Mayi Annabel Mtalimanja Atule Pansi Undindo Ngati Chair Wa MEC - Blessings Chaima Lozalio

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 16 окт 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Blessings Chaima Lozalio argues that Annabel Mtalimanja has a conflict of interest if she remains the head of the Malawi Electoral Commission, due to her alleged family connection to former Leader of the Opposition, Honourable John Tembo.
    Ku Nyasa VoiceBox, Blessings Chaima Lozalio wati Annabel Mtalimanja ali ndi mkangano wamalingaliro ngati atakhala wamkulu wa bungwe la Malawi Electoral Commission chifukwa cha ubale wake ndi mtsogoleri wakale wachipani chotsutsa John Tembo.
    #malawi

Комментарии • 22

  • @ZenuYatola
    @ZenuYatola 4 часа назад +3

    Chakwera achoke ndi mbudzi

  • @ZenuYatola
    @ZenuYatola 4 часа назад +1

    Mzimayi ameneyo ayenera atule pansi udido

  • @JohnKabila-v7q
    @JohnKabila-v7q 4 часа назад +1

    Chakwera achoke so walephela

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 4 часа назад

    Kodi Chifundo Kachali uja anamuchoseranji??? Coz nkulu amene uja ntchito amaiziwa.

  • @PaulRice-c5f
    @PaulRice-c5f 5 часов назад

    Iyeyo mtalimanja ndi anthu ovota amene akuphela ufulu ndani

  • @Jacksonmuhackeya
    @Jacksonmuhackeya 5 часов назад +1

    Chakwela ngati wamukonda ampase u president nanga siwankondesesa

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 4 часа назад

    Ndipo iyeyu tamutola kale mistake.ife takhala tikudandaula kuti anthufe Sitinalembetse iyeyu akulimbikira kuti tikalembetse ZaChisankho OSati za Ziphasozo pamalo polembetselapo.Aaaaaaa Sangakhaledi Chair person WA MEC ndiokondela.

  • @MonicaSteve-t5p
    @MonicaSteve-t5p 4 часа назад

    Akuyenera kutula pansi chifukwa ndi WA MCP sangayendese bwino zisankho

  • @JohnKabila-v7q
    @JohnKabila-v7q 4 часа назад

    Ine John ameyo achoke

  • @JohnKabila-v7q
    @JohnKabila-v7q 4 часа назад

    Achokebe mtalimanja Ku mec

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 4 часа назад

    Ati akusatira malamulo etii komatu akunama nkhani ya chisankho sitikuyenderanso malamulo

  • @Alice-z7t4z
    @Alice-z7t4z 3 часа назад

    Smartmatic machine asaloredwe achose

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 3 часа назад

    Mulungu alipo ndipo mavuto anthu akwaona atithandiza

  • @Fanie-i7z
    @Fanie-i7z 4 часа назад

    Atule pansi udindo basi okavota ndife osati ntalimanja wanuyo

  • @AubreygEliasizia
    @AubreygEliasizia 4 часа назад

    Mau amphavu

  • @tasmania527
    @tasmania527 5 часов назад

    Mbuzi ya munthu Mchawa iwe. Who are you to infringe the rights of Mtalimanja? She is going nowhere. When you're a thief you think of others around you as thieves too. It baffles my mind to hear DPP complaining about Mtalimanja as being sympathetic to MCP and yet it is not very long ago when the then MEC chairperson was enjoying bluenight parties with DPP in an open show of arrogance and a demonstration of party allegiance. Nde anthu inu pamodzi ndi DPP mukufuna kunamiza ndani? Kuzikonda basi ndi sankho.

  • @LessonChilomo
    @LessonChilomo 4 часа назад

    Atule pansi bac

  • @JamiesonKaunda
    @JamiesonKaunda 4 часа назад

    Atule pansi ndi chi mzimai chachinyengo.

    • @Alice-z7t4z
      @Alice-z7t4z 3 часа назад

      Exactly 🤞🤞🤞🤞

  • @PatrickMalenga-h5m
    @PatrickMalenga-h5m 5 часов назад

    Mukunama mukuphera ufulu ntalimanja

    • @cjaylucky
      @cjaylucky 5 часов назад

      Nayes akutipel ufulu wathu atule basi