Those follow Real Future Malawi 🔥 let's all gather here to see how Tunosiwe will respond to this interview..mwana wapa kaya Tuno Karonga to the world 🌟🔥🐐❤❤
I even subscribed to this channel these shows amandiwaza they're very entertaining 😂😂 great scripting that makes it almost look real and this one was just a perfect match of a duo 🔥🔥
I love you Tuno for the confidence and courage you have. Free to speak and you never give up.❤
Those follow Real Future Malawi 🔥 let's all gather here to see how Tunosiwe will respond to this interview..mwana wapa kaya Tuno Karonga to the world 🌟🔥🐐❤❤
Mafunso opepela okhaokha😂😂😂 and I like the confidence in tuno 💚
Koma ndiposo😂😂😂😂😂😂😂
Koyamba I used to hate this show koma pano ndaikonda it's lit and entertaining🔥🔥
Host uyuyu l think akayeseleko masewero ndachina manganya izizi siza aliyense😂😂😂
Mafuso opepera okhaokha... I love your confidence tuno
Koma ndaseka😂🙌ndipo they can never make me hate tuno🔥🥳😂
Aixe umuitaneso Temwa😂😂😂 Iweyo nd dolo adha 🔥 🔥🔥🔥
Keep the fire burning Blesikwa
kkkkk😂😂😂 ndakhalila mafupa😂😂😂
Ndidzichani idxi😂😂😂 @Tuno
these interviews make my day🤣
U are very beautiful indeed tuno❤️
Hahahaha mama Tuno ine ndipo simaonapo cholakwika pa Tuno ❤❤❤❤
Beautiful lady❤ I love you Tuno🥳🥳
Beautiful Tuno 🔥
I even subscribed to this channel these shows amandiwaza they're very entertaining 😂😂 great scripting that makes it almost look real and this one was just a perfect match of a duo 🔥🔥
😂 😂 😂 😂 Eeee komaaa
Ati dzichani izi😂km tuno ase😂😂
Mafuso achimidzi 😅😅
Macheza abuino awa😂😂😂😂😂
Koma tuno bwanji uyuyu sunamutukwane,... Ndopusatu uyuu
I love this show 😂😂😂
I can never hate u tuno❤😂
I can never hate u tuno ❤
Izizi usiye iwe talent ulibe nyani iwe
Ati kufika panopa zabanja umaona bwa 😂😂😂
tuno ase eeeh she's real in everything
mutu ngati mango host iwe, 😂
Ada awa satha kumfunsa munthu pa interview.
mumatha a Bule 😂 its good to have a sense of humour
Kkkkkkkk koma ths guy ati umava bwanj kukhala oyimba opanda nyash
Host akut bwanj😂😂
Palibe chimene wayankha canzeru tuno
Km2 mamuputa dala uyu 😁 simuziwa KUTI anavomereza kt iyei ND Mun2 yekha basi 😅
😂😂😂unakumana nazo not like m'mene umamupezelela chippie
Am waiting for the final one please do fast for me I want to see Tuno kuti apanga respond bwanj 😂 koz eeee 🙌Tuno ndi ......?
l like the guy the show is just interesting kuswakuswa
😂😂 koma hehehe 😅😅
Ndendende a Chisi a mutikuferanji😅😅
Tuno🔥
😂😂😂zokoma
🤣🤣🤣 ulibe thako
Oky funso lina 😂😂😂😂
Koma ndipo aaaaa point iyiyi yandiwaza kukwatila sitikwatilira anthu please girls kubanja umakakhalako wekha anthu mukwatilirawo sakhalako 😂😂😂😂khaya zanu izo😂😂😂😂
Kkkkk blesikwa umakwana uli ndi voice yogwesa mphwayi
Mafunso ako ada akundiwaza zed😅😅 akumveka mwau gheto gheto ndi uniga kkk, naye Tuno ndiye sasamala zamunthu😂😂
Anthu Inu mukusononeza ana hahaha 😂😂😂😂😂😂
Koma host anaxitenga personal kwambiri 🤣🤣anabwera ndi milandu
Thus his concept bwana
Palibe chimene ndanvapo apa tuno ndikape
Aaaaaah shatapu😂😂😂😂
Play it on speed you will love it more 😂😂😂🥳
Km uyu pajamwati zinalake ndi @bless
A part from kuvula pa social media hahahaha
Koma Tuno anatopa😂
Blesikwa ndi Fire. Ali ndi njira zomufoola munthu
🤦🏾♀️🤦🏾♀️🤦🏾♀️
😂😂😂
Koma ofusa mafusoyo mafuso ake opoira am not blame tuno
Kkkkkk mupwetekana
🎉🎉🎉🎉
Kkkkkkk comedy show
km interview iyi ayaya ikundikhutitsa ishiiii😂
Koma iwe ukufunsa za mwano eeeh koma muli kachilingamo.. chilungamo chinayandikana ndi mwano
Kulibe zokhalira hahahahaha koma guys eeeeee ...tuno ur beautiful
Interview or nkhondo?
kod interview yanji abale simisala koma iyi abale?
😂😂😂😂😂iiih
😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂kmn uzifusako ma fuso azelu nawe adha
He's not professional
Kkkkkk zachamba etti
🤣🤣😭
Ma questions ake koma 🚮
😅😅😅
Inu musamangoduladulaa aaaaaaaah 😢
One day idzathera ma pernaty
Ada awa ayamba kundisangalatsa 😂
😂
Umakwana
Interview ya bho iyi
Anthu agwirizana kuti azivuta khangati
Rage bait😅
😂😂😂😂😂
😂😂😂
😂😂😂😂😂iiih
😂😂😂😂😂iiih