LIMPOPO FM SIYIKUWASIYA A PRESIDENT ILI NAWO NAWO POSOWETSA SKC PA PROGRAM YA SIMANGENI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 28 окт 2024

Комментарии • 40

  • @MarkinaJohn
    @MarkinaJohn 2 месяца назад +6

    Boom!!!

  • @RachelNkhoma-vn2jo
    @RachelNkhoma-vn2jo 2 месяца назад

    Mfumu solomo ina pempha nzeru ndipo Yudasi anampeleka Yesu anakakhala ngati mfumu solomo chakwera ndibwezi Mulungu anakapatsa nzeru zoyendetsera dziko komano akumpeleka chilima kuimfa ngati Yesu nkhritu anatifera ife kwaiye ukhale ulemelero ndi matamando kwa onse amene anatifera ife, ambuye chita nawo achina yudasi onse asowe mtendere ngati yudasi.Tiwaikize mmapemphero onse amene anafera dziko lathu

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 2 месяца назад

    Mumandisangalatsa guys momwe mumasekela 😅😅😅😅😂😂😂yomweyo mr Silimangeni Razaro Chikangawa 😅😅😅😂😂😂

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 2 месяца назад

    iyooo nyekhweeee

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 2 месяца назад

    😅😅😅😅😂😂😂Silimange mr Chikangawa mwafikako kuoo ngati 😅😅😅😅😅😂😂😂yomweyo galu iwe usampatse ndimpatsa😅😅😅😅😅😂😂😂

  • @JowasiMasina-fy8ji
    @JowasiMasina-fy8ji 2 месяца назад

    Kulibe ngozi yovura zovala munthu imeneyo inawonetsa kale kuti zachipogwe chabe bwanji ngozi yaku Nkhotakota ija sanayimitse kusaka anthu😎

  • @JesseKanjanga
    @JesseKanjanga 2 месяца назад

    Kumuvula zovalako Mulungu anawabisila mzelu ndicolinga coti tidziwedi kuti anacita kumupha. Munatilakwira mr cikangawa

    • @RachelNkhoma-vn2jo
      @RachelNkhoma-vn2jo 2 месяца назад

      Munthawi yakusadziwa Mulungu analekelera,Iwo samadziwa kanthu kuti Mulungu akuwoona analolera agwire ntchito yawo koma samadziwa kuti Mulungu wanna nzeru

  • @cynthiandekhakatundu6890
    @cynthiandekhakatundu6890 2 месяца назад +5

    Tikudikira report laa Ndege

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 2 месяца назад

    Mulungu awalanga onse amene anapanga chipongwe pa kupha achibale onse amene akumwalira pano pangozi zosiyana siyana mulungu ndiamene akuziwa zonse koma kwa chakwera ndiye ndi muthu oyamba kupha abale athu onse amene akufa pangozi zisiyana siyana ndiye mulungu athane nawo onsewo

  • @cmsanyama200
    @cmsanyama200 2 месяца назад

    Angoni ali ku Mzimba ndi ku Ntcheu, Mchinji komanso Mwanza.

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk 2 месяца назад

    Ndizowawa kwambiri, ya azungu anaturutsa within 20 minutes,😭😭😭

  • @BraghtYohane
    @BraghtYohane 2 месяца назад

    Choipa chisata mwini

  • @GiftMoses-k6b
    @GiftMoses-k6b 2 месяца назад

    Chakwela pa mtumbo pamako limodz ndi Bambo ako .Tikufuna report ya Ndege

  • @JowasiMasina-fy8ji
    @JowasiMasina-fy8ji 2 месяца назад

    Zikomo talandila moni ife kuno timakunyadilani Nthawi zonse

  • @ClementKhomba
    @ClementKhomba 2 месяца назад

    Ife angoni akuntcheu sitikufuna zopusa za achewa awawa akutizolowela Mazila awo onse!

  • @EdwardMukholi
    @EdwardMukholi 2 месяца назад

    Pa 30 chakwela chikangawa kkkkk uli madzi

  • @RajabShahida
    @RajabShahida 2 месяца назад

    Ya chilima siyizatha mpakana kalekale

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 месяца назад +2

    Mcp anthu onse ndi asatana kwambiri ndi mr chikangawa

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 2 месяца назад +1

    Ndipo chakwera asakhale ndi mtendere ndi onse a pa banja pake

  • @cynthiandekhakatundu6890
    @cynthiandekhakatundu6890 2 месяца назад +5

    NKHAANI YA CHILIMA IDZATHA POKHAPOKHA TADZIWA CCHILUNGAAMO ...

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 месяца назад

    😂😂😂😂😂 koma anthu inu mukufuna Apule atani nanu😂😂😂

  • @GreyShadreck
    @GreyShadreck 2 месяца назад

    Tikudikilila 😂😂😂

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk 2 месяца назад +3

    Ku Nkhata-Bay kuribe angoni, kuri Atongaaaaaa😂

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 2 месяца назад

    Mcp ndi manganya ndi amene anapha maremu sauros chilima mcp ndi team yawo onse ndi mbumba yoyipa kwambili chikangawa

  • @OrackPhili
    @OrackPhili 2 месяца назад

    Report lituluke la chilima

  • @MorisSumaili
    @MorisSumaili 2 месяца назад

    Anchikangawa

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 2 месяца назад +1

    Koma ndiyedi inu aaaaaa

  • @patrickdamalekani9863
    @patrickdamalekani9863 2 месяца назад

    Report ndilo tikudikila pno

  • @StephanoMaganizo
    @StephanoMaganizo 2 месяца назад

    Tikudikilatu kuno ku America report imeneyi

  • @beatricenkhoma1109
    @beatricenkhoma1109 2 месяца назад

    Ndipo makutu athu Ali aimilira udikira kumva za report

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska 2 месяца назад

    Lero mmati kutuluka report

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 2 месяца назад

    Chikangwa kkkkkk

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 2 месяца назад

    Chakwela anapha chilima kuti akhalebe president 2025, lelo banja lina lapha mwana wawo kuti lilemele kunathenje, Kodi Achewa Zophanazi Bwanji Kodi pofuna maudindo??
    Report landege kuchita manyazi kutulutsa

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp 2 месяца назад

    Report

  • @DaudiLesta
    @DaudiLesta 2 месяца назад

    Umakwan

    • @PangoliniTV-z1t
      @PangoliniTV-z1t 2 месяца назад

      Mr kagaunde mumakwana inuo more 🔥🔥🔥

    • @KAFERANYASULU
      @KAFERANYASULU 2 месяца назад

      Kumangochi kulibe angoni ndi ayao