Mudziko Muno Mulibe Chitetezo Phalombe Big Boy

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 окт 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Phalombe Big Boy asserts that Malawi is not secure. He made this statement after a soldier was allegedly attacked by thieves within the boundaries of Cobbe Barracks in Zomba.
    Pa Nyasa VoiceBox, Phalombe Big Boy wanenetsa kuti dziko la Malawi silili bwino. Iye wanena izi msilikali wina yemwe ati anamenyedwa ndi mbava m’malire a Cobbe Barracks ku Zomba.
    #malawi

Комментарии • 43

  • @lyiemax
    @lyiemax 2 месяца назад +4

    Ife a Malawi timaombeladi mmanja zinthu zopusa ❤❤

  • @Luismartinhomartinho
    @Luismartinhomartinho 2 месяца назад +1

    U continue playing with history God bless you

  • @JoyceKasongo-s8k
    @JoyceKasongo-s8k 2 месяца назад

    Wangalula big boy

  • @PreciousChlima
    @PreciousChlima 2 месяца назад

    Mukamachula kuti alhomwe mulibe nzeru usamsleee wamva wanyau iwe upole moto wamva ukapitiriza muona pole,, big boy goes on,, asirikali zofuna zawo Mesa amaderera mukamawauza,, iwo ndiodziwa akuti akusata malamulo

  • @lyiemax
    @lyiemax 2 месяца назад +1

    We are really not safe in this country ❤❤❤

  • @AbuOsman-ts6ef
    @AbuOsman-ts6ef 2 месяца назад

    Walakhula bwino big boy

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 2 месяца назад

    Dziko LATHU silinaopsepo ngat panopa dziko LATHU njala kuphedwa anthu ziwembu katangale,God help Malawi muphuleni Malawi pamoto.

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON 2 месяца назад

    Mmmmuwuzeni kuti sitikudya mafuta a petrol ife koma so misewu sitinga dumphe pasewu ndinjara zopusa mabweya amake mafiah yoooooo mr chikangawa yooo 😂😂😂😂

  • @bensonmughandira
    @bensonmughandira 2 месяца назад

    Please MDF, chitanipo kanthu pazomwe zachitika ku Cobbe barracks.

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 2 месяца назад +2

    Usamati munthu wina wagura mifuti tchula straight kuti chakwera wagura mifuti wagawa kwanyamata ake

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 месяца назад

    Amene amatsutsawo nde kuti amadya nawo ndlama za mcp

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 2 месяца назад +1

    Achiya bwino aakuba amenewo, bde mawa kunsewu

  • @VanessaAlinafe
    @VanessaAlinafe 2 месяца назад

    Zoona zake ife amalawi tilimumavuto kwambiri ameneyo achoke tisalolere amalawi kumuvotelaso achoke basi

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 месяца назад +1

    Ndipo chakwela sitizamuiwala mu mbili ya Malawi koma chimwe ndimava nacho chisoni athu akuvutika kwambili kuno ku Malawi ambuye atithandize ndithu

  • @MikeHarawa-q4v
    @MikeHarawa-q4v 2 месяца назад

    Zoona big

  • @bensonmughandira
    @bensonmughandira 2 месяца назад

    MDF operation ija bwa ,munaichita 199..Pagani changu.

  • @nafejonga972
    @nafejonga972 2 месяца назад

    Ndipo he is no more

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 месяца назад

    Ndipo live munthu uyu satana kwambiri mr chikangawa

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 2 месяца назад

    Mkulu ameneyu ndi ogona eti munsewu amadutsa olemera okha Chilomwe chikumuyabwa eti?

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 2 месяца назад

    ☹️☹️☹️☹️ koma ndilibe mau dziko lamalawi 🤔

  • @rhajabBinIman
    @rhajabBinIman 2 месяца назад

    They don't have a love for each other

  • @adamashrafi5875
    @adamashrafi5875 2 месяца назад +1

    Malawi watani aliyese akasowa ndiwo kuthamangila pa media kubwebweta zopanda mutu

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon 2 месяца назад

      IZI SI ZODUKA MUTU NAWENSO UKUFUNA KUNENACHANI IWEYO CHIBADWIRENI UNAYAMBA WAMVAPP KUTI MSILIKALI WAPHEDWA NDI ACHIWEMBU KOKHALA KU BARACKS? LERO CHACHITIKA NDICHIYANI CHITETEZO KULIBE KUNENE MUSATSUTSE CHIFUKWA CHOTI MWADYA ZA MCP

    • @ChristopherKawilam
      @ChristopherKawilam 2 месяца назад

      Inu ngat ndinu a MCP please shut up your mouth tisanaku lakwile wava

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon 2 месяца назад

      @@ChristopherKawilam iweyi wakuuzakiti ndine wa MCP NDINDANI sindipanga zandale ine ndiyekuti iweyo ndamene sunamve message yanga uyambitenso KUWERENGA komaso iwe sungalakwireine uzilakwirawekha ase ndipo ine sindinyunwitsidwa NDIMUNTHU uone ma sms angaomkachikena then uyambitenso kuyankha zikuonesakuti wathamanga kuyankha usanamve

    • @ChristopherKawilam
      @ChristopherKawilam 2 месяца назад

      @@HalisonSolomon Koma Sina pange reply comment yako tuu

  • @UmariBashiri
    @UmariBashiri 2 месяца назад

    Zoonadi Big

  • @HumphreyKachepa
    @HumphreyKachepa 2 месяца назад

    Ukunena zoona palibe choyimbila manja kubwera kwa mafute pa stima koma mafutawo osasika anthu awa ndi afiti

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa 2 месяца назад

    A Malawi ndi anthu opusa kwambiri zitsiru zeni zeni za anthu

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 месяца назад

    Anthu auleso kukonda kulongolola ndikutukwana basi. Musauka ndipo mukhaula

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 2 месяца назад

    LERO NDIYE AZIONATU ASILIKALI CHIFUKWA CHOTI NAONSO SAKUMVA ASANKHA KUGWIRA NTCHITO NDI CHIPANI LERO ZAYAMBA KUWAVUTA OKHA

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 месяца назад

    Komanso Asilikani amalawi anagona kwambiri panopa sizikuyenda ndithu

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 2 месяца назад

    Ai ndithu takumvani

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb 2 месяца назад

    Anthu ndiopusa akumapitabe kunsokhano wa mfitiyu

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 2 месяца назад

    Palibe chobisika,tonse tinadziwa kut siwakuba ,Koma ndiotumidwa,zigawenga Za boma.God knows

  • @MercyKatongo-p9b
    @MercyKatongo-p9b 2 месяца назад

    Sure sure correct

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 2 месяца назад

    Tidasankha molakwikathu pano tikulira

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 2 месяца назад

    Misewu komweko kulilongwe kokha nde asati sokosere

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 месяца назад

    Alomwe ndinu mbuzi zawanthu mcp 2025 boma musobva

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda 2 месяца назад

    Yaa

  • @BillyBentryMunthali-d2u
    @BillyBentryMunthali-d2u 2 месяца назад

    Mhuzi ndiweyo galu a kobe barack aphana okha okha ndiponso 20 million singakwanitse anthu 20 million kod School yake iti ? Imene munaphunzira zimenezi

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 2 месяца назад

    NKHANI IYI SIYOPITA NAYO KUTALI ANTHUO ANACHITA KUTUMIDWA NDI BOMA ZOSATHEKA MUNTHU WAMBA KUKAFIKA KU BARRACKS NDI ASILIKALI OMWEO ANATUMIDWA MWINANSO AKUFUNA KUBISA UMBONI WA KU CHIKANGAWA