher 3 месяца назад +1

    Koma umphawiwu utionesa mabvuto

  • @JoyceGondwe-ve1zu
    @JoyceGondwe-ve1zu 3 месяца назад +1

    Nkhani ya bodza bwanji samayimba photo poyamba Nkhani Akuti iwowo amacheza pa phone ndianzawo kuti apeza ntchito yeniyeni

    • @rosemfuni
      @rosemfuni 2 месяца назад

      Inenso kudabwatu kuti nde phone amacheza ndanzawoyo inali kuti? Zabodza basi

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy Месяц назад

      Khani ndiyowona iyi wakwathu uyu

  • @NaduMbewe-zz6iw
    @NaduMbewe-zz6iw 3 месяца назад +1

    Mmmmm koma

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 3 месяца назад +1

    Mmmm sorry brother

  • @OwenJambo
    @OwenJambo 3 месяца назад +1

    Tjoo sory bro

  • @JulietKamanga-2
    @JulietKamanga-2 3 месяца назад +1

    Ayao kujoweni

  • @KingsleyLuka-f7b
    @KingsleyLuka-f7b 3 месяца назад

    Dala umafuna zimenezo umakawayamba dala

  • @JosephNkhoma-c9c
    @JosephNkhoma-c9c 3 месяца назад +1

    Mbuzi yamnthu iyi yopusa mesa ikanapeza Dola pamenepo

    • @EmoMphande-ui3xi
      @EmoMphande-ui3xi 3 месяца назад

      Iiiiiiiii inu akanafa uyo kungokhala munyumba dairy ,komaso mayiyo ndiwaboza sakanamupasaso or 1 land cz miyezi 4 amalekeranji kumupasa ndalama

    • @PRECIOUSMKUTE
      @PRECIOUSMKUTE 2 месяца назад

      😂😂😂😂

    • @CatherineChalema
      @CatherineChalema 2 месяца назад

      😂😂😂 Anabadwa mopepera chabe, mantha afisi

  • @kestinaphiri
    @kestinaphiri 2 месяца назад

    Mbuzi ya munthu

  • @SliviaJosephy
    @SliviaJosephy Месяц назад

    Hahahaha akileni unabwera kuno wakwathu uy yoooo ,,

  • @Cathysoza-o1m
    @Cathysoza-o1m 2 месяца назад

    🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣Azimzawo apa wap

  • @BunaahAdamh-q2v
    @BunaahAdamh-q2v 3 месяца назад +1

    Mmmmmmm xoopsa

  • @StonardPhiri-f8i
    @StonardPhiri-f8i 3 месяца назад

  • @EmoMphande-ui3xi
    @EmoMphande-ui3xi 3 месяца назад

    Vuto anatengeka kwambili mmmmm

  • @RabeccaMwikho-f9h
    @RabeccaMwikho-f9h 2 месяца назад

    Kkkkkkkk ati ndayamba kulila kkkkkkkkk

  • @talandilabenedicto
    @talandilabenedicto 3 месяца назад +1

    Wangondiwonongera bundle

  • @TensonMunthali
    @TensonMunthali 3 месяца назад

    Ay zikomo

  • @Felixbanda-q6p
    @Felixbanda-q6p 3 месяца назад

    Bola unamulawa

  • @HamzaChimatilo-b9r
    @HamzaChimatilo-b9r Месяц назад

    Muyao akakane chigololo? Mmm ndakaika

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe Месяц назад

      😂😂😂😂😂Bwanji mu Yao watani kusakanako

  • @JIL-m3j
    @JIL-m3j 3 месяца назад

    Muchiyankhulo chanji?

  • @JIL-m3j
    @JIL-m3j 3 месяца назад

    Akamapita ku Polisi akunama.

  • @EsteemEnterprise-pe1tp
    @EsteemEnterprise-pe1tp Месяц назад

    Chitsiru Cha munthu.

  • @rashiddhu
    @rashiddhu 2 месяца назад

    Wabodza uyu 😂

  • @darlingtonkamanga4858
    @darlingtonkamanga4858 Месяц назад +1

    Eish

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 3 месяца назад

    Machimo

  • @WinerdShadreck
    @WinerdShadreck 3 месяца назад +1

    Figures

  • @FelixDamuza
    @FelixDamuza 2 месяца назад

    Onama uyu

  • @PRECIOUSMKUTE
    @PRECIOUSMKUTE 2 месяца назад

    Unali ndi foni why didn't you call your friends as you said kut unali nawo konko???

  • @NellieChikuse
    @NellieChikuse 3 месяца назад

    It's bad

  • @AidaLivilinga
    @AidaLivilinga 3 месяца назад

    😢😢😢😢

  • @TuteThole
    @TuteThole 3 месяца назад

    💔💔💔

  • @Esther-r8c
    @Esther-r8c 3 месяца назад

    She is a ritualist

  • @PRECIOUSMKUTE
    @PRECIOUSMKUTE 2 месяца назад +1

    Your story doesn't make any sense,,,😔

  • @JustinaMwah
    @JustinaMwah 3 месяца назад +1

    Omg

  • @SimonMkwangwanya
    @SimonMkwangwanya 3 месяца назад +1

    Komaso ndikanakhala ine ndikanakhala koopya kuwapasaso mimba

  • @edwardgondwe
    @edwardgondwe 3 месяца назад

    Taponyani ka alinafe timvere

  • @JIL-m3j
    @JIL-m3j 3 месяца назад

    Bodza

  • @PRECIOUSMKUTE
    @PRECIOUSMKUTE 2 месяца назад

    Ase mzimayi wa fifty chakut years akakupose mphavu???

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 3 месяца назад

    😂😂😂😂😂

  • @LikangaManuel-sk8yp
    @LikangaManuel-sk8yp 2 месяца назад

    Mmmh doesn't make sense this is stupid

  • @ThembaniJikah
    @ThembaniJikah 3 месяца назад

    😂😂

  • @SimonMkwangwanya
    @SimonMkwangwanya 3 месяца назад

    Kusakhutisidwa ichichakoma ichchakma pusi gada

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft 3 месяца назад +1

    Munanyanya achimwene kutengeka

  • @JailosFirston
    @JailosFirston 2 месяца назад

    😢